This movie is great. I loved it. Kanyimbo kakeko kabwinonso ndikungokaimba any where mtimamu kkkkkkk. (mwanayo amanena zoona kuti atsikana ophunzira mabanja amawavuta 😂😂😂😂😂)
I leaved malawi yes 2003 to where may i am today 2020 in mocambique doinng a work as mecanic but that means we are in last days look 2 timothy chapter 3 verses 1-5" look verse five. Mind you!
GREAT MOVIE BUT I WOULD REALLY LOVE IF IT HAD A BAD ENDING FOR THE ABUSING TEACHER BEING ARRESTED AND HIS CONTRACT TERMINATED BUT AS IT IS, ITS LIKE THE GUY PLAYED A WINNING GAME.
That's a very good ending of the movie. Apopo ndiye ikanakhala za obvious coz aliyense expected kuti sizimuthera bwino mkuluyu but the ending surprised us. Komanso this is the reality on the ground. Most of these cases go unpunished
Nonsense.... Phunziro ulibe umu I waste my time mkuonera izi...... Anafunika chhidyanj a chose ntchito mkukakhara kundende...... Kom pot ND film yakumalawi😂😂
Actually this is exactly what the producers want. To provoke your mind. Izizi ndi zomwe zimachitika Ku Malawi kuno, aphunzitsi otere amangopangidwa transfer. Samafuna kuti movie should have predictable ending koma itipangitse kuganiza kuti zimayenera zikhale bwanji. Eyetu