Malawian vybe Kartel anthu amaimba koma poimba ndikumatha kusintha mawu ngati Vybe Kartel nepman iwe ndi 1....uli mu class yakoyako boss man...salute madala
Nepman, aaahh!! zabwino zonse man, I was stuck in traffic some months ago, this HITS made feel so good then there was an African party and I played this, waoh ...keep it up . DUNCAN in Washington dc.