Kkkkkkkkk ine ndinabadwa nthawi ya bakili Ali pampando ndinkangova history pano ndizindikila kuti mcp chipani chakupha zoona kundiphera chilima wanga ine
Upandu uliwonse ukukonzedwawo back to the Sender in Jesus christ name Eeeeeee Oyipa athawa yekha popanda othamangisaaaa kkkkkkkkk Black box ipezeka bwanji ku state House? Apatu mwazigwilitsatu kuti mudaphadi wanthu waja ndiinu 😂😂😂 yomweyo chikangawa iweeeee zikubwera uziona sunati
Ngati mukuziwa kuti ndinu a MCP plz zomatitokosa Ife amene ndikuliva kuwawa dziko lino muno musamaike ma comment ano onukhawo sitikwafuna koma tikumanabe mu 2025 panya pano inu a MCP
Comrade plz mukuonjeza ma udiou apadela bundle ikudula tazingonenan zofunikazo plz plz timaikonda program yanuyi koma muzingonena zofunikazo bas ma audio enawo timakhala tawamvela kale kwina
Kodi tikamanena dzakupha,,kodi Evison matafale anapha ndi MCP????? Kodi wankulu wa asilikali uja mr mankeni chigawa anapha ndi MCP??? Kodi mwana wa school uja malemu Robert chasowa analakwa chiyani,,,kodi anamupha ndi MCP???? Athu 9 ma brothers athu amene anaphedwa ku MZUZU aja kodi anapha ndi MCP????? tiyakheni please.
Inu mwakhutha nyemba eti,,,kapena ndi kachibanzi mwalandila ku chokela kwa sekulu wanuyo,,pano sithawi yonyodzana ino koma ndi thawi yokonzela zithu pamodzi ndi boma limene lilipoli,,inu simunatumidwe ndi a malawi aii idzo ndi zamutu mukunama kuti mukuyakhulila a Malawi propaganda imeneyo,,ndiponso mumangoyakhula chotsecho muli ku dziko lanzanu pita ku Malawi mukakonze ziko,,mukwiyo umeneo tikudziwa kuti chakwela sanakupatse chibanzi
Ngati mukuziwa kuti ndinu a MCP plz zomatitokosa Ife amene ndikuliva kuwawa dziko lino muno musamaike ma comment ano onukhawo sitikwafuna koma tikumanabe mu 2025 panya pano inu a MCP