Тёмный
No video :(

MAU A MPHAVU A KAMLEPO KALUA WACHENJEZA BOMA PA ZOMWE ZIKUCHITIKA KWATENTHA 

Malawi Trends TV
Подписаться 39 тыс.
Просмотров 16 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

29 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 58   
@user-kf8pt6om6s
@user-kf8pt6om6s Месяц назад
Powerful message has been at the helm of bad history even life presidency was from there and this woman leading Parliament ali pa tsogolo kutsogolera zoipa.
@amoschataika7440
@amoschataika7440 Месяц назад
Zikhale sinthani chikhalidwe anthu asakhalire kukudandaula the whole Country. One day you will regret these words of Uncle Kamulepo. Mai Zikhale please speak to your Husband.
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 Месяц назад
Dont forget that he is a zimbabweani....toom much foreign nationals in malawi gvnmnt
@amoschataika7440
@amoschataika7440 Месяц назад
@@chippakaribafox2865 I second you. What agry and cruel Man.
@raytavares2256
@raytavares2256 Месяц назад
This man is talking as a father, a professional leader and a real Christian who has passion and love to his people and country. You can discern that he is venting his feelings from a pure, innocent heart without any guile or malicious slandering intentions. I hope our Christians brothers and sisters from the whole world will learn something from him concerning true love, integrity , respect and honesty with a loyal attitude. 😢
@MonijaKataika
@MonijaKataika Месяц назад
Voice of the anointed..If this country had people like you sir would hav been singing a new song in politics.. voice of peace with excellent approach.. may God bless you .
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Месяц назад
He was the one who start democracy in Malawi.he deserve to be respected
@troublemwanza8705
@troublemwanza8705 Месяц назад
You are speaking the truth Mr honourable Kamlepo kaluba
@MfipaKapwera
@MfipaKapwera Месяц назад
Wunenesko Mr Kalua A MEC wangaphalilanga wanthu vawuzeleza yayi if they have voices must cosult NRB not us.
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js Месяц назад
Thank you Homourable for speaking out,let this government not impose rules on people.May God help us to overcome this.
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm Месяц назад
Powerful 👊
@StewartMustafa
@StewartMustafa Месяц назад
U r our hope, coz u have bn there when u we were fighting against one party regime. So these pple should not take us back those days. This z our country
@user-si8eb2ub5s
@user-si8eb2ub5s Месяц назад
God is good all the time
@BrightNkhoma-xz4bg
@BrightNkhoma-xz4bg Месяц назад
Nduna kumadandaulidwa nde ukutanipo ..... Nduna ..........😢😢 Oipa tima everything
@LamieTiger
@LamieTiger Месяц назад
Salute Mr kamulepo
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 Месяц назад
Sakudziwani big, awuzeni ana akamuzu awa mimbulu
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js Месяц назад
Let God humble them all.Everyone is praying
@MosesTangwe
@MosesTangwe Месяц назад
This man is genuine he is true fighter 💪 ndipo that he said is powerful cause masankho akubwelawa azakhesa mwazi ochukula apo mkuyamba chabe, koma mulungu simunthu
@IssahAluba
@IssahAluba Месяц назад
MCP is going apdete true
@LuskaMoses
@LuskaMoses Месяц назад
Maona ngati matalauza adzasitha ntimatu😢
@DevisonHala
@DevisonHala Месяц назад
Tili ndi inu bwana chitanayeni akapume chakwera akutinyasa zochita zake
@user-yx6oo2pc3r
@user-yx6oo2pc3r Месяц назад
Yamanjayo ikhale basi chifukwa anthu abomawa sakunva ndipo akudzitenga ngati madolo. and chimene mungadziwe olemekezeka a Kamulepo simunthu wamba ai. mwina enanu simukudziwa. mundifunse ineyo mr Raphael Katimba za Kamulepo Kaluwa. Mr Kamulepo Kaluwa pamodzi ndi malemu Chakufwa Chihana ndi a Elson Bakili Muluzi kuphatikizapo ma Bishop a chikatolika. monga a James Chiona Archdiocese of Blantyre a Mukholi Chikwawa Diocese and Alani Chagwela Zomba Diocese and Alexander Asolari Mangochi Diocese and Ambuye Chisendela Dedza Diocese and Ambuye Chimole Lilongwe Diocese and a Bishop Zunza a Mzuzu Diocese kuphatikizapo a Chakufwa Chihana kuphatikizapo a Bakili Muluzi kuphatikizapo ndi anthu ena monga a Patrick Mbewe and Dr Ntafu and Dr Kasimu Chilumpha. Pakanapanda anthu awawa sibwenzi ku Malawi 🇲🇼 kuli Democracy ndipo ineyo ndi amene ndikudziwa zimenezi. enanu simumadziwa zimenezi . Kapena kuti kodi Malawi Congres Party ya Dr Hastings Kamuzu Banda inali yoopsya bwanji ? ndiye kuyambila lero ndikuchenjezeni a Malawi 🇲🇼 anzanga musamunvele Beni Longwe Kapena Redson Mulo Kapena a Malata chifukwa onsewa ndi ana sakudziwa kuti kodi chifukwa chiyani Dr H Kamuzu Banda ndichifukwa chiyani nthawi imeneyo anavomeleza kuti Democracy ibwele kuno ku Malawi 🇲🇼 panali zifukwa zimene Kamuzu anaķhutitsidwa nazo. ndipo chimene mungadziwe mungadziwe inuyo a Chakwela pamodzi ndi nduna zanu Kamuzu sanali munthu Kamuzu he was very educated president the whole Africa and Dr Kamuzu Banda he was not like you Chakwela you just coming from ubusa oweta mbuzi ndikudzakhala president wadziko ndichifukwa chake zonse zakuvutani pazaka 4 zimenezi even mwana wa std 1 akudziwa zimenezi kuli mwalephera ndipo inuyo muyenela kuvomeleza kuti mwalephela ndipo inuyodi ngati mumapempheladi choonadi ngatidi muli busa weniweni bwelani poyela ndipo muwauze a Malawi 🇲🇼 kuti ndavomeleza kulephela kwanga. tsopano tibwele ku ndale iweyo Chakwela sipresdent oyamba kulamulira mudziko lino ndipo mbuyo mwakomu mwapita ma president angapo amenenso amachita zanzelu kuposa zimene ukuchita galu iweyo.
@MIMIEZenga
@MIMIEZenga Месяц назад
Ziyakkulani chichewa tiziva bwino bwino
@user-rz9rm4cb8x
@user-rz9rm4cb8x Месяц назад
Waziwaa bwanj kut akuyankhula chizungu
@user-on2me8ek5w
@user-on2me8ek5w Месяц назад
Please ziyankhulaniko chichewa kut tonse tizimva nawo enafe sitinapite ku sch
@MonijaKataika
@MonijaKataika Месяц назад
Kkkkk ndasekatu ine
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf Месяц назад
Very powerful message.Akuterotu kuti no I'd no registration is it true?
@BrightNkhoma-xz4bg
@BrightNkhoma-xz4bg Месяц назад
Akuyamba zimbwana a Malawi electrical commission
@MayendaRichard
@MayendaRichard Месяц назад
Zoonadi
@SangwaniKawawa
@SangwaniKawawa Месяц назад
But one day is one day
@EliasKawuwa
@EliasKawuwa Месяц назад
Who has been killed? Why can't you concentrate on the reasons of your arrest? You should know that MCP soon will go,and next party will come in, and you will be there accusing it again,if you are not considered, like this Malawi will never develop, the only problem with us Malawians is that anything that happens to us ,we are quick to politicize it,when somewhere somehow we are the ones we are at wrong, Nooo ,we need to be subjective when we are doing things
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj Месяц назад
Zikhale ng'oma usamadzitenge ngati dolo kunalinso anzako pano ali kuti
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Месяц назад
Ndipo zikhale ziwa kuti tsiku ndilimodzi mbuzi ikakodwa amalonda Ali pafupi uzalila koma athu sazakivelani chisoni inu a mcp muzitenga ngati inuyo ma Dolo ndipo athu akukudandaulani usana ndi usiku
@user-fi7ko7bl6f
@user-fi7ko7bl6f Месяц назад
Tell them the Liyaya!😅😅😅
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Месяц назад
🙏🙏🙏🙏🙏🙏
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 Месяц назад
Sitilora za ma ID, Noooh
@SifatiMoses
@SifatiMoses Месяц назад
Pa nkhani ya ma lD angosiya kukamba chifukwa tingawatukwanepo apa, malamulo akuwadziwa bwino mene amakambira ngati awadyetsa apita nawo.
@elijahrambiki1149
@elijahrambiki1149 Месяц назад
Zimene ikupanga m23 ku DRC kuja ifeso titha kupanga chifukwa tatopano
@user-co3wr3rn4h
@user-co3wr3rn4h Месяц назад
Munthu mulala chomene wapakaya mcp chipani chankhanza
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb Месяц назад
Zimatheka banji kuipa khope ndi mtima omwe
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Месяц назад
Kuipa nkhope yachakwera ngat mkati mwake monse chakwerayo
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js Месяц назад
Tell them that Abels blood still speaks,what more with recent blood.
@MandalaChaona
@MandalaChaona Месяц назад
Ndipo ndizoona akulu akulu amenewa Zikhale, Kumkuyu , Chimwendo, Valentino ndi ena onse akuthedwa otchuka lero chifukwa chodziwa kupha. Mudzafa imfa yowawa . Mukudzudzulidwa koma simukufuna kuchepesa kuzunza ndi kupha Amalawi. La 40 lizakwana. Evil men
@MphatsoIshmaeladam
@MphatsoIshmaeladam Месяц назад
Kuli kulonga ufumu mmawa, kodi Zikhala ng'oma kapena music?kkkkkk azafa ngat mbudzi amalawi asukusula pano sitili mu 1960s
@BrightNkhoma-xz4bg
@BrightNkhoma-xz4bg Месяц назад
Azipeza atakula 😢
@JumanKanjala
@JumanKanjala Месяц назад
Koma awa ndi akatundu mayakhulidwe mwa dzelu ulem wan
@HassanJameskananjie
@HassanJameskananjie Месяц назад
Tiyeni tithibulane basi
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 Месяц назад
Munth ukakhal wabodz ngakhal tsik lina unene zoon Anth samakhulupirir iwe nthaw zambir umakond kukamb nkhan zabodz Paj udakazik pamseu utazimang ndilamb
@MdAli-ll2dj
@MdAli-ll2dj Месяц назад
Iweyo or manyasi ulibe 😮😮😮
@sweeneykamwendo6251
@sweeneykamwendo6251 Месяц назад
Well spoken Honorable Kalua
@stevenfrancism3638
@stevenfrancism3638 Месяц назад
Gwape iwe.
@MdAli-ll2dj
@MdAli-ll2dj Месяц назад
@@stevenfrancism3638 😋😋😋😋😋😋😋😋🤑🤑🤑🤑🤑🤑👊
@user-rz9rm4cb8x
@user-rz9rm4cb8x Месяц назад
Iwe ndi kanyimbi wakhuta ma leftovers a chakwera
@JohnAsendi
@JohnAsendi Месяц назад
Pomwe a yankhula ameki a zipani zosusa muyambire pomwepo kuzuzula inu musamago e tulo ngati mbuli
Далее
Bishop Jacob Wamwea guborwo mbeca ciake ciothe ni mikora
1:08:46
Where Did Cain's Wife Come From?
40:16
Просмотров 689 тыс.