Lets look into this lady not the party. She is a real woman with love and passion for people. We need more ladies like her in Malawi for a change. I just love her. U will win in your constituency wherever you will stand and will help you win. Keep up the love ❤
From the conversation, Abida isa hard working and so passionate about what she wants to achieve. She can inspire many women in the country. All the best madam Mia. As for Brian, munadekha bwinotu , Excellent conversation.
You can be a good member of the church but if the church that you belong to mbili yake ndi apuse apuse God needs Children and The pastor wanu akhale oipa nkhosazo zimanka zikumayamwila khalidwe loipa la leadership wao...May the good spirit open her mind kut mwina achoke mu church icho akalowe mpingo wina abusawo asayende nawo limodz..that's my opinion nkupanda nzelu kwangaku
Ndakuponyerani kamtengo mai .kufotokoza zomveka beyond mere politics but true servant leader .mwafokoza bwino ndithu za kuunduna wanu,ntchito yanu ku constituency ndi magwilitsidwe a constituency fund, kuthandizira fundraising kudzera ku ma donors ena hence complementing government efforts.mwandifotokozeranso bwino about global economic challenges and the position as of Malawi.Wina asaname kuti adzabwera miracle kuthetsa mavuto apart from efforts currently being done under the servant leadership of Dr.L.M Chakwera mothandizidea ndi nduna ngati inu Mai.Mulungu Allah akhale nanu ndi kuchulukitsa madalitso anu kuti satana achite manyazi.
Yakhulani zokomela anthu ankombezi palibe chomwe anthu akupindula pa uphungu wa Abida mwini wake Mia akayesesa mai awa chilungamo chikuwavuta anthu akuvitika ku chikwawa nkombezi zioneka 2025
Banja la sidik ndi labwino, koma chifukwa cha kulowa ndale sizili bwino! Maka nthawi imeneyi ya chakwera, onani mene akupangira ndi aluya? Maiwa akanasiya kufuna mpando umeneu wa wachiwiri kwa vc president,amuna ao ali kuti,akanango khala phungu basi