Тёмный

PAZOMWE ZIMACHITIKA MU NDEGE / HON MOSES KUNKUYU 14 June 2024 

HOT 265
Подписаться 72 тыс.
Просмотров 67 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

13 июн 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 190   
@NedsonKanjira-qj2ig
Sizoona zimenezo zoti anthu alowetsapo ndale ,Koma anthu akumva kuwawa kwambiri
@user-qv4yu2ir2k
Akulu inu musaoneke ngati dolo poyakhula just weit iwenso ulipa list yoti ulangidwe sharia low oyipa iwe hope nga khumba chonch
@joshuasambo9776
Chakufwa Chihana once said and quote " Kambuku ndi kambuku basi, sangachoke sidyalina nkusanduka fisi ayiii" MCP showing it's true colors
@user-ol1hf7ru1v
Mwaphera tsogolo ana aeni Ake ndipo mtendere uzakusowani Moyo wanu onse
@LovelyCardinal-sn5bb
Good Explanation from Hon.Moses Kunkuyu.Mwayankhula bwino kwambri
@jameskachulu8141
Akhukuyu nanuso zinazi muzikana anthu sangakulipilire inuyo chifukwa cha mfuti yanu inapha Alan witika ija mu chipasa ulemu chipani chanu mcp singawine kamba ka inu anthu inu atidwe nawo
@patrickkapinga7091
Apwanga mulimva dziko likutembenukirani
@MarkManyowa
Aaaah kuyankhula Mwantudzutu uku please
@user-do2cs8nf4b
Mizimu ya anthu amenewa ikubvutitsani nonse amene watenga nawo mbali pa imfa za anthu amenewa😭😭😭
@actuarialscience2283
Akufotokoza zomwe zimachitika mundege koma zinthu zopanga record za mundege zinasowa.
@hagiraamini6554
Amuses kumkyu Abwana, musadandaule, zonse, tisiye manja mwa Chauta, amene anatirenga tonse. Athu akhoza kukamba zambiri, I u musadandaule, chikwa, Mulungu yekha ndiamene akudziwa zoona.
@jogechawa6192
Uyu ndiye mfiti amazitenga dolo
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw
Kalonga shawa mwazizilitsa mtima wanga zikomo! Tisasokoneze mwambo wa mfumu yathu ya angoni! Kauseni mumtendere wawa
@user-is5dl7np9g
Mkwabwino koposa KT mauthenga a MMA foniwo aponyedwe pa social media coz kupitisa Kwa awo akafukufuku, kupangitsaso Kuti chilungamo chibisidwe coz we never know Kuti akafukufuku wo mwawadyetsa kale but we need the truth
@KelvinJpchimphepo-sh6nc
Apeleke koyenera kutiko ndiye inu simufuna kuzivesera zimenezo akalakhura mndegemo mkufuna tivere zanu osati eni ovakupwetekedwawo chifukwa ndamene amawona zmene zikuwachitikira, yudas chenjera uzikhweza ndichingwe ngat wadyesedwa chibanz
@josiahshaibu2055
Mayakhidwe ake exactly akuwoneselatu kuti akuziwapo kathu akuthawa chulungamo
@MphatsoJames-kh2un
Iwe ndiye uti akumkuyu ndinu omveza chisoni kwambili kunyasa khopeko zikukukhalani ndizomwe mukuyakhulazo.
@LinahNgulube
Mwamulakwira chilima😭😭
@DanielChima-zl2uo
Mavuzi pwiii agalu inu machende anu muuzane a MCP zigawenga izii
@KelvinJpchimphepo-sh6nc
Ndikungova chinyengo chokha chokha, chilungamo chiwoneke basi, enawa adyesedwa chibanzi,
Далее
Namadingo RM5 Lucius Banda part 2
15:29
Просмотров 3,9 млн
GWEDE-GWEDE LERO PA 6 AUGUST 2024
21:08
Просмотров 6 тыс.
На фейсконтроле 💂
09:41
Просмотров 811 тыс.
KU MCP KUSAMBWAZANA ZAMASEWERA AYI 🔥🔥🔥🔥
24:59
KOMA ZOMWE AYANKHULA A MICHAEL USI UKU 🤔🤔🤔
35:54
නාමල පිපුණාවැ
32:03
Просмотров 11 тыс.
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Просмотров 119 тыс.
MZIKA ZOKHUZIDWA NDI ATOLANKHANI 🔥🔥🔥🙌🙌
22:50
На фейсконтроле 💂
09:41
Просмотров 811 тыс.