Ku Malawi konse nyimbo iyi Ili pa number 1 . Azimayi akuwoneka achilengedwe ndipo ndi 100% mmene tikuyenela kuwoneka munthu wokhulupilira. Ambuye akudalitseni mochuluka azimayi
Nyimbo iyi imandikumbutsa nthawi imene ndinaluza azibale anga 5 pakamodzi ndipo moyo unali owawa koma nyimbo iyi imasisimura ndikulimbitsa moyo wanga 😭
Nyimbo iyi kunena chilungamo pa nyimbo zonse zaku Malawi Ili pa number 1 . Mavalidwe awo avala mau Mulungu . Mawonekedwe wokhawo ndi natural palibe fake Chilichonse chili pa 100%. Congrats azimayi akwathu .