Тёмный

Ntanyiwa Naye Akati Athe Mau Eeeeh!🙌🙌🙌 

Malawi Extra
Подписаться 11 тыс.
Просмотров 30 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 55   
@marryphili5419
@marryphili5419 23 дня назад
Takunyadiradirani adadi tikufuna mubwerere basi zinthu zavuta mu malawi tatopa ife amalawi 💃💃💃💃♥️♥️♥️
@MacMakaluwa
@MacMakaluwa 22 дня назад
All the time ndimaona Ngati amapanga zokomera mzika. Apapa ndadziwa Kuti ukupanga za chipani. Bola Winiko amwene
@AnthonyChirwa-t4g
@AnthonyChirwa-t4g 24 дня назад
Tanyiwa inu ndiakatundu bwanji kusowa mtima wanga ndimava bwino ndikava mau anu ndi abon kalindo ndi dj mnyanane inu matiinilila ife ndi dpp utm afod ndi udf tikulowa muboma chikangawa achoke basi
@FatimaUmali-pc8sy
@FatimaUmali-pc8sy 23 дня назад
Koma wa bakili muluzi TV alipo?????
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 23 дня назад
​@@FatimaUmali-pc8syuyu watulutsa video inaaa uyu pompano wa Bakili Muluzi TV ndimakinanso naye eeeee😂😂😂
@user-fd7fg1bx4y
@user-fd7fg1bx4y 23 дня назад
mtanyiwa machine
@GodisoneNoel
@GodisoneNoel 23 дня назад
Dpp 🔥🔥🔥🔥
@Biath-m4b
@Biath-m4b 23 дня назад
Mtanyiwa ❤
@user-il8cn7ko9m
@user-il8cn7ko9m 22 дня назад
Chipani cha uzimu , umuthu, chilungamo, dpp my vote forever ❤❤
@user-fy7qk6kk5s
@user-fy7qk6kk5s 23 дня назад
D.P.P nde boma lathu panopa tagwilizana tonse amene tikukhala Kuno ku Joni tikubwera kudzavotera Adad
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 24 дня назад
Mtanyiwa ndiwetu Katundu,, Ndipo musatope kutipatsa ma update a zonse zomwe Chikangawa wakonza, apa wapita kukabisa umboni wa Zotsatira za Kugwa kwa Ndege.
@user-il8cn7ko9m
@user-il8cn7ko9m 22 дня назад
Eheeee a mcp mwanyaaaa manyiiii khalamba wa zeru , oopa mulungu, osapha , osaba , wachitukuko , osati chikanga satanayo , bulutu chakwela , nfiti , abwerere ku chipiku
@user-mk4ju6iw7c
@user-mk4ju6iw7c 24 дня назад
Thanyuwa mumakwana big
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi 23 дня назад
Chikangawa akumva kuwawa
@user-fy7qk6kk5s
@user-fy7qk6kk5s 23 дня назад
Chitukuko,chilungamo ndi nsima imeneo nde D.P.P . A.P.M 2025 boma tithokoze gwilizano umenewu gwape chakwera umanama
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 23 дня назад
Mtanyiwa tililimozi komkuno eti
@user-wb9ji3oe5o
@user-wb9ji3oe5o 23 дня назад
Tatumizani zithunzizo kuti tizione zigawenga za police
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 23 дня назад
❤❤❤❤ Mthanyiwa
@MatthewsJohn-kv8fj
@MatthewsJohn-kv8fj 23 дня назад
Boma ilo my vote not chikangawa mubusa wa satana
@LidyaGoodson-fb4tt
@LidyaGoodson-fb4tt 23 дня назад
Amen
@RadsonTimoteo
@RadsonTimoteo 23 дня назад
My Chipani ine ntimau myaaaaaaa
@SELEMANJAMESB
@SELEMANJAMESB 23 дня назад
chikangawa akuva nyunyunyu antanyiwa, kom achikangawa alimoyo ndizimene zichitika kukomesa
@ChilekaMoyenda
@ChilekaMoyenda 24 дня назад
❤thanyuwa
@YaqoobStandwell
@YaqoobStandwell 23 дня назад
Amene akumatulukawo akuchita because ndi akazitape koma awona kut ku dpp kulibe chinyengo
@user-mk4ju6iw7c
@user-mk4ju6iw7c 24 дня назад
Mumatibvesa kukoma
@David-z9o4m
@David-z9o4m 23 дня назад
Boma ilo!!!!!!!!!!!
@OdettaLowrence
@OdettaLowrence 23 дня назад
Zabwino zonse adad Moto buuuuuu!!!!
@MosesSolomoni
@MosesSolomoni 23 дня назад
APM my VOTI
@giftsululu4274
@giftsululu4274 23 дня назад
Asiyeni agogo akaleke zidzukuru
@ISSAYUSUF-qy1mt
@ISSAYUSUF-qy1mt 23 дня назад
Mtanyiwa mmakwa kuno kunapeya kumachinga
@SamuelKamanga-w8z
@SamuelKamanga-w8z 23 дня назад
Apa zilibwino osaopa till pambuyo pa adadi
@johnkatumbu6846
@johnkatumbu6846 23 дня назад
Wa Bakili Muluzi TV ndamuonaso konkuno😢
@EvanceEdson-fz1vn
@EvanceEdson-fz1vn 23 дня назад
He was there
@PeterJames-i8y
@PeterJames-i8y 23 дня назад
MCP yadzimbidwa ndi convention ya DPP
@kingsleyChisenga-i8g
@kingsleyChisenga-i8g 23 дня назад
Opposition ndiyomweyi sitikusintha 🔥
@MuhiyeBright
@MuhiyeBright 23 дня назад
Munthu wanzeru zake ndi owopa mulungu kumakhala bizy ndi mcp mene alilili Malawi pano ufiti chani aaaaa dpp woye 2025 boma kufuna osafuna kulowa basi moto kuti buuuuu
@user-zv3cy2xj5p
@user-zv3cy2xj5p 23 дня назад
Tighting security without a machine gun what is that?
@JoeLu-c4d
@JoeLu-c4d 23 дня назад
Zabwino zonse apm
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 23 дня назад
kkkkk zinamizanani agalu inu ife phee a utm atatu aaaa ife phee ndi pp , fp n PDP mcp boma 2025
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 23 дня назад
Ndikufuna nsalu ya DPP
@user-zv3cy2xj5p
@user-zv3cy2xj5p 23 дня назад
Akanika kuchedzera chifukwa cha ukalamba
@EvanceEdson-fz1vn
@EvanceEdson-fz1vn 23 дня назад
For security reasons, he is most wanted after chilima. He is threat to MCP
@ChinombaDyana-nz4tt
@ChinombaDyana-nz4tt 22 дня назад
Akachezere Ku convention ngati kape
@MussaNgoma-r2k
@MussaNgoma-r2k 23 дня назад
If you are a freedom fighter u don't support any party .Galu iwe
@joebrown1158
@joebrown1158 23 дня назад
Iweyo ndiye galu weni weni mwana woyipitsitsa kwambiri mwana wa satana m'dyelekezi iwe
@aligrayjeo1071
@aligrayjeo1071 23 дня назад
Some of your productions Mr Ntanyiwa are not good chief try to improve your station production especially when you doing your program we know u still growing as a radio koma try to be more creative with your productions.
@user-xs3pk1vp8i
@user-xs3pk1vp8i 24 дня назад
Bodzalo DPP inatha kale nkhalamba
@BettyByson-t4z
@BettyByson-t4z 24 дня назад
Zikomo zikutheka zikukuwawa kod wanya ase
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r 24 дня назад
Wanu nyamata uja Mr chikangawa akutan
@DoreenAllan-tg1dz
@DoreenAllan-tg1dz 23 дня назад
Yantha ndi MCP chikangawa part 😅😅😅
@Ernestkamvazina
@Ernestkamvazina 23 дня назад
I think ameneyu satana akumuzemberera
@EmmaEmma-q4u
@EmmaEmma-q4u 23 дня назад
😂😂😂Akulila awo ndi chikangawa anzawowo kkkk izatelo 2025 kutayaka moto ku mangochi nde manyazitu ufumu Wa mcp uzathela pompo kuti ng'ambi😅😅😅😅 love you muthu wankulu big man muthu wankulu Peter Ana a school anyamata ati profeti yawo ndi egrish km azigona njala. Takana ife ❤❤❤
@MATTHEWSANDREWMANDUTU
@MATTHEWSANDREWMANDUTU 23 дня назад
Mmmmmm inenso ndasimikiza kuti Dpp ndi 1 bc enawa akutizuzawa nrhawi yao yatha basi
Далее
Exclusive Interview with Reverend Alexander Kambiri
30:56
VIM Essentials Course for Beginners
3:41:21
Просмотров 72 тыс.