Тёмный

NKHANGA ZAONA PA LIMPOPO FM NDI COMRADE NTANYIWA A POLICE AWIRI AMWALIRA KU CHIKWAWA 14 Sep 2024 

MALAWI 265
Подписаться 8 тыс.
Просмотров 26 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

18 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 71   
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 4 дня назад
Mbambande Ntanyiwa 🔥
@SakaLack
@SakaLack 4 дня назад
Akhalinse wa Limpopo FM comrade Tanyiwa mkulu wake wa Born Kalindo yemwe anabeleka mfumu ya fajiri JB ndi mulongowake Kaliyati Yemwe apeleka thukuta Kwa ZIKHALE NG'OMA Mfumu yayikulu ya kuchikangawa 😂😂😂😂
@SophieLupiya
@SophieLupiya 4 дня назад
Umakwana
@user-td6qe4gr6w
@user-td6qe4gr6w 4 дня назад
God have mercy
@chimwemwenkute3839
@chimwemwenkute3839 4 дня назад
Welcome comred mtanyiwa
@JimmyZimbiri
@JimmyZimbiri 3 дня назад
Good malawian ambassador
@JECKYGREY
@JECKYGREY 4 дня назад
Yes
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 3 дня назад
Number 1ntanyiwa MBAMBANDE
@joebrown1158
@joebrown1158 3 дня назад
Mtanyiwa chifukwa chiyani umafuna kusangalatsa anthu ndi zinthu za mkutu za ziii ndani amene amasangalara ndikumava za kondwani Namkhumwa chonsecho aliyense amadziwa kuti Namkhumwa ndi traitor ?
@user-rg4du4vu9r
@user-rg4du4vu9r 4 дня назад
Chakwera anathawa ntchito ya murungu murungu wakwiya naye uzithaima aise wangoyamba bus imaphweka akamayendasa anzako unkanyoza peter iwe rero nawe zakuvutatu kkkkkkkk yomweyo chikangawa chifunga
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 4 дня назад
Muchire msanga comrade Ntanyiwa
@user-lr2wx5xd9d
@user-lr2wx5xd9d 4 дня назад
Following limpopo
@SABITIKAISI
@SABITIKAISI 4 дня назад
Khumene amwalile
@BistonMacheso
@BistonMacheso 4 дня назад
Ku citytso kuli mamvuto kwambiri anthu aku Blantyre city akumvutikatso malipiro akulandira 50,000 pamwedzi ineyo ndinali Koko ndanayisiya ntchito 50 salare
@augustMag
@augustMag 4 дня назад
Amachedwanso ndi genda miyala ine ndimayembekeza kuti amutumizira ng'onatu Mtanyiwa Limpopo FM 🔥🔥🔥🔥
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 4 дня назад
Nanenso ndimadandaula kuti comrade Ntanyiwa alikuti,, bravo comrade 💪💪
@DigleDafter
@DigleDafter 4 дня назад
A police kusamarika azifera zaweni choncho bas ndipo achepa 2 woo😂
@dyba-x9w
@dyba-x9w 4 дня назад
KUGWA MMANJA A MULUNGU MKOOPSA ZATIBWERETSERA MAVUTO
@ReksonMorees
@ReksonMorees 4 дня назад
Hy
@AllanChabwela
@AllanChabwela 4 дня назад
Inuyo ndi 1
@S-rr1eu
@S-rr1eu 3 дня назад
😂 Nankhunwa sakuziwa😮 choenera kuchita , ndare anangogwela .
@ClementJohn-gk3nl
@ClementJohn-gk3nl 4 дня назад
@LameckManuel-f3q
@LameckManuel-f3q 4 дня назад
Ulemu wanu bigy
@OwenNyambose
@OwenNyambose 4 дня назад
Comrade mtamyiwa
@user-og3ow8qj7l
@user-og3ow8qj7l 4 дня назад
Mukamayendera, mufikenso ku Malawi Posts Corporation.
@henrymedeliko8727
@henrymedeliko8727 4 дня назад
Something serious 90 mk yachepa azinjoya ndizovalazo forsake comrade menyani nkhondo
@Felie-p7l
@Felie-p7l 4 дня назад
Timakunyadilan bwana
@user-td1nu6iy2y
@user-td1nu6iy2y 3 дня назад
Mmmmm koma kumalawi mupwetekana mpake ndinasamuka eishii
@user-id8rr8or6d
@user-id8rr8or6d 4 дня назад
Mtanyiwa kumapeto mwat Chani bwanji adad mwataniso""
@user-id8rr8or6d
@user-id8rr8or6d 4 дня назад
Pa nkhani ya salary mtanyiwa MMM tikuvutika kumbali yamalipiro"
@VeronicaYohane
@VeronicaYohane 4 дня назад
Zonsezi ND chikangawayu amphetsa anthu osalakwa inu
@VenançioZocueza
@VenançioZocueza 4 дня назад
A biziweki adafupika ndinzeru zomwe,dyera garu
@SiyaRwagasore
@SiyaRwagasore 4 дня назад
Musaweluze woweluza ndi mulungu komanso osabweza choyipa wobwenza ndi mulungu musamale osachimwa nthawi yatha lekani mikangano
@FamousJohnathan
@FamousJohnathan 4 дня назад
Tatulutsani audio yaku chikangawayo comrade
@FrankMasaka-s7u
@FrankMasaka-s7u 4 дня назад
🔥🔥🔥🔥
@JaimitoAlbertocamandoCamando
@JaimitoAlbertocamandoCamando 4 дня назад
Tionjezereso ena kupha awiri achepa
@GraceMasiye
@GraceMasiye 4 дня назад
Monga mwa msembe zanu eti
@MadalitsoPhiri-c5f
@MadalitsoPhiri-c5f 4 дня назад
Tikudikira ndichidwe zaku chikangawazo a Mtanyiwa
@JamesRoben-dy7bx
@JamesRoben-dy7bx 4 дня назад
Achepa awilio akanachuluka amaonje a mwano
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 4 дня назад
Ulibho big
@EmanuelMwanza-ko7tm
@EmanuelMwanza-ko7tm 4 дня назад
Mulibwereso nkhani ya likoma island
@GraceMlauziNkhoma-ml7tv
@GraceMlauziNkhoma-ml7tv 4 дня назад
😢😢
@frankndawandawa6666
@frankndawandawa6666 4 дня назад
Koma yea
@mabvutochimkondenji910
@mabvutochimkondenji910 4 дня назад
Chakwera ayenera kuyenda ndi pulezident wadziko 2030 woooo imene yinja ndi ngozi basi
@PililaniLikomwa
@PililaniLikomwa 4 дня назад
Mmmmm wakutumani ndani kuti muvele
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 4 дня назад
​@@PililaniLikomwandipo asoceratu awa apite ku Mbc
@LloydLuwis
@LloydLuwis 4 дня назад
This mboma ndiya MCP
@PililaniLikomwa
@PililaniLikomwa 4 дня назад
Inuyo Ngati zimakunyasani musamavele
@Edithmchinza
@Edithmchinza 4 дня назад
Ndipo ndee asocheradi
@IbullaTaimu
@IbullaTaimu 4 дня назад
Machende ako aise ngozi ya mbuyako zikukusangalasa zomwe akupanga nyau/chikangawa
@mtunduwathatambala9848
@mtunduwathatambala9848 4 дня назад
KODI NKHANGA ZAKANIKA KUONA KAGULISIDWE KA CHILUMBA CHA LIKOMA ? TAIFUFUZA KU TIMES,TIUZENI POYELA TINVE KWA INU..
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 4 дня назад
Zogula mafutazo ndi zipatala zonse ku chiradzulunso timauzidwa kuti Ambulance iliko koma mafuta kulibe tigule
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 4 дня назад
Tikudikila lipoti lakuchikangawalo
@user-id8rr8or6d
@user-id8rr8or6d 4 дня назад
Ambulance imakhara ndi mafuta aboma kumakhara Kuba mbava
@ArthurMaulidi-g4r
@ArthurMaulidi-g4r 4 дня назад
Comrade,Malawian diehard
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 4 дня назад
😂😂😂mbuzi za apolice
@LameckNgwira-t6s
@LameckNgwira-t6s 4 дня назад
Bon voyage
@DanielMbewe-jo9vv
@DanielMbewe-jo9vv 4 дня назад
I feel for Malawi🇿🇲🇿🇲🇿🇲
@DavidJabesi-r1h
@DavidJabesi-r1h 4 дня назад
More fire ntanyiwa , writting from mozambique.
@user-on6eh2jl1s
@user-on6eh2jl1s 4 дня назад
Ulemu wanu ntamyiwa
@mabvutochimkondenji910
@mabvutochimkondenji910 4 дня назад
chakwera boma boma lomweri basi
@WitnesChirwa
@WitnesChirwa 4 дня назад
𝙺𝚘𝚖𝚊 𝚖𝚝𝚊𝚗𝚢𝚒𝚠𝚊 𝚖𝚖𝚖𝚖𝚖 𝚖𝚞𝚜𝚊𝚣𝚊𝚏𝚎 𝚖𝚞𝚜𝚊𝚗𝚐𝚘𝚜𝚘𝚠𝚊 𝚗𝚍𝚒𝚗𝚞 𝚛𝚎𝚊𝚕 𝚏𝚛𝚎𝚎𝚍𝚘𝚖 𝚏𝚒𝚐𝚑𝚝𝚎𝚛
@kadijhahaji
@kadijhahaji 4 дня назад
Yes
@abelkalulu2904
@abelkalulu2904 4 дня назад
Bama ndilomweli
@Felie-p7l
@Felie-p7l 4 дня назад
Timakunyadilan bwana
@WitnesChirwa
@WitnesChirwa 4 дня назад
𝚠𝚒𝚗𝚊 𝚊𝚍𝚣𝚊𝚏𝚊 𝚗𝚐𝚊𝚝𝚒 𝚐𝚊𝚕𝚞 𝚗𝚍𝚒𝚝𝚑𝚞 𝚌𝚑𝚘𝚒𝚙𝚊 𝚌𝚑𝚒𝚖𝚊𝚝𝚜𝚊𝚝𝚊 𝚖𝚠𝚒𝚗𝚒
Далее
Will Keir Starmer Explore Albania Migrant Deal?
11:22
Mfumukazi comedy series 28 August 2024
27:49
Просмотров 50 тыс.