Тёмный

RICH MPHEPO SAKUCHEZANAWO ULENDO UNO ZOMWE ZALAKWIKA CHICHEWA CHIKUPELEKEDWA MAXIMUM 

Malawi Trends TV
Подписаться 47 тыс.
Просмотров 3,7 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 26   
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 4 часа назад
Koma inuyo Richard mphepo umakwa big brother 🙌 💙 ulemu wanu mr man 👨 👏 god bless you 🙏 👍 be strong 💪 brother 💪 🙏
@MosesLackson-l4f
@MosesLackson-l4f 4 часа назад
You're really fighter salute your wisdom brother
@MandalaChaona
@MandalaChaona 30 минут назад
Straight talk brother. Ndipo Chakwera akuzipusisa yekha osati Malawi. Zomwe achita awonetsadi Uchitsiru ngati simtsogoleri wa Dziko. Kuli Chibwana Ku Bomako 😜😜😜 Zodiac Radio inagudwa ikudya nawo za ku Chikangawa 😜😜😜
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 4 часа назад
Sakuziwa zomwe akuchita azazindikila pasogolo too late mulungu ndie mwini chilungamo ndi mtendere sangatisiye Ife Monga ana ake
@GanhoGolli
@GanhoGolli 58 минут назад
Kuyankhula chilungamo❤
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 4 часа назад
That is true this government is sad anthu akuba awa kumadyeza anthu chiteze koma chikangawa akupsetsa mtima kwambiri we don't need this government again 😒 🙄
@alfredkanyawire3524
@alfredkanyawire3524 3 часа назад
He is indeed a freedom fighter look what is happening now m,bomamu
@alexsumani6823
@alexsumani6823 3 часа назад
God bless you too comrade Mphepo
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 3 часа назад
Chilungamo chiende ngati madzi,,chakwela ndewakhulu wakatangale mu malawi 🇲🇼 muno
@AllanChabwela
@AllanChabwela 44 минуты назад
Phala lenileni amwene
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 часа назад
Limbani mtima zoti muli ndi president Malawi muno dziko lomvesa chison uyutu simulomwe uyu akuyankhula apayu wina mumva Mphepo kuti mlomwe osaphunzra
@ChikupizgaKajawaMkandawire
@ChikupizgaKajawaMkandawire 57 минут назад
Kkkkkkkk
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 3 часа назад
MUMAONA NGAT NDINDANI AKUSOKONEZA DZILOLI SIOMWEWO MA JUDGE ANAMACHENDE OMWEWO ,AKATI ZIPEWA NGAT MAOFOZI AKHOSA AGALU AMENEWA CHILUNGAMO CHILIKUTI ? AGALU INU ? MULUNGU SIMUTHU
@spargomw
@spargomw 3 часа назад
I agree with you❤❤
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 часа назад
Wanena zoona apa koma anthu awawa sakudziwa kuti kuli Mulungu koz oopa Mulungu amadana ndi machimo
@MandalaChaona
@MandalaChaona 16 минут назад
Uchitsiru+ Uchimzete = Chitserekwete hahahaha ma push Ups Koma ndinaseka 😂😂😂 ife athu ndi mapemphero kwa mwini Namalenga MULUNGU weniweni Osati timilungu ta ku kasiyato babaric👹🔨⚒️⚒️👹
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 часа назад
Zodiak yake itinso ya MCP imene ija akusamala zakwao aja osati za Amalawi Zodiak manyaka
@ChikupizgaKajawaMkandawire
@ChikupizgaKajawaMkandawire 55 минут назад
Kodi RU-vid izingozaza ndi nkhani zanu zopusazi?? Inuyotu chakwerayi anabwela kudzakhala
@MandalaChaona
@MandalaChaona 24 минуты назад
😜😜😜👹⚒️🔨🐊🐊🐊👹 Chikangawa 😜😜😜😜
@ChikupizgaKajawaMkandawire
@ChikupizgaKajawaMkandawire 17 минут назад
@@MandalaChaona mumva kuwawa
@DanielKangozi
@DanielKangozi 3 часа назад
Kuyakhula kwabho
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 3 часа назад
Dziko la malawi lafika polilitsa ndi popsyesa mtima
@kasimmussa-c5v
@kasimmussa-c5v 3 часа назад
Ulemu wanu bg akwapulen 😂😂
@TofficSaid
@TofficSaid 3 часа назад
Akuopa umboni wandege chikangawa uyu
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 4 часа назад
Ulemu wanu big man wanena zoona
@ChikupizgaKajawaMkandawire
@ChikupizgaKajawaMkandawire 54 минуты назад
Zopusa basi
Далее
Свинья неудачник ( Liar's Bar )
24:01
Просмотров 493 тыс.