😂😂😂😂😂 apa ndikusowa poti ndigwile umu muli bomba agiling'ande nde afumu kazi aliyese ali yekha yekha osayankhulitsana apadela ati mzimu ukagona ndinjala eish koma mafalayi anakonza nthawi zose amasokoneza zinthu Kkkk mumatha guys next nde kuliso Bomba ❤❤❤
Watching live from Cape Town RSA,, Mfumukazi acting imandiwaza kwambili nkabwela kumeneko will make sure kuti Nzajoine nawo basi and be part of this Group 🔥🇲🇼