Тёмный

NKHANI ZALERO KU TIMES 4 September 2024 

HOT 265
Подписаться 79 тыс.
Просмотров 19 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

15 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 48   
@RashidKusum
@RashidKusum 11 дней назад
Ndarama sizomwe akungoyendera chakwerazo zawusiru basi
@MustapherLino
@MustapherLino 11 дней назад
Ndi chakwera amene anapha chillima iwe ukuti bwanji ife tikudzuwa
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 11 дней назад
Ineso ndikuziwa
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 10 дней назад
Vuto chakwela akuba ekha ndalama that's why azizakewo akwiya
@VanPaul-sv9yx
@VanPaul-sv9yx 10 дней назад
Ndipo live akudana nazo akanyere uko😂😂😂😂
@VanPaul-sv9yx
@VanPaul-sv9yx 10 дней назад
Boma ndilomweri hahahahaaa😂, koma anyani ena akamaikira kumbuyo boma lazifwambari ndimangoimbira mmanja kuphamzi, ndipo B M Tv ija osazaiphwekesa ndiakatundu ameneaja, akati kamajekete hahahaaa😂😂😂
@RashidKusum
@RashidKusum 11 дней назад
Kumango kwera ndege kurephera kutukura ziko koma kumakakwera njinka kunja
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v 10 дней назад
Tikufuna umbino wanji munthu yemwe adapha Chilima ndi Chakwera chifukwa Cha u president 2025
@VanPaul-sv9yx
@VanPaul-sv9yx 10 дней назад
Saulosi anali wandale ndiye zikuyeneraso kukambidwa mu ndale kumene iyaaa mboli zanu anyani inu takuonelerani anthu okhupha
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v 10 дней назад
Mkwezalamba machende Ako atakhala wamwalirayo ndi bambo Ako kapena mkuluwako ukanamva bwanji
@OmarManjawira-up3ns
@OmarManjawira-up3ns 11 дней назад
Usi sakudziwa ilionse ndi panja peni peni akagwere
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 10 дней назад
Chakwera akuwononga chuma cha dziko Lino zikuchita kuonetseratu kuti akudya komaliza coz akudziwa kuti chake palibe ndiye inu anthu omutsatira tiziti simukuona?? Maso anu Ali kuti?? Mugwira chikolopa tiyeni nazoni muziona.
@RukayaIssah-h7t
@RukayaIssah-h7t 10 дней назад
Paja mukuti boma ndi lonweli 😂😂😂😂😂 lipirani anthu ndalama zawo Kaya mesa boma ndi lomweli God always best
@GraceChenda-q2g
@GraceChenda-q2g 10 дней назад
Za ziiii
@DennisTobias-b4r
@DennisTobias-b4r 11 дней назад
Ukupita kwanu ku states house kwaola ndi fisi uyu
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 10 дней назад
Inu a mcp maphwala Anu nonse pamodzi ndi manganya panyo pakenso
@JummaRattik
@JummaRattik 11 дней назад
No worries about money you should be worried your life 😅😅😅😅
@BairdThomas-c2k
@BairdThomas-c2k 10 дней назад
ajona utola nkhani wanu tinautuluka ife chifukwa chamau omwe amatuluka pakamwa panu maka pokondela boma lomwe likupha anthu panoli kuzela munjala, mundege ndinjila zina zambili zomwe akugwirisa ntchito pozuzira amalawi( jona ndi andevu zamwayi ) maspeech anu tikamamvela ndi kuonela amatiuza chomwe muli ndi chikangawa mulungu akuthandizeni
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 11 дней назад
Mkwezalamba ndiwe chistilu chambiri
@user-hx6ly3cl8m
@user-hx6ly3cl8m 10 дней назад
anthuwo akupanga chilungamo chifukwa inuyo Ausi inuyo mukugwila ntchito mukulipidwa ndiye anthuwo akupanga m,bindikilowo akugwila ntchito sakulipilidwa ndiye nkumati anthuwo akudya chain anthuwo apaseni ndalama dzawo sakupempha agwila ntchito
@Fatima-f5c
@Fatima-f5c 11 дней назад
Chakwela akangobela mavot m,malawi muno tigenda sayizi pandumbo tionesana
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 7 дней назад
Boma laboza ili
@MisheckAselo
@MisheckAselo 11 дней назад
Aaaaa Boma ili 😂😂😂😂
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 10 дней назад
Kwezalamba kukamwa kwakuluko banzi wadyayo uzayisanza
@laisoneesmael8530
@laisoneesmael8530 11 дней назад
Ndi wa MCP ameneyo
@MosesShaibu-ee8hn
@MosesShaibu-ee8hn 11 дней назад
Kodi ndi zowona ndege ingawuluke yosakwanilazipangizo?
@SueWahna
@SueWahna 11 дней назад
Omwe amayikila boma kumbuyo aja atipo Chan pa khaniyi tikamat Boma likulakwisa Kom sikutukwana kwake kuwophyeza omwe Ali ndimaso omwe akuwona 😢😢 chathu ndi chisoni Amalawi
@VanPaul-sv9yx
@VanPaul-sv9yx 10 дней назад
Ndiagaru ojiya ameneaja bro😂😂😂😂😂 ndipo Usi ndi mbuzi yamuthu kwabasi sakuziwa chomwe akuyikira kumbuyo
@henryphiri6100
@henryphiri6100 11 дней назад
Iye amangoganiza zopha omwe anathandiza.sadik mia.chilima.msowoya anamuthamangitsa.watsala Mkaka ali paulendo naye
@ErnestChansa
@ErnestChansa 10 дней назад
Chakwela chikangawa wawononga ndalama fiti yama fiti
@AmosScott-z9x
@AmosScott-z9x 11 дней назад
Miseu ija mumaliza km nthawitu nde sili mbali yanu this is September
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 11 дней назад
Chokani apa agalu inu
@KennethMugabe-f9l
@KennethMugabe-f9l 11 дней назад
Mkwezalamba ndichikapenso chamunthu ete
@BrownNkhoma-k6v
@BrownNkhoma-k6v 9 дней назад
Zodiac
@felixjoseph8161
@felixjoseph8161 11 дней назад
Ndalama angochindira chakwera uku
@Cubotenterprise
@Cubotenterprise 11 дней назад
Apereke mboli zaooooo
@Cubotenterprise
@Cubotenterprise 11 дней назад
Hehehe❤❤😂
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 11 дней назад
Mapitsi achani inu chakwera akuziwa
@tracybennie7783
@tracybennie7783 11 дней назад
Tibwasula. Nkumene. Ifa. Yawachiwili. Wa. Dziki. Lino. Munene. Bwino. Bwino
@LoyidKarebe
@LoyidKarebe 11 дней назад
Palibe mukukambapochazelu amkwezalamba bola mukanangosiyaosalankhulapo
@UseniMailosi
@UseniMailosi 11 дней назад
Kumalawi kulibe boma ausi
@LoyidKarebe
@LoyidKarebe 11 дней назад
Amkwezalimba mwatichaniapa
@MsondaBanda
@MsondaBanda 11 дней назад
Tayani vindege vakumala ivo,
@BlessMnyenyembe
@BlessMnyenyembe 11 дней назад
Chipanda fundo
@JusticeBornNdhlamini-fp7ic
@JusticeBornNdhlamini-fp7ic 11 дней назад
🤔🤔🙌🙌🙌🙌
@OmexMainala
@OmexMainala 11 дней назад
😄😄😄😄😄😄 mesamumat ilindiboma lazitukuko mwaonatu mawagwilitsantchito mwangongole ndizimenezo
@SungananiSadi
@SungananiSadi 10 дней назад
Judas eskariote
@BrinoKadzakumanja
@BrinoKadzakumanja 11 дней назад
Mukunama boma ndiromwer
Далее
БЕЛКА РОЖАЕТ? #cat
00:21
Просмотров 502 тыс.
9월 15일 💙
1:23:23
Просмотров 1 млн
REPORT LA NDEGE - HOT CURRENT __15 September 2024
30:39
ANTHU ANG'ALULA AWA 🙌 🙌 🙌 15 September 2024
16:54
KWACHEMA 🔥 🔥 🔥 15 September 2024
11:29
Просмотров 8 тыс.
БЕЛКА РОЖАЕТ? #cat
00:21
Просмотров 502 тыс.