Тёмный

LIMPOPO FM 13 JUNE 2024 ..COMRADE NTANYIWA ..MCP ILI PA MEETING KULIMBILANA U VICE PRESIDENT 

Club Junta
Подписаться 41 тыс.
Просмотров 70 тыс.
50% 1

Развлечения

Опубликовано:

 

26 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 338   
@JosephMaulidi-m9s
@JosephMaulidi-m9s 3 месяца назад
I salute Limpopo f m with comrad Ntanyiwa
@BilalAliyah-k1f
@BilalAliyah-k1f 3 месяца назад
My best channel ever Limpopo
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana 3 месяца назад
Chilima wandililitsa 3 days osagona mmmmmm imfa yowawa kwambiri 😢😢😢
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 3 месяца назад
If what is being said on Limpopo FM is true,then Chakwera has no right to continue running the affairs of Malawi. By now ,he was supposed to be out of state house.Malawi get united and replace Chakwera with someone who is ready to lead Malawi with passion. The kind of politics is exposing are of olden days. People must not wait for 2025 to vote out mcp just deregister this political party if what is reported on this platform is true.(My Opinion)
@gladyschisomo4324
@gladyschisomo4324 3 месяца назад
Owapanga replace ndi uyo amuchotsayo ka ndinkona amudula moyo kuti a president who akhalepobe chilima was the next president
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 3 месяца назад
Du u think is this is true bro? If it is true, how came this people are says this to day cos chilima has died while all this days amamunena chilima-yo? Don't trust this bro......
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 месяца назад
Good Messnge my brother Zoona Chakwela you mast go
@patrickndojime1632
@patrickndojime1632 3 месяца назад
Ulemu wanu big brother kumeneko ku Limpopo FM radio 📻 station
@PeterMillimbo
@PeterMillimbo 3 месяца назад
A President opuma a Dr Muluzi ananena mobwerezabwereza kuti osazavotera chipani Cha MCP koma dziko mmmmmm kugontha
@BakaliPhili-es3xj
@BakaliPhili-es3xj 3 месяца назад
A tikufuna kuwona Zina 😭😭😭
@IdressaMussa
@IdressaMussa 3 месяца назад
Chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti chakwera mfiti 😊
@ChifundoNinje
@ChifundoNinje 3 месяца назад
We love Limpopo fm
@alicembetewa5151
@alicembetewa5151 3 месяца назад
kaliyat nde wanena anthu asasiye kutumiza mapic pa social media chilungamo chichitike true,tisamaide pena social media
@HopeZemban
@HopeZemban 3 месяца назад
THAT is my point that I have surgest postmodem it need to happen with immediately effects 💔💔💔💔💔😭😭
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 3 месяца назад
We need true story that's or brother nothing is or RIP CHILIMA 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🫵🫵🫵🫵🫵🫵
@sedicmuzammil8530
@sedicmuzammil8530 3 месяца назад
Guys izizi ndi zowona munthu wamkulu ngati ameneyu malilo angoyika popanda postmortem ayiiiiii sizowona
@MamuMagombo
@MamuMagombo 3 месяца назад
Welcome limpopo fm 100%
@sylvesteralfred8355
@sylvesteralfred8355 3 месяца назад
Ineyo ndikanakondano a Malawi tikanasiya kumangodandaula koma osapangapo ma actions izi ndizomwe amationelera nazo Action is what supposed to be taken than kumangodandaula pamene maumboni okwanira Malawians please lets woke up and take ma actions Please!
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 3 месяца назад
Limpopo fm ndi khan zina eeesh muli ukadaulo ofufuza or a tnm and airtel akudabwanso ulemu wanu big boss timvera kwainu
@esaumhone9056
@esaumhone9056 3 месяца назад
😂😂😂
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 3 месяца назад
Owooooo bushiru akhale vice president basi tatha ife koditu iyeyo bushiru yo watengamo magazi ake
@RowlaBanda-dv1qk
@RowlaBanda-dv1qk 3 месяца назад
Ndipo nde tathadi
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 3 месяца назад
The best Radio station in central Africa...God bless you all the time.
@IigIgf
@IigIgf 3 месяца назад
There's no peace for the wicked God will judge them all rest in peace mr chilima
@Joy-wr8nx
@Joy-wr8nx 3 месяца назад
Takomzeka we need Justice for our chilima
@BensonChilundu
@BensonChilundu 3 месяца назад
Mkulu wanga pitiliza kuvumbulutsa china chilichonse.Vuto maboma omwe tisankha masiku ano amatitenga ngati zitsiru zawo koma tsopano adziwe kuti tinasukusula kumaso ndipo china chilichonse chikhale pa mbalambanda.Mr Comrade,ndakuvulilani chipewa ndipo pitilizani kuphulisa mabombawa.Ndafunanso kukulimbikitsani kuti menyani nkhondo kufera abale anu kuno kumudzi omwe akuvutika ndi chipani cha congress chomwe mtsogoleri wake ndi Chakwera
@SymonNamalomba-sh3fu
@SymonNamalomba-sh3fu 3 месяца назад
Manganya uja amadziwa sindikukaika ndinthu
@marthansaliwa7732
@marthansaliwa7732 3 месяца назад
Kusewera ndi mizimu. Iwakhaulitsa aona. Sanatitu
@shawn2765
@shawn2765 3 месяца назад
Kodi radio station imeneyi ndingaipeze bwanji
@paundfeston
@paundfeston 3 месяца назад
NTANYIWA AISE NDIWE KATUNDU UMUTHAWISA WANKULU AMENE
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 3 месяца назад
True story this is mcp we need true story that's or this is home land 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🫵🫵🫵🫵🫵🫵
@QueenVunga-fb9sj
@QueenVunga-fb9sj 3 месяца назад
Zobitsika za Yamba kuululika mulungu mutimenyele nkhondo iyi patokha sitintha 😭😭 Rest in peace vc wanthu😭😭😭
@gladyschisomo4324
@gladyschisomo4324 3 месяца назад
Bushiri???? Amayoooooooo dziko lija lapita basi mwana wamunthu watsala pang'ono kubwela
@patricksamson4852
@patricksamson4852 3 месяца назад
Grace chinga mawu ako anthu awakumbukira chipani cha mwazi
@MorrisMapiri
@MorrisMapiri 3 месяца назад
See gone are days when Malawi was blind. Gvt must know that today they kill one but tomorrow ten will rise against you and you kill ten tomorrow the next will come hundred unti everyone become your enemies.
@amoschataika7440
@amoschataika7440 3 месяца назад
Ntanyiwa you are number one
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c 3 месяца назад
Palibenso akutitsegula mmaso
@AndyBandasindire
@AndyBandasindire 3 месяца назад
Kadziko kochepa kma kuchitika zoopsa kwambili
@MussaAli-jw5pq
@MussaAli-jw5pq 3 месяца назад
Timakunyadirani all the way from Eastern Cape Port Elizabeth SOUTH AFRICA
@EagerChicken-qj6xu
@EagerChicken-qj6xu 3 месяца назад
Akayezedwe kuti mtundu wa a malawi udziwe chomwe chamupha pulezident warhu.
@nyanguoipa6996
@nyanguoipa6996 3 месяца назад
Akuluakulu tigwilane manja posawona mipingo kapena zipani . Timenye nkhongo imeneyi chifukwa ana athu ndiomwe azaone mavuto msogolo muno.
@IbrahimLibwalo-kz1ip
@IbrahimLibwalo-kz1ip 3 месяца назад
Big up bro
@sthoramexjrsa902
@sthoramexjrsa902 3 месяца назад
Limpopo ndiyomwe itiuze zezene always with you
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 месяца назад
Chakwera uli ndimwai poti ndine osauka koma kumaliro uku ndi kapanga history munthu amene ndi kufuna ndi chakwera umusata chilima😢😢😢😢
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 3 месяца назад
The people surrounding the president didn't advise him correctly because of their selfishness!. They shouldn't have advised him to stand for the second term after signing an agreement. They would have changed the constitution to suit the agreement.
@kingbravious1
@kingbravious1 3 месяца назад
Ine ndimaona ngati chakwela amene ku MCP samufunanso that's why amamupanga advice zolakwika kuti athu azimuona kuipa
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 3 месяца назад
You are right
@ceciliamastala6824
@ceciliamastala6824 3 месяца назад
Eh eh koma where do people get all this information 🙌 ndawopa
@sylvesteralfred8355
@sylvesteralfred8355 3 месяца назад
Komanso Akathawa President'yo zimafunika kuphwanya za boma zonse kuti abwelere ndipo achikepo pa mpata simple basi athawe kumutha kwake nkomweko uchitsilu ife ayi tatopano
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg 3 месяца назад
Anthu amenewa mmmmm asasiyidwe iyayiiii
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 3 месяца назад
Izotu more 🔥 Comrade Ntanyiwa moto kut buuuu
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 3 месяца назад
Achakwera ndi gulu lawo asapite kumaliro masatana amenewa aphedwenso onsewo mmodzi mmodzi or 2 by 2 moyandikana
@BlessingsMkwembe
@BlessingsMkwembe 3 месяца назад
Osaopa go go go mpaka chilungamo chidziwike
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 3 месяца назад
Ubwino wake oku phanso amafa, komanso ama phedwa, Yehova adasankha Davide kukapha Goliath,koma Davide sanali msirikali Ayi,takhalani, Wanthu akungo mva chisoni sikutitu amenewa anga vute Ayi,koma kuopa kuphesa Wanthu ambiri mbiri,pa Malawi palibe Malo omenyera nkhondo kungoti chibwana nkusowa chikondi mphamvu ya Satana ndiye yakula .Tsono osa kalipa Chakwera adabwera Chifukwa cha Chilima Malo mothokoza basi ango mupha mzeru kusiyana,koma Yesu anati musaope okupha thupi koma mzimu Chilima wamva kuwawa pophedwa koma mzimu kumene uliko uli Bwino popeza wachita kuphedwa Ambuye nso amukhulukira ndi wena wonse anali momwemo,
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg 3 месяца назад
Khani iyi ndiyoona ma phone amalemuwa alikut?
@KazembeSemion
@KazembeSemion 3 месяца назад
Mmmmm paka pamenepo
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no 3 месяца назад
Analakhula molimba tima 😭😭😭 wafera Malawi wake 😭😭
@LemieMwalendo
@LemieMwalendo 3 месяца назад
Mr Chilima your soul will rest unless muthu wakuphani adziwike
@mkupabanda-nd2vb
@mkupabanda-nd2vb 3 месяца назад
Kodi nyimboyo anaimba ndani guys? Big up to limpopo fm
@LajabiAnisaa
@LajabiAnisaa 3 месяца назад
Kkkkkkk be serious my friend anthu akulila samalieo inu muli busy kufusa sanyimbo anayimba ndani
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 3 месяца назад
Komatu chomwe angadziwe Amalawi sadzayiwala za ifa imeneyi 😢😢😢😢😢😢
@staceycossam5933
@staceycossam5933 3 месяца назад
We ready to do that please brother
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 3 месяца назад
Angofuna kuziyalusa palibe apindula akotikwiyisa amalawi
@Abraham-ue2rt
@Abraham-ue2rt 3 месяца назад
More fire 🔥
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 3 месяца назад
Abushiri? Wasataniki winanso ameneyo
@henrykapinga1433
@henrykapinga1433 3 месяца назад
No secret under the sun indeed
@DannieChimenya
@DannieChimenya 3 месяца назад
Tiwuzeni zoona biggy Limpopo Fm 🔥🔥🔥🔥🔥
@AuspiciousKalambula-hp7gj
@AuspiciousKalambula-hp7gj 3 месяца назад
Big up boss inuyo ndi nkhani Zina!!!
@RebeccambeweHiwa
@RebeccambeweHiwa 3 месяца назад
Inu ndie mukutiimiliratu more fire limpopo
@LangfordMabaso-z7u
@LangfordMabaso-z7u 3 месяца назад
Asathawe chakwela waziputa dala ndi galu
@BakaliPhili-es3xj
@BakaliPhili-es3xj 3 месяца назад
Ndipo ameneyu asathawedwe
@AgnesMatola
@AgnesMatola 3 месяца назад
Mumatiimila Sir....Apitiliza bwanji panali M"gwilizano buluzii ameneyu.... koma kanyimboko
@daisynyirongo
@daisynyirongo 3 месяца назад
👂
@ritchardchakuma5725
@ritchardchakuma5725 3 месяца назад
Samola maschelo sistimu asathawe choyipa chisata mwini
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 3 месяца назад
Koma a dala kadulati nawonso aPita konko afa ngati galu
@rabeccakhonje9548
@rabeccakhonje9548 3 месяца назад
Shaaaa
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 месяца назад
Mai kaliyati Joyce banda ma hule adziko lapasi
@BeatriceMANDEVUGONDWE-iv4gr
@BeatriceMANDEVUGONDWE-iv4gr 3 месяца назад
Zikugwirinza koma galu iwe
@EagerChicken-qj6xu
@EagerChicken-qj6xu 3 месяца назад
Akubanja chonde musalole.
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no 3 месяца назад
Takozeka kugwebana
@TwalikiWisiki
@TwalikiWisiki 3 месяца назад
Zowonadi pakufunika postmortem,, chonde akubanja la onse amene mwaluza abale anu,, chonde chonde chonde ndagwira mwendo a UTM musalole kuti mtsogoleri wanu ayikidwe musadapange postmortem chonde chonde,,
@kithchikhawo3181
@kithchikhawo3181 3 месяца назад
Apanga kale
@MorganBanda-oc2jx
@MorganBanda-oc2jx 3 месяца назад
penanso zikumazawoneka ngat kuti tabwereranso kuwulamuliro wa atsamundatu......
@AgnessKavalo
@AgnessKavalo 3 месяца назад
Shaaa Bushiri vp????timwaliro mosavuta
@patrickmadukani4314
@patrickmadukani4314 3 месяца назад
Ndipo agalu awa afika nazo ponyasa kwambiri 😢😢😢
@jackiendlovu9564
@jackiendlovu9564 3 месяца назад
Yes mr you're right tili okhonzeka kusonkha
@AnnaPhiri-b8t
@AnnaPhiri-b8t 3 месяца назад
Zomwe zokulimbirana vice president zakupha zokhazokha chipani Cha mwazi
@JustinLipipa
@JustinLipipa 3 месяца назад
Boma ili ndilakupha mcp sizasitha chipani chamagazi ichi .
@JosephNgona-f9v
@JosephNgona-f9v 3 месяца назад
Zoonadi vicePresident kuikidwa osaona kut chumupha chan zikudabwitsa tisonkha ayezedwe basi .asaikidwe mpaka choonadi chidziwike basi ine osaopa
@RobertFegstone-v3g
@RobertFegstone-v3g 3 месяца назад
Goodwork
@WysonAdamu
@WysonAdamu 3 месяца назад
asiyeni abise chilongamocho Koma afune asafune thawi inzafika Komaso aziwe Kuti Ife Malawi tikufuna mayankho
@LeviMitambo
@LeviMitambo 3 месяца назад
Mfundo imeneyo bwana mtanyiwa
@SaidiMustafa-y3q
@SaidiMustafa-y3q 3 месяца назад
🙏🤝🤝👏👏🙏🙏🙏Sowona
@DanielZitande-y1d
@DanielZitande-y1d 3 месяца назад
Abale ndi zovuta koma please tiyeni tigwilane manja tisonkhe ndipo tisaope wina aliyense mulungu ndiye amenye nkhondo
@UmariBashiri
@UmariBashiri 3 месяца назад
Brother inuyo Mulungu Akupatseni Moyo wautali.
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 3 месяца назад
Pana bushir atilamulire ife yo ndiye kulowetsaso fiti inanso imeneyo
@GrecianWyson
@GrecianWyson 3 месяца назад
KOMA MR KOMORED KKKKKKKKK IWEYO ANAKOZA ANAKUVUTIKILADI KUKUYAMWITSAN MAN ULEMU WANU🎉🎉🎉🎉
@DonaldPonda-p2q
@DonaldPonda-p2q 3 месяца назад
Kufuna kutchuka kukhala ndi ndalama zochuluka popanda kugwira ntchito chosatira chake ndiizi kumangopha anthu nkhati nkhuku waonekera chakwera usi siufuka popanda moto
@dalitson3558
@dalitson3558 3 месяца назад
Achewa ndi anthu oipa kwambiri
@peternashyo9850
@peternashyo9850 3 месяца назад
Choonadi chidziwika, ngozi zimachitika koma iyi yasiya mafunso ochuluka opanda mayankho.
@MoweeBright
@MoweeBright 3 месяца назад
Ali mpopo musawope tili pambuyopanu chilungamo chiziwike!!!!!!?!
@KennethFilimon
@KennethFilimon 3 месяца назад
Tiyeni tonse tizisiye m,manja mwamulungu oky
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 3 месяца назад
Black box ili KUTI?
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 3 месяца назад
Watching from Kenya very bad tell us Limpopo FM
@SolomonShaibuh
@SolomonShaibuh 3 месяца назад
Kmatu Ntanyiwa akusaka
@MoosaSame
@MoosaSame 3 месяца назад
Chilungamo chokhachokha big up mn
@malawigeneralguide1646
@malawigeneralguide1646 3 месяца назад
Kwachema.....I have downloaded this VN.....eeeish nkazi wa Bingu uja si munthu,......💔💔💔 🕊️🕊️🕊️🕊️🕊️
@jackiendlovu9564
@jackiendlovu9564 3 месяца назад
Akumusankha bushili akufuna dziko lanthu lizaze ndi atsogoleli asataniki okha okha kodi? Mukupita naye Malawi okoma uja???.
@EnockDixon
@EnockDixon 3 месяца назад
😮😮😮😮
@paundfeston
@paundfeston 3 месяца назад
BWANA NTANYIWA ini ndikatundu
@JabessHarry
@JabessHarry 3 месяца назад
Asapezeke kumaliro ameneo
@dontreybanda278
@dontreybanda278 3 месяца назад
Chakwera akufunika sniper please please allow me.
Далее
NYC Mayor Adams indicted on federal criminal charges
5:31
Landing In Blantyre Malawi - Air Malawi
3:02
Просмотров 32 тыс.
VHEMBE FM interview NICODERMIC
13:26
Просмотров 5 тыс.
Amalawi tidzameta maliro a Chilima 2025
7:57
Просмотров 51 тыс.
Elizeo Bambo Nthalika: Tu quoque Brute.
27:58
Просмотров 3,2 тыс.
17 000 000 за Бой / Алёна, блин!
0:44
17 000 000 за Бой / Алёна, блин!
0:44