Тёмный

NTCHITO ILIKO! KOMA NGATI ZOMWE WANENA MKULU UYU ZILI ZOONA, NDEKUTI MALAWI SAZALEMELASO MPAKA KALE 

BS Malawi
Подписаться 115 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

NTCHITO ILIKO! KOMA NGATI ZOMWE WANENA MKULU UYU ZILI ZOONA, NDEKUTI MALAWI SAZALEMELASO MPAKA KALE
Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
#MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

Опубликовано:

 

18 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 36   
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete День назад
Ziko la Malawi anyamata ndiambili lets vote for him ❤❤
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w День назад
Let's vote for Denis, let's protest put denis on a president sit
@ayamijackson1443
@ayamijackson1443 День назад
Uyu ndiye Ibrahim traole wen wen ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w День назад
Denis my my president ❤❤❤
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza День назад
Long live big man tikusapotani❤❤❤❤
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete День назад
This man is very good alibwino kwambili
@JanetChifundo
@JanetChifundo 12 часов назад
Mungoyimila upule mukhoza kusintha Malawi ❤❤
@IsraelMlelemba
@IsraelMlelemba 10 часов назад
Power of knowledge n understanding change Denis,
@user-vx5kv8dz3d
@user-vx5kv8dz3d День назад
Uyuyu nde Ofunika upresident
@alexsumani6823
@alexsumani6823 День назад
In Malawi labor is cheap
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule День назад
Number one my bro
@georgejim51
@georgejim51 13 часов назад
First speech 💬💬💬💬 Unandifikspo pobwezela ngongole
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza День назад
Great big man❤❤❤
@chiletsokazembe-ri4ic
@chiletsokazembe-ri4ic 9 часов назад
aka ndikoyamba pamoyo wanga kuva munthu akuyankhula pagulu mwazelu chonchi komaso osanyoza utsogoleri omwe ulipo panthawi yomwe akuyankhulayo; thanxs my brother
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe День назад
Ine ndidzakusankha iwe Denis Mahata kuti upùlumutse dziko.lathu la malawi li.amen
@MalamaMithi
@MalamaMithi День назад
mkuluyu ndi goat kwambiri
@MustafaAjalu
@MustafaAjalu 6 часов назад
Muthu uyu❤❤❤❤
@alexsumani6823
@alexsumani6823 День назад
Akatundu bambo
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe День назад
Malawi ayambe ku printer ndalama.
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w День назад
Mahata ndi star ku Malawi, ukufunika utsogoleri. Osati mbuzi zilipo panozi ayi.
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 20 часов назад
Uyuyu akufunika uprezdent ndithutu
@michaelkallyz2425
@michaelkallyz2425 День назад
I think these IDEAS were spoken by Bingu but Malawi chose not to listen...
@LukeBiscuit-x2u
@LukeBiscuit-x2u День назад
❤❤❤❤❤
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q 14 часов назад
Chilungamo chowawa chonsecho ndi kumwa ma bukhu kweni kweni
@giftgama1325
@giftgama1325 21 час назад
Zaziii bwanji
@PreciousPhiri-f2h
@PreciousPhiri-f2h День назад
Ndiwe chimdalitso cha fuko lathu MALAWI! MULUNGU AKUSAMALILENI KUFIKILA ZICHITIKE ZABWINOZI KU NTUNDU WATHU WA MALAWI 🇲🇼
@HendrickBanda
@HendrickBanda День назад
♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️
@IsaacKaphesi
@IsaacKaphesi 5 часов назад
Kma vuto kuphoka kwachinyama sakumuziwa president wathuyu titani kuti anthu amudziwe
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb День назад
Mkuluyo akulankhula zonama anthu akudandaula devaluweshoni ikuchuluka.
@AchinaKellz
@AchinaKellz День назад
Iwe nde kape kape ufuna utiwuze chani
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili День назад
Gulitsani chabe kamalawika chifukwa zakukanikani or mukagawe chabe Tz idyeko,Zambia naye adyeko,Mozambique naye adyeko nkhani yatha not as such tikukhaliramu
@GiftKananji
@GiftKananji День назад
Vuto ndiloti anthu oipa sangamukonde chifukwa anthuwo adazolowera zokuba atha kuzamupha
@bobykhan3583
@bobykhan3583 20 часов назад
he sounds like wa BAKILI MULUZI TV LILIME LAKE 😂😂Its my opinion i could be wrong
@HassanIssaAbdulKarim
@HassanIssaAbdulKarim День назад
Kodi ma comedy munasiya?
Далее
Ice Bear would appreciate some cheese 🧀
00:18
Просмотров 13 млн
South Africa on 19 September 2024 Today
17:46
Просмотров 1,3 тыс.
APM WAFIKA NDIPO WALANDIRIDWA MWANYOOO MU MZUZU
4:09
Просмотров 1,1 тыс.