Тёмный

Limpopo woyee yatelaso ndi program ina muja zikhalira wabwelayi ndi Mr Don’t Trust 

Malawi Trends TV
Подписаться 48 тыс.
Просмотров 11 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

17 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 42   
@mollymasangano473
@mollymasangano473 2 месяца назад
Akuwapanga anthu khaza kuwangwaditsa pa Road block osawakwapula bwanji just Mlulanjeko tapitani pa Road blockhouse anthu akuwanzuzatu don't allow this.
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 2 месяца назад
Mbambande Limpopo fm best radio station
@GeorgePatels-go7wj
@GeorgePatels-go7wj 2 месяца назад
Very true but the opposition is too wick
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u 2 месяца назад
Chakwera ndi wakuba, kusawukitsa dziko kuti anthu a m'dziko akhale ngati opempha polandira zithandizo zake pomwe Ali wakuba, wakupha, Mizimu igone ku malawi congress pate and tiyeni tiwonelere chisangalaro cha satana kunamiza anthu ku Balaka pomwe akudyetsa Kasiya yokha, Shame to u Mr Lazaro😢
@RitaKainga
@RitaKainga 2 месяца назад
Endless salute kwanonse pa Limpopo
@FisherAction
@FisherAction 2 месяца назад
It will happens bcz the wickness of opposition leaders bcz they just need to be leading the country why they keep quite like this
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 2 месяца назад
You deliberately forgot that you are the same people who remove DPP and UDF and you said APM failed to govern you and now you want APM and Atupele to do what ?
@EfeloYovita
@EfeloYovita 2 месяца назад
kodi ndingaijoine bwanji Radio imeneyo
@EfeloYovita
@EfeloYovita 2 месяца назад
tiuzeni zochita chonde ndijoine Radio station
@MohammedMajiga
@MohammedMajiga 2 месяца назад
Koma ine ndandadaula kwa athu akwathu kumangochi ayiwalandi
@PatrickMailos
@PatrickMailos 2 месяца назад
Or ine ndadandaula
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 месяца назад
Oohoh Mwambi uja wasinthikanso, Panopa Ndipayepayele Chakwela Anapha Vice Wake, osati fisi anapha nkazache
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 месяца назад
Mulungu kumwambako musalore satana apambane timenyereni nkhondoyi
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf 2 месяца назад
Amalawi ndife mtundu womvetsa chisoni. Timakopeka ndi zinthu zochepa zomwe sizingatipatse tsogolo lililonse. Tatiyeni tiziganiza mwakuya pa zatsogolo lathu ndikuyesetsa kumapanga zisankho zabwino. Kodi umphawi wotere udangobwerera ife tokha pansi pano?
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 месяца назад
Mvuto amalawi sitimachedwa kuiwala akopeka chifukwa chachimanga kuiwala kut feteleza tikugula modula ambuye kumwambako imvani kulila kwathu musalole kute athu awa alamuleso
@MerryWayson
@MerryWayson 2 месяца назад
Ine nde ndadandaula ndianthu akwathu Ku Mulanje iiii
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 2 месяца назад
Adzatimenyera khondo mulungu ife tili chete enafe sitigona kupephera kusala kudya kt mulungu achitire chifundo dziko lathu lamawi osakaika ayakha
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 месяца назад
Anthu agule ndi ankhadza anazolowera zaugule
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 2 месяца назад
Tayu votani pai please choonde ndaphata manyalo ako pai javoten pakujabulusa nyantongiii nibulutu maningi
@JohnAsendi
@JohnAsendi 2 месяца назад
Uthenga umenewo ndi oona koma osati muzinena kuti mupite kwaovota okha ayi upitenso Kwa atsogoleri omwe kupanga tizipani tating'onoting'ono chifukwa ameneyo ndi omwe angapangise kuti MCP ioloke apange n'gwilizano ndi zipani zazikulu monga momwe anapangira 2019. MCP inde imwaza ndipo idzativinya mpaka tidzabiba matumbo komanso MCP siliyo Abuchili Ali momwemo potengera zomwe anayankhula zulo tichenjele amalawi ndithu MCP khaya
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 месяца назад
Koma akunama awa olo angawe chimanga chawocho anthu olo ali osamva koma apa amva kuti akubwera ndikunamaso komanso mr tanyiwa mumanena nthawi ndi nthawi
@wilfredkazembe676
@wilfredkazembe676 2 месяца назад
Big mmalawi sazatheka sitichedwa kuyiwala ife wolo muthayakhula motani koma mukutimasula ndi kutiwonetsa koma chimanga chimenecho chikangopelekedwa ayamba yemweyo
@OweniMolokooweni
@OweniMolokooweni 2 месяца назад
Ndipo kwambili Malawi ndi mbunzi
@PatrickMailos
@PatrickMailos 2 месяца назад
Allah yaalam 😢
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 2 месяца назад
Azapanga KU Lilongwe konko zimenezo
@JohnAsendi
@JohnAsendi 2 месяца назад
Chimanga chibwere bola chikhale Kenya guys voti ndi muntima
@ronaldordinga6537
@ronaldordinga6537 2 месяца назад
Inu manyaka osewa ndi opposition party palibe yemwe akuwoneka pa ground pano opposition yose ya makape sakusiyanaso ndi MCP amandinyasa a opposition nawo
@petertaulo8014
@petertaulo8014 2 месяца назад
Zoona Don't Trust 😅
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 2 месяца назад
Aaaas propaganda iyi ya dpp . Mcp ili busy kumanga malawi osati zopusa zaumbuli ukukambazi
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 2 месяца назад
Koma chakwela ngati amavela ladio iyi eeeeeee
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 2 месяца назад
Ine ndikuganiza kuti samamvera
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 месяца назад
Nde chimanga cho adzagawe mpakana liti, nthawi yonseyi anali kuti anthu akhala akufa ndi njala chimanga mutachibisa
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 2 месяца назад
Zatha fundo sopano muraka raka kufufuza komwe kuli ana achakera kut muwanyonge' anthu opanda chikond pandale Inu onse oyipa' bingu munat oyipa' pita' muluz oyipa' lelo chakweraso kkkkk anthu opanda zelu Inu!!!
@nifachitima3477
@nifachitima3477 2 месяца назад
Mummm kkkk
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 2 месяца назад
Fundobimeneyi kkkkk koma ndale zazaka zino!!!
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel 2 месяца назад
Iweeee panyopako sopano watikwan nda akazi ako omwe ndi ana ako omwe
@EstherBonga
@EstherBonga 2 месяца назад
😂😂😂😂Iwenso watikwana ndi chikangawa wakoyo watuma ndani unvele pachiphisi pako ifeyo we love them anayankhula ndi ife ndipo sanatikwane
@petertaulo8014
@petertaulo8014 2 месяца назад
Iwe ndiye ukutukwana ndani?
@daltonjafali3856
@daltonjafali3856 2 месяца назад
Ndiwe savage kwambiri kutukwanako wapindula chiyani
@MaritaBanda-p4z
@MaritaBanda-p4z 2 месяца назад
𝕜𝕠𝕞𝕒 𝕟𝕕𝕚𝕪 𝕫𝕚𝕞𝕒𝕜𝕦𝕨𝕒𝕨𝕒
@GeorgePatels-go7wj
@GeorgePatels-go7wj 2 месяца назад
Very true but the opposition is too wick
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 2 месяца назад
Just you go and be the opposition so that things will be working according to how you like because you're the same people who voted for Chakwera and now what you want opposition to do for you ??
Далее
💅
00:24
Просмотров 108 тыс.
Теперь DOOM пройдёт каждый
00:17
Просмотров 330 тыс.
💅
00:24
Просмотров 108 тыс.