Тёмный

KOMATU BON KALINDO SAMAMVA NANGA ZOMWE WAYANKHULA LERO PA 14 AUGUST A BOMA AKAMVA ZITHA BWA? 

Makosana
Подписаться 113 тыс.
Просмотров 62 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

25 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 122   
@HAJIUBAYIDABLACK-x3x
@HAJIUBAYIDABLACK-x3x 2 месяца назад
Bon Kalindo yekhayo amene akuwonesa kuti ali seriously zoti Malawi wathu asinthe chifukwa alibe chikhumbokhumbo chokhala nduna ya boma kapena kukhala president Koma akufuna kuti dziko lathu lichite bwino Never give up Mr Bon Kalindo,God bless you alot
@allanjosamu
@allanjosamu 2 месяца назад
@@HAJIUBAYIDABLACK-x3x inu ndabodza simunamutsatile koyambilira anati bwanji sanamusakhe nao pa unduna
@ZexNkhoma-p8t
@ZexNkhoma-p8t 2 месяца назад
You are the best ever.. Bon kalindooooo the DC...! .
@OmexJimu
@OmexJimu 2 месяца назад
❤ big man mumakwana
@JamesAnusa-vd6hh
@JamesAnusa-vd6hh 2 месяца назад
❤❤❤❤❤❤❤❤L love it
@franciscochigadzo855
@franciscochigadzo855 2 месяца назад
More fire DC
@MoosaSame
@MoosaSame 2 месяца назад
More fire ❤❤ Booooon Kalindoooo more fire 🔥
@Shelifibraheem
@Shelifibraheem 2 месяца назад
You the man of standing, the DC of the nation
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 2 месяца назад
Bon kalindo wa show show kumuona wina obenela umakwana mr nyoooo osaonesa kutopa
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 месяца назад
Zoonadi misewuyi sichakwera ndi Peter osati Mr chikangawa ai , mr chikangawa koma kupha,kuba ndikuonong'a
@FabianMhango-zk6nv
@FabianMhango-zk6nv 2 месяца назад
On point DC
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 2 месяца назад
Ine ndinasiya kukhulupilila munthu padziko lapamsi, Ndinasankha kukhulupilila yesu yekha, Ndiomwewaso anatiuza kuti tivotele mcp Peter Achoke, Lelo akatimso peter ngwabwino, Mxm Kulibwino apitilize oipitsitsa emweyu basi,sindikuonaso wabwino
@usherjamson174
@usherjamson174 2 месяца назад
100 💯 true DC
@AishaMatola-e7c
@AishaMatola-e7c 2 месяца назад
Inu ndiine ling ndichala ❤❤ mandiyakhulila bwino kwabasi
@FosterChinzimuBanda
@FosterChinzimuBanda 2 месяца назад
The DC ng'alulasation time ❤
@GodisoneNoel
@GodisoneNoel 2 месяца назад
Sipasipot ndipepara zopusa zen zen
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 2 месяца назад
Mfundo zogwira mtima kwambiri ❤❤❤
@GraceMkandawire-t7m
@GraceMkandawire-t7m 2 месяца назад
Born kalindo ndi machine opangila machine anzake more fare mwana owopswa kwambiri inu inuyo ine ndiri kumbuyo kwako
@daviechannel8603
@daviechannel8603 2 месяца назад
Ndipo ndizoona chakwela mulungu atithandize abale koma chakwela ndikumachula anthu akumudzi ayi zikomo
@kanazidesigners7203
@kanazidesigners7203 2 месяца назад
Udaluza kwanu member of parliament adakuona kulephela kwako iwe
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 2 месяца назад
Welcome mr bon kalindo true man , man of just
@RichardMatumbo
@RichardMatumbo 2 месяца назад
True tilindili money made mudzikolatthuli😅 thanks Mr bon
@CatimboJosé
@CatimboJosé 2 месяца назад
The DC
@MosesSalle
@MosesSalle 2 месяца назад
Fire fire malume
@EmmanuelNkosi-ts8bn
@EmmanuelNkosi-ts8bn 2 месяца назад
Iwe why sukufuna kuyima ngati president kuti uzalongosole zinthu
@StevenFombe
@StevenFombe 2 месяца назад
Kalindo, jommo lesson to us ,
@joechitsulo2740
@joechitsulo2740 2 месяца назад
Nanu nde mumaikiranji sound ku background
@mbonilekisebe2286
@mbonilekisebe2286 2 месяца назад
Umakwana president wathu wa anthu osauka.... Mwana owoopsa kwambiri.... Hahahahaha much love the DC
@MenardoJunior
@MenardoJunior 2 месяца назад
The DC🔥🔥🔥
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 2 месяца назад
Aaah iwe Bakili muluzi waganiza bwanji, kdi amene uja moti nkumuika mu gulu la azisogoleri abwino? Kwa ine si zoona ai.
@JessieKholopa
@JessieKholopa 2 месяца назад
Mwana ooooopysa kwambiri 💪💪💪💪🔥🔥🔥🔥
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 2 месяца назад
Kkkk winiko angamuvotere ndi angati ndimaguru womapeza 21 votes Malawi yonse
@StalloneButao
@StalloneButao 2 месяца назад
Mr president of poor people l love you and understanding you very well. Palinso vuto la driver pamseu Maka nkhani ya ma categor, ku road traffic anasiya kupanga ma categor koma pamseu akutivuta daily tikudula GR. Kod tikaitenga category?
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 месяца назад
Techno brain ibwerere basi atony general ndiwa corruption, Koma Mcp nde ayinso tu manyaka eni eni eishh
@SimonMochede
@SimonMochede 2 месяца назад
Our real president ❤
@MussahDaud-w8o
@MussahDaud-w8o 2 месяца назад
Ampase donia Ina yasalayo nayenso timpange ngati zomwe anatipangila zachilima zija 🤣🤣🤣🤣
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 2 месяца назад
Ma passport kugonera konko ngati ku Admarc . Komanso mangochi immigration NDI mzuzu immigration mpaka pano kuli ziiiii . Koma boma ili
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 2 месяца назад
Kuyankhula chizingu Cha slang si nzeru Koma ndi umbuli ndaonela pa chakwera president opanda nzeru
@KondwaniJohn-mm3gk
@KondwaniJohn-mm3gk 2 месяца назад
Activist owapanga anthu direct kuti pitani ku DPP 😂😂😂😂
@maskinmsungeni8763
@maskinmsungeni8763 2 месяца назад
Kkkkkkkkk kung'alura zoona
@EVANCEKAGONEGONE
@EVANCEKAGONEGONE 2 месяца назад
Za passport zoti ndi a fegi nzoona ine umboni ndilinao
@AicyGlance
@AicyGlance 2 месяца назад
This is goodness of you our Malawian Activist😂😂😂😂 taying'alure mwina nafe tingaone kusintha
@ElizabethEmalason
@ElizabethEmalason 2 месяца назад
Mbambande mukanakhalap anthu ambili❤ bwez malawi mwan ukanasith rest in peace bingu wa munthalika ankalifunil zabwin malawi
@BesterChaima
@BesterChaima 2 месяца назад
More fire
@IzzyAsir
@IzzyAsir 2 месяца назад
my freedom fighter the D!!!!!C osaopa
@GeraldChikalema
@GeraldChikalema 2 месяца назад
Ife since January amwene til date
@fahadwalipeya8656
@fahadwalipeya8656 2 месяца назад
The DC....
@carlosZiyadi
@carlosZiyadi 2 месяца назад
Mpukunena zoonadi big apa tamumvetsetsani kalindo osamangothamangira kumumanga ayi achakwera mwatani kondi tamumvani munthuyo
@GidionMateche
@GidionMateche 2 месяца назад
Aaaah kumangovera km osazigwiritsila ntchito chifukwa Adah awawa zeru zawo zidathela kutsitsi
@jonaslabisonnthyola8036
@jonaslabisonnthyola8036 2 месяца назад
Aliyense akuti azawina never 2025 Apm boma
@jonaslabisonnthyola8036
@jonaslabisonnthyola8036 2 месяца назад
Chilima anaphedwa ndi Chakwera zochita kuoneka chifukwa ankafuna kuthetsa alliance Chilima akhale Moyo tivotera Chakwera apo bii tizavotanso
@johnandrew3111
@johnandrew3111 2 месяца назад
Ati ampatse ndege yatsalayo ikamutayilenso kuchikangawa
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 2 месяца назад
Walankhula bwino angolipangitsa pinyolo dzikoli ku Zambia,Tanzaia Mozambique agawanepo chabe apa
@BlessingsNkhata-q7h
@BlessingsNkhata-q7h 2 месяца назад
@Littlefair7
@Littlefair7 2 месяца назад
Koma a Joyce Banda musamawayike gulu la atsogoleri abwino, anayambitsa kuononga dziko, anagwetsa kwacha, cashgate, komanso anapita dziko lakutali kumakadyera kumeneko ndalama zomwe anapeza mdziko muno, kumapereka misonkho dziko la america mmalo motukula dziko lawo, APM nthawi imene ija amayenera kuwamanga mayi JB.
@scoltenroma6240
@scoltenroma6240 2 месяца назад
Mumakwana the DC🔥 inuyo mumatha
@SamNkhomo
@SamNkhomo 2 месяца назад
Inu mungo imila u president ukuku nkhalani
@StevenFombe
@StevenFombe 2 месяца назад
Atolankhani ena ndiocititsa manyazi ,khalani ngati brain Banda, Gregory lCj, et c
@michaelchimwala-x8t
@michaelchimwala-x8t 2 месяца назад
apapa nde mwayankhuladi kufotokoza ndpo ngat ena aboma akumangen ife tithananawo tatopano
@SteveniBanda
@SteveniBanda 2 месяца назад
Tiyenawo tiyenawo kkkkk asanze misokhoyathu amenewa
@FrankKaufa
@FrankKaufa 2 месяца назад
Kalindo, Bola musakhale ngati anamiwa. Chifukwatu paja anamiwa anagudwa. Pano Alizi!!!
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 2 месяца назад
Kodi chikangawa wabweladi kuzamulamulila ndan ameneyi
@SelbyMapogole
@SelbyMapogole 2 месяца назад
Uyuyuu adadza kudzatumikila a malawife
@allanjosamu
@allanjosamu 2 месяца назад
Ndie kusayamikako kumeneko
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 2 месяца назад
Winiko watha nzeru alibechonena ndi ichakwera
@JosephMwadzama-f4u
@JosephMwadzama-f4u 2 месяца назад
The DCCCCCCCCC🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@RobertNyaude
@RobertNyaude 2 месяца назад
Kalindo
@ELLENZAPS
@ELLENZAPS 2 месяца назад
Uyuyu or atakhara prezdent lelo osati agwape alipowa mbamva
@BwanaGD
@BwanaGD 2 месяца назад
Kkkk dziko loyendetsedwa ndi banja munthu ndi mkazake ndi ana ake malomoti dziko liyende ndidzikoso haa kulepheleratu
@ThomasBlack-hw3jr
@ThomasBlack-hw3jr 2 месяца назад
Ndakondwa Nao kwambili tiyeni alibweleke bas
@christophermukaka7403
@christophermukaka7403 2 месяца назад
Reality
@jacomw5797
@jacomw5797 2 месяца назад
Bon Kalindo The DC Mwanaaaa wowopsa kwambiri mMalawi 🇲🇼
@ImanRashidi-so4oo
@ImanRashidi-so4oo 2 месяца назад
✊✊✊✊🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@gersommalama
@gersommalama 2 месяца назад
Inu a Kalindo anthu osauka mmalawi muno ndiambiri zedi ndiye inu ayimileni pa chisakho 2025 kuti osauka mulowe m'boma. Tione ngati inu mulidi president wa osauka kapena ndinu otumidwa ndi andale chabe
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад
The DC munthu woopsa kwambili
@GodfreyKamphiripiri
@GodfreyKamphiripiri 2 месяца назад
Zoona zake zimenezo fireeeeeeeeee DC
@EmmyYafete
@EmmyYafete 2 месяца назад
Akwere Doniya basi kkkkkkk
@frankiechasokoneza5802
@frankiechasokoneza5802 2 месяца назад
Thabo chakaka nyirenda he is the who causes this problems that facing our country
@JervisDicksonMzinda-vu9vr
@JervisDicksonMzinda-vu9vr 2 месяца назад
IS HE THE ONE WHO CAUSED FERTILISER, FUEL, COOKING OIL , SOAP , PASSPORT, LICENSES , TO BE VERY EXPENSIVE? IS HE THE ONE WHO CAUSED MALAWI KWACHA TO ALL THE VALUE IN JUST 4 YEARS? DO YOU HATE THABO? WHO WOULD YOU LIKE TO BE ATTORNEY GENERAL? YOUR RELATIVE OR SOMEONE FROM YOUR TRIBE? THERE ARE SOME PEOPLE IN MALAWI WITH A Tendency TO Accuse SOMEONE MALICIOUSLY, JUST BECOME THAT SOMEONE DOESN'T COME FROM THEIR TRIBE. MORE PRONOUNCED IN MALAWI. WHAT TRIBE ARE YOU?
@frankiechasokoneza5802
@frankiechasokoneza5802 2 месяца назад
@@JervisDicksonMzinda-vu9vr yes boss he is the one who terminated the contract of technal brain with immigration He's the who collapses Salima illovo sugar just mention few boss
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 2 месяца назад
The DC...... Kuyankhula mopanda mantha
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 месяца назад
Mpatseni ina donia 😂😂😂😂
@KennethKamoto
@KennethKamoto 2 месяца назад
Muzilankhula zoterezi abwana
@JervisDicksonMzinda-vu9vr
@JervisDicksonMzinda-vu9vr 2 месяца назад
Ndiyesa a Kalindo munapangitsa meeting ndi MRA mumvekere "mademo kulibe tikambirana". Ndiye munkalengezeranji za mademo? Tingoyitana "Mtambo basi" Inu simungazithe. Mukunyozetsa NTCHITO ya eni.
@DamianoYohane
@DamianoYohane 2 месяца назад
Ma demo sanalepheleketu
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 месяца назад
Yowoyani walala
@michaelchimwala-x8t
@michaelchimwala-x8t 2 месяца назад
mcp most Go 2025
@DamsonSabitt
@DamsonSabitt 2 месяца назад
Paja unanenelatu kuti uBuDula m'memo chifukwa anakumana udindo pano ukumenyela ufulu Dpp nicholinga upezeko cholowa
@KondwaniMamveka
@KondwaniMamveka 2 месяца назад
Umakwan Dc kung'alura bc
@LeonardBanda-hg3sw
@LeonardBanda-hg3sw 2 месяца назад
Inuyo mmakwana mwangalura
@SteveniBanda
@SteveniBanda 2 месяца назад
Auze kkkkk osawopa 😂😂😂🫵
@MarryUnyolo
@MarryUnyolo 2 месяца назад
Uyu ndye munthu amene akufuna kuti dziko lathu lisinthe
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 2 месяца назад
Boma lolephela mistake ndi amalawi Bakili maluzi amatiwudza pafupi pafupi MCP chipani chikupha komatso chankhadza chongosiya ndale bakili anthu inu kalindo mai bandachihana mtambo ndi mabishopu ndi adzibutsa ndi anthu ena chifukwa munali ambili amabwalo milandu anali asilikali nkhondo a police netse NGATI MALAWI ALIPAMOTSO NDINU NGATI CHILIMA ANAPHEDWA NDINU NDI CHILIMA TSO ANADZIPHETSA YEKHA nde modzilimbika mtima titha kunena kuti bolani kalindo chihana anasiyana nawo mwatsanga komabe munali mutadzala mbewu YOYIPA YA MCP NOTSE MUDZIPEMPHA CHIFUNDO KWA MULUNGU PADZIMENE MUNATICHITILA AMALAWI TSOKALI ILO 2025 MCP IKABELA VOTE MAVUTOWA KUPITILA KUTI AMALAWI TIKHAWULE DZENI DZENI NSOKA SUMALITSAKA SAKA LELO IDZI DZITSOWA OLESERSA
@masianobrighton
@masianobrighton 2 месяца назад
Akundimvekera chifuwa uyu
@PatrickMalenga-h5m
@PatrickMalenga-h5m 2 месяца назад
Iwe unachokeranji mu utm boni zinakukanika ulibe zeru
@ChifundoJohn-w3t
@ChifundoJohn-w3t 2 месяца назад
Pa mtumbo pako wakutuma ndani kt uzimvela za kalindo chonsecho ukuti alibe mzelu
@PhilbertoChaimah
@PhilbertoChaimah 2 месяца назад
Achalume mumativesa kukoma
@boscochimdidi
@boscochimdidi 2 месяца назад
A kalindo tamayankhulani zonveka inu ngati mukunena zoona kuti ndinu president wa anthu osauka sibwezi mukumatilozera kuti tipitaso ku DPP ife musamatinamize apa inu mumapanga fight for your stomach mukudya bwino ndinu akukupatsani ndalama anthu otsutsa boma ife tikuvutika inu mukudya bwino nde muzinama kuti ndinu president wa anthu osauka mmmmm osamatipusitsa pano tinapenya amalawi,
@LikongweMecry
@LikongweMecry 2 месяца назад
Kkkkk
@SignUmar
@SignUmar 2 месяца назад
Zoona bon
@AthonyChibwe
@AthonyChibwe 2 месяца назад
Kalindo auze amenewa
@MphatsoKhwengweya
@MphatsoKhwengweya 2 месяца назад
Mbambande kalindo .kunyethima kunyethima kuswa kuswa , kung'alula kung'alula 😂😂😂
@CheloyaaChikwatuu-ob2mt
@CheloyaaChikwatuu-ob2mt 2 месяца назад
😂😂😂😂😂
@SteveniBanda
@SteveniBanda 2 месяца назад
Ndipo ndizowona kkkkk tiye nawo ndizowona awuze chibwana chachiluka kwambili kubomaku
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 2 месяца назад
❤Umakwana
@KennethKamoto
@KennethKamoto 2 месяца назад
Logic ilipo.ndithu
@ThomasMwandila-tn7cf
@ThomasMwandila-tn7cf 2 месяца назад
Iwendiye watikora ziko siungayendetse iweyo,ukufuna udindo 2025 takuziwapano choringa chako,
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 2 месяца назад
Akukambana zoona DC
Далее
Китайка и Пчелке Холодно😂😆
00:21
Jomo wamukana Bon Kalindo
4:20
Просмотров 71 тыс.