Very nice and colourful dance from chichiri prison.We celebrate you president Nyusi and Lazarus maccarthy chakwera as you are presiding the official opening of Malawian trade fair.Achakwera palipose mungayende timakukondani kwambiri ndinu mtsogoleri wamaso mphenya aakuru kukonzanso ziko la malawi kuti libwelere mwakale ndipo zaysmba kale kuchitika.Osusa ali mmazi.
Now it makes sense, kani ndi a kaidi eti. Nde kuwaveka uniform ya mabwana awo kuti chani. Mabwana mwawavula kaye uniform kuti a kaidi a kavinile. Koma uchitsirunso