Тёмный

Malawi Ayikanila Ngongole Ku IMF 

Malawi Extra
Подписаться 11 тыс.
Просмотров 3 тыс.
50% 1

Khalani nafe pano pamene tikukupatsirani nkhani mwatsatanetsatane zomwe Zikuchitika mu dziko la Malawi - Nkhani Kuchokela Ku Times Tv

Опубликовано:

 

12 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 16   
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 19 дней назад
Chipani chongodalira ngongole basi palibe chomwe mukuchita
@princekaponda
@princekaponda 19 дней назад
Mumatolela zokwanila .... Koma mumabapo kwambiri ... Mudzingowa phinja amalawi ndimisokhoyo
@TenoPop5-cl4zt
@TenoPop5-cl4zt 19 дней назад
Very good. Let them hold the funds until after the elections. Angabe komaliza apumbwa amenewo. Shame on you
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 19 дней назад
Mmmmmm Kuba kuli thooooo mbuli
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 19 дней назад
muziba bwino zigawenga za anthu mbava uzitolera kumapwalako
@KnowledgecGodwin-xo4pw
@KnowledgecGodwin-xo4pw 19 дней назад
Boma lomangokongola palibe chanzeru ma transport okamusakila bakili muluzi tv nditanyiwa apanga bwino kukukanizani agalu inu
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 19 дней назад
tikufuna lipoti la chikangawa iwe kunkuyu ndichigawenga chakwera asatana inu
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 19 дней назад
Mmesa munampha chilima mizimu ya 9 ikupwetekani muwona
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 19 дней назад
Minister of finance kkkkkk the face
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin 19 дней назад
Achita bwino kukaniza Zimatibweletsela mavuto kuno Ngongole zanuzo, Aziti mukwatilane akazi/ amuna okhaokha, Zatikwana ife zimenezo
@davidkadyakapita8836
@davidkadyakapita8836 19 дней назад
Achita kukunidwa ngongole .Ndalama zikungothera mmatumba mwa andale basi zochita sowe. Ma salaries m boma adakalibe ofoila,mankhwala mulibe mzipatala,anthu akugona ndi njala.Kumatupa ndithu kusowa zakudya matupi.Mapwala anu mwamva.
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 19 дней назад
Aaaaaa akumkuyu kodi khani ya arani witika ilipati muthu woipa iww
@FraserNyozan
@FraserNyozan 19 дней назад
Kkkkk
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 19 дней назад
Koma ndiye akukanirani inu nanuso kukumvutani kunena Chakwera kuba ndi kupha ndichomwe akuziwa basi
Далее
Running for Congress in a gerrymandered district
32:02
Просмотров 1,2 тыс.
УДОЧКА ЗА 1$ VS 10$ VS 100$!
22:41
Просмотров 337 тыс.
Nancy vs Che Nkope - Bambo a Sikono
10:36
Просмотров 7 тыс.
Exclusive Interview with Reverend Alexander Kambiri
30:56
EXCLUSIVE WITH MCCCI PRESIDENT DR WISELY PHIRI
55:47
Просмотров 1,4 тыс.
REPORT LA NDEGE LIJA MU CHICHEWA CHOMVEKA BWINO
2:18:14