Тёмный

MNYAMATA WA MCP KUNDIRANDE WAPEZEKA ATAFA KUNYUMBA YAKE NDIPO MOSES KUMKUYU WAYANKHULA IZI PAMALIRO 

Makosana
Подписаться 110 тыс.
Просмотров 11 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

20 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 210   
@Gwedeza-q3f
@Gwedeza-q3f 2 часа назад
Mkuthekanso omwewa ndiwo apanga chipongwe chifukwa ndale Zanu ndizotchipa ndizakupha
@geofreysabola5497
@geofreysabola5497 2 часа назад
It's sad chifukwa ndi wa MCP how many people amaphedwa kundirande how sad as a nation on Malawian expenses shame and zachibwana kwambili
@HamzahTwaib
@HamzahTwaib 4 часа назад
Ndalama zokuba inuyoooooo anthu akumoto ndinthu 😭😭😭
@EmmanuelMphande-f4l
@EmmanuelMphande-f4l 3 часа назад
Anamwa mowa ameneyo musanamize anthu
@Willardmakande-p2q
@Willardmakande-p2q Час назад
We have to start with SKC
@SandraBanda-hd1li
@SandraBanda-hd1li Час назад
Panyo... pako.... Kunkuyu..,.. Osanena... za. imfa .....ya.Witika.... unapha... uja... bwanji... ndiwe..... Chitsilu
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em Час назад
We need justice for SKC first
@chrisboyce2
@chrisboyce2 3 часа назад
Mr Kunkuyu kms MCP yomwe mumve ichi ife kuno ku Ntcheu tikufuna Chilungamo pa imfa ya BIYENI kms anthu 8 aja osaiwala Witika Osati mabi! Ukukamba apawa aiii ndipo Ukamuuze Chimwendo kuti ali ndi masiku owelengeka.
@ThandiShandu-l6w
@ThandiShandu-l6w 2 часа назад
Mbuzi pita page ya chilima not here kuphatikiza zinthu basi ufisi eti
@adamsmhone
@adamsmhone 2 часа назад
Zachisoni amalawi kt mphaka tiyambe kuphana! zosakhala bwino. Km a kukunkhuyu mawu amenewa munalepeleranji kuyankhula mau amenewa kt kd pazana panayankhulidwa chani ngati mene mukuyankulira apa???? Km zomvesa chisoni!!!!
@IshmaelNesta-rb8dx
@IshmaelNesta-rb8dx 56 минут назад
​@@ThandiShandu-l6wndi pa page pa MCP apa??? Nawe pita ku page kwako
@juruEzra
@juruEzra Час назад
Time will come, koma wina mulife don't run
@afropedia_edutainment
@afropedia_edutainment 4 часа назад
Tiyambe kufufuza imfa ya Chilima ndi Witika. Chifukwa ndiwa MCP ndiye imfa imeneyi ikhale yowawa? Ai kupha ndikwa MCP. Musalire lero. May the soul of Mabvuto rest in peace. Kunkuyu siyani kuononga dziko
@AdamMntonintshi
@AdamMntonintshi 3 часа назад
Ndipo live
@ThandiShandu-l6w
@ThandiShandu-l6w 2 часа назад
Nawe Garu odya zoola ukamba zosiyana awasimaliro mbuzi iweti
@Yoxym
@Yoxym 2 часа назад
​@@ThandiShandu-l6wkoma amayenera kuyamba Kaye commission of inquiry
@EdsonKamwendo
@EdsonKamwendo 4 минуты назад
Where is Allan Witika? Your daya are numbered
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 3 часа назад
Ka imfa akaka ndikakang'ono Tikufuna tchutchu wa imfa ya chilima
@ChristopherChilambe-g4z
@ChristopherChilambe-g4z 3 часа назад
Ndipo live why not commission of enquiry
@MadalitsoChingoma-si5jf
@MadalitsoChingoma-si5jf 3 часа назад
Biyeni may his soul continue resting in peace
@ElsaMalunga
@ElsaMalunga Час назад
Man witika fist ok ngati waphedwa sizabwino nooo km wapanga izi sanakhoze inuso akukuyu yakhulani momanga osati momasura
@MaryNgola
@MaryNgola 34 минуты назад
Kunkuyu aligwaaaa ngt sakudya Ndrama zokuba zabomatu😂😂😂😂nkonowo ngt wama ARV
@yasiniKalonga
@yasiniKalonga Час назад
Apha NDA MCP mwina amamuona kufanana ndi born Kalindo 😂😂😂😂😂😂
@IdirissaCharles-s8g
@IdirissaCharles-s8g 45 минут назад
Moses kukuyu machende ake ndipo chisilu chamuthu dpp ikukhuzapo chani wafa wafa bass iweso kukuyu ndichakwera ukudikira zomwezi oky inalilah wainailah rahihuna
@FelixKachera-je4yk
@FelixKachera-je4yk 3 часа назад
Nyimbo ikhale Symon and Kendall..... Nkhoya yobweza iwawila kumsanaku
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o 3 часа назад
Akukhuyu hule uja minthu mwawo mumayenda zandale bs kumaliro ndale hule uja apite kusitenji kurowesa ndale
@MaggieBanda-ft5tu
@MaggieBanda-ft5tu Час назад
Mwapha nokha
@TimeAbilu
@TimeAbilu Час назад
Kulankhula kwabwino(komano akuchikangawa aja bwanji) no inquary
@KabikaBuba
@KabikaBuba 24 минуты назад
Nanga nkhani yakuchikangawa bwanji si anthu ofunikila
@LeviChakwira
@LeviChakwira 54 минуты назад
Muyambe kafukufuku wa imfa ya chilima first
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o 3 часа назад
Bwanji maliro apolis ena aja akukhuyu sadapite anali bizy kukatamanga bt ndichikangawa zakunyero basi
@lungisanishezi1023
@lungisanishezi1023 Час назад
Tafufuzani vice president chilima galu iwe kumkuyu
@Gwedeza-q3f
@Gwedeza-q3f 2 часа назад
Witika alikuti
@KabikaBuba
@KabikaBuba 23 минуты назад
Mwaiwala kuti nanu ndiakupha
@WisemanMvula-c6n
@WisemanMvula-c6n Час назад
Na umo mukupulikira apo ntheee ndimo nase tikapulikiranga pa nyifwa za ngozi ya ndege
@KeyEnoncent
@KeyEnoncent 4 часа назад
ngani Mr Witika mukuti bwanji nayo iweso muntu wakumpa forsake
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira 4 часа назад
Sitina iwale khani ya witika
@Memorymlumbe-j1v
@Memorymlumbe-j1v 3 часа назад
Mmmmmm basi vomerezan ngat mmene tinavomerezera za chilima,cheteee
@TameeraInglis
@TameeraInglis 59 минут назад
Fufuzana kayr. Za omwe adapha. Achilima muliuze. Sziko agalu inu
@RaymondMikondo
@RaymondMikondo Час назад
Ifiti imazibakirat ngat za nzeru
@JkFosa
@JkFosa 2 часа назад
ameneyo ma battery ake ifa yachili osafufusaza bwanji
@MadalitsoChingoma-si5jf
@MadalitsoChingoma-si5jf 3 часа назад
Speechless 1 million ingagure Moyo wamunthu very shameful
@FrankChione-k6m
@FrankChione-k6m 3 часа назад
Muyambisa nkhondo inu ndimisala yanuyo nfundo mulibe
@marthaphiri3600
@marthaphiri3600 4 часа назад
Nanga imfa ya anthu naini ku chikangawa sizinali zopusa?
@ElizabethKumwenda-f5h
@ElizabethKumwenda-f5h 4 часа назад
Muyambe mwafufuza za anthu 9 aja kenako imeneyi za Allan witika zili pati
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh 26 минут назад
Ndiy ngati ndege amaba ma phone uyu ma phone ndi ndalama zinabisala pati
@stevennthukwa
@stevennthukwa 4 часа назад
Koma ndikudabwa akuyankulawo , akanakhala ena please ,kodi ku mcp kulibe ena?mcp khalani pansi muziona othuma according ndimbili yake please
@EnerstBanda-m4s
@EnerstBanda-m4s 3 часа назад
Ifesotu tinamva pa misonkhano mukunena zoti pavute bwanji Dr Chilima salamulira ndipo munanenetsa kuti papangidwe sacrifice and munamuphadi pomaliza pake and up to now mukukana kupanga commission of inquiry meaning mukudziwapo kathu amfiti inu achabechabe mwapangitsa Anthu kukhala amkwiyo mdziko muno chifukwa chosachitapo kathu pa zaimfa ya Dr Chilima, witika ndi chipongwe chapa Mbowe omwe anapanga mukuwadziwa koma osawamanga
@StephanoRaphael-c7e
@StephanoRaphael-c7e 2 часа назад
Kodi chilima ndi anthu Ena aja Ana ndi able awo a Alibe,? Commission of inquiry bwanji simukukhazikisa mukuopa chani
@phillimonmaila4269
@phillimonmaila4269 Час назад
Mawa anthu ena azakambanso choncho pa maliro ako
@FrancesPeter-xw3vb
@FrancesPeter-xw3vb 3 часа назад
Aaaaaaa akulu bwanji? Simudayankhule za imfa yachilima
@KondwaniKholiyo
@KondwaniKholiyo Час назад
Yachilima inja bwanji mukuchedwa iwe kukuyu
@DanielZunguza
@DanielZunguza 2 часа назад
Nanga witika analakwa chani?
@BlessingsMarley-l2x
@BlessingsMarley-l2x 39 минут назад
Iwe ife za imfa iyiyi sikutiwawa kwenikweni koma nkhani ndi ya Biyeni SCK ndi anthu 8 aja osati zoduka mutu ukukambazi ayi Kodi a chipatalawo atayeza thupilo alipeza ndi madala? Kapena kuti mwina anachita kuombeledwa? Lelo mukuti mukufuna mufufuze zoona zenizeni za imfa imeneyi bwanji simukufuna mufufuze za imfa ya yemwe anali wachiwili wa chikangawa lion 🦁🦁🦁🦁
@EsnatMeleka
@EsnatMeleka Час назад
Ndiwe galu bas nkhope yonsayo
@MagadaleneManjengwa
@MagadaleneManjengwa Час назад
Tipange zakuchikangawa osati zopusazo nanu
@TenganiObety
@TenganiObety Час назад
Mwapha nokha mufuna mupedze dzifukwa kwa ena MCP tikukudziwani
@ElsaMalunga
@ElsaMalunga Час назад
Kd ndarama mwathira mafutazo kupita kumarilo anuyo ndi zanu kapena misokho ya amalawi zopusatu ayi tavana
@GreyMtungama
@GreyMtungama 2 часа назад
Za witika,zikadzadziwika winadi adzagwetsa nkhope pasi
@TenganiObety
@TenganiObety Час назад
Dzikakhala zanu zimbveke za ena ayi?
@danielmagwaya1074
@danielmagwaya1074 4 часа назад
Ndege inagwa bwanji ku Chikangawa musatipondeleze plz mwat muli ndi akadawulo oziwa kufufuza za Saulos Chilima zikukanika pat
@PociahMack
@PociahMack 3 часа назад
Ndiye mukafusa ndani ngat iyeyo amagwila ntchito yowulusa ndege, kakusen aku airport ndi MDF akuyakheni
@MagadaleneManjengwa
@MagadaleneManjengwa Час назад
Chakwela adapha chilima waphindu osati mbuzi yopanda phinduyo
@BlessingsSeleman
@BlessingsSeleman 3 часа назад
Nambotu baba ajogope mlungu jwakulolaga ya mumtima
@aminkums515
@aminkums515 2 часа назад
Chimodzimodzi mmene muzagwesele nkhope pazakuchikangawa
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh 39 минут назад
Zagwa mmanja mwanu lero mesa mumati tisalire biyeni wathu
@ArronBenson-g6d
@ArronBenson-g6d 3 часа назад
Ku nkuyu mutu ngat diwa
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n Час назад
Tiyambe kufufuza za chilima ndi Witika
@ThembaniJikah
@ThembaniJikah 2 часа назад
Mapwala ake nkunkuyu Nanga imfa ya witikA+9 people's on cruch plane +Raph kasambala
@SympathyChikwanda-ck7mk
@SympathyChikwanda-ck7mk 2 часа назад
🇲🇼
@temwachaima817
@temwachaima817 3 часа назад
Kukanika za saulos chilima za ziii
@EdsonMulendo
@EdsonMulendo 3 часа назад
Pa maliro sipolankhula mwa mtundu umeneu nzoyambitsa zipolowe izi kunkuyu akuyenera amangidwe
@CharlesChagudubuka-rm6bh
@CharlesChagudubuka-rm6bh 36 минут назад
Kodi mesa Inu akunkuyu mumayankhulira boma? Nanga mukuyankhula ngati mneneri wachipani bwanji?,aa koma
@NdamvaScnp
@NdamvaScnp 2 часа назад
panyapako kunkuyu ifa ya anthu mudawapha mudenge aja bwanji simukufufuza panyini pamako
@raphaelmuliya6362
@raphaelmuliya6362 Час назад
Akunkuyu ndinu opepela kwambili, zimenezo simfundo zapamalilo, kumasiyanitsa malilo ndi ndale
@Chikwawa
@Chikwawa 4 часа назад
Kodi Chilima ndi ena aja analibe ana ndi abale?Inu mukubweretsa mavuto ochulutsa mdziko muno.
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 3 часа назад
Be careful ndi moses chigawenga choopsa chomenechi
@TameeraInglis
@TameeraInglis Час назад
Ayambe kukumanga iweyo unapha witika galu iwe
@EmmanuelJesmanphiri
@EmmanuelJesmanphiri 3 часа назад
koma maliro tisamawa pangile ndale ndizowona wagona.musayike kuti adale ndi omwe akutele akukuyu khani zaifazi zilipo zingati ku ntcheu ku thyolo ku mangochi ku balaka anthu akufuna kuziwa zoziwika koma tisasatengele ndale ndithu
@EDSONNAKULENGA
@EDSONNAKULENGA Час назад
Amawaseka tawi yachilimabwaji olilawo ziwanikuti chitoyofufuza siyapolisiayi komaachipatalaalikuti
@rajtwaihassan
@rajtwaihassan 2 часа назад
Tiyambe kufufuza ifa yanthu 9 kuchikangawa
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 3 часа назад
Kumkuyu chidaz chako
@Gwedeza-q3f
@Gwedeza-q3f 2 часа назад
Mwapha munthu cholinga muphiphilitse imfa Za anthu 9 Ndale zakh Malawi ndizotchipa bwanji
@EDSONNAKULENGA
@EDSONNAKULENGA Час назад
Achakwelaanayakula zamagazi mwachitapochani zadenge akukuyu
@RosinaPatel
@RosinaPatel 2 часа назад
Muyambe kufufuza za biyeni..
@TamalaKambanje
@TamalaKambanje 3 часа назад
Aaaaaaa yambani zinazi
@PeterPhiri-nd6op
@PeterPhiri-nd6op 3 часа назад
Mumene munawombela mumanja inu paja wa utm anagwa ndi ndege
@AlfredTengani
@AlfredTengani 3 часа назад
Kunkuyu ndi kape uyu saziwa ndale
@EDSONNAKULENGA
@EDSONNAKULENGA Час назад
Musagamule apolisi asanafufuze zikusalilani
@OwenchangnyaMkandawire
@OwenchangnyaMkandawire 3 часа назад
Ukuyankhula zopanda nzeru,chitsiru iwe.
@ChiwaloWilliams
@ChiwaloWilliams 2 часа назад
A mkukuyu tayambani za witika chigawenga chinzanucho choipa chamusata
@wellington-w2e
@wellington-w2e 4 часа назад
Uyu ndi mamuziwa ndi wamisala anapengapo
@wisdomblack-u8n
@wisdomblack-u8n 3 часа назад
Athuwa mituyawo sikugwila coz m'malomopanga zamaliro akupanga za ndale coz akulimbana ndiachikwanje manga achikwanje kwao ndikundilande????????? Apapa muthuyotu aku mkuyu amupha okha cholonga chofunakuipisa ena......... ..koma sizitheka kut muipise ena anthu akufuna kafukufuku wa ndege ya chilima
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 3 часа назад
Zifwamba ndi mcp
@SelinaNamagowa
@SelinaNamagowa 2 часа назад
Mukukanika inuyo kuliuza dziko za imfa yapa 10 june ija, kmatu penapake muzinkhala serious mukamapanga zinthu zanu, ena anjanso anali azibambo makomo mwawo, kmanso anali azimayi makomo mwawo azitsogoleri tiyeni tiziyang'ana mbali zonse tikamapanga zinthu
@StephanoEbele
@StephanoEbele 2 часа назад
Akuluwa mmmmm,apolice ayambile inuyo
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio 3 часа назад
Iwenso ndichifwamba unapha witika
@JohnChauma
@JohnChauma 2 минуты назад
Inde abwana izi mukuyankhulazi sizikusiya ndi zomwe mumayankhula chilima alimoyo kod inu akubanja la k .s .c .inuyo Akukuonani motani popeza inu ndye ndi mwana yemwe akuchita kudziwiratu kuti .m c p ndiyomwe yapha anthu 9 anja
@ChisomoBanda-jo4ix
@ChisomoBanda-jo4ix 3 часа назад
Iwe udapha witika. Nyembako
@StephanoRaphael-c7e
@StephanoRaphael-c7e 2 часа назад
Inu kodi zakuchikangawa zikuti bwanji
@SeyaniTrouble
@SeyaniTrouble 4 часа назад
Ukutinyasa iwe panga zoti muyakhule za cilima osati zimenezo
@AshanAlexx
@AshanAlexx 3 часа назад
Aaaah koma guys Moti malilo amenewa ndiofunikila kwambiri Ku Boma eti, aaaah chabwino anthu anja muzaonaso kuwawa kwake next year
@AnnieMandala-z7o
@AnnieMandala-z7o 3 часа назад
Imfa ya Witika,zilipati kodi.?
@SamisonLevison-z5p
@SamisonLevison-z5p 2 часа назад
Wafa basi kankwililen pantumbo pale ameneyo
@JacklineNiwahereza-ni3pm
@JacklineNiwahereza-ni3pm 3 часа назад
Imfaa yaa chilima sumukufufuza basi iyiii nde muziti chani chani nkhani iyiii ndiyamalilo osayankhula zogawanitsa anthu mogwilitsa mawu ozembetsa
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 4 часа назад
Mcp ndiyokupha mwayambira kale mukuphana inu musanamizile ena ayi uku kutolana zachibwana izi ndipo muziphanabe inu simunati
@WonderfulMaulana-q6d
@WonderfulMaulana-q6d 2 часа назад
A Kumkuyu mwaziziwa lero zimenezi?,za anthu9 aja bwanji simunaliudze dziko?.
@michaelchimwala-x8t
@michaelchimwala-x8t 24 минуты назад
Musayiwale kuti nanu munapha chilima APA mukudabwa chani
@PhilimonThegha
@PhilimonThegha 3 часа назад
Iwe mbewa nkukuyu imwe ndimwe wakukoma wa MCP
Далее
The REAL Truth Behind the DVD Logo
01:00
Просмотров 29 млн