Тёмный

LIMPOPO FM YABWELETSA PROGRAM INA MMAWA UNO KUSAMBWADZA ONSE AMBALI YA BOMA 

Malawi Trends TV
Подписаться 42 тыс.
Просмотров 8 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

15 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 36   
@JosephFulayi
@JosephFulayi 10 дней назад
Live auzeni a Ben longwe
@JosephMwadzama-f4u
@JosephMwadzama-f4u 10 дней назад
Matimilira boss keep it up❤️❤️🔥🔥🔥🔥🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@MerryWayson
@MerryWayson 10 дней назад
Tinakusowani Mr Kangaude more 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 A Beni mutu sukugwira kkkkk
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 11 дней назад
Afiti okupha ana ayabolosi😅😅😅😅😂😂😂Chikangawa nthawi yako yatha tsopano wayaliluka basi mfiti iwe,mbusa wabodza😅😅😅😂😂😅😅😂😂
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 9 дней назад
❤❤ we love you in Malawi ✊
@WillianBanda-p7d
@WillianBanda-p7d 10 дней назад
More fire More fire comrade
@AbudulJohn
@AbudulJohn 11 дней назад
Ndiye iwowo aziwa kuti Ndege inali ndi mafuta ochepa nanga bwanji osathila mafuta amadikila chani ? Amafuna igwe kenako ndiye azithila bwino mafutawo? Munkhani imeneyi muli mafutso ambili opanda mayankho. Komaso Asilikali amagwilisa ntchito Ndege yopanda black box? Nanga ngati munali black box anachosamo ndi ndani?
@ThomasMlowoka
@ThomasMlowoka 10 дней назад
Limpopo 💪💪
@allieadam3235
@allieadam3235 11 дней назад
Ine Alli Adams kuno ku Pretoria ndimadalitsika ndi Limpopo Fm, Mukutiyimirira ndithu,
@GeoffreyMacheso
@GeoffreyMacheso 10 дней назад
ana achepa mitu sikugwira fire
@TinaChilombo
@TinaChilombo 11 дней назад
Iifeso timamva kukoma ku may fair JHB tikamamva ma programme onse arimpompo FM ndine Mazirah sakah
@DeliaKaduya
@DeliaKaduya 11 дней назад
Koma a limpopo inuyooooo! Mulungu azikutetezani stuff yanu yonse, popanda inu ife a Malawi tili chabe,, mumatiuza zinthu zomwe mwaife tokha sitingakwanitse kuziziwa, ulemu ochuluka muzilandira nthawi zonse
@MemorySambani
@MemorySambani 9 дней назад
mulungu azikudalisan🙏
@TadiousBanja
@TadiousBanja 11 дней назад
Uku ndiye kugwira Ntchito moidziwa ,tiye nayoni
@thomasmalenga8194
@thomasmalenga8194 11 дней назад
Kodi anthu inu amene mumakwaniza kupita kumeneko kuchikangawako bwanji sumatha kutijambulila ife anthu tili kutalife. Kuti tithe kuwona mthengo umene unagweza ndege wo. Ndipamene panagwela ndegepo. Chonde. Tijambulilen 😢
@lingsonmitunda293
@lingsonmitunda293 10 дней назад
The spiderman 🕷 ulemu wanu bwana Kangaude
@eunicesaiti
@eunicesaiti 11 дней назад
Following boss, ma Ulemu anu.
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz 11 дней назад
Yomweyo ya chikangawayo 😂😂😂😂
@TressLuka
@TressLuka 11 дней назад
Kulitu Nyekhweeee adaphawo. 😅😅😅
@HappyMunthari
@HappyMunthari 11 дней назад
Umakwana ipase fire end tipite pa msewu anthu awa atopesa
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 11 дней назад
More fire comrade
@MariaMonteolimpio-n1h
@MariaMonteolimpio-n1h 11 дней назад
Ok
@KondaniPhiri
@KondaniPhiri 11 дней назад
Ndipo tikudikila. Mpaka akagwire ndende agalu amenewa
@EdwardMkwera
@EdwardMkwera 4 дня назад
Antanyiwa takambilanani ndi amalawi first kuti asayesere mabvoti chifukwa anthuwa akufuna kubera chonde tiyeni tipite pansewu
@LeonardMhone-cg1tk
@LeonardMhone-cg1tk 10 дней назад
Chipanda chilima sanakalowa mmboma awaaa
@SurpriseNgobeni-k6z
@SurpriseNgobeni-k6z 11 дней назад
Tilibwino Ife Kuno Ku Pretoria East Mo 🔥
@WillianBanda-p7d
@WillianBanda-p7d 10 дней назад
Nkhani ya chikangawayo, mkhalitsepo pamenepo,uyu president asatiputsitsepo ayi ndi report yabodza
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 11 дней назад
More 🔥 LIMPOPO FM❤❤❤
@TadiousBanja
@TadiousBanja 11 дней назад
More 🔥 mr presentor MCP ndi khalidwe lawo
@LeonardMhone-cg1tk
@LeonardMhone-cg1tk 10 дней назад
Sinawonepo Army commander opepera ngati uyuuu
@MwanaDallah
@MwanaDallah 10 дней назад
Chikangawa yomweyo afitiwo
@yusufbakali
@yusufbakali 11 дней назад
❤ You mumakwanisa live from Laudium
@nessiemfunie
@nessiemfunie 11 дней назад
🤞🤞🤞🤞🤞🤞
@GladysBanda-h2w
@GladysBanda-h2w 10 дней назад
olo.muzik yokhayo😂
@ThomChirwa-py8xo
@ThomChirwa-py8xo 11 дней назад
Ukuigwila ntchito mngani wami
@GeoffreyMacheso
@GeoffreyMacheso 10 дней назад
amve m.bebe moto
Далее
BON KALINDO LERO PA 16 SEPTEMBER  2024 |
16:18
Просмотров 4,4 тыс.
Каха и жена (недопонимание)
00:37
Jetu-ndine_Produced by Edoh-Kay & E.K.C RECORDS
4:04
Record Label Ya Ku Malawi, ipindula?
13:59
Просмотров 13 тыс.
Rev Alexander Kambiri  Odala Akufa Mwambuye
19:05
Просмотров 209 тыс.
Каха и жена (недопонимание)
00:37