Тёмный

KU MALIRO A LUCIUS BANDA ZOMWE AYANKHULA PA 4 July 2024 KU BALAKA 

HOT 265
Подписаться 81 тыс.
Просмотров 13 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

2 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 17   
@ChimwemweSynoa
@ChimwemweSynoa 3 месяца назад
Sad news
@GiboSunset
@GiboSunset 3 месяца назад
Gulukunyinda the big nyau Chakwera alinso komweko,tamugendani galuyo.Mmutu mwake muli magawo 2.Gawo loyamba kuli zoipa zokhazokha gawo linalo kulibeko kanthu😢😢😢😢😢
@eliaskhofielias8152
@eliaskhofielias8152 3 месяца назад
KuMalawi kulibedi international legend ndaonela pa lucius banda.anali chabe legend wa malawi mokha basi.akanakhla wa international akanamuika ngakhale news zakinja achina BBC,even pa south africa pomwe atisiya iyepa akanamulengeza pa SABC News ngat anachitila Oliver ntukudzi. anafera kunja ku USA koma news break down news everywhere the whole world including SABC NEWS.mpaka kumpangila programme yake yomukumbukila pa morning live.koma banda not..
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 3 месяца назад
Ndalama dzaboma mukubadzo bwanji mukachepeseko mphono mukungokhala ngati nkhumba
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 3 месяца назад
Iweso billy usaname apa iwe ndi soja panalibe ubwezi soja anali mbava anadya ndalama dzose dza Paul chaphuka anadya ndiye akatibulana konko
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 месяца назад
😂😂 Chimwendo Banda mphuno Ngati nkhumba munthu akafa mbili siyimaipa ndinu a MCP mwamupha😢😢
@CharlesmakveliNyirenda
@CharlesmakveliNyirenda 3 месяца назад
Kkkk chimwendo ndi wa usilu 😂😂 chi mutu kukula ngati matako a Monica chakwela ku chepaso😊😂
@Magamax-qc4jg
@Magamax-qc4jg 3 месяца назад
Tizamusowa mr BANDA 😢
@MalekanoChikaonda
@MalekanoChikaonda 3 месяца назад
😢
@IqraKandulu
@IqraKandulu 3 месяца назад
Bily asaname amamunyoza
@MikeMerecah
@MikeMerecah 3 месяца назад
Ena kuchita kupha bora licias anavutika akapume ngati mkotheka,,,,,,,
@marthamusukwa7935
@marthamusukwa7935 3 месяца назад
Rest in peace Soja
@PreciousMkomo-yn6ge
@PreciousMkomo-yn6ge 3 месяца назад
Rest in peace Soja
@BENSONRANGWANI
@BENSONRANGWANI 3 месяца назад
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
@AlexSilence-p3l
@AlexSilence-p3l 3 месяца назад
Rest in peace soja
@CharityChirwa-t1e
@CharityChirwa-t1e 3 месяца назад
Tizakusowani Abanda zambili tilibe pachifukwa choti amalawi mukanyengo kochepa taluza athu ofunika kwambili zimuwanu uwuse ntendele osayiwala moni kwachilima moni kwa matafale moni kwakasambala moni kwa po champhuka wina kwa chibade wina kwa atoti manje wins kwa katelele wina kwa matse 💔💔😭😭😭😭
@VungaQueen
@VungaQueen 3 месяца назад
Amen Moni ukawafike ndinthu anthu awa muzimu yawo iziutsa mumutendere
Далее
Lucius Banda - Ndalira
7:29
Просмотров 180 тыс.
BRIAN BANDA NDI BON KALINDO_KWACHEMA🔥🤔
50:51
Просмотров 47 тыс.
Born Kalindo Wazuzula Boma Lero Pa 2 October 2024
16:11
Lucius Banda feat Patience Namadingo -Reggae Mash up
10:41
Mfumukazi - 4 July 2024
27:47
Просмотров 16 тыс.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Просмотров 119 тыс.