Тёмный

MA PLAN A MCP ALOZA KWA NORMAN CHISALE KOMASO PETER MKHITHO KUTI AWAONETSESO NGATI SKC 

Malawi Trends TV
Подписаться 50 тыс.
Просмотров 15 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

27 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 59   
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 2 месяца назад
Amen Amen YESU khristu tithandizeni
@DalitsoMichongwe
@DalitsoMichongwe 2 месяца назад
Amen pastor 🙏🙏
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 2 месяца назад
Amen and Amen Ambuye tithandize ndithu, palibe chomulaka iye Mulungu wathu
@BistonMacheso
@BistonMacheso 2 месяца назад
Yes ndipo satana akunama kwambiri Heb 12:28:29 mulungu wanthu ndimoto
@MadalitsoBokosi-j3u
@MadalitsoBokosi-j3u 2 месяца назад
Mu zina la yesu khristu malawi asitha mulungu sangalore kt athu ake tikhalire kulira misozi yathu mulungu akuona ndipo akuva ndiwazatheka bwanji
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 2 месяца назад
SIZINGATHEKEYI MCP IKUNAMA MALAWI WAKE SI WALEROYU AYEREKEZE ACHOKA CHOTHAWA
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 2 месяца назад
Amen 🙏
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 месяца назад
Yesu amaona
@KellyMemba
@KellyMemba 2 месяца назад
Amen
@MercyNkhoma-b6h
@MercyNkhoma-b6h 2 месяца назад
Koma Mcp mmm imaganiza zaupandu
@DigleDafter
@DigleDafter 2 месяца назад
Ngoz zopangidwa izii bushiri chakwela Joyce ndamene akuzuza miyoyo ya Malawi 😢
@AdamYas-ec9oc
@AdamYas-ec9oc 2 месяца назад
Mumatimilira nditu inu mumakwana
@SaidiKing-b9o
@SaidiKing-b9o 2 месяца назад
We decre the blood of Jesus in Malawi
@BistonMacheso
@BistonMacheso 2 месяца назад
Akunama kwambiri satana Ali Pasi pamulungu yesaya 54:17 kulibe chida chimene chizapindura pamoyo wa malawi
@EfeloYovita
@EfeloYovita 2 месяца назад
agame changer please yendani yendani muziko lamalawi mnkumalankhula zimenezi akumudzi akumva ndi ochepa chonde akumuzi aziwe kuti dziko likulamulidwa ndi asatana sitikuwafunaso 😊
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 2 месяца назад
Achitsilu wachakwela ndi bushiri ndi joyce
@WezzieMwandira-k3p
@WezzieMwandira-k3p 2 месяца назад
Tatopa ndi mcp please
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 2 месяца назад
Amen ndipo live
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 2 месяца назад
My favourite song❤❤ zoonadi Amasamala ndipo zonsezi Mulungu akuona
@ChavukaGumbo
@ChavukaGumbo 2 месяца назад
Amen atumiki
@BFWCPHIRI1978
@BFWCPHIRI1978 2 месяца назад
Game changer sanyinimutsidwa kkkkkķkkkkkkkkkkkk oky
@MaikNkhoma
@MaikNkhoma 2 месяца назад
Kkkkkkk koma agaluini chisale angasonthe chani dzikolino
@AlwddadAlwddad-nq3sb
@AlwddadAlwddad-nq3sb 2 месяца назад
May God protect Malawians in Jesus name
@MatthewLameck
@MatthewLameck 2 месяца назад
Ndimakumbukila mawu a Grace chinga anati chizabwela chipani cha magazi
@EvanceRazaki
@EvanceRazaki 2 месяца назад
Amen ambuye achitepo kathu ndpo boma limeneli ayiii
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 2 месяца назад
Pankhani za ngozi ku malawi 🇲🇼 muonetsetseni bushiri is a silent 🤫 killer ameneyo, chakwela Aliso mukatimo wakanuka ndi ndalama chakwela
@PatricaTchuwa
@PatricaTchuwa 2 месяца назад
Sure!!
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 месяца назад
Bushiri ndiopa kwambiri ku Malawi anthu ambiri sadziwa
@GeorgeBanda-x6l
@GeorgeBanda-x6l 2 месяца назад
mmmmm ayi koma zaonjeza ndithu eeee mulungu atichitile chifundo pemphelo losweka ntima mulungu salinyoza.
@MariamJaffali
@MariamJaffali 2 месяца назад
💔💔💔💔koma zafika posauzana amalawi tinalakwa chani ndi chakwera ife 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 месяца назад
Yehova ndiye m'busa wathu ndipo sitidzansowa,tifungatileno tiyankheni ndi kutichotsera choyipacho pakati pathu mu mphamvu yanu.
@JonathanMunthali-n3c
@JonathanMunthali-n3c 2 месяца назад
Tikalowa mboma Tizabwezela ma jaji azalowa atsopano olo macomissioners a police
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 2 месяца назад
Uyu pena amanama kwambiri, Bola Mr Bon kalindo amanenako zoona uyu bodza kwambiri
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 2 месяца назад
Ngakhale atasogoza ena koma nawo azapita kumanda komweko,ndipo mtendere sazaupeza anthu oipa
@AndwerBanda
@AndwerBanda 2 месяца назад
Mboliyake nyaiyo
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 2 месяца назад
Akudziwa kuti DPP ikalowa mboma iwo akalowa ndende
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 2 месяца назад
Chikangawayi akufun iyiziwe malawi bwino bwino sopano kapena tikpange kuti asiye udindo wakeyo muthu oyipa ameneyu kwambasi
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 2 месяца назад
Akunama kwambili abulutu a MCP amenewa💪💪💪💪🇲🇼
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 месяца назад
Akusewera ndi a Malawi a mcp akunamatu
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 2 месяца назад
Chakwera ndi satana ndithu
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 месяца назад
Mr chikangawa akunama ndipo apa akufuna awaziwe anthu kukwiya kwawo
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 месяца назад
Zoona tikuyenera kugwada pansi kupemphelera ziko lathu ziko lija kuno chakwera walitora kupha anthu akukhesa mwazi wa anthu osalakwa mmmm mulungu akuyendere chakwera
@PaulinoJone-u9t
@PaulinoJone-u9t 2 месяца назад
Boma ili latipha?
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 месяца назад
Ndipo akunama kwambiri anthu amenewa
@isaaczuze
@isaaczuze 2 месяца назад
Chakwera ndiwasatanic ....munthu oyipa kwambili ...atipha tonse galu ameneyi
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 2 месяца назад
Mumuyan'ganisise bushiri ndi chakwela. Mai joice banda mukanumo alimo
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 месяца назад
Fiti zose izi
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 2 месяца назад
Chakwela ndisatana ñdithu
@NoorRasheed-re5vh
@NoorRasheed-re5vh 2 месяца назад
Mumadyanay bwino DPP Panozikukuwawanitu
@viennasamuel2976
@viennasamuel2976 2 месяца назад
Ndipo zoona zina ndi izo amakasainila dzana dzanali,malawi wakhala gulu la maiko osaopa mulungu,chifukwa cha uysogoleri wa chipani cha mwazi ndi thukuta
@SuzgoChapa-y4m
@SuzgoChapa-y4m 2 месяца назад
shaaaàa
@EvanceRazaki
@EvanceRazaki 2 месяца назад
Boma lachabe chabe lakhadza
@FrankChanza-l3g
@FrankChanza-l3g 2 месяца назад
Kd nhawi yoseyi anali kt
@mbelengamavuto2517
@mbelengamavuto2517 2 месяца назад
😂😂😂😂😂
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 месяца назад
Amen 🙏🙏🙏
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 2 месяца назад
Amen 🙏
@FiskaniLungu
@FiskaniLungu 2 месяца назад
Amen
@JacquelineChindamba
@JacquelineChindamba 2 месяца назад
Amen
Далее
Nancy vs Che Nkope - Boma ndi lomweli
17:23
Просмотров 4,8 тыс.
Nightmare | Update 0.31.0 Trailer | Standoff 2
01:14
Просмотров 629 тыс.
Wait for it 😂
00:19
Просмотров 4,9 млн
MWINI NKHOSA -- Pastor Frackson Kuyama// Ndirande
59:01
Ndoda kuona Baba - PROPHETESS MEMORY
18:15
Просмотров 24 тыс.