Тёмный

KUYANKHULA KWA DR MICHAEL USI KU THYOLO MU CHURCH CHA SEVENTH DAY 

HOT 265
Подписаться 81 тыс.
Просмотров 5 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

17 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 27   
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 2 месяца назад
Paja amalawi chabwino ndi choyipa, choyipa ndiye chabwino, Kodi VP alakwisa pati atakhala albinos killer peter muthalika mtati zili bwino. Thank you so much VP I love you so much USI ngati momwe nditakonfela chilima you two people God bless you. My chilima rest in peace ❤❤❤
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr 2 месяца назад
Koma ndalama inaphadi ambuye Yesu, manganya kumakamba zomuyamika Chakwera momwe 4 yearsyi wayiyendetsera zoona. Mmalo mumakamba zodzudzula bomali,, Chilima RIP ndipo sindimvetsatu kuti munapita bwana mmmmmh ambuye munalolenji 😢 Mary Chilima our mother and aunt God be with and your family. Adzayankha mulungu, Usi ukuyamba kubowano ndikukuturuka
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 2 месяца назад
You can not corrupt God
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 2 месяца назад
Ndi mulungu yemwe ziphuphu, ndani sakuziwa kuti Chikangawa Party yakugula kuti uwapusitse anthu ndi campaign.
@tingamasi106
@tingamasi106 2 месяца назад
Mukusewera ndi mulungu mpaka kumufanizira ndi chikangawa? Akukanthani yehova wamakamu
@ClydeNyasulu-tk6fj
@ClydeNyasulu-tk6fj 2 месяца назад
Ndikochenjera mopusa aka shupit
@tingamasi106
@tingamasi106 2 месяца назад
Chikangawa akaimilire mulungu? Agalu okupha inu
@felixjoseph8161
@felixjoseph8161 2 месяца назад
Amanganya musafanizire mulungu ndi mbava chakwera
@tingamasi106
@tingamasi106 2 месяца назад
Tsikulina uzatsamidwe ndi malovu ako omwe ndipo kufa kuzakhala komweko mbuzi
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 месяца назад
Usi ukuonjeza kwambiri, mpaka church? Kodi Boma lanji longokhalira kugawa ndalama?
@MadalitsoChisale-j2o
@MadalitsoChisale-j2o 2 месяца назад
Zokundimvekera mwandalendale eeee
@stevovosalimu5443
@stevovosalimu5443 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂ndipo osakayikaso zikupita komweko ndinthu
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 2 месяца назад
​@@stevovosalimu5443osati kupita komweko ay koma ndizomwezo ndithu.
@Rose-wu5ef
@Rose-wu5ef 2 месяца назад
Iwenso ndi fiti kwambili
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 месяца назад
Koma iweyo akuzimitsa dikila sikiziwa chikangawa party
@Gmtmphats124gy
@Gmtmphats124gy 2 месяца назад
Kodi adale inu mwayamba kumayenda macherch pano dzaka 4 sosez simayendela macherch Kodi mwaona kuti thawi yatha ndye mwayamba kuyendela mpingo oky takuonan
@Rose-wu5ef
@Rose-wu5ef 2 месяца назад
Iwe uposa kwambili
@WisdomBlack-uu7zt
@WisdomBlack-uu7zt 2 месяца назад
Hmm mm only God knows
@Rose-wu5ef
@Rose-wu5ef 2 месяца назад
Chakwela okupha chilima bwanji ukunana iwe shoti
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 месяца назад
Kodi ulaliki mungopatsa anthu ndimaonekedwe athupi Bwanji? Zilekeretu chipani chalitchi zithe
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 2 месяца назад
Amen mpingo
@HappyMwale-qy6up
@HappyMwale-qy6up 2 месяца назад
Mupenga mpaka man fsto mu chch
@TestReznov
@TestReznov 2 месяца назад
Mpando wa president si mpando wa mulungu. Ndi wa satana.
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 2 месяца назад
Kampeni mpaka church kodi inuyo manganya
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 месяца назад
Mpando wa chikangawa chakwera ndwakuti galuwe
Далее
ANA A KUMPANDA - Pastor Frackson Kuyama
26:40
Просмотров 11 тыс.
moto tag - AirTag для Android
00:47
Просмотров 597 тыс.
💅
00:24
Просмотров 108 тыс.
ZOMWE ALANKHULA A DR JOYCE BANDA KU CHIKWEWO, MACHINGA
30:53
Rev Alexander Kambiri SIDE A  YA MWAMBO WA MALILO
23:05
acts of prophet miracle paul
17:23
Просмотров 20 тыс.
A DAVID MBEWE KU BLANTYRE __12 October 2024
24:40
Просмотров 15 тыс.
Rev Alexander Kambiri Mzuzu C.C.A.P
52:44
Просмотров 15 тыс.
Rev Alexander Kambiri SIDE  B   YA MWAMBO WA MALILO
24:51
KWACHEMA KWAMBIRI LERO__16 October 2024
21:29
Просмотров 13 тыс.