Тёмный

Report La Saulos Chilima Lifika Monday - NTANYIWA KUYANKHULA 

Malawi Extra
Подписаться 16 тыс.
Просмотров 41 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

29 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 138   
@vincentchristopherbanda3748
@vincentchristopherbanda3748 2 месяца назад
I love you, Mr. mtanyiwa , please mokupemphani comrade muzikhalako serious mukamakhula . Izi zomangosekazi panthawi yomwe mukuyankhula nkhani za serious sizitivekela bwino . Chonde tasinthani tamakhalakoni serious. Tili pambuyo panu always. Mulungu azikudalitsani.
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 2 месяца назад
Thank you Kodi amaseka chan nanga akutiuza nkumasekanso kapena akuseka ndani
@LukaThawe
@LukaThawe 2 месяца назад
Kodi mukuganiza Kuti akunena zoona galu ameneyu ndiye mukuchedwatu
@mariezorgen7735
@mariezorgen7735 2 месяца назад
LORD please save your country 2025 is Far far your children needs you Malawi is sinking,,,,prayers for you
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy 2 месяца назад
AMEN 🎉
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 2 месяца назад
Amen 🙏🙏🙏🙏
@violetpotani
@violetpotani 2 месяца назад
Ndipo can't wait... We love you sir
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 2 месяца назад
Thank you x2 so much sir mr Ntanyiwa akwelume wetu. Sikomo x2 kwedyenji ligongo.lyakuposya lipote.la ngosi dya chikangawa plane accident..Chechakwera asisiledye.leporidyi.namɓò walakwe talikoposye malawi lisesenili.aaenti sana ..we wa chiyao.abiti
@HamzaMkwanda-bh8dc
@HamzaMkwanda-bh8dc 2 месяца назад
My best radio limpopo
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo 2 месяца назад
Monday kwatalika tikufuna tidziwe chomwe chidamupha chilima
@constancedikhalatheamjojo2064
@constancedikhalatheamjojo2064 2 месяца назад
Mponsoo as soon as pocb
@fatimaayamie
@fatimaayamie 2 месяца назад
Your number 1 comrade mtanyiwa mumatiimirira musadzafe mudzangosowa
@ChristinahNkwanda
@ChristinahNkwanda 2 месяца назад
Chonde Ambuye Mulungu wathu Mutichitire chisoni tichotsereni satana ameneyu muchikondi canu chigwetseni Mu mphabvu zanu Ambuye AMEN AMEN AMEN AMEN AMEN AMEN AMBUYE .
@evalisterphiri8435
@evalisterphiri8435 2 месяца назад
Chilungamo chiyende ngati madzi, God bless you brother
@MercyKatongo-p9b
@MercyKatongo-p9b 2 месяца назад
Sure the whole country we want the report Mr chikangawa
@JeanfatsanJere
@JeanfatsanJere 2 месяца назад
Mbuzi ya munthu iyi Uyo tikangomangilira pantengo basi 😢😢😢 mulungu akufuna titengepo Mbali tokha
@IbrahimRamzy-s9i
@IbrahimRamzy-s9i 2 месяца назад
Comrade Mtanyiwa udzangosowa mbamba, usadzafe ai
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 2 месяца назад
Tikufuna lipoti Mulungu akhale Ku mbali yanu Mtanyiiiiii 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃💃
@GeoffreyMaulana-rh5rx
@GeoffreyMaulana-rh5rx 2 месяца назад
Alla will protect you all the time comrade Ntanyiwa
@yourmaya1157
@yourmaya1157 2 месяца назад
Comrade Mtanyiwa ipeperereni muipatse moto 😅😅
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад
I can't wait for the report please wa bakili muluzu TV also bring the report
@PaulKambuzi
@PaulKambuzi 2 месяца назад
Umakwana mtanyiwa❤❤❤❤ so much
@MahometAli-e8w
@MahometAli-e8w 2 месяца назад
Comrade Antanyiwa woyee mumatimva ku Koma
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 месяца назад
We are proud of u comrade ntanyiwa
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 2 месяца назад
Comred ndi 1 Iyaaaaaa love u Ntanyiwa❤❤❤❤
@ChikuSambakunsi
@ChikuSambakunsi 2 месяца назад
Still mourning SKC
@MahometAli-e8w
@MahometAli-e8w 2 месяца назад
Inu Antanyiwa mumatichotsa ma stress ndi Radio station fm yanu Limpopo woyee
@MerryWayson
@MerryWayson 2 месяца назад
Ndipo libwele lipoti pano achoke Chakwera
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 2 месяца назад
Moto kuti buuuuuuu 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 fire chilichonse chidziwika Chaka chino
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 2 месяца назад
Kali konse tikawona
@MercyKatongo-p9b
@MercyKatongo-p9b 2 месяца назад
We can't wait for the report guys
@LytonGalison
@LytonGalison 2 месяца назад
Mr mtanyiwa khan zanu mbali ina szimaveka bwn kamba komangoseka zmenez muchepese please
@DivineMercy-df2pu
@DivineMercy-df2pu 2 месяца назад
Libwera Monday after wina wake atakakwerako njinga.That report has been manipulated.
@dyba-x9w
@dyba-x9w 2 месяца назад
waiting for the report
@MPHATSOKALUWA-lm2uy
@MPHATSOKALUWA-lm2uy 2 месяца назад
Ngt galimoto ykuyaka kungogundana nd yizake what more ndege kuchoka mmwamba kugunda phiri
@saulbipa6882
@saulbipa6882 2 месяца назад
Chifukwa mafuta mnalibe
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona 2 месяца назад
Ndi radio station yokhayi ndikamamvela mtima wanga umakhazikika pansi pitirizani kutiulutsira nkhani zabwinozi
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 2 месяца назад
They are sticking to utmost after killing him.May God humble and expose them
@constancedikhalatheamjojo2064
@constancedikhalatheamjojo2064 2 месяца назад
We need to hear..chinapha apule athu
@Esther-t4l
@Esther-t4l 2 месяца назад
Watching from RSA more 🔥
@asahelmachila3026
@asahelmachila3026 2 месяца назад
Obvious, the report that will come out has been changed to suit the MCP Chikangawa government. I know comrade Ntanyiwa will give us the real and correct report
@PatrickMtira
@PatrickMtira 2 месяца назад
Mukamayankhura mr mtanyiwa chonde muzichepetsa kusekako ife timadikira inu kt timve zambiri kuchokera kwa inu plz plz
@berlz12k
@berlz12k 2 месяца назад
Ndipo galu ameneyu watikwana Malawi yavuta iyi silibwino,Zimbabwe Zimbabwe tu tikapusa naye mxieww!
@georgemagwira2737
@georgemagwira2737 2 месяца назад
Limpopo FM radio waing'alura live live Anthu oipa ngati awa sindinawaonenso ndipo mulungu awalange molapita
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 месяца назад
Moni mntanyiwa from Zambia
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw 2 месяца назад
We proud of you Mr ntanyiwa
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 месяца назад
Akufunika di a choke chakwera atitha, Nanga ngozi zake zimenezi nde Afa angati podzafika 2025 Our heavenly father who at in heaven please have mercy upon us
@RobenAlik
@RobenAlik 2 месяца назад
Ife makuthu ngati kalulu ku mvera😊
@anniegundaphiri423
@anniegundaphiri423 2 месяца назад
Comrade mtanyiwa you are the best
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 2 месяца назад
UTM inatuluka mumugwirizano wa tonse alliance ndiye asatanic enewo akutani kulandira mr Chikangawa. MCP ma plan avutadi eti
@JimmyMhone-b5p
@JimmyMhone-b5p 2 месяца назад
Akagone kwasing'anga ena akazunguliridwa ndi gule wankhulu kkkkkk
@alfredmongola900
@alfredmongola900 2 месяца назад
Comrade mtanyiwa umakwana Kodi umachokera kuti ukuoneka ngati ndiwe wa thyolo kwa bvumbwe
@alfredmongola900
@alfredmongola900 2 месяца назад
kwa bvumbwe tiriko bho kaya comrade mtanyiwa uliko ku south africa
@willytengani1193
@willytengani1193 2 месяца назад
Waiting for report mr tanyiwa😂
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 2 месяца назад
Ng,alulani atanyuwa kkkkkk nanga muli bwanji Mr tanyuwa ine pheee pano kumvera tanyuwa
@JasperKaleni-dx6nn
@JasperKaleni-dx6nn 2 месяца назад
This is my radio 📻 🙌 😂❤
@Lunnah-b1t
@Lunnah-b1t 2 месяца назад
Koma chakwera chikumbu mtima chizikupezani tsiku ndi tsiku ,zoona mnzako chonchi ,ana achilima asanduka ana amasiye ambuye akulangeni ndithu ,
@ThomasStephan-tg6ng
@ThomasStephan-tg6ng 2 месяца назад
Ndikuti lipoti ikangotuluka Malawi please tiyeni pansewu amalawi ndikupemphani amalawi tiyeni pansewu mademo chakwera achoke akutiphera anthu atimalizila uyu tiyeni pansewu
@JusticePhiri-x8e
@JusticePhiri-x8e 2 месяца назад
lord keep us safe, save your children
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 2 месяца назад
Kodi khani ikutero koma guys eeeee mpaka kutenga ma T-shirt a UTM koma Manganya Mulungu amuone ndithu kuphunzira njinga ya kapalasa kkkkkkk😂😂😂😂😂😂😂😂
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 2 месяца назад
Comrade pls musamaiwalenso kwa Munundo kwandauza kumakwasa mudzitipatsatso moni timakunyadirani Comrade
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 месяца назад
Kkkkk mnyengo zopalasa bicycle
@robertkabade5011
@robertkabade5011 2 месяца назад
Mr NTANYIWA mumakwana big man tiyende basi pa sewu is a best solution
@stevekomwa1609
@stevekomwa1609 2 месяца назад
Moto buuuuu
@MoosaSame
@MoosaSame 2 месяца назад
Big up bro ❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 месяца назад
Akumupusisa Chakwera kuti aziti Utm tilinayobe anthu amenewo ndi a MCP osati utm
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 2 месяца назад
God will expose the truth
@HendersonNambera
@HendersonNambera 2 месяца назад
Live chiradzulo Monday morning basi❤❤
@gibodadap-sley96mark92
@gibodadap-sley96mark92 2 месяца назад
Ntanyiwa ndiwe shasha kwambiri
@YammsyZebron
@YammsyZebron 2 месяца назад
Moni mtanyuwa from Middle East
@MPHATSOKALUWA-lm2uy
@MPHATSOKALUWA-lm2uy 2 месяца назад
Tinazionadi zmmez kut avala za utm
@PaulMwachande
@PaulMwachande 2 месяца назад
Akulu mumanena zoonadi taziona zodabwisa taziona zulo anthu omwe amakhala pasogolo ndi achipani cha mcp lelo anali kusogolo ndi ovala za chipani cha UTM kwinaku kuli angoni zodabwisa taziona zulo koma akunama ana achepa tionana 2025 bas
@StellaCharmer
@StellaCharmer 2 месяца назад
Ndipo ndinali aodabwa kuona atalava za UTM akuvina😂😂😂 koma ma plan ndiye amunthelatu chikangawayu
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 месяца назад
Comrade ntanyiwa mulungu azikudalisani
@blessingssaiti
@blessingssaiti 2 месяца назад
Best Limpopo ❤
@NumerFestonewidisson
@NumerFestonewidisson 2 месяца назад
Limpopo is the best
@saulbipa6882
@saulbipa6882 2 месяца назад
Yerrrrre anyanata inu mumalankhuladi zenizeni
@JoyceGowenPatel-w5h
@JoyceGowenPatel-w5h 2 месяца назад
God have mercy on poor Malawians
@AllanChabwela
@AllanChabwela 2 месяца назад
Ndikuona kuchedwa kucha 😊
@RonaldodalitigerSpencerDaliRic
@RonaldodalitigerSpencerDaliRic 2 месяца назад
comrade ying'alureni kunja kawacha
@AlgentChilanga
@AlgentChilanga 2 месяца назад
Ipaseni moto ntanyiwa ife tiripano kunvera Inu kkkkkk
@Sabina-hw4js
@Sabina-hw4js 2 месяца назад
We can't wait for the report
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 2 месяца назад
ANtanyiwa Bakili muluzi TV nonse musadzafe mudzangosowa 😂😂😂😂😂😂😂
@Rose-wu5ef
@Rose-wu5ef 2 месяца назад
Chakwela atipha tonse tizichonse ng,ona izi pls
@Yungjoe786
@Yungjoe786 2 месяца назад
Kukamumpha handsome kusiya chi bucket cha munthu kkkkk
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 2 месяца назад
Nde mkumati chipani chachikulu chija chikuzivutiranji kumavekananso makaka a zipani zina,nde tiziti chani???
@Amgwagwa
@Amgwagwa 2 месяца назад
Lukuchedwa bwanji
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 2 месяца назад
❤ is good nice radio
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h 2 месяца назад
Nzoona 2025 kwatalika,,,,ameneyu achoke basi.
@YusufuMatiki-p4z
@YusufuMatiki-p4z 2 месяца назад
❤❤❤❤❤❤❤ Inu ndi wani
@YusufuMatiki-p4z
@YusufuMatiki-p4z 2 месяца назад
Antanyiwa timakukondan ngt mene ntimamukondera chirima🎉❤❤❤❤❤❤❤❤
@NtchindiChirwa-l8o
@NtchindiChirwa-l8o 2 месяца назад
Nonse okhala chigawo Cha kumpoto please athuwa asakunamizen zinthu zilibo heavy chakwera more fire anthu tikugula njinga zamoto ngat zaulere azathu akumwera anazorowera kupasidwa zaulere please osawavera tikasintha boma ovutika ndife
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 2 месяца назад
Vuto ndi lot inu simultaneously kumalawi nchifukwa chake inu mademoiselle omwe inu mukufuna sangatheke bwelani tizizayendela limozi ku madeemoko
@vincentchristopherbanda3748
@vincentchristopherbanda3748 2 месяца назад
I mean mukamayankhula nkhani zomwe ndiza serious. Simungamayankhule nkhani za infa ya munthu kapena ngozi at the same time ndikumasekaso. Ndimakutsani kwambili ndipo nkhani zanu ndimazikonda kwambili mulungu azikupatsani moyo wautali mr.
@evanschikwatu8733
@evanschikwatu8733 Месяц назад
Kd Inu galimot zayamba lero kuchita ngozi,? Kapena mukupangila kapeni munthu wazaka 87 mukunama palibe wina angapambane pachisankho chidzachi kuposa bwana chakwela, lmao uchedwa niumphawi kkkkkkkkkkkk aaaaaa!
@GiftKatawa
@GiftKatawa 2 месяца назад
Mtanyiwa udzatuluke 6am
@LovenessKapindula-t6e
@LovenessKapindula-t6e 2 месяца назад
Mumakwana bwana maso a malawi Ali painu
@EdnahShantell
@EdnahShantell 2 месяца назад
❤❤❤❤
@Malume2024
@Malume2024 2 месяца назад
Mwachita bwino report likufunika
@LukaThawe
@LukaThawe 2 месяца назад
Mbuzi iyi zamanye basi
@DalitsoMichongwe
@DalitsoMichongwe 2 месяца назад
UTM NDI BOMBAAAAAA💣💣
@eliaskhofielias8152
@eliaskhofielias8152 2 месяца назад
Report ikubwera after wina wake atapitako kukaviviniza za report yandegeyo mfiti chakwera.eeee koma munthuyu sanalidi m'busa he was a devil.ku u bishop kuja amakhalarako nyanga eeeh mkumati ndimunthu wamulungu.
@MaxWell-d7o
@MaxWell-d7o 2 месяца назад
Iponde fada🎉🎉🎉🎉
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 месяца назад
No musoro ,
@StainThika
@StainThika 2 месяца назад
Umakwana ntanyiwa
@DesmondTaulaye
@DesmondTaulaye 2 месяца назад
Ang'alure
@KassimSteven-j1z
@KassimSteven-j1z 2 месяца назад
Pamene abakalapa kwa papa mmmmm amukanako mmmmmh
@AMOSMBAWA
@AMOSMBAWA 2 месяца назад
Noseriwawo wuno olimbuli
Далее
BON KALINDO - MAI KALIATI MUKHALE OSAMALA
12:22
Просмотров 30 тыс.
General Election 2024: What's in store for education?
1:00:06
This is how Halo felt as a kid 🤣 (phelan.davies)
00:14
Temple Terrace Candidate forum 10-17-24
57:34
Просмотров 1,4 тыс.
A SULEMAN ndi ACHISALE KUYANKHULANA MOSAOPA
21:24
Просмотров 23 тыс.