Тёмный

KUTAMBASULA ZOMWE ZACHITIKA M'MALAWI MUNO 

HOT 265
Подписаться 80 тыс.
Просмотров 22 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

28 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 26   
@RhoxinahMalamba
@RhoxinahMalamba 3 месяца назад
SKC my vote 2025
@spargomw
@spargomw 3 месяца назад
Chakwera amatitenga a Malawi ngat zitsiru zake, ndi zija adatenga ndalama kukagula Fertilizer ku Butchery. Lero akutenga anthu okoza misewu a maiko ena mkumati azichita kafukufuku wa Ndege? Mukuchita zonsez chifukwa chot wakufa salankhula? Mizimu ya a Chilima nd azizawo aja siidafe ayi. Mukakumana nayo patsiku la chiweluzo
@SildaKatundu
@SildaKatundu 3 месяца назад
Enquerry ya bodza ,sitiimva a Malawi
@Jasonnyatwa
@Jasonnyatwa 3 месяца назад
aMalawi kuputsa mukakhulupilila anthu atatu abwelawo palibe akuzenipo zooza , pokhapokha a UTM akhalepo komaso zapani zina, km so ndondomeko zisatidwe 1x1 tisazave kuti Black Box sinapange record lina lililose,
@MartinKapanga
@MartinKapanga 3 месяца назад
chakwela akuyamikila chilima chifukwa anamwalila chakwela chakwela ulape mokwanila iwe Busa iwe kaya
@DumisaniMhango-e4i
@DumisaniMhango-e4i 3 месяца назад
Malema anthu ambili akugulaso ku south
@KenDuweh
@KenDuweh 3 месяца назад
Anthu afika ku Germany 🇩🇪 woo awawudza kale zozanena after akamalidza kufufudza fact ndiyoti ngt anachotsa black books nde kut panali plan yochotsa moyo wa wina wake
@TanaqWorldwide
@TanaqWorldwide 3 месяца назад
Zichitike zmenezo
@MarggieBhulla
@MarggieBhulla 3 месяца назад
I will vote for Chilima though he is no more.
@BeartriceMwale
@BeartriceMwale 3 месяца назад
Behind you aise...... Tipanga zimenezi
@SildaKatundu
@SildaKatundu 3 месяца назад
Akatswiriwa akumana ndi aboma okha okha omwe ndi odya ma banzi kale
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l 3 месяца назад
Kod mmesa kufufuza kumayamba ndi ntembo kuti anafa ndi chani kueza matupi awo then ndikumafufu za ndegezo kuti izigwa chifukwa chani
@LukaAfromad
@LukaAfromad 3 месяца назад
Imfa ya chilima idakhudza kwambili osat masewera
@GiftJustinNjazi
@GiftJustinNjazi 3 месяца назад
AMalawi ndife opusa chilungamo sichingapezeke chakwwla achoke basi sitikufuna boma lopha anthu ife anthu akulila maliro iye akugwetsa kwacha nde mungamati maliro amalira nawo ameneyo?
@JaffaliShaibu
@JaffaliShaibu 3 месяца назад
President wa chipani amasankha ndi anthu mchipanimo koma vice president wa chipaniaasankha ndi president wa chipanicho. Tiyeni tichenjere ndi kusankha mwanzeru anzanga a UTM. Ulendowu ngwautali uwu......
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 3 месяца назад
Agawan muon chifukwa yemwe amasung chikwam wapit nacho
@EdwardMukholi
@EdwardMukholi 3 месяца назад
Bwinotu akumangani chifukwa chakwela ndi munthu woipa
@mayambalajames5542
@mayambalajames5542 3 месяца назад
Tabadyan ndalama zachakwelazo panyelo Panu Panu agalu
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 3 месяца назад
Bola asakhale kuti akawatenga ku butchery kapena ku pharmacy
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 3 месяца назад
😂😂😂😂😂
@godfreyalberto7425
@godfreyalberto7425 3 месяца назад
Commission of inquires ndiyosathandiza Ku Malawi
@CourageSydney
@CourageSydney 3 месяца назад
Anthu onse Atha chifuwa lion chakwera
@TanaqWorldwide
@TanaqWorldwide 3 месяца назад
Timva zinthu guys
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 месяца назад
Chakwela you mast go watikwana,
@flytonenkunika-pi9dn
@flytonenkunika-pi9dn 3 месяца назад
Good ideas please ife zamabodza ayi
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 3 месяца назад
chakwera ndi amene anapanga chiwembu chimenechija palibe chimene angafufuze amenewo chakwera wabisa zonse chakwera ndi chigawenga
Далее
MBC TV 16 March 2024
28:59
Просмотров 7 тыс.
JUDICIARY OPEN DAY 2024 LIVE CHE MANDOTA PERFORMANCE
14:19
BON KALINDO LERO KUTOKOTA
16:05
Просмотров 12 тыс.
SADTU holds 10th National Congress
2:13:10
Просмотров 9 тыс.