Chawezi u can't be a leader ndipo ndikunenetsa the guy in the middle he is slow take things easy but what is saying make sense chawezi ur using book a that's not wisdom mibawa make middle guy to be the general manager ur company will grow
Pazomwe Chawezi akunena zoti kulilanda boma ndalama,akuzifunsa kuti kuyambira pomwe a Malawi akhala akulipatsa boma ndalama mdziko muno chikusintha ndi chiani choposa kugwetsa Kwacha. Chawezi amatokota ngati wa nzeru koma ndithu akudya za MCP. A Malawi sanavotere Tonse. Tonse inayambika after kuvota kuvota ndipo manifest ambiri anachokera ku UTM yomwe mtsogoleri wake waikidwa mphati kamba kupanga enforce transformation. Dziko lonse lapansi dziko lililonse limakhara ndi source of income a Chawezi unganene kuti Malawi source of income yake ndi chiani? Ndalama yomwe imatoleredwa mdziko ndiyochuluka kwambiri ndipo itha kutukura dziko lino popanda kudalira kupempha olo titati aliyense azipeleka K 100 pa tsiku. Chawezi ungandiuzeko kuti Malawi amadalira chiani pofuna kudyetsa dziko lake ndipo ndi minda iti ya boma imabweretsa zokolora nkhokwe za Malawi. Boma ndi minda iti limalima fodya to boost foreign currency without depending on local famers? Admarc,ndikutiko kuli mbeu zomwe zingathandizire kudyetsa nzika? Eskom ndi Waterboard ma services awo ndi olipilitsa bwanji amakanika kupititsa business yao kwa anthu with a fair price komanso kukanika kupanga attend customer akapezeka ndi vuto. Why ma cities athu mulibe ma traffic lights yet anthu akudula matikiti daily akalowa ntauni. 1 million ikuvuta pati kumachita kuti miseu yonse yakale ndiyokumbika yet achinyamata akuthawira ku Joni. Ma department onse ndatchulawa amazipangira ndalama okha koma sangalembe anthu ntchito mkumati 1 million job ndizovuta. Ku Eskom kuti alembe anthu ochuluka potengela ndi demand ofuna magetsi,ku Waterboard the same,ku city council,ku National roads authority,ku Admarc mukundiuza kuti 1 million job siingapezeke in months. Kulavwaza misonkho ya a Malawi mkomwe Kwa chukula. MALAWI ndi dziko laling'ono ndipo we are not in a position of importing Chilichonse sizoona. Kupita ku tchito kukasolora basi osati kukapanga ziganizo zotukula dziko mumati zoyenda bwanji?