Тёмный

MAFUNSO OVUTA OMWE ATOLANKHANI ANAWAPANIKIZA NAWO A BON KALINDO LERO PAMENE AMACHITITSA CONFERENCE 

Makosana
Подписаться 88 тыс.
Просмотров 91 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

7 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 358   
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt Месяц назад
Kuyankha mafunso mosanyengelela munthu the DC😂😂😂.
@PropeeLucious
@PropeeLucious Месяц назад
Mafunso ake ATI amalephera kuyankha o ha ha ha ha ha
@stevechikaonda3145
@stevechikaonda3145 Месяц назад
Tinene kuti wopaanda nzeru nduyu walemba kuti atolankhani anapanikiza Kalindo, coz he has been consistent and confident in his responses to the posed or you just wanted to lure us and watch this
@edsongeorge8032
@edsongeorge8032 Месяц назад
nkhaniyi ndiyoona malume opanda nzeru ndamene walemba izi.
@macrinenduna1024
@macrinenduna1024 Месяц назад
Pamenepa mukati atolonkhani anapanikiza mafinso, ndifunso liti lajejemetse Malawi Fist?
@user-vt4zo7eo2s
@user-vt4zo7eo2s Месяц назад
Ineso sindikupeza olo limodzi
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Месяц назад
Palibe malawi first number one
@MarkJere-c2d
@MarkJere-c2d Месяц назад
Njila imodzi yofuna kut muonele kaaaa kkkk
@user-zy1eh3pt8v
@user-zy1eh3pt8v Месяц назад
I had the same question 😂😂😂😂
@edsongeorge8032
@edsongeorge8032 Месяц назад
@@user-zy1eh3pt8v inenso I wanted to ask kuti ndipati pomwe Bon kalindo ?
@danielmurichi5673
@danielmurichi5673 Месяц назад
Anyamata wa ali serious bwino kwambiri Keep it up osagonja ndipo boma limeneli lisamale osama one ngati malawi ndiiwowokhawo nafeso ndi malawi Pasafe olo mmodzi panewa kuteloko nkhondo idzayamboka chifukwa nthawi tiliyi ndiya democracy Tikufuna ufulu oyankhula osati kuopsezedwa
@user-sb2mw3xz4j
@user-sb2mw3xz4j Месяц назад
😂😂😂Koma KALINDO eish big respect,
@KingfrahMachado
@KingfrahMachado Месяц назад
Ndipo inu a bon mulungu aziwe pachilungamo chimene mukuonesa kwaife amalawi osauka❤
@TEACHTHEWORDMINISTRIESINTERNAT
@TEACHTHEWORDMINISTRIESINTERNAT Месяц назад
In fact chilungamo chake anayenera kuti adzigula sticker ndi amene wagwidwa atazemba pa boarder. Wokhulupirika apatsidwe sticker yaulele, wozemba akapezeka agule sticker ngati mbali imodzi ya chindapusa.
@alexmakwangwala1615
@alexmakwangwala1615 Месяц назад
Iwe nde Munthu 🔥🔥🔥
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 Месяц назад
The DC woyeeeeee 🎉🎉🎉🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@KingfrahMachado
@KingfrahMachado Месяц назад
Akapusa mwezi sivuto end President aziter kuyakha mopanda mantha💪💪💪🔥
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z Месяц назад
We love you Mr DC
@CharityGondwe-bw9gs
@CharityGondwe-bw9gs Месяц назад
Mumatiimilira mr kalindo ndi azanuwo murandire ulemu❤❤❤❤❤❤❤
@InnocentMtafya
@InnocentMtafya Месяц назад
Musaiwale atamupatsa u ambassador kupita kunja, anazasanduka munthu wina nkumati a Malawi sioafela koma makobidi nde dilu, mwaiwala, eti anapepesa...🤔🤔mmmhhh!(Ndalamaa eeeh!!!!)
@SteveniBanda
@SteveniBanda Месяц назад
Kkkkk go ko nko sambe madzi achitedze basi 😂😂😂 😂😂😂 kalindo umakwana
@SteveniBanda
@SteveniBanda Месяц назад
Osadanda tililimozi ati u ze 💪💪💪🔨🪓🗡️ bwino zatikwana
@user-ik5sz8hc6f
@user-ik5sz8hc6f Месяц назад
Bon .you are very intelligent gentlemen. Iam behind you❤❤❤❤❤
@BenedictFriday-c2w
@BenedictFriday-c2w 24 дня назад
The DC keep it up the good work
@DollarChagamba
@DollarChagamba Месяц назад
Palibe fuso lomwe lawakanika kuyankha
@user-bi5lg8mg9y
@user-bi5lg8mg9y Месяц назад
Mr Bon kalindo z very strong weapon speech
@StanleyDama
@StanleyDama Месяц назад
Do y know the meaning of weapon ?
@SteveniBanda
@SteveniBanda Месяц назад
❤❤❤ 1277 kkkkkk
@SteveniBanda
@SteveniBanda Месяц назад
Gwira chito kalindo 😂😂😂😂 kuswa kuswa kung'alura kung'alura😂😂 tiyenawo osawasiya😂😂
@ChipanganoPhiri
@ChipanganoPhiri 24 дня назад
Big boss
@user-rb7mp3rv7g
@user-rb7mp3rv7g Месяц назад
Pamenepa mafunso ovuta alipati please ma topic anuwa tamaonani Kaye aaaa😂😂
@martinndawala8125
@martinndawala8125 Месяц назад
Amangofuna anthu akhale ndi chidwi chowonera 😂😂
@HanishKenneth
@HanishKenneth Месяц назад
Kutchaya kugwetsa we are united
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju Месяц назад
The DC🔥🔥🔥🔥🔥🔥MRA sikuganizira ife ochita malonga...in add off kubweretsa sticker ndi njira imodxi yofuna kusokoneza ife a business kuti tisamapindule ...Boma lionepo bwino apa....
@PetroGondwe
@PetroGondwe Месяц назад
Kalindo is a true light to Malawian paths.youths wake up please,osamangovina amapiano fight for your nation and your future.
@aubreyvisuals2416
@aubreyvisuals2416 Месяц назад
Kkkkkkk ati amapiano 😅
@daviebanda5098
@daviebanda5098 Месяц назад
Kkk akut amathamanga ndimasuti😂😂😂😂 booom the DC🔥🔥🔥
@AronZayaweh
@AronZayaweh Месяц назад
Masiku atha kale awaa chakwela abwelele kudambw
@UssenNjirinah
@UssenNjirinah Месяц назад
Kkkkkk mpaka pele ajawuleje kudambwe Kwene chinyago changatama ku state house chijaule kwawo kwawo kudambwe
@user-dl4ud7mp4n
@user-dl4ud7mp4n Месяц назад
😂😂😂😂😂
@user-fd1tu6ku1r
@user-fd1tu6ku1r Месяц назад
Mr Chikangawa akutitola kwambiri
@PatYøna
@PatYøna Месяц назад
Yesterday I saw achinyamata akulemba anthu a kwa tongole in area24, ndinafusa modzi wa Iwo anati atumidwa kuti alembe anthu osati obwera but amagazi ... Kuti adzilandira ntukula pakhomo every month and fertilizer. But onse ogula malo ayi asamulembe. Is this fair abale inuuuu 😢😢😢
@PastinaHope
@PastinaHope Месяц назад
Tikuthoza kwambir a bon karindu pa zime mpatipangira ife osauka mulungu akhare ND Inu nose ❤❤🎉
@FrancisMbwana-z5l
@FrancisMbwana-z5l 29 дней назад
Very powerful from kalindo
@DysonChiumia
@DysonChiumia Месяц назад
The DC🔥
@abdulsalammkwepu3321
@abdulsalammkwepu3321 Месяц назад
The DC🔥🔥🔥🔥
@EffordKapichi
@EffordKapichi Месяц назад
You are our weapon chief
@user-ee1ci2ku6o
@user-ee1ci2ku6o Месяц назад
We are frant of you mr kalindo DC 💪💪💪💪
@KimuIbrahim
@KimuIbrahim Месяц назад
Kalindo woye
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi Месяц назад
Kalindo ndinkamuna ogona kukhomo kosachinjika abro 🔥🔥🔥🔥 Yehova apilile kumusunga ndimoyo wautali
@YamikanipilatoPilato
@YamikanipilatoPilato Месяц назад
Number one chi dc
@BlessingsNyirenda-ru7ss
@BlessingsNyirenda-ru7ss Месяц назад
More fire born kalindo
@williammasiano1194
@williammasiano1194 Месяц назад
Viva Malawi 1st ...eish anthu amafika potopa
@emmanuelmuyilaa
@emmanuelmuyilaa Месяц назад
Koma kumeneko❤
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Месяц назад
Kumpoto kumwera tikuoneka ngati sindife amalawi. Koma achigawo chapakati ndi a Malawian. Kumupoto kulibe chilichose i love you Mr DC and your members mademo alhalepo tikufuna chilungamo si nkhondo koma kukoza ziko lathu
@JonathanHeadson
@JonathanHeadson Месяц назад
Mafunso akeso ati ovutawo nanu
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 Месяц назад
Kuchokera 2020 mupaka pano chimene tapidula ndibomali kukumangidwa boza kulankhula mozikona kulekerera muchitidwe wa katangale kulembana pamutundu ntchito kuononga immigration kuononga ACB kuononga admac kuononga apolice kuononga nkhalango ya chikangawo po gwesako ndege kuononga nrb kuononga chipani cha utm kusunga nduna zachiwewe muchipani zopanda phindu. Ndizina zambiri zaonongeka kumalawi ndichitukuko chimene talandila kumalawi for 4years mmmm
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 Месяц назад
Stima yayamba kubweretsa mafuta sidaone
@isaacthawani5442
@isaacthawani5442 Месяц назад
Ndie awa akut mafuso ovuta mene akuyakhiramo sukuona kt dola ndi kalindoyo mbuzi iwe
@FloridaMakwinja-eq2ek
@FloridaMakwinja-eq2ek Месяц назад
The DC moto wokhawokha
@ClementKawinga-ik7wn
@ClementKawinga-ik7wn Месяц назад
Chakwera bomaaaaaaaa palibenso amene ndikumuona basi ndi Lazarus
@DonPhiri-u2j
@DonPhiri-u2j Месяц назад
Ife tikungodikira mulungu atithandize coz ulosi wa malemu grace chinga unanena kale kuli kuti kukubwera chipani cholimbana ndi mwazi komaso thukuta kma mukamaliza zonsezi muziwe kuti mulungu achitapo mbali yake ife tikuyembekeza pamulungu osati munthu amen
@PeturosiNyirenda
@PeturosiNyirenda Месяц назад
😂 bon kalinda nd 1🎉
@PropeeLucious
@PropeeLucious Месяц назад
Ndati ndikuuze I kuti bon kalindo akupusisani eye ndi ganyu imeneyi please please achinyamata musamangotenga ndizina zili zonse mtambo anakunamizan pano ndi bon kalindo please changamuka achinyamata mmalo mosaka ndalama kuti moyo wanu usithe muli busy kuchemelera munthu wina mmmmmmm
@SalaJawali
@SalaJawali Месяц назад
Utiuza zopusa zo ife tilibe Maso owonela kuti dziko muno zinthu sizilibwino
@robenallie6985
@robenallie6985 Месяц назад
Iwe ndi wa mcp
@SharonNdadza
@SharonNdadza Месяц назад
Nawe akupasa a mcp ndrama? Chonsechonso azimbuyanu akuvutika mma midzi uko
@PropeeLucious
@PropeeLucious Месяц назад
@@SharonNdadza ndye zoyankhula za kalindo zipangisa kuti ambuye asavutike mmmmmmm mbuli za kalindo muzafa chifukwa chosatilq zinthu zopusa ngt zimenezo
@PropeeLucious
@PropeeLucious Месяц назад
@@SalaJawali iwe ndye kalindo ndi amene angasithe zinthu musanamizidwe kuti kape ngt amene uja palibe chimene angaphule
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Kalindo ndi wa DDP chonde a Malawi musapuse naye akudya ndalama za peter anapatsidwa target
@SharonNdadza
@SharonNdadza Месяц назад
Muli ndi umboni?
@MadalitsoChipangula-i3z
@MadalitsoChipangula-i3z Месяц назад
Mwana uvuta kwambiri the Dc zimenezi ndizo zofunika kwambiri kunokwanthu kumalawi
@stevenbanda6665
@stevenbanda6665 Месяц назад
More fire bon
@jamessingini-fh1bz
@jamessingini-fh1bz Месяц назад
I cant wait pa 8 August ,bravo team Dc❤
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy Месяц назад
The DC ❤❤
@ChikondiMaguza
@ChikondiMaguza Месяц назад
Am coming to join u guyz❤
@TachikoMwanamanga
@TachikoMwanamanga Месяц назад
The DC 🔥🔥❤️
@PeterChilombo-ou2cd
@PeterChilombo-ou2cd Месяц назад
zoonadi atipeza kale kuno 25
@OMEXTWAIBU
@OMEXTWAIBU Месяц назад
Chakwela my vote ❤
@HiAlvin
@HiAlvin Месяц назад
DC awavula Ngati anadya ndalama akabweze alephera kufusa
@RasLuntha
@RasLuntha 28 дней назад
We must fight for our rebarty and freedom
@mkupabanda-nd2vb
@mkupabanda-nd2vb Месяц назад
Mafunso onse ayankhidwa, what else do u want?
@TanazioUziyele
@TanazioUziyele Месяц назад
Aaa akalindo ndale
@Atheeeefire
@Atheeeefire Месяц назад
Respect the DC keep the fire burning
@user-eo2hl9ug1h
@user-eo2hl9ug1h Месяц назад
Muyende..bwino...Isha. Allah
@COSMASSDAVITY
@COSMASSDAVITY Месяц назад
D.C MWANA OVUTA NDIWE NYO😂❤
@MercyJohnsonkanchure
@MercyJohnsonkanchure Месяц назад
Mr DC ulemu wanu kuti yimilira Amalawi
@evalisterphiri8435
@evalisterphiri8435 Месяц назад
This is true, ma profit ndiochepa kale koma BOMA ili palipose utulutse ndalama and now this mmm.... Mademo akufunikadi
@user-ik5sz8hc6f
@user-ik5sz8hc6f Месяц назад
Komano bon kalindo wawayankha bwino.Lopanda nzeru ndiboma ndiutsogoleri omwe ulipoli.Pa 8 go konko
@user-sm4vo2uo7g
@user-sm4vo2uo7g Месяц назад
The dc mwana wachabe
@DanJohn-ws5gl
@DanJohn-ws5gl Месяц назад
Mbambande the DC
@user-oe3dz7dy4j
@user-oe3dz7dy4j Месяц назад
Zoona amacharger ndarama popereka chidindo,,, your true fighter kalindo
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c Месяц назад
Born kalindo respect big up
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Месяц назад
Ife tikudikila pa 8 pano ✊💪✊
@serakillo8668
@serakillo8668 Месяц назад
Born ❤❤❤ ndi one guys timakufirani abro❤❤❤
@MagunjeNewa
@MagunjeNewa Месяц назад
Mr Born kalindo hoyeee
@user-ri8em6my2e
@user-ri8em6my2e Месяц назад
Bon tiwomboleni asatana amenewa asatibere chonde 😭😭
@user-pe2tu1ip3v
@user-pe2tu1ip3v Месяц назад
Good news ❤good work
@WillmotChiuimia-vr6ou
@WillmotChiuimia-vr6ou Месяц назад
Yes , kuyankha kwabwino ndinthu mmm ndikanapanga nawo mademo amenewo yes yes
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m Месяц назад
The DC ❤❤❤❤❤
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Месяц назад
Mulungu akusungeni ndi moyo gays wina aliyese ukumba zenje pa inuyo agwelemo yekha mudzina la yesu
@RobertChisenga-ci2mq
@RobertChisenga-ci2mq Месяц назад
I wish bon kalindo azakhere minister of the land Kaya zikhare ng,oma mai yolam kukuyu Azakhara mwaufumu muno kaya.
@heartilygarven2624
@heartilygarven2624 Месяц назад
Ulemu wanu Mr DC kuyankha mopanda nkhawa
@estherkachingwe3605
@estherkachingwe3605 Месяц назад
God bless you Mr Bon kalindo
@PeterChuma-jr1vz
@PeterChuma-jr1vz Месяц назад
Atolankhani agonja kunooo kkkk kuyankha mosaopa
@AgnessKavalo
@AgnessKavalo Месяц назад
Kkkk komatu bon kalindo amathamanga ali mu suit 😂😂😂😂😂😂😂 koma mdaseka mokweza mau 😂😂😂
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Месяц назад
The DC president wa anthu osawuka 💪✊ we always with you
@smartselemani2070
@smartselemani2070 Месяц назад
Sweet talk with hidden agenda.
@InnocentMtafya
@InnocentMtafya Месяц назад
Ambwiyee !!! Mafunso afunsidwa ndimayembekezela zachabe ,koma ambwiyeee!!!
@GiftSoko-w4h
@GiftSoko-w4h Месяц назад
KATUNDU BOOOOOOOOON KALIIIIIIINDOOOOOOOOO LOVE YOU MY GUY
@GladsonBanda-m3e
@GladsonBanda-m3e Месяц назад
Apresitent chamba chilitho nkumati tikuimira anthu kumangadi zingongo you should read as an example kalindo
@Littlefair7
@Littlefair7 Месяц назад
Atolankhani aku malawi ndi mbola, amafunsa zopepera kwambiri. Utolankhani weni weni unapita ndi achina Eunice Chipangula osati izi zathovwa.
@Agin2pex-ms3di
@Agin2pex-ms3di Месяц назад
Buka matevu 🎉
@IanAllstal
@IanAllstal Месяц назад
Kodi kalindo umkachedwa ndi ma drama chifukwa chani? The D C 🔥🔥🔥
@macksonmkandawire5718
@macksonmkandawire5718 10 дней назад
Bon kalindo kkkk make ndi vice president sopano
@user-ii6lu1wy5f
@user-ii6lu1wy5f Месяц назад
We are with you Mr DC
@GreenBadani
@GreenBadani Месяц назад
💪👍💞
@innocentmusuli7380
@innocentmusuli7380 Месяц назад
Mongo bwereza zomwe ndakhala ndikunena kuti any time, any day, any week, any month from now achinyamata azuka ndikuchosa nyasi zonse belive this
@MaloneBanda
@MaloneBanda Месяц назад
Good work 💥💥💥💥
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh Месяц назад
Akalindo ayaluka mademowo kumwela Koko
@user-rk4ch1ly3z
@user-rk4ch1ly3z Месяц назад
Achina kalindo ndiakamuna osati masewela.
@isaacharoon5652
@isaacharoon5652 Месяц назад
Kalindo akuchita bwino,komano kwa anthu amene amaononga zinthu za anthu,inuyo a kalindo anthuo muzawalipila,chifukwa anthu akuba amalowelela.simutisaukisaaaaaa?
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 Месяц назад
Chokani apa inu mulibe strategy iliyonse other than mademo. Don’t worry tikakufinyani konko
@MarthaBango
@MarthaBango Месяц назад
😂😂😂😂😂iiIi ati masuti kothamanga😂😂
@DoulassSamuel
@DoulassSamuel Месяц назад
Iweyo born ukungofuna udindo usatinyasepoapa
@LucyTatianahChikwekwe
@LucyTatianahChikwekwe Месяц назад
More fire 🔥🔥🔥 the DC
@TANMBWANA
@TANMBWANA Месяц назад
Mr chikangawa zawavuta
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs Месяц назад
Dc 🔥🔥🔥
@MarthaMalopa-kw9xw
@MarthaMalopa-kw9xw Месяц назад
Pali funso lomwe lalepheredwa kuyankhidwa apa?
Далее
ПРОСТИ МЕНЯ, АСХАБ ТАМАЕВ
32:44
Просмотров 2,3 млн
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BON KALINDO
59:52
Просмотров 86 тыс.
FREDO MASINTHA
12:07
Просмотров 4,3 тыс.
Saulos Chilima press briefing; 1 July 2022
16:56
Просмотров 64 тыс.
BON KALINDO KUNG'ALULA MWA NYOO!! 5 September 2024
43:54
HOT CURRENT KUNG'ALULA MOSAONA NKHOPE 1 September 2024
55:12