Тёмный

Kupha Chilima Apanga Zopusa | Khad Wapitiliza Ku ng'alura 

Mukuziwa?
Подписаться 19 тыс.
Просмотров 96 тыс.
50% 1

#chilima #skc #utm #mcp #malawi #trending #news #viral

Опубликовано:

 

26 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 258   
@AlickMDayi
@AlickMDayi 3 месяца назад
I think Chakwera he must resign guys because he lie to us us a Nation He give us a long information about the death of Chilima He didn't speak the truth on the whole sanga that been happening
@clesheinvestments
@clesheinvestments 3 месяца назад
Nanunso chotsani Ndale za Udani,be more civilized. Chakwera has nothing to do pa Ngozi ya Ndege yomwe yachitika ku Malawi. Remember at first zimamveka kuti Chakwera force Chilima kuti apite ku Maliro ku Mzuzu kenako MDF ndikudzalongosola zonse momwe zinakhalira nthawi yomweyo Adani a Chilungamo ndikudzasintha Tone. Tiyeni tiike kuopa Mulungu pa TSOGOLO.Tsikulina we will be answerable pa zomwe tikulankhula ndikuchita pa Dziko pano. Mulungu akuona
@rabeccamataka8655
@rabeccamataka8655 3 месяца назад
Iiih abale
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 3 месяца назад
Chotsani ndale zomangoda anthu with no any valid reason. Chotsani ndani za tribalism
@FredrickSalamu
@FredrickSalamu 3 месяца назад
I agree with you on the fact that we don't analyze and digest what people tell us. lt looks like when it comes to political sense we sleep
@DivineMercy-df2pu
@DivineMercy-df2pu 3 месяца назад
Jane Assah ananena kuti a MCP anapita kunyumba kwake kukamuophyeza kut akapanda kuwina pa yenda mwazi.People never believed her but today see what they havee done to our Chilima
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад
❤❤ we need people like this man God bless you sir 🙏
@esaugabriel8852
@esaugabriel8852 3 месяца назад
Osamawatenga a Malawi ngati opusa. Bwera uzapange mademo akowo ma propaganda omwe mukubweletsawa aphetsa anthu ku ntcheu. Ndeno inuyo musamangolubwa kumeneko
@DaudeLiojo
@DaudeLiojo 21 день назад
Iweyo athu ake akutcheu amene ukawaphewo ndi ati chirugamo chiwoneka mudapha athu osarakwa kuwasiyitsa ana anawa akurira mizimu yaathu 9 iri padziko pano kuwurura chirichose
@FortuneTemuwa-gm3sv
@FortuneTemuwa-gm3sv 3 месяца назад
Lestening and following up from zombaa
@AnthonyPhiri-bm4vs
@AnthonyPhiri-bm4vs 3 месяца назад
Mulungu akupase zelu zambiri broh ❤❤
@SamsonSamson-gh6gs
@SamsonSamson-gh6gs 3 месяца назад
Ndipo zoona
@futurekanjanga1290
@futurekanjanga1290 3 месяца назад
Keep doing ur best.....we rally behind u
@givenchobe1977
@givenchobe1977 3 месяца назад
Chilima is at peace! Heaven has welcome son of Malawi, he fought a good fight he has finished the race, RIP.
@flourencejamu6455
@flourencejamu6455 3 месяца назад
Amen
@GghtKatungahbandah
@GghtKatungahbandah 3 месяца назад
Listening from bembeke dedza surely this is un understable
@AlgentChilanga
@AlgentChilanga 3 месяца назад
We are waiting for you big boss
@BlessingsMadaSiment
@BlessingsMadaSiment 3 месяца назад
Please we are all waiting on 🫂
@ZioneMkangadzula
@ZioneMkangadzula 3 месяца назад
Enamu mungopanga support koma mulikunja bwerani
@GenialaChalera
@GenialaChalera 3 месяца назад
Iwe chitsiru ngati ufuna kupanga ndalama chifukwa choti utamike ndiwe galu
@SpaPierre
@SpaPierre 3 месяца назад
Koma ine ndikuona ngati Kell Kay ndi Janta asazachezenso. Chifukwa Tay Grin kukwatira kudzamuvuta chibwerereni coronavirus disease uja sakuonekanso
@theodoralimeza5945
@theodoralimeza5945 3 месяца назад
😂😂😂😂😂😂😂
@SpaPierre
@SpaPierre 3 месяца назад
@@theodoralimeza5945 eti amwene 😂😂😂
@ChikondiBanda-ce8tk
@ChikondiBanda-ce8tk 3 месяца назад
They're now in panic mood. They underestimated Malawians on their plans because of greed and stupidity.
@EliMakwinja-jo6ok
@EliMakwinja-jo6ok 3 месяца назад
It’s too late now they underestimated
@DinganiKhumalo-zq1rd
@DinganiKhumalo-zq1rd 3 месяца назад
I am surprised Malawi as small in size as it is can it take more than 24 hours without tracing the plane??? Watching from here in Bulawayo
@bobykhan3583
@bobykhan3583 3 месяца назад
i love the way you are putting your words bro ❤❤Big 👆
@PhillspicJere
@PhillspicJere 3 месяца назад
Munthu wanzeru zake akamvere iwe munthu wakuti sulikuno, umbuli uwu, black box imatengedwa ndi eni omwe anapanga ndege, nobody else muziwanamiza ma cadet anzanuwo achisiru inu
@manfredzalirabetha2440
@manfredzalirabetha2440 2 месяца назад
Zoona bro amasule awa aanthu oipa mpakana kupha muthu owaika pa mpando??
@LastenWesele-wq8jh
@LastenWesele-wq8jh 3 месяца назад
Koma inuyo muli ku joni ndiyeno mukutiwuza kuti tipite ku mademo mmmm iwe awuze abale ako ayambise mademo popeza ntchuma amadya ndi anthu andale ife tifele zayeni
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 3 месяца назад
That's true bwana auze mudzi wa kwao upite ku ku mademo ife asatiputse ayi
@Saintly060
@Saintly060 3 месяца назад
Exactly
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt 3 месяца назад
Live from Mozambique. Keep it up.!
@eunicesaiti
@eunicesaiti 3 месяца назад
Following from England 😢😢😢 , Our Vice president SKC Rest in Peace 😢😢😢😢
@AngolanChinga
@AngolanChinga 3 месяца назад
We support you big boss mulungu akhale nanu
@samdiverson9733
@samdiverson9733 3 месяца назад
Big up to you brother let's change our nation
@chancylodzani638
@chancylodzani638 3 месяца назад
Even he must resign i suport u
@HusseinAdamLidezo
@HusseinAdamLidezo 3 месяца назад
Continue working 💪 hard 💪 🙌 🙏
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 3 месяца назад
We are proud of your intellectual capacity Biggy. We're waiting to hear from you.
@JeremiahNgwira
@JeremiahNgwira 3 месяца назад
He is trying to use you and you are supporting him?
@ShelingtonMtemula
@ShelingtonMtemula 3 месяца назад
We are support you following from canada
@chrisboyce2
@chrisboyce2 3 месяца назад
We are support you following from Ntcheu Central BAWI near Nsipe
@OmanOman-t6o
@OmanOman-t6o 3 месяца назад
More fire from Dubai
@lewischakhwantha3907
@lewischakhwantha3907 3 месяца назад
Time. Everything has the right time. Speak truth, and if you can defend it, stand ready to defend it with evidence. These videos will surely speak in your defence if at all they contain truth.
@jamesmulangalimatemba5351
@jamesmulangalimatemba5351 3 месяца назад
Watching from pietermaritzburg south Africa
@AngolanChinga
@AngolanChinga 3 месяца назад
Big boss you have freedom to tell as what you know osabisa pano wina aliyense chakwela sakukondwela naye chakwela is fack man munthu oipa kwambili ndiponso mulungu amulange kapolo ameneyo wapha chilima noh kubisa pano we will fight with him kut tikhale ndi freedom yabwino atill end of life
@NumbDee
@NumbDee 3 месяца назад
True malawians are bitter
@EgamaPhiri-fg3yi
@EgamaPhiri-fg3yi 3 месяца назад
I only voted in 1994 but am coming back to vote again to push out MCP.
@OFG-th3st
@OFG-th3st 3 месяца назад
Let's go 🔥😁
@stainbanda2424
@stainbanda2424 3 месяца назад
Tsono iweyo uzatsogolere mademowo osati kumangokamba uli kwamereca pamene anthu kuno akuphewa.
@ellahmwams831
@ellahmwams831 3 месяца назад
Tili mbuyo mwanu bwanji 💪💪
@Lizzie-h1k
@Lizzie-h1k 3 месяца назад
Salute ..salute😂😂😂😂😂...kalata ya ku Donier ndaikonda 😂😂😂😂😂
@juliusnjerengo2610
@juliusnjerengo2610 3 месяца назад
Company ya Donier inatsekedwa kale coz sinkapanga ma profit, it was Germany company.
@JamesMwangolera
@JamesMwangolera 3 месяца назад
Wow we are waiting
@NeversonThefuture
@NeversonThefuture 3 месяца назад
We r behind u bro, keep it up bro
@Leo-fj6gz
@Leo-fj6gz 3 месяца назад
Uyuyu wandikwana…. Ma speech ake oyambisa nkhondo basi 😢
@preciouskadembo1932
@preciouskadembo1932 3 месяца назад
Waiting patiently
@shadreckmaloya-rw2cd
@shadreckmaloya-rw2cd 3 месяца назад
Yes we need people like you to change Malawi
@MadalitsoSabe-nb1qc
@MadalitsoSabe-nb1qc 3 месяца назад
Most of the enemies you have today are people you once helped in life.
@BlessingsSilanga
@BlessingsSilanga 3 месяца назад
Keep it up my gee 💪
@MosesChiponda
@MosesChiponda 3 месяца назад
Umakwanitsa Khad
@AubreyMulupiwa
@AubreyMulupiwa 3 месяца назад
Malawi wachema uyu
@ElonBlack1999
@ElonBlack1999 3 месяца назад
Thank you for supporting the truth.
@PatrickMwamwanyeta
@PatrickMwamwanyeta 3 месяца назад
Ipase 🔥🔥🔥🔥🔥
@clesheinvestments
@clesheinvestments 3 месяца назад
Kusankha kukhulupilira zonama kusiya Dala Chilungamo. Wake up MALAWI tisamapusitsike ndi phokoso akuchita Anthu ngati awawa ndi ZOPANDA nzeru izi. Winnie Nyondo anatulutsa Uthenga omwe Chisomo Chimaneni anamutumizira pa nthawi ya 10 : 10 AM kulongosola za Nyengo yoipa inaliko tsiku limene lija. Ine ndi wa UTM koma za uchitsilu zomwe CHITSILU ichi chikulankhula mmmmmmmmmmm I can't and I will never buy.
@esaugabriel8852
@esaugabriel8852 3 месяца назад
Bweran my Malawi osamangolubwa uko inu
@henrykaunda5141
@henrykaunda5141 3 месяца назад
Mvuto inuyo mlikunja nde ma demo tipanga bwanji? Penapak naniso m'matipusitsa
@faiditv5535
@faiditv5535 3 месяца назад
That good New s
@VictorSiwale-d1h
@VictorSiwale-d1h 3 месяца назад
Chilima has become another God in Malawi and Malawians can not manage him, nkhani ya chilima azangoipondeleza ndikuwapatsa chi banzi alipansogolowo😢😢😢😢
@timothymhone2340
@timothymhone2340 3 месяца назад
Unathawa Bungu ku malawi usatipusise apa
@SolomonShaibuh
@SolomonShaibuh 3 месяца назад
Live from Gaza
@sylvesteralfred8355
@sylvesteralfred8355 3 месяца назад
I support that idea of going to dornier company to ask information I think going to help, don't stop bro ulemu wanu
@miraclendonani2996
@miraclendonani2996 3 месяца назад
The company was closed down in 2002
@RaymondKaumba
@RaymondKaumba 3 месяца назад
Wasuta maso kufiira ngati fisi
@vytwistthelion98
@vytwistthelion98 3 месяца назад
Okupha inu muyaluka
@RaymondKaumba
@RaymondKaumba 3 месяца назад
@@vytwistthelion98 katuleni umboni baba osafa ndi mtima
@SymonPaul-s8h
@SymonPaul-s8h 3 месяца назад
Izo nde mzeru big boss
@JoshMkandawire
@JoshMkandawire 3 месяца назад
Following closely until full information is shared & our action as malawians is required. Black box tiyiwone and hopefully, the data shouldn't have been tampered with by then .... Mawa following live kunonso
@PhillspicJere
@PhillspicJere 3 месяца назад
Zikuonesa kuti a DPP mukuziwapo kanthu zaimfa ya SKC chifukwa ma propaganda Anu awonjeza agalu inu mutu ndi mphuno zonyasazo agalu inu, Chakwera amumenyera nkhondo ndi Yehova, mukuopa kukamuchosa pa vote mwayamba kukamba zopusa
@MussaJohn-gt8ep
@MussaJohn-gt8ep 3 месяца назад
may Allah reward you big
@fatimamalinda6038
@fatimamalinda6038 3 месяца назад
Ma demo achan mmalo mopanga zthu mwa Bata Tiyen tisiye mzimu wa skc uziuztsa mu mtendere Osat uonelele zipolowe
@theawakening265
@theawakening265 3 месяца назад
I have questions 1) is this guy here in Malawi? 2) you say remove chakwera ,what is the alternative for chakwera?
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 3 месяца назад
We are following you always brother come on.
@gophiri1674
@gophiri1674 3 месяца назад
Anthu ofunila dziko la Malawi zoipa nde anthu ake inuyo. Mukadadikila report ituluke. Malawi 🇲🇼 wake si walelo simungatinamize or kutipusitsa.
@YoungMwacho
@YoungMwacho 3 месяца назад
Where is Timothy Mtambo? Amene anathandizira Chakwela kukhala president, come and speak you devil 👿. Munthu oyipa mtima unaphesa anthu ndi kuwonga katundu wa anthu chifukwa chofuna kuikapo pa upresident Chakwela. Panopa aMalawi azindikila kuti Peter anali gentleman komaso akadali gentleman. Safuna ziwawa.
@TAONGAKAYANGE
@TAONGAKAYANGE 3 месяца назад
Big up bro🎉
@ThokoMsonkho-hy4uc
@ThokoMsonkho-hy4uc 3 месяца назад
ACHAKWERA palibe chomwe akupanga dziko muno. Pa imfa ya Chilima waonetsa umbuli ndi uchidebe wawo. Amamuwopa kuti awalanda upulezidenti pogwiritsa ntchito zomwe adasainilana pa gwirizano. Shame on Chakwera
@ajudyaustine984
@ajudyaustine984 3 месяца назад
Keep the fire burning big Malawi needs people Like you to be developed no fear and never give up
@jumawasi9038
@jumawasi9038 3 месяца назад
Live from Moldova 🇲🇩
@robertkalima874
@robertkalima874 3 месяца назад
Iwe Mcp ndiboma singatekeseke ndi iwe. Peza zina zochita. Opusa ndiwe. Mbuzi
@raytavares2256
@raytavares2256 3 месяца назад
A murderer being a minister of a house of Parliament?
@ronaldchilinda2855
@ronaldchilinda2855 3 месяца назад
Chepetsani mkwiyo...A Malawi musavele za awa iwowa akudya bwino kunja cholinga ife tiphane tokha tokha. Anthu osakonda dziko lawo awa.
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 3 месяца назад
We're waiting brother
@StephenMchawi
@StephenMchawi 3 месяца назад
I agree with
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 3 месяца назад
Nkaka, kudzimva kwabasi, dziko mpaka kulitenga kukhala mmanja mwawo, mpakana kuyamba kuwopsyeza ngati nthawi ya kamuzu chimenecho chilungamo. Koma awona polekela. Ngati Zakanika asayambe kupha anthu Andale ndi atolankhani mwatiwonjeza a MCP.
@bluewaverecords9192
@bluewaverecords9192 3 месяца назад
Amene mumaimba come record your songs at my music studio in Lilongwe...
@SuleimanRabsonMkhunga
@SuleimanRabsonMkhunga 3 месяца назад
Your respect broo
@MeltonMumba-rn9mf
@MeltonMumba-rn9mf 3 месяца назад
Truth on the ground big
@adamtlalane
@adamtlalane 3 месяца назад
Kofunika kuyima ndikulimba mtima ngati afika popha vice president what about u and i
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 3 месяца назад
Omenyera ufulu nonse gwirani ntchito yanu mosamala chifukwa a gulukunyinda amenewa ziwembu sanathane nazo
@josephmwale6844
@josephmwale6844 3 месяца назад
Nice work
@Lizzie-h1k
@Lizzie-h1k 3 месяца назад
Zikhale akapitilize kugulitsa kaunjika...kunkuyu akapitilize zake za ulonda....Chimwendo akapitilize ulimi w fodya...enawo akudziwa komwe anachokera!....
@AngolanChinga
@AngolanChinga 3 месяца назад
👍
@uladikenneth1762
@uladikenneth1762 3 месяца назад
Thank you brother
@MarriumMubarak-r4n
@MarriumMubarak-r4n 3 месяца назад
Achimwene munthu samadzinenera yekha room yomwe mwalowayo ndi yodziwika a military akupezani.
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 месяца назад
Good Messnge my brother Chakwela you mast go
@JustinGosten
@JustinGosten 3 месяца назад
Ndikuyakhukana ndi Putin apapa zokhuza zida zankhondo don't worry atioanga supply
@BlessingsNjanji-dj7oq
@BlessingsNjanji-dj7oq 3 месяца назад
Go deeper aseh,tilipambuyo pako
@ChifundoNinje
@ChifundoNinje 3 месяца назад
We love you brother don't worry
@stevenchirwa5028
@stevenchirwa5028 3 месяца назад
Khondo yiyambe agalu awa akuwononga ziko lanthu 😊
@rasheedbwana5900
@rasheedbwana5900 3 месяца назад
We're loosing you soon bro😢...so painful am feeling pain for you my brother
@MalumboJerr
@MalumboJerr 3 месяца назад
😂😂😂😂
@GiftChalunda-ss9qu
@GiftChalunda-ss9qu 3 месяца назад
Ndiyambitsa Boko halamu ya Ku Malawi apapa ndaona kut Malawi mfuti munasephana nayo ndinali Ku Afghanistan kophunzila sniper since 2002 ndaphumzila zambili zimene olo n'silikali wakumalawi sakuziziwa ndiphulisa mutu wa chakwela any time a Malawi osadandaula Umu ndi Mene wayakhulila nsogoleli wa gulu la Boko halamu wa kuno kumalawi
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 3 месяца назад
Khad,, ndugwirizana nawe kwanthunthu, ndi utsilu kwabasi kulamulidwa ndi mbuli, Ng'oma, kunkuyu, chimwendo banda Okula mitima okhaokha
@shariftayali3660
@shariftayali3660 3 месяца назад
Pamtumbo iwe ukufuna uphetse anyamata Mwana Wa njoka pita
@titusbusybrainsukali3860
@titusbusybrainsukali3860 3 месяца назад
Zoona zake!!!
@paulmalimwe9754
@paulmalimwe9754 3 месяца назад
Will you be there kuzionetseroko kapena mufuna kutiphesa tili kumalawife chabe?
@robertkalima874
@robertkalima874 3 месяца назад
Bwerani man tidzapange mademo. Unavota kodi iwe wosochera
@EdwardMwale-p2j
@EdwardMwale-p2j 3 месяца назад
Kumademo tipita tifuna kucotsa pamupando agalu amenewa ifeyo makomanda zatinyasa zimene wapanga chakwela
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 3 месяца назад
chilima wafa imfa ya ngozi osati zomwe mkunenazi ayi mgati mli ndi umboni go to court . ndinu anthu omwe mkusokoneza anthu kuti aziyamba zipolowe nkhondo siyabwino tu😊
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 3 месяца назад
Tipita kumeneko ndipo sitikuopa
@AngolanChinga
@AngolanChinga 3 месяца назад
Iwe mapwaka ako zot chakwela ndiwakupha sukuziwa awawa ndi amene akunena chilungamo end every one he knows kut chakwela wapha chilima we knows
@jogechawa6192
@jogechawa6192 3 месяца назад
Faki yu mako ndi bambo ako afe
@AngolanChinga
@AngolanChinga 3 месяца назад
End i don't scared you you are doom madah fack
@ShazieWaya
@ShazieWaya 3 месяца назад
​@@AngolanChingaUmboni mwautenga kt?
@owenmanda1741
@owenmanda1741 3 месяца назад
Friends turned nemesis
@sue12344
@sue12344 3 месяца назад
Hey Donier company does not exist anymore. Stop telling people lies
@JeremiahNgwira
@JeremiahNgwira 3 месяца назад
Chilima musiye apume mumutendele. Inuyo ngati mujambula tumizani zinthuzi tiziwone zomwe amachotsa blackbox. Ndiponso ukunama donier kampany inatha coz was declared bankrupt. So to which Donier company did you write the later to? Some of us are well informed Sir, unlike a malawi enawa omwe amakhulupilara bodza.
Далее
Beatrise (пародия) Stromae - Alors on danse
00:44
KUNG'ALULA MOSAONA NKHOPE_BON KALINDO
16:59
Просмотров 30 тыс.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Просмотров 265 тыс.
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Просмотров 118 тыс.
Bambo agwira akazi Awo pachigololo
16:28
Просмотров 4,1 тыс.