Тёмный

Manganya Wabalalika (Kwagwanji) 

Malawian Cameras
Подписаться 28 тыс.
Просмотров 107 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

19 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 196   
@user-xy4hq6sx7v
@user-xy4hq6sx7v Месяц назад
Achita bwino kutuluka mu mgwilizano ine sindine wa utm ndinkasapota mcp koma mmm njoka ndi njoka singasinthe manga
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 Месяц назад
Ndiwe wabodza
@kumbukanchikosa8864
@kumbukanchikosa8864 Месяц назад
Mkulu ali pakati yo ndi wa boma😅 olo ndemanga zomwe akupeleka zikuonetsa
@SalimMeer-fk9do
@SalimMeer-fk9do Месяц назад
Honorable Njawala is the right person to take the mantle seconded by Akweni these people Genuine and they have the capacity to full fill chilimas vision
@user-xj6zr6wh8d
@user-xj6zr6wh8d Месяц назад
Which njawala? You dont know him
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em Месяц назад
Viva UTM viva, SKC rest in peace ,we shall remember u always
@AustinAllan-lh5ij
@AustinAllan-lh5ij Месяц назад
Of course am udf fan koma tiyamikile utm .mwina azindikilano ndizopweteka kuti tikulira kumatiuza kuti dziko tikulionela mu tintedi 😢amvekele anthu akumudzi sayenela kudya zamafuta ayi zikomo
@daviskamonde4882
@daviskamonde4882 Месяц назад
The best decision we have been waiting for from the idea.
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Месяц назад
Achita bwino kusiyana nadzo zigawenga dzamagazi mmanja 😢😢😅
@user-ls5zj8qn6k
@user-ls5zj8qn6k Месяц назад
Brian banda sadzateheka kkkk ❤your the best ever
@mathewsmakina7845
@mathewsmakina7845 Месяц назад
Bambo Banda Times Radio simamveka Kuno Ku Nsanje North kwamlolo kapena Kuti kufatima timaonera Times TV yokha siwonse amene alindi TV Kuno tayesetsani Kuti anthu azitha kumakumverani pa wires chonde tayesetsani
@MebleNgulinga-hi6rg
@MebleNgulinga-hi6rg Месяц назад
Good decision 👏 Awasiye okha akharemo okuphawo okha ndi mwaziwo mchipani mwawomo
@AlbertDuke-of9nn
@AlbertDuke-of9nn Месяц назад
up2 now sindikhulupilirabe kuti chilima anamwalira.
@MalawianCamera
@MalawianCamera Месяц назад
@@AlbertDuke-of9nn that's exactly what I feel it's unbelievable bro
@user-rl8xs2kf1o
@user-rl8xs2kf1o Месяц назад
Amuchita bwino manganya kuchenjera kuposa kalulu asova
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z Месяц назад
May GOD bless you guy's mumatha kuyankhula kopanda mantha
@WisdomPhiri-sh9we
@WisdomPhiri-sh9we Месяц назад
Actually with me here in Zambia l also observed the same basically on the death of SCK. Usi was not grieved with it and infact he was happy thinking that now will be given that opportunity of being VP.
@StainlyMunthali
@StainlyMunthali Месяц назад
Good move , so give yourself enough time to strategize . Next time put everything on paper and make it public kuchitila pa mawa .
@user-ez7th2rv7g
@user-ez7th2rv7g Месяц назад
Let's hope that there will be an improvement
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Месяц назад
Kkkkkk bamboo ache sikono agwira chimphwisi ndi manja kkkkkkkkkuona kuti utani
@user-lp8wj3vq4x
@user-lp8wj3vq4x Месяц назад
Kkkkk km ndiye chipwisi chipwisi.... kms ndimunthu oipa manganya
@chiccosuliwa
@chiccosuliwa Месяц назад
Ubwino wache azakhala ali pa pension mpaka kalee phindu lawo ndilimeneroo kkkk
@alexmanda5634
@alexmanda5634 Месяц назад
Loud and clear 🎉❤​@@chiccosuliwa
@omardyman8083
@omardyman8083 Месяц назад
Osaiwala pajatu munthu uja ndi mzimbabwe amene uja
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z Месяц назад
Kuchenjera mopusa usi
@user-ls4vy8mx9m
@user-ls4vy8mx9m Месяц назад
By coming out UTM it's a blessing in disguise some strong leaders will emerge
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel Месяц назад
Abrayani asangarara ngat avota palimbepo chingasunthe mcp apa
@user-uk3bz1hr5t
@user-uk3bz1hr5t Месяц назад
Koma mukuyankhura mosunthikatu 😂😂😂😂😂
@mathewsmakina7845
@mathewsmakina7845 Месяц назад
Usi ndiwa MCP nchifukwa anakaimila independent Ku chilimba ndiye muziti ndi wa UTM ayi sizoona ayi
@TonyN.Misoya
@TonyN.Misoya 29 дней назад
Akhaula amboo. Asikono😢😢😅😅kkkkkkkkk
@WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un
@WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un Месяц назад
Tiona wa UTM wenwen asizinatore ena viva Malawi 🎉🎉🎉
@AgnessKavalo
@AgnessKavalo Месяц назад
Apo manganya wagwiladi chiphwisi 😂😂😂😂
@davlinjuma6428
@davlinjuma6428 Месяц назад
The commentator in the middle is MCP operative
@youmad9087
@youmad9087 Месяц назад
Wrong. You are utm operative
@GraciamChopih
@GraciamChopih Месяц назад
Manganya ndiwa mcp and a chakwela anatenga wawo yemwe kumuika pa mpando wa u vp
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 Месяц назад
Tikunvera kwainu
@abisonchitukula6986
@abisonchitukula6986 Месяц назад
And Chilima appointed someone from MCP as his running mate and Vice President.
@davlinjuma6428
@davlinjuma6428 Месяц назад
Your analysis is domant, you got a barn
@OmexLyson-ub7kw
@OmexLyson-ub7kw Месяц назад
Kwagwanji program it's amazing
@paulvimbamvula9508
@paulvimbamvula9508 Месяц назад
We need unity, and Malawi 🇲🇼 then will not go further for we have division mindset
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg Месяц назад
😂😂😂 ndevu zamwayi ❤❤❤❤ chilungamo chilibho utm yaruphadi koma amayitsina mwakabisila kkkk
@mathewsmakina7845
@mathewsmakina7845 Месяц назад
Sanalakwe Mayi kaliati chifukwa atolankhani enanu mumatumidwa ndi MCP Kuti mudzikafunsa mafunso okomela Boma
@youmad9087
@youmad9087 Месяц назад
Kuganiza kombwambwana kumeneko. Funso ndi funso basi palibenso funso la opposition olo la boma
@ChrifordBiziel
@ChrifordBiziel Месяц назад
Stikuwopa komaso palimbe chowopsya apa
@EuniceKalilombe
@EuniceKalilombe Месяц назад
Chilima nali munthu onganiza bho,ife tikulira,kom anso ifa ya Chilima ikutiwawa. Ndipo tikufuna mayakho obveka bwino. A usi aaaaa timakayikira.
@StevenKaunda-p7g
@StevenKaunda-p7g Месяц назад
APM CHONDE MUTETEZENI KALIYATI IFE KUNO KU SA PLS MZIMAYI WAONESA DEMOCRACY IYU
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 Месяц назад
A chitsilu inu a DPP awatetezadi a kaliyati kma akungofuna adzawaolotse 2025 kma MCP will pass dziko lino kuli democrancy tiyeni pa ground
@alicehananiya
@alicehananiya Месяц назад
Za dziiiii​@@yowasschitsosa5348
@elizankankha84
@elizankankha84 Месяц назад
You guys ndie mumatiimilira 💯, keep it up
@emilynthite6545
@emilynthite6545 Месяц назад
A U T M aganiza bwino kwabasi
@MahallaMinistries-fv1hw
@MahallaMinistries-fv1hw Месяц назад
Atsukuluzi aafunika sharp glasses ngati nkutheka, I feel
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili Месяц назад
Apm May God bless u 2025 bomaaaaa
@RazackSongiso-i5m
@RazackSongiso-i5m Месяц назад
He is one of them that's why he was not there!!!!!
@JamesNalifu-wz2lu
@JamesNalifu-wz2lu Месяц назад
Amenewo lasukuliziwo ndalichosa ameneyo kuyambila lelo ndi wadyela ameneyo
@user-bz1bi8gp1k
@user-bz1bi8gp1k Месяц назад
kukhala ku chikamwini ndikulimba mtima UTM yapilila mzambili
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc Месяц назад
Good one
@JohnTchirati
@JohnTchirati Месяц назад
I salute UDM pothesa mgwirizano mwansanga kuchitira kuti alongole tsogolo la chipani chawo. Usi akuonekela poyere mu ma actions awo after the deceased
@Moses51
@Moses51 Месяц назад
Makendulo ayake until next year
@wilsonali7890
@wilsonali7890 Месяц назад
Manganya now in sinking ship 😂😂😂
@TamaraMhoni-jo9ow
@TamaraMhoni-jo9ow Месяц назад
Bola pangani zothekera Malawi alira mokwanira abale mmmmmmm puputani misozi yamalawi Mulungu akupaseni izeru zochuluka kopoas sinthena Malawi
@user-nd9cm3yl7e
@user-nd9cm3yl7e Месяц назад
Asabalike manganya 😊
@RodneyMKholopa
@RodneyMKholopa Месяц назад
Chosamva anachiphikira mmasamba
@JasonMailos
@JasonMailos Месяц назад
UTM ❤ that's very good
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg Месяц назад
Wakhala pakatiyo ndiwa mcp akundidabwitsa mayankhulidwe ake musamale mr mubookatu mmimba
@RodwellNkhanizamowa
@RodwellNkhanizamowa Месяц назад
Nde vuto ndichani?
@AllanBinali
@AllanBinali Месяц назад
Chosamva anachiphikila masamba, Chilungamo sanong'ona
@earthware2311
@earthware2311 Месяц назад
Komano MCP tiyembekezele kuti singazatengenso bomayi
@RabGaxman
@RabGaxman Месяц назад
Brian Banda ❤❤❤
@oviedoa.sidreck5170
@oviedoa.sidreck5170 Месяц назад
Andevu zamwai Sali mu good mood
@EarnestKazembe
@EarnestKazembe Месяц назад
Exactly they speak justice
@JoshuaMagodi
@JoshuaMagodi Месяц назад
Iye abalalika bwanji akuziwa chomwe anapanga asanzatu ameneyo chomwe iye anàdyacho
@LiamTennessee
@LiamTennessee Месяц назад
a UTM achitabwino kutuluka mu chinyengo chimenechi, 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Wina apenga misala,, palibe mwana wanzelu amene angapitilize ubale ndi anthu omwe anapha bamboo Ake,,this is what we call loyalty ,, ndiyamike kwambiri ndi kuthokoza Iwo Aku UTM chifukwa chopanga chiganizo Ichi, a Chakwera this is my message to you this is just the beginning of sorrow, hear me out ÑO amount of money will erase memories of the 9 souls you killed in chikangawa including that of kasambala in our lives as citizens of this country, and no amount of Dollars will serve you from the wrath of God,,and from the anger of Malawians,, you have just prooved this nation that you were,was ,is and will never be who you claimed to be,, Chaka Ichi muchimva ululu Ngati wanjoka,,and you are a witness of this since the 10th simuzapeza mtendere forget,it is my prayer that the living God expose you strip you naked so that Malawians will see the real you ,,
@SandraIssa-lo8il
@SandraIssa-lo8il Месяц назад
Very true, I used to be a die-hard of MCP, but after what happened on 10th May, mcp shall never see my vote in my entire life and that of my generation. MCP ndichipani chamagazi. Analakwa kwambiri, osangomutulutsa munthu kuchipani bwanji, koma mpakana kumupha, nkuphansi miximu 8 yosalakwa???? Ndipo anthu amenewa sadzapezanso mtendere ndipo mkwiyo wa Mulungu utsikire pa iwo, ngati simawa, mkuja next month or next-year, but one day, they shall be exposed and punished severe for their evil acts. That death hurts until now, and the spirit of chilima and those of departed will never rest until the truth shall vote to light out. Anthu oipitsitsa kwambiri. Mukwona ngati ino ndithawi ya Kamuzu eeeti? Mukanthidwa muona, athakati inu
@bahatimwakasole4899
@bahatimwakasole4899 Месяц назад
Manganya takes Malawians as his audience for his dramas all the time. It's difficult for a professional joker to totally conduct himself as a normal person at any given time. Even Chilima might have regretted afterwards, after he had appointed him as his VP
@dumisanimoyo3152
@dumisanimoyo3152 Месяц назад
Ngati achokamo nde kuti chakwera si Presidentiso iyayi
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 Месяц назад
Kkkkkk kani ndwe mbuli
@chachaamoah3592
@chachaamoah3592 Месяц назад
​@yowasschitsosa5348 .mbuli ndiwe pamenepo ndiye kuti boma palibe chifukwa anthu sitinavore Mcp tinavotera tonse alliance osati MCP chipani chakupha .atsogoleri ake alibe nzeru .nzeru zimene alinazo zakupha basi.anthu oipa nkhope ndi mtima yomwe😊
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 Месяц назад
Kkkkkk mkaz akachoka ekha panyumba busness yamamuna ingaime mphawi iwe odyela mundale udzafa osauka
@MoosahChikwakwa
@MoosahChikwakwa Месяц назад
😂😂😂😂 so you said manganya is hanging up without ladder 😂😂😂 you see usi this is what we call politics 😂😂😂 another point which touch me heart is, they must judge themselves why kids are dying?😂😂😂 Aaah now the question is, kubwalo la fiti kumakhala wamzeru?😂😂😂😂 Koma I think it's too late to say I'm sorry 😂😂😂 people have been crying for so long 😢😢😢 including the death of chilima and 8 others . From God we belong and to him we will be returning.
@AnnieBanda-rb2dk
@AnnieBanda-rb2dk Месяц назад
Nchifukwa chake galu chakwera anamumpha muzake chilima, amaopa mugwilizano wa 2025, asiyeni agalu a mcp akhale okha anthu akupha awo agalu
@atupeleumali9853
@atupeleumali9853 Месяц назад
Njoka ndi njoka....achita bwino kutuluka...
@SifatiMoses
@SifatiMoses Месяц назад
Sanalakwitse kutuluka mu chipani chakuphachi, manganya ndi mtira kuwiri uyu.
@JericoNkhoma
@JericoNkhoma Месяц назад
M C P ni fiti tu odya nyama za anthu
@iangondwe6857
@iangondwe6857 Месяц назад
chakwera alipheee thawi ina anaberedwapo ma vote
@NaphiChiwaya
@NaphiChiwaya Месяц назад
Good move utm I support them
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili Месяц назад
Kuthetsa mugwirizano wachita bwino kwambiri kakekake
@ManganiStanley
@ManganiStanley Месяц назад
Ine ndikufuna Mai Patricia kalitati to be a prezendent of thi party I will happy coz she is strong woman
@user-qp6hk3sn5k
@user-qp6hk3sn5k Месяц назад
Kutha kwa chipani uku
@bahatimwakasole4899
@bahatimwakasole4899 Месяц назад
Manganya was never grieved for the death of SKC.
@InnocentMedison
@InnocentMedison Месяц назад
Mbambande a UTM tilikoko
@youmad9087
@youmad9087 Месяц назад
Odya zake alibe mlandu
@hassammaulana4529
@hassammaulana4529 Месяц назад
Kuganiza kwa bwino koma plan B ya achakwela kutenga mr usi yapoira basi
@hastingsbalaleya
@hastingsbalaleya Месяц назад
Brian Banda Paja unawakwenya akajamu. Ku ngumbe iwe
@InnocentAssan-st3hb
@InnocentAssan-st3hb Месяц назад
Ussi he's not showing up as utm member we have all know that
@ruthkundwe7448
@ruthkundwe7448 Месяц назад
Akulu pitani mukatulukile ku chipani kwanu
@RaymondSalanga
@RaymondSalanga Месяц назад
Kodi sizingatheke kuti karongayi ikhale mbali ya Tanzania? Chonde tikupempha or else tikhale patokha
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z Месяц назад
Eee andevu za mwai mumatha kuyankhula ndipo chilungamo
@user-mf3re9gc2o
@user-mf3re9gc2o Месяц назад
I have told you that vote saponya mkamwa mwa ng'ona Za mumabango
@PeterChilombo-ou2cd
@PeterChilombo-ou2cd Месяц назад
iweyo wavaee ndiwe wa mcp
@MimuOmar
@MimuOmar Месяц назад
Kkkk koma m'busa uyu!!!!
@PaulRobertKamanga
@PaulRobertKamanga Месяц назад
Akukamba zoona most sapota ya utm amati anangosankha wawo yemwe
@OliverNkhoma
@OliverNkhoma Месяц назад
boma la mgwirizano latha kulibennso president
@kennethmagombo6934
@kennethmagombo6934 Месяц назад
Well and good
@ChristoneChilongo
@ChristoneChilongo Месяц назад
Eeee achita bwino azisiye ,Ng,ona,zo
@EarnestKazembe
@EarnestKazembe Месяц назад
Achita bwino kutuluka
@giftmlelembaphiri4897
@giftmlelembaphiri4897 Месяц назад
Njoka ilibe m'bale
@JOLAMNDODO-yo4wm
@JOLAMNDODO-yo4wm Месяц назад
No questions necessary here..
@IbrahimAdam-pb7rn
@IbrahimAdam-pb7rn Месяц назад
Musiyeni manganya Ndi moyo wake
@user-lr5bz7qk2d
@user-lr5bz7qk2d Месяц назад
Iwe utm sanalakwise manganya anachoka Kale kale
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di Месяц назад
Anthu inuyo 🔥🔥🔥🔥
@FatimaMsusa
@FatimaMsusa Месяц назад
Best move... Viva utm viva
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 Месяц назад
Yachita bwino utm ...sinalakwise
@DalitsoPhiri-sq5nl
@DalitsoPhiri-sq5nl Месяц назад
Let UTM be cz even SKC he's was already out from this alliance reason being zomwe anapanga pa u alliance sunakwanilisidwe
@jonas-xh4hz
@jonas-xh4hz Месяц назад
nkhaniyi ndi yabwino sibwino kumakakamila pakati pa mimbulu
@TifnessChembezi
@TifnessChembezi Месяц назад
😂😂😂😂😂😂
@user-yw6wt6jz9z
@user-yw6wt6jz9z Месяц назад
Good idea
@MosesShaibu-ee8hn
@MosesShaibu-ee8hn Месяц назад
KODI UTM NDIYAMASIYEPANO? NDIYAKHENI ABALEANGA😭😭😭😭😭
@user-lp8wj3vq4x
@user-lp8wj3vq4x Месяц назад
Pp ndiye chipani choipa abakhala komweko kwaanthu akumpha mfiti zokhazokha zimalizane
@user-mt5cu5se2p
@user-mt5cu5se2p Месяц назад
Tikuti kuli chiyakire😂😂
@RodneyMKholopa
@RodneyMKholopa Месяц назад
The truth is an offence but not a sin
@user-xb1re8dl3v
@user-xb1re8dl3v Месяц назад
Munthu yemwe anapeleka chilima ndi usi
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb Месяц назад
MCP yanyaaa... Mpamene mudziwe chomwe chidapangitsa bin laden kukabisala kunkhuti..
@Moses51
@Moses51 Месяц назад
Usi adayankhulepo ngati UTM president After death chilima
@louisbonongwe8537
@louisbonongwe8537 Месяц назад
He is a betrayal.kusinthanitsa.RIP SKC
@Moses51
@Moses51 Месяц назад
@@louisbonongwe8537 ankhako yenkha kumeneko ngati chidina
Далее
Meisjes van 12 en 14 opgepakt vanwege branden
3:25
Просмотров 10 тыс.
10 CHALLENGE ⚽️ CELINE vs MICHIEL vs BRAM
0:59
Просмотров 2,9 млн
TIKU 30 JUNE 2018 B
27:20
Просмотров 217 тыс.
Hulp stroomt toe voor afgebrande kerk in Epe
3:07
Просмотров 2 тыс.
TIKU 9 JULY 2016
27:20
Просмотров 135 тыс.
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH ENOCK CHIHANA
56:27
Просмотров 57 тыс.