Тёмный

KWAVUTA PA HOT CURRENT YA LERO 22 ~ ANG'ALULA ZA CHIPANI CHA MCP NDI DPP KOMANSO BUNGWE LA MEC 

BS Malawi
Подписаться 120 тыс.
Просмотров 9 тыс.
50% 1

KWAVUTA PA HOT CURRENT YA LERO 22 ~ ANG'ALULA ZA CHIPANI CHA MCP NDI DPP KOMANSO BUNGWE LA MEC
Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
#MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

Опубликовано:

 

21 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 67   
@Richieman-90
@Richieman-90 Час назад
DPP my vote ✅
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx Час назад
Northern region are very civilized people
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe Час назад
my vote MCP ❤ 🙏 🗳
@KelvinKapalamula
@KelvinKapalamula 13 минут назад
True definition of democracy❤
@Yusto-g
@Yusto-g 47 минут назад
Dpp my vote ❤❤
@GrandChima
@GrandChima 2 часа назад
This is very democratic ❤❤❤❤❤
@miltonkanyamula9486
@miltonkanyamula9486 Час назад
Musangodzudzula a mcp,ndi dpp..utm during a candle memorial ceremony,analankhula kuti kuno ku ntcheu mcp isadzapagitseko msokhano. Even councilor kapena mp asadzayelekeze kuyimila ku ntchewu...nanga imeneyo ndi democrancy..yet nobody condemned it....
@geofreydzinyemba6107
@geofreydzinyemba6107 18 минут назад
Well done guys mumalankhula chilungamo keep it up please
@EnerstManess
@EnerstManess 2 часа назад
I think atumbuka amasunga zikhalidwe kwambili
@EsetaGerate
@EsetaGerate Час назад
Nzuzu ndiyomwe yatero kwinako chimwendo Banda amapanga zamanyi
@Pumla-y1m
@Pumla-y1m 2 часа назад
Kuphalombe achakwera apitakhangati osaonakakathu
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 2 часа назад
Well done guys
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n Час назад
Dpp woyee
@ZaithwaMatchado
@ZaithwaMatchado Час назад
Athu Aku mupoto NDI ophunzira komanso mafumu awo alibe dyera
@hassanmpate7538
@hassanmpate7538 Час назад
Koma zonse mumayankhula zija dzikoli likubwelera mbuyo kapena likupita ku tsogolo? Vuto ndiloti mumanamizila ngat simumatenga mbali chonsecho muli ndi mbali
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 8 минут назад
Amwene dzikoli a MCP anadzala maziko atangolowa m'boma Kuti Ngati mkotheka tibwerereso mu 1 party system mchifukwa chake amasuka mkumapanga zomwe akufuna mosaopa komaso mopanda manyazi,tatiyeni muone zomwe ndikutanthauza 1 Speaker wanyumba ya malamulo ndi wa MCP 2 Mkulu wa MEC ndi wa MCP 3 Mkulu wa MDF ndi wa MCP 4 Mkulu wa a police ndi wa MCP ndekuli ma position Ena akuluakulu omwe muli a MCP okhaokha ndicholinga choti akwanitse Ku panga capture tonse m'dziko muno,Pano alimkati kugula andale komaso oimba Kuti pasapezeke owatsutsa.
@zondanitzulumusicfly.5202
@zondanitzulumusicfly.5202 Час назад
Well done guys, no codderlism
@BonfaceGumeni
@BonfaceGumeni Час назад
.zx
@Andersonenerst
@Andersonenerst 2 часа назад
Ine dzina langa ndine viliginia kalivale ndipo ndidzavotera chakwera ❤‍🔥❤‍🔥❤‍🔥
@IssahBannet
@IssahBannet 2 часа назад
Machende akowanva
@KaleyaMatola
@KaleyaMatola 14 минут назад
Dpp my vote
@miltonkanyamula9486
@miltonkanyamula9486 Час назад
Nkhani ya ku NRB ikubvuta chifukwa kumeneko ndi komwe a dpp akakhala akugwiritsa ntchito pobela zisankho..so this is why akusowa nazo mtendere..mbava ikabeledwa imamva kuwawa kwambiri.. ndiye ndizimenezi
@daviskamonde4882
@daviskamonde4882 Час назад
Wonder msiska is pro MCP!!
@MalizeniOliviaBridan
@MalizeniOliviaBridan Час назад
Mtalimaja akhala bwanji pachilungamo mpamene alindimba iyeo ndiwa MCP anganve zonena zaosutsa
@GoefreyBanda
@GoefreyBanda Час назад
Uku ndiye kuyakhula mwachindunji mumakwanila osaima pachipani km kung'alula zipani zatse
@upilenamangale
@upilenamangale 28 минут назад
Yogulitsa likoma tinayezeka paja last week.... ibwera liti...
@moffatsoko8547
@moffatsoko8547 Час назад
Kuno kumpoto si dana tose ndife atumbuka muthu mozi
@Greatness664
@Greatness664 Час назад
Stupidity. Why should MCP hold a rally close to the DPP rally? W
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 30 минут назад
M'dziko muno anthu tikuonereredwa kwambiri, sizoona MCP Kuti ikapangeso rally patsiku lofanana komaso moyandikana. Khalidwe limeneli limayeneka kudzudzulidwa.
@SJBWAKHULUMA
@SJBWAKHULUMA Час назад
Kumupoto kuno nkhondo ina chitika kale ndi (asamunda) si tifunatso nkhondo kuno nkhondo si Imanga mudzi
@HastingsBanda-m3z
@HastingsBanda-m3z 45 минут назад
Zikanakhala kuti amayenda pansiwo anali a DPP mukananva ndipo inuyo mukudziwa pamenepo
@owenkacheya
@owenkacheya 56 минут назад
Pankhani ya sapato za a policezo ndye pamenepo kuwani ndithu ambiri amachita kumanyengerera kwa ma gaurd a gaurdaworld
@edicalmdala1802
@edicalmdala1802 2 часа назад
Awawa ndi ma big guys
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga Час назад
kodi chisakhochi anthu ake asakha anthu adela lose lamalawi
@Kennedy-s5k
@Kennedy-s5k 2 часа назад
Kamwalile we want to chat
@MalizeniOliviaBridan
@MalizeniOliviaBridan Час назад
Awandara pondikumpoto akhala kunaliku lilongwe sizikanathabwino
@RaffickAllie
@RaffickAllie Час назад
Inu Tundu wa Achewa angapange choncho.. ku Mzuzu konko idzi
@Yona-w1y
@Yona-w1y Час назад
Anyamatainu amasuleni
@SandraChibaka
@SandraChibaka 2 часа назад
Inuyo ndima Dolo guyz
@GeoffreyEllias-m9l
@GeoffreyEllias-m9l 2 часа назад
Inu ndimakape ndani amene anakhapidwa kuphalombe?
@Pumla-y1m
@Pumla-y1m 2 часа назад
Ayo ajona pakukutu mumazipakatu zitosinokha
@KaleyaMatola
@KaleyaMatola 14 минут назад
Dpp
@EVanceBonganiBanda
@EVanceBonganiBanda Час назад
Nkhani Madera ena umbuli udachuluka
@PhillipAcquaron
@PhillipAcquaron Час назад
Atumbuka nd anthu ozindikira kwambiri
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 часа назад
Kumpoto tili ndizelu kuposa achewa achewa alibe zelu nyau too much
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di Час назад
Azibambo Inu ndi amabodza ndani akhapidwa ku m"mwela?
@PatrickGulani
@PatrickGulani 51 минуту назад
dpp boma
@Pumla-y1m
@Pumla-y1m 2 часа назад
Ayiatolakhani chonde pokhoza zithu musalowese zibwana mukumbusa bwanjizakale tikhozezichonde mukatimukufuna kumbusakuso yezakuti sitingakhonzezithu ayisicho akuluakuluchonde
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 Час назад
Panthaw ya dpp chilim adamenyedw kummwer
@ChifundoJohn-w3t
@ChifundoJohn-w3t Час назад
Mtumbuka ndi munthu ozindikila 😅😅😅😅😅😅sali ngati mchewa wazikwanje ndi nyawu
@ntombiunice8637
@ntombiunice8637 Час назад
Chifukwa ndi ku North
@christopherchikankhen
@christopherchikankhen Час назад
Anthu ambiri ku mpoto ndi asukulu
@ChisomoKaliwo-f7x
@ChisomoKaliwo-f7x 2 часа назад
Mumakwana mithutha yathu
@ChrissyBhima
@ChrissyBhima 21 минуту назад
Andevu zamwayi tazinenani chilungamo,a m c p kumwerq sakupangako misonkhano?adpp anapita Ku Lilongwe sanakhapidweko?nanga adpp anakhapa ndani wa m c p?chilungamotu chikukuvutani,tazitambasulani zinthu,musamakondere,m c p ikuchita zinthu zoipa zambiri koma inu palibe chomwe mumayankhula , DPP ndichipani chantendere koma inu mumachida pachifukwa zanu plz chepesani zomwe mukumayankhula
@CarynSasamala-g5o
@CarynSasamala-g5o 22 минуты назад
😂😂😂guys anthu osewo ndi a dpp muziwe chimenecho sangamenyane akuziwana ka
@FillimonHarrisonNgozo
@FillimonHarrisonNgozo Час назад
Yimeneyo Ndiye MCP. Siyaphokoso Ayi, koma yena Aja Azikwanje Aja eeee
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 40 минут назад
Tsono MCP imakhapa anthu pa mbowe paja ndi iti?
@McphersonMsulira-zx2lj
@McphersonMsulira-zx2lj 35 минут назад
Anundwe sanalimbe mtima koma anali mbali ya McP coz anudwe omwewo sanapange zomwe anapanga nthawi ya dpp muthawi ya Mcp
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 3 минуты назад
Eya panopa MDF anaigwira chifukwa mkulu wake ndi wa MCP
@aubreymathinga9049
@aubreymathinga9049 Час назад
Big Bullets ndi Mighty Mukuru wandrers amatengana kuno nkukamenya mpila kulilongwe wina nkuluza! Koma nkutenganaso kuzafika kuno ku Blanyre popanda kumenyana. Andale taphunzilaniso kulolena ngati ife ampila
@Jacksonmuhackeya
@Jacksonmuhackeya 2 часа назад
Zikuchita kuonekelatu ngati wapita ku unga kukadya nao misonkho ya a Malawi mbali yache yaziwika Rifa sapita ku cump kwa timu akudikila kusewela
@Kennedy-s5k
@Kennedy-s5k Час назад
Ndilibwino know kuguenee
@AdamMntonintshi
@AdamMntonintshi 27 минут назад
Dpp my vote 🗳 ❤️
@michaelchimwala-x8t
@michaelchimwala-x8t Час назад
Dpp my vote
@ChisomoKaliwo-f7x
@ChisomoKaliwo-f7x 2 часа назад
Mumakwana mithutha yathu
@TisopeMkozo
@TisopeMkozo 46 минут назад
Dpp my vote
Далее
Election rejection: fears of a contested result
48:47
Просмотров 4,2 тыс.