Great work guys, I am following from Zimbabwe. Can you add English subtitles so that those who doesn't understand Chichewa can enjoy as well. Keep up the good work.
koma Chemandota ndi Morgen mukanakhala mapasa ine nkanasiya kubereka, kkkkkkkk. Kankhani, plz keep it up you have a God given gift umaoneka serious, kkkkkkkkkkk. langizo langa kwa Chemandota ndi Morgen 'Kankhaniyu akutoperani!' Warm love guys.
Big bro inu mumatha ndipo But please man may you remix your episodes in one disc kut anthu athe kumawonera pa nkhomo mma weekend mu Zitha kukhalat zinthu zokongola kuwonera pa banja izi!! May Allah bless you brother