A marriage wa season- karanka bra ya black yasowa: bambo Giling'ande pali anzanu anayi anafa kale Giling'ande ali pa muzere wa kufa komabe nyama yatha banja lathapo
giling'ande ndi actor wabwino koma amachulutsa zochitika zimene zimaonetsa kuti akupanga sewero, but acting is about being real, azipanga ngati amfumu akazi samaoneka ngati akupanga sewero ayi