Тёмный

MCP YAONA ZAKUDA LERO PA HOME PAWO - BEN PHIRI, CHISALE,STAMBULI NDI RG 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 63 тыс.
Просмотров 4,5 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

12 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 65   
@ChristmasChapeta
@ChristmasChapeta Час назад
Chisakho chingochitika poti malamulo Koma boma labwelera kwawo Ku DPP Tinangopita Ku holiday
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 24 минуты назад
Pa home ground patelera kkkkkkkkkkk akumva bwanji chimwendo 😂😂😂😂😂
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 часа назад
Boma ilooo always blues 💙💙💙💙
@ZimMlw
@ZimMlw Час назад
Chipani changa ichi❤❤❤ love you dpp
@VAILETBANDA-t1g
@VAILETBANDA-t1g Час назад
Chisale mphamvu kuchipani ipase moto
@IshmaelJerard-u9w
@IshmaelJerard-u9w 44 минуты назад
Apm my vote❤
@WhiteRichard-cw2fo
@WhiteRichard-cw2fo Час назад
DPP my vote 💙💙💙💙💙 chipani chokondedwa kwambiri ndi athu
@OsmanYusuf-u1v
@OsmanYusuf-u1v 27 минут назад
Sameer Suleman ndi chisale eishiiiii team iyiyi ibudula mpunga wa mcp 2025 adad motoooooo
@StanleyChabwera
@StanleyChabwera Час назад
Bwana chakwela tangositsani zithu zokomela athu akumudzi fetrizer chakudya zipangizo zaulimi...sugar athu midzimu aziphika kachasu ana azipita ku xool.....please boss
@LongweLeya
@LongweLeya Час назад
Vote yanga ili ku DPP basi ena awa anabwelela ku njoyaaaa
@rashidadan2533
@rashidadan2533 52 минуты назад
Mopempha DPP , mavuto omwe ali kumalawikuno pofunika tsiku lina kuzayasa kandulo , Chifukwa muli uthenga
@VAILETBANDA-t1g
@VAILETBANDA-t1g Час назад
Chisale usazafe ambuye akupase moyo kulindisa chipani
@MonicaSteve-t5p
@MonicaSteve-t5p 37 минут назад
DPP woyee boma ilo lokomela aliyese❤❤
@DoreenLivata
@DoreenLivata Час назад
Dpp woyeee 💙💙kma ndaseka tikuchedwa kuvota
@MustapherLino
@MustapherLino Час назад
Dpp woyeeeee Peter mutharika woyeeeee 😂😂😂😂 ipatse moto
@FelixMwakhula-cm2yy
@FelixMwakhula-cm2yy Час назад
Central region ija DPP has indeed penetrated next MCP ikupitadi kwao
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 11 минут назад
Dpp imuotcha machende Chakwera
@FatimaAdam-r5y
@FatimaAdam-r5y 55 минут назад
Chakwela akomoka ndithuuu❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@PraiseKawerama
@PraiseKawerama Час назад
Big up home boy Ben phiri
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza Час назад
Ma blues woyeeeee boma iloooooooh❤❤
@JumatayaDavie
@JumatayaDavie 2 часа назад
DPP kuswakuswa
@NicolasKamunga-rv9vr
@NicolasKamunga-rv9vr Час назад
Tambara agwidwa pakhosi 2025
@DominicYohane
@DominicYohane Час назад
Ndimaona ngat mwachita kuwabukatu anthuwa.
@FrancisKaliwo
@FrancisKaliwo 2 часа назад
Ben phiri ndi akatundu DPP mumatha bravo
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Час назад
🔥🔥🔥🔥💕
@michaelchimwala-x8t
@michaelchimwala-x8t Час назад
Mbuzi achakwera
@LongweLeya
@LongweLeya Час назад
Kuti buuuuuu🎊🎊🎊🎊🎊🎊🎊DPP OYEEEEEEE
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 Час назад
Zoona aboma analikuti,mphekesela itayamba kuti atiwoze zoona???
@MercyKziphondo
@MercyKziphondo 2 часа назад
Apm my vote
@pilirani3536
@pilirani3536 2 часа назад
Adad omwewo oyéeée
@GeorgeBanda-x6l
@GeorgeBanda-x6l 2 часа назад
❤❤ ipondeni fader pa home ground kufa ndi imodzi
@FlengieAustin
@FlengieAustin Час назад
Dpp woyeeeee😂😂😂😂😂
@MlaziJames
@MlaziJames Час назад
Dpp moto ❤
@Anni00Zungu
@Anni00Zungu 2 часа назад
Am proud of DPP Always more fire my party
@InnocentHassan-m3r
@InnocentHassan-m3r Час назад
DPP mumakwana
@ZioneMkangadzula
@ZioneMkangadzula 2 часа назад
ndarama zaconvid iwe zilikuti zachikima isakhare kampena
@FuloseMwalibwe
@FuloseMwalibwe 2 часа назад
Dpp iripo kulilongwe woyeeee
@memoryziyaya2593
@memoryziyaya2593 2 часа назад
nzomwe mkuonasatu eee koma
@StanleyChabwera
@StanleyChabwera Час назад
Mukumva bwanji pa home pano.....kkkkkk
@PhillipLucky
@PhillipLucky 25 минут назад
Dpp yomweyooooo kut wawawa
@swadikimbwana7680
@swadikimbwana7680 2 часа назад
DPP ooyeeeee!!!!!!!!!!
@YusufuKaifa-r2y
@YusufuKaifa-r2y Час назад
❤❤❤❤
@StanleyChabwera
@StanleyChabwera Час назад
Pomwe pali athupo mpoponda pakuoneka?
@EnerstMkandala
@EnerstMkandala 2 часа назад
Koma ndizoona izi koma ndiye kwavuta,
@Janekapats
@Janekapats Час назад
Wina agwa ndi dphiphiituuuuuu eshhhh
@LawrenceMalinda
@LawrenceMalinda Час назад
DPP woyeeeee
@mathews1004
@mathews1004 2 часа назад
DPP ooooyeeee
@IsumailaAwalu
@IsumailaAwalu Час назад
@MathewsMilli
@MathewsMilli 2 часа назад
Ithyoke Ithyoke pano ndi pakwathu.
@IbrahimJackson-i8h
@IbrahimJackson-i8h Час назад
Kkkkk bandula
@CatherineChigudu
@CatherineChigudu 2 часа назад
Eyiii
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 2 часа назад
Boma ilooo❤❤❤❤❤
@SimbeyeSimbeye-z7l
@SimbeyeSimbeye-z7l Час назад
Apm boma
@lloydmalinga1198
@lloydmalinga1198 2 часа назад
Boma ilooo
@Catherinegondwe-r4l
@Catherinegondwe-r4l 2 часа назад
Boma iloo
@BeautyBlack-ls5pg
@BeautyBlack-ls5pg 2 часа назад
😂😂😂😂
@HappinessKapombeza-ut9mo
@HappinessKapombeza-ut9mo 2 часа назад
BOMA ndilomweli eti?
@AugustineChimaliro-e5i
@AugustineChimaliro-e5i 2 часа назад
Ndipo inu DPP my vote
@ZioneMkangadzula
@ZioneMkangadzula 2 часа назад
zazii iwe kamba mfundo
@KhumboNyerenda
@KhumboNyerenda Час назад
Muli ndinfundo ndinuyo
@Janekapats
@Janekapats Час назад
Ingomwa panadol wa extra uchiratu
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Час назад
​@@Janekapatskkkkk
@imranhabibu1743
@imranhabibu1743 Час назад
❤❤❤
@MartinKapito
@MartinKapito 2 часа назад
DPP woyeeeee
Далее
Which version is better?🎲
00:14
Просмотров 3,8 млн