Vuto ku Malawi athu amene akuononga dziko ndi mitundu iwiri Malawi yonse pali (Achewa) (Ayao) mitundu imeneyi ndi imenenso ku school ndi (0-10) ndeno ndi mwambi uja amati ikaola imodzi mu bwato ndekuti zonse zaola,,ku Malawi ndi koola chifukwa cha mitundu iwiri,,tidzavutika mpaka kale or tidzagawana dzikolo.
Salankhula za mzeru awa ayi amafunika mbuli zimzawo aziwamvera mulibemo choonadi koma msanje ndi imene yakula mwa akuluwa ndi ena onse amene akuwawombera mmanja kuphatikizapo APM osewa ali ndi maloto a chumba sindingavoterenso APM 😅😅anthu anji asanje osayamikilako munthu akachita za bwino iwo zinawakanika pano aziti adzakomza iwo ndi Mulungu ayika ano ndimasiku otsiliza zambili simungakwanitse mpakana zittakwanilitsidwa andale ndi a bodza ndi ochepa amachita chilungamo koma enawo aaaaaa azipusitsa mbuli zimzawo aziwamvera amenewo ine ñdiye ayi 😅😅 bola kumavera yesu mboni yokhulupilika yopanda chinyengo nthawi zonse chilichonse, ndale basi kumangotsotsa chilichonse Ngati satana mudzakolola ndale zomwezo basi mpaka kumanda woooooo work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die 😢😢😢