Тёмный

Maria wa zaka 15 amalera azibale ake 

Rodwell Lumbe
Подписаться 17 тыс.
Просмотров 25 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 93   
@JackAluya
@JackAluya 15 дней назад
May God bless you beother mulungu akumbukile pantchito yabwino yomwe mukungwira
@victormwamadi2725
@victormwamadi2725 8 месяцев назад
You are doing great job my dear brother.❤❤️❤️
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 2 дня назад
Amene amapereka ganyu mulungu azipasa abwino chifukwa popanda nganyuyoso zovutaso
@saisonmwenda1275
@saisonmwenda1275 8 месяцев назад
God have mercy please Ana Ana kumaphala chochi makolo awo alimoyo zoona kumangoziwa kubeleka bansi afunika afunika chilango makoloso nawoso bushiri thandizani apa please 🙏 anawa awone kuwala pa town
@ShukranBatsonMitanga-wp3xp
@ShukranBatsonMitanga-wp3xp 8 месяцев назад
God bless you brother man it's not easy... Bambo wa anawa komwe aliko adziwe kut azawafuna anawa tsiku ndi limodzi Mulungu simunthu.. God bless you more
@MGgghu
@MGgghu 8 месяцев назад
I can't hold my tears 😭 moyo uyu ndiovuta guys ntchito mwaiamba achimwene
@AlnodBundi
@AlnodBundi 8 месяцев назад
Modzi wa zaka 14 ndtha kulera ine popanda vuto lilirose kulibwno ganyu ndkagwile ineyo
@kondwanimwangobora7696
@kondwanimwangobora7696 8 месяцев назад
😭😭🙌 God have mercy Keep up the good work brother man,God bless you moreeeee😭❤️🙏
@andrewjohnsiwinda7050
@andrewjohnsiwinda7050 23 дня назад
God bless u brathet
@Bonisiwentamo
@Bonisiwentamo 2 дня назад
Mulungu ndiwachifundo chonde azathu omwe muli ndikutheker chonde thandizani
@ellenphilimon
@ellenphilimon 5 месяцев назад
u are doing great job Rodwell continue
@EdwardGeorgeKasabola
@EdwardGeorgeKasabola Месяц назад
Eyiii😭😭😭😭koma Malawi ali pamabvuto azaoneni ndithu Ambuye atithandize
@issahamana
@issahamana 8 месяцев назад
😢😢😢😢 nkhani iyi yandikhuza mmoyo kwambili God have mercy
@vatineseduwin
@vatineseduwin 8 месяцев назад
anthunu tamabelekan ana oti muzitha kuwasamala kuzuza ana tu uku 😢😢
@Ngtokyo6594
@Ngtokyo6594 8 месяцев назад
Keep doing your job sir ..
@SteveMdalajunior
@SteveMdalajunior 8 месяцев назад
😢😢 there's God your tommorow will not the same that's my prayer
@IbrahimKarim-hw5ix
@IbrahimKarim-hw5ix 6 месяцев назад
Your doing a great job Rodwell
@giftblack7690
@giftblack7690 8 месяцев назад
😭😭😭 zosayenda mmmmm mulungu ndiwachifundo amapanga njila popanda njila
@ThoccoChiwangani
@ThoccoChiwangani 8 месяцев назад
Ambuye azindikhululukira chifukwa ndine osayamika kunjaku anthu akuvutika🤔
@EvelynLuka-s7o
@EvelynLuka-s7o 8 месяцев назад
God have mercy on them 🙏, end iyiyi idzakhala mbili yawo Mulungu asitha nyengo zako pompano
@BlessingJohnas-hu7lj
@BlessingJohnas-hu7lj 8 месяцев назад
Zomvesa chisoni kwambiri. Koma boma lizitha kutengapo mbali please kwa ana ovutika ngati amenewa.
@AllanBanda-t3u
@AllanBanda-t3u 8 месяцев назад
Pemphelo langa mulungu akanthe makolo oyipawo kulikose komwe aliko then adalitse anawa in the name of Jesus
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb Месяц назад
Kodi mukamapangisa ana ganyu kumakhala kuthandiza kapena kuzumza malo mongwapasa anawo koma mpaka mwana wang'ono akugwirileni ganyu anthu oipa
@Freedomchennl47
@Freedomchennl47 8 месяцев назад
Mulungu ayang'anilen ana amenewa
@raymondmwale3136
@raymondmwale3136 8 месяцев назад
Very sad. Ana azunzika
@Mphananso
@Mphananso 8 месяцев назад
Mmm ndagwetsa msozi 😢 kukhalila ana phala😢
@ISLAMICPUBLIC-d6l
@ISLAMICPUBLIC-d6l 8 месяцев назад
Mulimbikire bro
@theresachirwa4819
@theresachirwa4819 7 месяцев назад
Ndimomwe ndinakulila ine koma mulungu simunthu pano nduyendera galimoto but it's hard 😢😢😢😢
@manphiri2778
@manphiri2778 8 месяцев назад
Mamuna salila koma ine ndalila i feel the pain
@nerrcejngulube
@nerrcejngulube 8 месяцев назад
Mmmm yy walipanga musinjilo wapapi kuchimbila wana pawekha 🤔🤔😭😭
@EgitinaBanda-xs4yx
@EgitinaBanda-xs4yx 8 месяцев назад
Eeeish Lord hv mercy
@VioletMbale
@VioletMbale 2 месяца назад
Eish please God help
@ViyezgoMtika
@ViyezgoMtika 28 дней назад
Let's help these children please
@EvelynNsamala
@EvelynNsamala 7 месяцев назад
Anthu owapatsa ganyu anawa yakulira dish ija mpaka k50?kulakwatu ukuu
@essieDimba-wv2jn
@essieDimba-wv2jn 8 месяцев назад
God have mercy
@DamsonMcdonald
@DamsonMcdonald Месяц назад
Eish!!!!! So sad 😢😢😢😢😢
@agnessdaniel7592
@agnessdaniel7592 8 месяцев назад
Moyo uwu pena iiii 😪😥😥
@RabeccaMisheck
@RabeccaMisheck 5 месяцев назад
😭😭 mercy Lord
@TiongeKatuya
@TiongeKatuya 8 месяцев назад
I can't hold my teas
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op 8 месяцев назад
Eshii koma zovesa chisoni
@Mejanakwawa
@Mejanakwawa 8 месяцев назад
Mm zovesa chisoni 😂😂😂
@DroliiDongowa
@DroliiDongowa 8 месяцев назад
Makolo anji osaganizira ana
@MarthaChikosa
@MarthaChikosa 6 месяцев назад
Makolo, makolo chonde samalani ana iiiiiiiii ayi mmmm
@MtenjeHassan
@MtenjeHassan 8 месяцев назад
God have mercy..
@kedibonesegametsi2493
@kedibonesegametsi2493 6 месяцев назад
I can't believe this 😢😢
@theresachirwa4819
@theresachirwa4819 7 месяцев назад
Ine modzi wang'ono ndikhoza kulele ndikuziwa momwe akudutsa mwana because ndinadutsamo
@edgarmax-pi1bx
@edgarmax-pi1bx 8 месяцев назад
Utha kuyamba kuganiza kuti mulungu kuribe mwava iiiiii pomwe ena akutaya zakudya dziko lapasi iri
@NancyZiyaya
@NancyZiyaya 6 месяцев назад
Chisomo chiwafikile mmmm this is sad
@RaphiqueYusuf
@RaphiqueYusuf Месяц назад
Zonthu zomvetsa chisoni kwambiri.
@GetrudeLucius-bw6xd
@GetrudeLucius-bw6xd 8 месяцев назад
God have marcy on them
@mirriamwilliam-nq9wg
@mirriamwilliam-nq9wg 8 месяцев назад
Can't hold my tiers,,, mmmmm abale amipingo titengeko mbali
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb Месяц назад
Amzathu akumipando akugula galimoto dairy
@rachidermak8827
@rachidermak8827 7 месяцев назад
Nitumizeleni nanbala yanu bosi
@YamzyNedson
@YamzyNedson 8 месяцев назад
Eshhh💔 kom anawa akukhala moyo ovutika kwambili ndisaname nditaonela video yii ndalira mumtimamu Plz ku bomako athandizeni ganyu yomwe akugwirayoso mmmm ayi sizoona abale, We all human beings let's assist each other while we are still live.
@Adini-d2f
@Adini-d2f 8 месяцев назад
Boma likumaba ma billion ambilimbili andu kumafutika mulungu azalange ziku lomalisa😭😭😭
@KhestonWillow-gc1pe
@KhestonWillow-gc1pe 6 месяцев назад
Zofunikira ndithu
@alicehananiya
@alicehananiya 8 месяцев назад
Eee nkhani yomvesa chisoni kwambili kom adzimayi tikalandila chilango kwa mulungu chifukwa cha nkhadza kuzudza ana ngat wamwalila? Ayi ndithu
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo 2 месяца назад
Mulungu wanga khudzani banja ili kawapatsen chosowa chawo
@ShamilKumwembe
@ShamilKumwembe 6 месяцев назад
Mmmmm kulakwaaa😢
@NumbDee
@NumbDee 8 месяцев назад
Ndalira eish
@Stuartkachali45
@Stuartkachali45 8 месяцев назад
Nkhani yovetsa chisoni kwambiri😢😢😢😢😢
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 8 месяцев назад
Mavuto 😭😭😭
@GogoAdams
@GogoAdams 8 месяцев назад
Eeeeh dziko lampasi ana akuvutika yawa
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 8 месяцев назад
Ambuye Chitani chifundo💔💔
@esteryndau8546
@esteryndau8546 7 месяцев назад
K50 kwacha ingagule chani abale bolani hundred kwacha
@Doreen-r3w
@Doreen-r3w 8 месяцев назад
Zandkhuza kwambiri ndpo ndalira kwambiri ndakhuzika, anthu ena akusowa ana ,ena akusiya ana opezeka kale why god, mulungu chitanipo kanthu kwa ana awa yehova muwonesere ukulu wanu kut tikuziwen kuti inuyo ndi mulungu amene simulephera
@WalesKamoto
@WalesKamoto 8 месяцев назад
Nkhani yomvesa chisoni
@FelisterMvula-i6f
@FelisterMvula-i6f 8 месяцев назад
Zovetsa chisoni 😢😢😢😢
@wonganiKalima
@wonganiKalima 8 месяцев назад
Pena umaona ngat ukuvutika,koma ukaona azako💔😭... God have mercy
@MemoKadaleka-wc5nb
@MemoKadaleka-wc5nb 8 месяцев назад
God have mercy 😢😢
@NaduMbewe-zz6iw
@NaduMbewe-zz6iw 8 месяцев назад
Mmmmm zosaenda
@theresachirwa4819
@theresachirwa4819 7 месяцев назад
Misozi ingotuluka ine
@DysonDube
@DysonDube 8 месяцев назад
Koma ntchito yako aise eeeee
@SunshineNsengwa
@SunshineNsengwa 8 месяцев назад
Zosayendatu 💔
@mustafahaji2599
@mustafahaji2599 8 месяцев назад
Makoro ameneo ndizisiru
@HanifaTabia
@HanifaTabia 6 месяцев назад
Eshii zovuta
@JoabevasonMpinganjila
@JoabevasonMpinganjila 8 месяцев назад
❤❤
@LeahPhiri-l2u
@LeahPhiri-l2u 8 месяцев назад
Zomvetsa chisoni😢
@louisbonongwe8537
@louisbonongwe8537 8 месяцев назад
Misonzi mmaso mwanga.
@RodneyChagoma
@RodneyChagoma 8 месяцев назад
onions here
@AnnaPhiri-b8t
@AnnaPhiri-b8t 8 месяцев назад
Zomvetsa chisoni misozi ikungotuluta
@Maxwell-e2d
@Maxwell-e2d 8 месяцев назад
Eiiish 😭😭😭😭
@henripeetembo969
@henripeetembo969 8 месяцев назад
Ooh no😭🙏
@elijahmsesa8048
@elijahmsesa8048 8 месяцев назад
Sad 😔
@mavismmeta5955
@mavismmeta5955 8 месяцев назад
Eish so sad
@EvanceWame-v7v
@EvanceWame-v7v 8 месяцев назад
Makolo maganizidwe ngati mphaka
@yassinjanna9564
@yassinjanna9564 8 месяцев назад
Eeish
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 8 месяцев назад
Zachison😢
@hugaallan-yw8fi
@hugaallan-yw8fi 8 месяцев назад
Iiiiiiiiii abale inu
@AnastaziaJagali
@AnastaziaJagali 8 месяцев назад
Ine ndadutsa momwemu ndli ND zaka 4 kma mulungu sataya wake pano ndli ndi khomo lorozeka, ambuye akukuzani
@RoseDaudi-g8i
@RoseDaudi-g8i 8 месяцев назад
😭😭😭😭
@ANATHIMAKHAZI
@ANATHIMAKHAZI 8 месяцев назад
😢😢😢
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 8 месяцев назад
😢😢😢😢
Далее
Kangaude Kucheza ndi Mr god know Part 2
59:17
Просмотров 23 тыс.
CRUISE 5 with Deborah Mbale MAI MBAMBANDE
57:16
Просмотров 37 тыс.
Как не носить с собой вещи
00:31
Raped by my Sister's Husband
19:50
Просмотров 37 тыс.
Mphatso's Life Story
25:25
Просмотров 27 тыс.
My Worst Experience  While at Kamiti Maximum Prison
30:32
Banja la ana 4 aulumali osayenda komanso osalankhula
12:58
Как не носить с собой вещи
00:31