Ayi koma mumatha kitumikila satana inu munakachipeza bwanji kumeneko 😅😅 eeeeeeeee kuli ntchito a Malawi amalawi kodi yesu atakupezani mukunena zopanda umboni mungatani osamvako mu mtima kuti ndikunenazi ndili ndi umboni? 😅😅 manyazi mulibe anthu inu work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die
Ukuyankhulawe ndi wa MCP. Apa ukufuna kusokoneza kafukufuku wa German. Chonde khala chete tose tiyang'anile chimene a German atanene, mukachulusa zokambakamba choona chenicheni chisokonekela chifukwa oganilizidwawo alibe pa ulamuliro wa ziko lino