Тёмный

Mfumukazi Comedy 01.3.23 

Malawi Lovers 🇲🇼
Подписаться 24 тыс.
Просмотров 49 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

15 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 49   
@IkilaMmeta
@IkilaMmeta 7 месяцев назад
Kd mfumu nkazi pena awonde pena anenepe bwanji kd 😅😅😅😅
@patriciamaunde
@patriciamaunde Год назад
Kom tu Gring, ande ndika handsome 😂😂😂😂
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 Год назад
Koma giling'ande 😂 mupakana Education is subject😂 program ya mfumu kazi giling'ande is the best for me 😂.
@kelvinkhudze6241
@kelvinkhudze6241 Год назад
Education is subject🤣🤣🤣🤣🤣 koma Giling'ande ndiovuta kkkjkk
@edythnamponya7701
@edythnamponya7701 Год назад
Tiing'alure🤣🤣Jameson ndi gututu
@isaacmussa2942
@isaacmussa2942 Год назад
😄😃😀😀 koma jemazoni watsitsa mphweya kkkkkkkk
@mussahdickson3538
@mussahdickson3538 Год назад
Mwayatsa moto koma taponyani ya 08 March 2023 mwatiiwaliratu
@piliranichikwapata349
@piliranichikwapata349 Год назад
Kkkkkkk koma gring,ande kkkkkkk
@williammoyenda7378
@williammoyenda7378 Год назад
Koma chaka chino makoloredwe ake tizikumba pasipo mwina chimangachi chiberekera pansi yellow munda onse shaaa koma ziliko
@jimmykutapa-rm5in
@jimmykutapa-rm5in Год назад
Mumakwana achipwanya
@bridgettembo-ir7px
@bridgettembo-ir7px Год назад
Kkkk apadera 😅😅
@lhordgowello688
@lhordgowello688 Год назад
Koma Gili ndiwe mbambande
@franciscoalexandre4168
@franciscoalexandre4168 Год назад
Namoyo 🔥 Moz🇲🇿
@ishmaelimranimenk9502
@ishmaelimranimenk9502 Год назад
Namoyo zikuoneka ngat ka jelas choncho....kkkk... guys osanama sindingasange nonsee mumandisangatsa;end nso phunziro lilipo ndithu maka lero:next tione chochita cha apadera kkk
@timothychipoka7201
@timothychipoka7201 Год назад
Zobeba, mathelo ake ndiotani plz? Zukhaka ngat Giling'ande wanyachula kkkkkkk
@lilianpenama3378
@lilianpenama3378 Год назад
Kkkk zilibwino kwambiri pitilizani takunyadira moto buuuuu.
@anniewhite3497
@anniewhite3497 Год назад
Kkkkk Apadera mukuonjeza apezerenidi chochita, Amfumukadzi muloleni Shoprite akuonekatu ngati wakukondani zenizeni😂 next gyz mumandimvetsa kukoma osaiwala chiphwanya ndi nzakeyo
@isaacmoses4602
@isaacmoses4602 Год назад
Education is subject 🤣🤣🤣🤣 koma Giring'ande.
@chifundomhango3324
@chifundomhango3324 Год назад
Mr Shoprite sopano kulengeza koyamba 😂😂😂😂😂😂
@edythnamponya7701
@edythnamponya7701 Год назад
Akuti education is subject
@promisemakawa1556
@promisemakawa1556 Год назад
Iyiyi inali bwino kwambiri kusiyana ndi 2wks yapitayi, keep up, pitilizan kutisangalatsa
@tanyaradzwamadhlopa107
@tanyaradzwamadhlopa107 Год назад
DC kkkkkk naye wayamba kulengeza kkkkkk
@ellensaisithom7556
@ellensaisithom7556 Год назад
Chikondi chiopsa amaona kuwawa mdioonera ,Anafuneya pakana kuvesera nyumba mwa aini Ake kuonjezatu
@aleksawilliams710
@aleksawilliams710 Год назад
🤣🤣🤣🙌,munafikatu anthu Inu
@dankanyowa5363
@dankanyowa5363 Год назад
Wow kkk Mr shoprite
@aishamussa-jq4ur
@aishamussa-jq4ur Год назад
Kkkkkk...komatu Mr Shoprite DC
@marymuhahara791
@marymuhahara791 Год назад
Ineyo koma kaya mukuwati a Nafuneya andikwana ndiamabodza kwabasi ofunika kuwathira nkhoko
@alinafekadango2596
@alinafekadango2596 Год назад
Kkkkkkkkkk koma khan zakee🤣🤣🤣🤣
@ronaldgowelo3865
@ronaldgowelo3865 Год назад
Umakwana Mr shoprite😃
@mussachitambi
@mussachitambi Год назад
Giling,ande anakoza kkkk
@veronikamalangano
@veronikamalangano Год назад
🥰🥰😍🥵
@nevermindmatemba-cs7mc
@nevermindmatemba-cs7mc Год назад
Kkkkk mipewa eeee
@moffatkalima1359
@moffatkalima1359 Год назад
Amalawi mukukoza kwambili chonde pitilizani ndakunyadilani .
@watipasomzungu9911
@watipasomzungu9911 Год назад
Giling'ande ndi katundu!
@thoccosporrophiri3780
@thoccosporrophiri3780 Год назад
😊
@ziyamikanmakowa5981
@ziyamikanmakowa5981 Год назад
Zili bwino ,pitilizani kutisangalasa
@matolawhyte-ie3iu
@matolawhyte-ie3iu Год назад
Kkkk koma yaa
@omegamtokoma3122
@omegamtokoma3122 Год назад
Kodi ndimudzi wakuti mumajambulila ko
@frankthomson7149
@frankthomson7149 Год назад
Giring'ande!! kkk dengerous child
@alfredbatumeyo9191
@alfredbatumeyo9191 Год назад
Jamison kkkkk
@mtotayusufu-lt1fo
@mtotayusufu-lt1fo Год назад
Jameson kkkkkk
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 Год назад
Dc ulemu wanu
@jacquesmarais6912
@jacquesmarais6912 Год назад
Kkkkk yeah
@joseblessmasauko7450
@joseblessmasauko7450 Год назад
💥✨✨✨✨
@alinafesawasawa3905
@alinafesawasawa3905 Год назад
🔥🔥🔥🔥
@stainleyhope9848
@stainleyhope9848 Год назад
koma anthu Inu hahahahahaha
@jacquesmarais6912
@jacquesmarais6912 Год назад
Kkkkk yeah
@mussaganeti
@mussaganeti Год назад
Mr choplite amakwana ulemu wawo amandimvesa kukoma kkkkkkkkkkk
Далее
Mfumukazi Comedy 22.3.23
27:04
Просмотров 28 тыс.
Mfumukazi Comedy
27:54
Просмотров 41 тыс.
БЕЛКА РОЖАЕТ? #cat
00:21
Просмотров 706 тыс.
@HeadmanChigodora Kuita bhizinesi nemukadzi
45:29
Просмотров 14 тыс.
hot current 2024
1:02:54
Просмотров 17 тыс.
MFUMUKAZI COMEDY
27:17
Просмотров 33 тыс.
Mica Iliadă: Cornel Ilie
3:40:40
Просмотров 143 тыс.
THE COURT..(Malawi )🤔
20:45
Просмотров 229 тыс.
CYCLONE FREDDY FUNDRAISING DRAMA #malawi
1:31:45
Просмотров 480 тыс.