Тёмный

LYTONE MANGOCHi WATI SAKUOPA IMFA 

Nkhani Za Malawi
Подписаться 1,2 тыс.
Просмотров 9 тыс.
50% 1

Chakwera akudziwa bwino za zigawenga Zomwe zimatumidwa kuti zizikhapa anthu azipani zina, watero Lytone Mangochi.
Zigawengazo zimapatsidwa ma K30,000 ndimunthu wina wamkulu mimba wa MCP.
Ndi chifukwa chake Chakwera salankhulapo kena kali konse.
Lytone Mangochi wati sakuwopa imfa ndipo adzafera ufulu wa a Malawi.
#malawi #foryou #southafrica #everyone

Опубликовано:

 

21 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 53   
@hamissimdoka9665
@hamissimdoka9665 7 месяцев назад
Inde zoona man mumatiyimirira continue good work man
@lyiemax
@lyiemax 7 месяцев назад
Powerful warning, proud of you Bwana Mangochi 🔥 🔥
@JuliusMandala
@JuliusMandala 4 месяца назад
💪💪💪💪💪💪💪💪👊🤛🤜 fayt bagera
@RiteRoderick
@RiteRoderick 7 месяцев назад
Mulibho Mr Mangochi guys tiyeni tiyeni tigwirane manja tipange mademo Chakwera atule pansi udindo
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 7 месяцев назад
Mulibho magochi boys ❤👌👌👌👌👌
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 7 месяцев назад
Amene mumasapoter mcp nonse ndinu agalu fiti za anthu .. mankhwala mzipatala mulibe njala ikupha anthu ..pano kumasapoter mcp kupwambwana
@ShaneElisha
@ShaneElisha 7 месяцев назад
My brother keep up
@SuleimanRabsonMkhunga
@SuleimanRabsonMkhunga 7 месяцев назад
Best warning mr mangoch
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 6 месяцев назад
Kkkkkkk mpaka ife tiri kujoni tibwere ku zavota aaaa kamba ina mangochi ukufuna tizaruze wait kumeneko tibwera tikanva kt kwacha yasiya kugwa not now
@emmanuelkhosa-ze6fl
@emmanuelkhosa-ze6fl 7 месяцев назад
Don't give up
@BrendaLupale
@BrendaLupale 7 месяцев назад
Inu a Mcp musamayankhule mopusa mwava mbudzi za anthu mukuyankhula ngati muli ndi mzelu apa chikhalireni kwanu ndinu amphawi muli busy kumuikila chakwera kumbuyo inu oputsa kwabasi Mcp ndekuti chani chipani chankhadza ngati chimenecho inu talodzani chomwe wakupangilani chakwera or makwanu mwakanika kuthila fertilizer minda mwanu nde mukufuna adzikutamani ndani munthu akunena zoona apa njala yachaka chino tikuvutikana nayo limodzi inu munganene kuti chakwera wakugulirani chimanaga mukudya makwanu zopusa basi
@musakunje2471
@musakunje2471 7 месяцев назад
MCP akuwopa DPP ikulowa boma 😢😢😢
@georgesmart3791
@georgesmart3791 7 месяцев назад
Ulemu wanu Mr Mangochi❤❤❤
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz 7 месяцев назад
Double salute mangochi
@MartinMajola
@MartinMajola 7 месяцев назад
Chakweli mbuzi yamuthu
@MaryChinkhuntha
@MaryChinkhuntha 7 месяцев назад
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 7 месяцев назад
Straight talk ❤❤❤
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 7 месяцев назад
Best worning lyton
@AgnesMatola
@AgnesMatola 7 месяцев назад
Mmatiyimila Sir
@hughmankalonga3769
@hughmankalonga3769 7 месяцев назад
Mbewa ikakhala kumpani siopa moto, poti inafa kale 😂😂
@MjombaMjuba
@MjombaMjuba 7 месяцев назад
Ndiwe mbuzi akutuma, wadya zingati Kodi? Chifukwa chiyani Peter kapena Bakili siwunkadzudzura mbuzi iwe
@MartinMajola
@MartinMajola 7 месяцев назад
Choka hiwee mwana wambule
@andsenJeke
@andsenJeke 7 месяцев назад
Pulezidenti oipa kobasi uyu
@EdwinMabviko
@EdwinMabviko 7 месяцев назад
Kodi ichi a Police angochiwona bwanji?
@AlexKatete
@AlexKatete 7 месяцев назад
Awa ndiye umayankhula chilongamo
@YasiduPemba
@YasiduPemba 7 месяцев назад
😅😂😅😂😅😂😅😂
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 7 месяцев назад
Zowonadi presdent waboza mumatiyimirila mr mangochi mbiri ya Abusa yinayipa kale amalawi akupusisika ndi baibulo .
@nellikkmwenda7087
@nellikkmwenda7087 7 месяцев назад
Kkkkkkkkkkk Eeeeee lullululululu lu auzeni agalu wa a mcp
@LukeshadrickShadrick
@LukeshadrickShadrick 7 месяцев назад
Mr mangochi bokosi Lako wakhoma kale???????? Iwetu wk ino siitha
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 7 месяцев назад
Zoona zenizeni mangochi
@JamesChimera-hw1nv
@JamesChimera-hw1nv 7 месяцев назад
Zakhalabwino agalu owuwa anali mmodziyekha kalindo koma tsopano mwakwana awiri wina ndiwe mangochi agalu akumalawi ziwuwanikwambiri
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 7 месяцев назад
Uphawi wakuvutani alytoni msiya ana inu
@cjaylucky
@cjaylucky 7 месяцев назад
NO PAIN NO GAIN
@tadalarhostinchiphwanya7891
@tadalarhostinchiphwanya7891 7 месяцев назад
Malawi ndiokoma. Awa ngofa ifa inu. Mwati mmutumu mumayenda?
@alimalawi2661
@alimalawi2661 7 месяцев назад
Inu so ndinu ndan amene mukusuza munthu uyu kama muli ndi zelu inu agalu kodi kutelo ku nde kut zimukuona kumene likupita kd chakwela ndindan amene ukumuta yo
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 7 месяцев назад
Kutamika, nthawi zina si bwino.dpp,inapha family ku 22 kusiya ana okha zinayamba lero?dpp,analetsedwa ndi yani.matama,basi tikutame.
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
@AhmadumkomaTambala-lr9gp 7 месяцев назад
ATA satipatsa
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 7 месяцев назад
Unafa kale iwe
@yassinn5634
@yassinn5634 7 месяцев назад
Nthawi yomwe a DPP aja ankamumenya Bon Kalindo Ali ku UTM, Pamene amaotcha magalimoto a UTM aja iyeyu anali asanabadwe. Asatinyase apa
@thokobanda5991
@thokobanda5991 7 месяцев назад
Osangofa bwanji galu iwe, iwe wapanga ziwembu zingati fisi
@cjaylucky
@cjaylucky 7 месяцев назад
Kom agalu ndiambil ndiwe thoko banda buz iweo banda
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 7 месяцев назад
Tibwela ndibazuka tizathibulane
@JosephNgozo-l4k
@JosephNgozo-l4k 7 месяцев назад
Inu a DPP musamayankhula kutiuza zochita ngati sitikuona zomwe zikuchitika. Tikuwerenga momwe tayendera kuyambira nthawi ya a Muluzi kufika lero. Chilichonse tikudziwa chabwino ndichoyipa chomwe. Ife ndi amene tikudziwa zochita tsiku la chisankho. Tayambani mwakonza ubale wanu ndi UDF, PP komanso UTM mukatero ndipamene tidziwe kuti democracy muyidziwa ndipo mukiyitsata bwino. Zoyankhula sizingatiuze momveka koma zochiya zanu ndi zomwe zitiuze zenizeni.
@SleepyBasketball-mo8kf
@SleepyBasketball-mo8kf 7 месяцев назад
Don't know what say u know nothing
@SleepyBasketball-mo8kf
@SleepyBasketball-mo8kf 7 месяцев назад
U don't know what you say u nothing
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 7 месяцев назад
Athokeni ngamo Mr Mangochi
@LukaThawe
@LukaThawe 7 месяцев назад
Mbuziiii iyi
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 7 месяцев назад
Ndiwe ndani iwe pa malawi uli ndi udindo wanji kut umulangiza chakwera iwe garu wachabechabe
@BFWCPHIRI1978
@BFWCPHIRI1978 7 месяцев назад
Galu iwenso ndiwe mndani kwa bigy mangochi,second boni kalindo
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 7 месяцев назад
Inuso ndidani kodi tili mu democracy pano kodi iwe sukudziwa ? Aaaaaa mulibe zeru akulu inu mukukodwera athu akamavutika mudziko muno
@RusselleStanley
@RusselleStanley 7 месяцев назад
Galu iwe mimba yowumayo
@AcsonSaulos
@AcsonSaulos 7 месяцев назад
Ngati suopa imfa kadzimange mbuzi iwe
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 7 месяцев назад
Tibwera ndimifuti
Далее
Шоколад приходит на Землю.
00:23
Просмотров 185 тыс.
She Couldn’t Believe I Did This! 😭 #shorts
00:12
Stich Fray - Zoti Ndimakukonda (Official Video)
3:21
Просмотров 910 тыс.
CHAKWERA TOUCHES DOWN IN BT
0:46
Просмотров 17 тыс.
Zipani Zotsutsa Dzukani - Bon Kalindo
5:59
Просмотров 3,5 тыс.
Swagdaddy ZM ft Aqualaskin - Nechalibobu (Visualizer)
2:26
Шоколад приходит на Землю.
00:23
Просмотров 185 тыс.