Komatu aJakev ma opinions ama viewers fe munakawapanga consider 😂 at least tisamawaone Kaye anthuwo, that would make it a bit more interesting to watch🤷♀️
Mkazi wa quality, wa vibe, wa business yake, ochezeka, koma ma guys akewo aaaah. Ma guys awawa nde ayi. Ine palibepo amene ndaona kuti ndioyenelana ndi Nya Uyu. Maybe next time.