Тёмный

KUCHIPANI CHA UTM CHADABWITSA ANTHU🤔🤔 

HOT 265
Подписаться 80 тыс.
Просмотров 91 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

28 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 169   
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 3 месяца назад
SKC was a general fitter analibe kuyankhula za munthu koma maso ake anali ku dziko la malawi kuti lizakhare pabwino, now Usi amayenera kuwafikira a U TM amnzake powawuza za kusankhidwa kwake
@leonardzchavula3139
@leonardzchavula3139 3 месяца назад
Its unfortunate that UTM has not shown any excitement on the appointment of Dr M B Usi,however constitutionally he was the appropriate choice.Had Chilima won the presidency in 2019 Usi was to be State Vice President. UTM has just to accept the situation.
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 3 месяца назад
I am on one of MCP whatsapp groups. I know that Usi is MCP. I am also an MCP member but I don't like Chakwera
@MirriamKambale
@MirriamKambale 3 месяца назад
He deserve deserve the appointment coz he was utm vp but it doesn't mean utm could have been overjoyed coz they're still in mourning time
@Betty-fe9ql
@Betty-fe9ql 3 месяца назад
His conduct from the 10th leaves a lot to be desired, your senior dies and you don't say a single word what's that
@chimwemwedulla6760
@chimwemwedulla6760 3 месяца назад
Inu zomwe usi anayalkhula komulunbiritsa kuja amaoneka ngati anali namalira amene uja?
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 3 месяца назад
Anamalira munali inuyo​@@chimwemwedulla6760
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb 3 месяца назад
Chitsiru manganya ndiwa MCp anampha chilima ameneyo anakambapo Chan Za lfa yachilima galu uyo ndi chakwera
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 3 месяца назад
Tikudabwa nawo anthu ena usiyu anaphanawo Chilima shame on him galu
@jelsonmlowoka8611
@jelsonmlowoka8611 3 месяца назад
Usova iwe ndiwe ndani kumuletsa usi kusakhala vp wa dziko, why did the utm owner appoint him as his runningmate at first, leaving you with no any position in the party?
@GibsonBanda-ey2gc
@GibsonBanda-ey2gc 3 месяца назад
umbuli
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 3 месяца назад
Nonse munakonza program iyi ndinu anthu opanda nzeru mukuonesakuti muli mbali ya mcp mumafuna kuti a utm akapeze ku parliament chosecho president wao wangoikidwa kumene m'manda, athaphedwa ndi mcp agalu kwabasi zikanakhala kuti zachitika mnyumba mwanu sibwezi mukukamba uchisiru mukukamba apau anthu opusa opanda chisoni
@BrightZionga
@BrightZionga 3 месяца назад
True bro
@rodgerskatengeza1903
@rodgerskatengeza1903 3 месяца назад
Constitution imapeleka masiku ochepa president or vice president akamwalira kuti asankhe wina
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 3 месяца назад
What is Dr. Usi bringing to the leadership of VP and UTM. will be the question.
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb 3 месяца назад
Inuso mphokoso kusowa zakamba position ndikuluza munthu malamuro ndichani zachamba et manganya amafuna Kare uvp Kare that way anamupereka chilima kwa mikangoyo mukusokosa kusowa zakamba
@JacobCimwinga
@JacobCimwinga 3 месяца назад
The truth is that SKC shoes are unfittable in all the alliance...and entire country leadership currently....but the country has to move forward.....ndale sizinthu zamuyaya ... it's about servanthood ... service to the people
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 3 месяца назад
Onse Ali apa ndi zitsilu , how Catherine be sitting and talking while the responders they say ,they are still mourning and it's true Malawian are mourning ndale zophana basi achewa opanda Pache inu
@lucksonnyirenda1168
@lucksonnyirenda1168 2 месяца назад
with UTM Dr Usi has failed as leader, he always sideline himself from his fellows, previously he dont associate with Utm members to please the president, even in this dark period he has failed to take a balance step by being to the part side & government side Usi has failed as a leader
@BrianAmos-s2k
@BrianAmos-s2k 3 месяца назад
Anthu amene aludandaula zanthawi sakudziwa zamalamulo amdziko
@IdrisYousuf
@IdrisYousuf 3 месяца назад
Àluthu aluamenewo aludandaulawo alukuti taludziwe😅😅😅😅😅😅
@chrispinechirwa2655
@chrispinechirwa2655 3 месяца назад
Choyamba tidziwe kuti mu zipanimu utsogoleri umasankhidwa through convention nde kusankhidwa kwa usi sikutanthauza kuti ndi mtsogoleri wa utm. By the way the government could write aletter to utm based on their agreement to prove that the alliance is still valid. Koma kungotenga munthu personally uuùuuu it's clear usi si wa utm
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 3 месяца назад
Ussi samapanga za UTM n the sad point ndizomwe timaziona munthawi yomwe anthu amapanga zamaliro a SKC ndi ena,iwo aja being munthu wamkulu wachipani pambuyo pakumwalira kwa achilima iwowo ndamene timayembekezera kuti ndiomwe azititonthoza ndikumatipatsa ma update amomwe tiyendere koma mmalo mwake anamusiira mzimai kumapanga zazimenezo n zinatengera kulimba mtima kwamai Kaliyati osatopa,osafooka kumatiyankhula amalawi nthawi ndinthawi,mukumbukirenso kuti ndi a Ussi omweo akuwafunsa zakuimila kwao kwaku Blantyre anakanitsitsa kutchula kuti akaimila chipani chanji yet munthuyo mukuti ndiwa UTM pamabvuta pati kunena zokuti akaimila UTM izo ndizachidziwikile kuti akulu amenewa UTM anaituluka kumangotsala kuti officially alengedze kuti atuluka
@AnnesBaulen
@AnnesBaulen 2 месяца назад
Zankutu,ngatiakutumani machende Anu ndi abwana Anu omweo kuphatikiza manganyayo
@Stewartchikoja
@Stewartchikoja 3 месяца назад
Kodi ngat wina adakhala Dzaka 4 osapenza mpumulo pa office yake how about 1 Yr chingasithe ndi chani ?
@AllaniWilesi
@AllaniWilesi 3 месяца назад
Ausi achita bwino inde koma asamanyengane nda azimayi ayeni pakuti Ali ndimbili yonyasa kwambili
@KennedyBaton
@KennedyBaton 3 месяца назад
I doubt of all this, am confused but what I know is that utm is not happy with that
@HellenKanyemba
@HellenKanyemba 3 месяца назад
Atolankhani thawing zina ndinu anthira kuwili achakwera sanamusankhe usi koma achilima ndio anasankha a usi koma achakwera angitsatira lamulo basi
@ChisomoPound
@ChisomoPound 3 месяца назад
Komaso kod tikumuyamikila chilimba kut anali Muthu wabwino ndipo oganiza boo funso langa Lili APA kod chilima anaona chani Kwa usi ?
@MikeKatola
@MikeKatola 3 месяца назад
Inenso sindikuona vuto bcz olo ufumu amalonga wina mfumu asanaike.so why utm akuonesa kukwiya.akukwiya ndi anthu oti sakuziwa kuti chilima ndi usi amagwirizana chani.
@Moffat-oi4yx
@Moffat-oi4yx 3 месяца назад
Akanganya inu mwalandila banzi chakwelayo akalemekeze malamulo osankha vp bwanji sanalemekeze malamulo Osaka ndegeija kumawalozela anthu kolakwika akudziwa chilungamo
@isaaczuze
@isaaczuze 2 месяца назад
Koma inu achakwera munalidi mmbusa kapena munali mmaluzi
@RonaldGama-gz9ug
@RonaldGama-gz9ug 3 месяца назад
Kodi a UTM wo mukuwafuna kuti atanipo Pa nkhaniyi coz they can't reserve the time anayankha zomwe iwo Ali ndiye chinanso ndi chani
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 3 месяца назад
Munena angati mutukwana angati anzathu patsogolo Ife basi zaziii nthawi ikupita tichedwa zinenani bola chakwera sadandaula anaona kale Kuti sanje zilipo kuteloku Wena mtima uwawa Kuti basi manganya wapita basi ayi zosiyilana mawa ndinu pepani mulungu akusungeni
@mzeewandembonyirongo2972
@mzeewandembonyirongo2972 3 месяца назад
Don't just say this...who do you think kuti akanamusakha? Mention her or him....
@RonaldGama-gz9ug
@RonaldGama-gz9ug 3 месяца назад
Eya akuyenera kutenga komweko ndi chifukwa chofuna kuwapusitsa
@ChisomoPound
@ChisomoPound 3 месяца назад
Khaniyi mutati muyione ndiyovutirapo vuto Lili APA anthu ambiri andale amafuna maudindo ngat awa ndiye pamakhala kuyang'anizana ndi diso lofila ngat iweyo sunasakhidwe,choti muziwe Pali zina zimachitika mwamalamulo tiyeni tibwelere mbuyo 2012 bingu wa muthalika atamwalira Ku dpp kunali ambiri amafuna udindo koma anayiwala kut Kuli lamulo lot ngat president watisiya vice ndi yemwe akuyenera kukhala mlowa mmalo ndiye izizi zomwe zikuchitikazi khani siyina ayi maudindo amenewa Kuli kapezedwe Ka ndalama mwaulesi
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 3 месяца назад
Inuyoso nanu aaàa manganyayu anapha nawo Chilima galu wamunthu uyu kakuwoneka mumask ka manganyaka kanachenjela udyo
@EstherAmadu-md3et
@EstherAmadu-md3et 3 месяца назад
Koma abale manganya angakhale wachiwiri wa ntsogoleri wa dziko mmmm dziko limafuna kutsogoleledwa ndi anthu a serious uyu anthu sangamunvele akapitilize ma drama
@marryphili5419
@marryphili5419 3 месяца назад
Ine Si wachipani Koma kunena zoona a usi akuziwapo chinachake pa imfa ya achilima chifukwa khope yake achilima atamwalira kumene iwo samawoneka wokhuzidwa ndi imfa imeneyi
@omarlux3434
@omarlux3434 3 месяца назад
Kod akanasakhivwa kaliyati mukanaso kut amaziwapo kathu mumafuna asakhe inu
@chikublea8982
@chikublea8982 3 месяца назад
Kodi nanga asakhe ndani
@AgnessKavalo
@AgnessKavalo 3 месяца назад
Anthu awa ndi asatanic
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 3 месяца назад
Manyanga mzimu wa Chilima ukukantha sua ufupika zeni zeni sunati Nyani
@yohaneben5452
@yohaneben5452 3 месяца назад
I think most of the people don't know more about usi,although he is vp of UTM but originally he is a member of MCP.
@felistassumani
@felistassumani 3 месяца назад
No need for imposing Usi on UTM. Usi has been so slippery in UTM. Let him go and we shall see if he is going to survive in MCP. UTM Executive may opt to accomodate him but as for ordinary members its a big NO! Why this time? Where was he all that time when our dear president was alive? Zachibwana a ayi. Usi safunika. Apite akachite zake aone ngati angadzatione.
@StewartMustafa
@StewartMustafa 3 месяца назад
Yes Usi can't survive in MCP if he doesn't know. But let's give him chance to proof him self whether he z an UTM member or not?
@AckimMhango-v1x
@AckimMhango-v1x 3 месяца назад
Vuto lalikulu ndi boma chifukwa linayamba kukhala ndi Usi before Chilima asanamwalile
@DysonKamama-yh7hq
@DysonKamama-yh7hq 3 месяца назад
Zitheka bwanji munthu anzako akulila koma osakakumana ndiakuchipani chanu before kulumbilisidwa, iye nkumakasangalala chilipo
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 3 месяца назад
My question exactly was he never suppose to ask his fellow utm members before making his mind???anywy zoona zidzaziwika mu nthawi yamulungu
@PociahMack
@PociahMack 3 месяца назад
​@@CharityChikomo-hl1gz zimene a mayakhula a UTM munthu amene anali ndi umunthu kunali kovuta kumakhala nawo, even akubanja paja anatulusa chikalata chowadzudzula.
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 3 месяца назад
Koma anthu Inu muli ndi nzeru?a utm apita bwanji kukaombela mmanja ali pa maliro?Kodi malamulo ake amtundu wanji week sinathe ena ayamba ukuvina kulumbilitsana a Malawi?which means it was planned this b4 imfa ya chilima khalani ndi nzimu waumunthu eeti
@HendrixBanda-l6d
@HendrixBanda-l6d 3 месяца назад
Cheap propaganda. UTM mukuganiza bwino kwabasi
@BrianAmos-s2k
@BrianAmos-s2k 3 месяца назад
Kusankhidwa kwa Michael usi wasatila ndondomeko yake chifukwa iye anali osatila wa the late SKC.komano tingodziwa kuti usi ali ku UTM kapena ali ku mcp?
@BrightZionga
@BrightZionga 3 месяца назад
Adalowa kalekle MCP
@BrianAmos-s2k
@BrianAmos-s2k 3 месяца назад
@@BrightZionga vuto ndilimenelo.Anayenela kukhalabe wa UTM kuti alemekeze ukuru former president of UTM
@MusaWilliam-t8n
@MusaWilliam-t8n 3 месяца назад
Chilungamo ndi amanganya anatengapo gawo lakuphedwa kwa saulosi chilima ndingakhale pakwanu pa inu mukuyakhula pali munthu amene anatenga nawo chigawo kuwapasa udindo iwowo kulibe kathu koma chilungamo anthu aku utm akudziwa kuti panali ngwilizano pakati pa manganya ndi chilima
@tamalangoma2765
@tamalangoma2765 3 месяца назад
May be you should blame late VP for choosing Usi ngati VP wake. Please stop making too much noise.
@chimwemwedulla6760
@chimwemwedulla6760 3 месяца назад
What noise achitsiru inu
@mathewssimbi3052
@mathewssimbi3052 3 месяца назад
Koma ngakhale palibe umboni okwanira mafedwe a chilima ndiwonkhumudwitsa kwambiri ndipo ndiwokayikitsa kotero mkovuta Kuti lero ndi lero akulu akulu a UTM adzikapezeka akuyimba nthungululu pamwambo wosankhidwa Kwa Ausi kotero kusapita kwao kumwamboku mkovetsetseka zongofunika tsopano kuwona kutsogolo
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 3 месяца назад
Nonse ndinu wanzeru zochepa mulankhuranu a UTM atiuzeso chani poyera zaku lephera kwao kosapezeka kolumbilitsa, pomwe anjawala adanena kale tikadalira nde mufuna atiuzeso chani za milandu basi
@RonicSouza-sk5ux
@RonicSouza-sk5ux 3 месяца назад
Usi didn't consult the party when he was told about the news of his presidency
@NefassiNefitarZaqueioZaqueio
@NefassiNefitarZaqueioZaqueio 3 месяца назад
Ngati palakwika kulumbilitsa a Usi nsanga ,tilolerane inuyo mukudzidzulanu sindinu angwiro muli ndi zofooka zanu choncho ngati late Chilima adasankha a Usi adaona kuthekera komwe kuli mmenemo. Kaya wina afune kaya asafune zili choncho basi olo mutukwana olo mutakhala chete ,zichitika zomwe mulungu wavomereza
@AlihIbrahim-w6n
@AlihIbrahim-w6n 3 месяца назад
Malamulo amanena kuti for 7days pasankhidwe munthu wina,,komaso sakanankhidwa wina koma Usi chifukwa anali vp wa chipani cha UTM,,so guys I don't know why we don't understand for this issues,,,we suppose to understanding because it's a rule,, it's not opinion for someone
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 3 месяца назад
Koma tu anthu mcp mukamapanga zithu mudziziwa kuti mawa ndi tsiku Lina
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 2 месяца назад
I cant believe malawi judges still wears whiteman hair.... "I once thought that educated pple are wiser"
@ChisomoPound
@ChisomoPound 3 месяца назад
Khaniyi mutati muyione ndiyovutirapo vuto Lili APA anthu ambiri andale amafuna maudindo ngat awa ndiye pamakhala kuyang'anizana ndi diso lofila ngat iweyo sunasakhidwe,choti muziwe Pali zina zimachitika mwamalamulo tiyeni tibwelere mbuyo 2012 bingu wa muthalika atamwalira Ku dpp kunali ambiri amafuna udindo koma anayiwala kut Kuli lamulo lot ngat president watisiya vice ndi yemwe akuyenera kukhala mlowa mmalo ndiye izizi zomwe zikuchitikazi khani siyina ayi maudindo amenewa Kuli kapezedwe Ka ndalama mwaulesi
@MerryWayson
@MerryWayson 2 месяца назад
Musakhale ndimafunso inu omwe mukuzitcha boma lachakwera cos mukufunsa mukuziwa kut Usi ndi chakwera ndiwomwe anapanga plan yopha chiluma anthu akupha inu. Mukuona ngat sitikuziwa kut Usi analu akulumikizana nseli ndi chakwera . Kut aphe chilima ndawi yomwevali moyo agalu
@hagayichiluwe
@hagayichiluwe 3 месяца назад
It's just reminding me that sanje kapena nkhwidzi exist
@CHIFUNDOCHINA-lp9lg
@CHIFUNDOCHINA-lp9lg 3 месяца назад
Vuto la USI anazionetsera KUTI Sali ku UTM,ATANGOMWALIRA CHILIMA,Nde chipani chisangalala bwanji
@Maliet-nh6kf
@Maliet-nh6kf 3 месяца назад
But why you killing others skc he made mcp to be on position later on decide 😈 chakwera pathako pako malo mobweza ulem ndikupha munthu😢😢😢
@isaaczuze
@isaaczuze 2 месяца назад
Anamupeleka saulosi chilima ndi Micheal usi ....manganya chisilu cha munthu.....manganya ku mcp wapitako yekha chisilu cha munthu
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 3 месяца назад
It not alaw, kut you must choose the vice president wachipani, that is a trap iwe manganya akupasa zingati why you didn't have time to settle and see it with your utm people
@isaaczuze
@isaaczuze 2 месяца назад
Nkhani iyi yakupha chilima sizatha mumtima mwathu .....mcp muziwe chilima apangisa kuti mcp ivutike osati masewela .....chipani chokupha ....amalawi sitizayiwala ayi
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona 3 месяца назад
Michael usi ndi wa MCP si wa UTM ayi anatuluka kale ndichifukwa anangoti bwela kuno sanafune ku pempha ku UTM chifukwa amadziwa kuti ndi wawo
@AminaPhiri-pp9tw
@AminaPhiri-pp9tw 2 месяца назад
Amalawi zinawamvesa chisoni kwambiri powona kuti ausi sanali busy ndi ifa yachilima ndipo analibeso chisoni chaifa imeneyi ndamene apeleka chilima ndipo nchochodi udasi
@RaphaelMaunde
@RaphaelMaunde 3 месяца назад
The appointment is right decisions but there is some issues between Dr Usi and UTM party Dr Usi was not royal to the party
@laurentbutao4084
@laurentbutao4084 3 месяца назад
Exactly
@RoseLameck-ub7sq
@RoseLameck-ub7sq 3 месяца назад
Ine dakalila malilo achilima singakambe kathu ndingodikila chaka chamawa ka vote bas chiweluzo nkaweluzila komweko ndichala changa😢
@KhonzoBlose-wq7zm
@KhonzoBlose-wq7zm 3 месяца назад
Manganya he is a snake ndiwa Mcp .every knows about that, chitsilu cha munthu
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona 2 месяца назад
Olakwa ndi usi chifukwa ngati achakwela anamufonela za nkhani iyeyo akanadziwitsa anthu achipani chake kuti zili motele titani amve maganizo awo
@isaaczuze
@isaaczuze 2 месяца назад
Anthu anakwiya chifukwa amene anapangisa kuti chilima aphedwe ndi micheal usi....manganya
@BRIGHTONALASON
@BRIGHTONALASON 3 месяца назад
Malamulo anthu salibwino komanso mmmmmm ena ifayi yawakomera nde chaona nzako chapita mawa towards you
@CarolineSelemani-p5p
@CarolineSelemani-p5p 3 месяца назад
Manganya ndi mcp,, if he was vice wa chilima, atamwalira dr chilima was just qite why
@BrightZionga
@BrightZionga 3 месяца назад
Aaaaa a nonsense chilima wakhala pamilandu those past 2years pa vp padali ndani you are talking bullshit
@KhonzoBlose-wq7zm
@KhonzoBlose-wq7zm 3 месяца назад
Move yonse yakuphedwa kwa Chilma amayiziwa asapuse fans.
@janemsiska3345
@janemsiska3345 3 месяца назад
Mukwonago video yatsiku amalengeza maliro manganese amasekelera
@TsholofeloTong
@TsholofeloTong 3 месяца назад
Usi please just go to your MCP because we already know that you're mcp member
@Maliet-nh6kf
@Maliet-nh6kf 3 месяца назад
Uyanya mcp kupha
@wellosmbewe6820
@wellosmbewe6820 3 месяца назад
Who is the president of UTM now and what is his speach
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 2 месяца назад
A Usi akafike,,amawaposa Mr Njawala zochita
@TaniaMphalumo
@TaniaMphalumo 3 месяца назад
Zauchisilu basi wasangalalanazo ndani utm muyisiye agaru inu
@StewartMustafa
@StewartMustafa 3 месяца назад
Gentlemen plzzz lets take this issue very seriously. Dr Usi z not wrong kulandila udindo kapena kuti VP. Ndizoona kuti Dr Usi anayamba kukhala ndi boma more especially president of the republic kalekale komano chomwe tingadziwe ndichakuti even The laye Dr Saulos Chilima adali pafupi ndi boma more especially to the President of the Republic. Now gents if u digest all of these it means these pple r wel organised coz they both take one step at a time. Now lets not talk a lot of things when its not time to do so. Time will tell whereby will will proof Dr Usi that is a member of MCP or He z still with us in Almighty UTM.
@williamsjonazie5764
@williamsjonazie5764 3 месяца назад
Choyamba tiwunikile Kaye kuti Kodi chakwera poziwa kuti usi ndi vice president wa UTM anawawuza za appointment ya usi? Ngati adatelo ndiye a UTM analakwisa kusapita koma ngati sadawauze za kusakhidwa Kwa usi adachita bwino kusapita chifukwa usi wangokhala vice president wa UTM koma ndi member wa UTM,executive ikanaziwisidwa mwa dongosolo and then invited kukalumbilitsa vice president. Nde anthu musamangofutsa mafutso mwina mufutse chakwera yo. Ndamene angalongosole momwe adayendesela ndondomeko yake.
@PreciousKARINGANIZA
@PreciousKARINGANIZA 3 месяца назад
Anampereka zake chifukwa chofuna mpando
@HypeGallery-ur9xd
@HypeGallery-ur9xd 2 месяца назад
Inuyo machende ano musawapinde athu mwadya inu😢
@masianobrighton
@masianobrighton 3 месяца назад
Amalawi let's move on zinazi tichedwa nazo mulungu salakwisa kodi amalawi mpaka liti tijusungabe mangawa look at APM for not accepting the fact someone is ruling now aaaa moti a UTM amafuna kufunsidwa maganizo pomwe thawi yochita appoint veep itakwana and azichedwa ndizosangala munthu mmmmmm. Malawi my country learn to accept God's plan
@isaaczuze
@isaaczuze 2 месяца назад
Kuteleko achakwera atafa lelo manganya akhala president.......nonononono... Manganya sakuyenela kukhala president ....munthu wamfupi ngati ameneyi ngakhale phazi lake ayi ndithu simunthu oti anthu onse aziyang,ana Iye
@MarkGonda-qr4vm
@MarkGonda-qr4vm 3 месяца назад
Koma ndiye azingopanga zamasewerotu amanganyawa
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 3 месяца назад
Manganya iwe ndiwe yudas chitsiru chachabechabe ndiwe unagulitsa chilima kamutu kako choka apa mzako wafera pomwepo basi iwe ukhalapo wapereka picture bwanji ku anzako a utm?u was vice to chilima who was killed by mcp tundalama tumene akupatsato tukutipitse mimba garu iwe no longer ku utm
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 3 месяца назад
Usi siwa utm ndiwa mcp uja musatinamizepo apa
@gwatandingo9502
@gwatandingo9502 3 месяца назад
Dziko La malawa amipingo ndamene anasokoneza ndi athila kuwili amasokoneza athu iwo ananena sakhani tsogoleri asakha akubweraso mwasakha thawi yolakwika kkkk koma guys mavuto Eni Eni and manganya anali wachiwili kwa wachiwili anayenera akhala iye kaya😢
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 3 месяца назад
A UTM ku sapita kolumbilitsa a Usi nkutheka sadalakwise mwina sadayitanidwe patha kukhara padalibe consultations,
@humphreysidie4747
@humphreysidie4747 3 месяца назад
Guys ineso ndufuna kumangidwa, this Usi guy knew everything, he sold Chilima
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 3 месяца назад
Awusi anarephera kutengapo gawo, kufa kwa skc relo palibe sngakondwe nazo asiyen azipanga zomwe amatha ndi kongweresi yakeyo
@CarolineSelemani-p5p
@CarolineSelemani-p5p 3 месяца назад
Total lay dpp sizikuwakhuza
@AmusedDimSum-hd5yp
@AmusedDimSum-hd5yp 3 месяца назад
how did you know that those who were not happy were utm members of the pary banzi mwadyayo musasokoneze zinthu
@FrancisStima-sc7zs
@FrancisStima-sc7zs 3 месяца назад
A UTM ananyanyaladi ndizona Koma anakakhala kt asakha aliyese akanavomelabe chifukwa andalewa amafuna ndalama osati kutisogolelai ndichifukwachake zipani zikungobadwabe aliyese akufuna kukhala pamwamba
@MCAnthonyNdau
@MCAnthonyNdau 3 месяца назад
Kodi akankhala kuti anali apulezident kuti ndiomwe atisiya Chilima automatically akanakhala pulezident Kodi kolumbilitsa sakanapita
@BrightZionga
@BrightZionga 3 месяца назад
A p k musati 100,% koz anthu sakuteloyi tikuti manganya adali mthila kuwiri
@StellaKaunda-v9y
@StellaKaunda-v9y 3 месяца назад
Vuto ndi MCP and usiyo iyaa
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 3 месяца назад
UTM this is your good time and best Future be united guys chipani chizalowa muboma pachokha don't expect kuzalamulira Malawi
@SuzgoMunthali
@SuzgoMunthali 2 месяца назад
Awa so akukamba no nonse
@InnocentMlowoka-ew4lo
@InnocentMlowoka-ew4lo 3 месяца назад
Atigwila ufiti pano.
@MCAnthonyNdau
@MCAnthonyNdau 3 месяца назад
Ndichimodzi modzi bingu atamwalila sitinakhale ndi pulezident wanyowani
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 3 месяца назад
Manganya sanali wa UTM analowa MCP kale kale mosadziwa anthu mumtima mwake anali wa MCP
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 3 месяца назад
Malamulo are there but we pick and choose what to enforce in Malawi" s constitution.
@HolyNickMbewe
@HolyNickMbewe 3 месяца назад
Mamembala a UTM akuziwa kuti Razalo wasankha nkhwali kuti ikhale pampando wa vp
@peterkinsLekera
@peterkinsLekera 3 месяца назад
Malamulowo anaphwanya kake akadangopitiriza panafutsa kale masiku 10 asadasakhe
@saidimwanyali8969
@saidimwanyali8969 3 месяца назад
Kodi pofuna kusanga ausi achakwera adayitana ausi oka kapena adayitana chipani chonse ndikumasanga kapena anawasanga kuseri
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 3 месяца назад
It can stay kufika pa 2 July ndipo panakhala popanda vice Kwa chaka bwa a Chilima atamangidwa
@OmexPoisonkaombe-cf7bz
@OmexPoisonkaombe-cf7bz 3 месяца назад
Kusapanda nseru anapha bwanji vice president wathu ameneyo bas
Далее
ZODABWITSA ZOMWE ZAONEKA KU UTM ZIKUTHANDAUZANJI?
29:49
Новый вид животных Supertype
00:59
Просмотров 193 тыс.
ADALOWA UTM ISADAYAMBE_22 September 2024
45:08
Просмотров 1,8 тыс.
US-Tanzania Tech Challenge
2:29:27
Просмотров 1,5 тыс.
Новый вид животных Supertype
00:59
Просмотров 193 тыс.