Тёмный

TAMVANI INU ZIKUCHITIA POMPANO A MOSES KUMKUYU AYANKHURA ZONKHUNZA MAFUTA NDIPO AKUTI ZILI MOTERE 

Makosana
Подписаться 111 тыс.
Просмотров 17 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 222   
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 6 часов назад
Ndiyemwe uja anatinamiza kuti Black box ilipo, ndipo yasungidwa pa malo abwino. Kenako ali mundege munalibemo black box. Tisamumvere
@Blessings-td4cr
@Blessings-td4cr 4 часа назад
Ndipo inu pantumbo pake uyu galu wachabechabe,,,ndi mfiti iyi ili ndi bodza.
@TaweniChavulaKamwendo
@TaweniChavulaKamwendo Час назад
😅😅😅😅
@beatsbymcstevens
@beatsbymcstevens 5 часов назад
this is a well-sophisticated briefing but we hope the implimentation stated will be followed as planned coz the issue is so out hand and the govt needs to react on immediate effect
@DominicMzumara
@DominicMzumara 2 часа назад
For me, it is lack of planning, lack of seriousness, lack of resilient measures. You should revisit your inventory management classes.
@kondwaniemapondo9106
@kondwaniemapondo9106 3 часа назад
Abwana kuzikola nokha chomcho, udindo unasochera uwu
@David-z9o4m
@David-z9o4m 46 минут назад
Kod mmwenye akuyankhulayi nde utinso?????
@WonderfulPrince-b9g
@WonderfulPrince-b9g 4 часа назад
Kodi mayi wakukamwa kong'ambika ngati kukamwakwa( ) alikuti? M'measa paja amati akukalandira mafuta ku mnsanje?
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 3 часа назад
Sunamve? Veselanso kut ngolo 30 za sitima zikubwela
@BrightonMchawa
@BrightonMchawa 3 часа назад
As a country we don't have enough source of foreign currency sitikuchita bwino
@FernasonMasiya
@FernasonMasiya 3 часа назад
Ine koma ameneyu amandinyasa kwambiri
@OwenMacheso-hd1ux
@OwenMacheso-hd1ux Час назад
Even me
@mbonilekisebe2286
@mbonilekisebe2286 Час назад
@@OwenMacheso-hd1ux me most
@BiliatMzungudala
@BiliatMzungudala 6 часов назад
Koma kunena zoona boma la mcp yatenga chinzonono
@MayamikoYMsusa
@MayamikoYMsusa 37 минут назад
Koma uchitsilu ,,siuposa apa,,(yendetsa dziko kapena restaurant?
@MagadaleneManjengwa
@MagadaleneManjengwa Час назад
Tiyeni tivomeleze Malawi 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 ilipamoto🔥🔥🔥
@ChristopherMasamba-bs5ms
@ChristopherMasamba-bs5ms 5 часов назад
Shaa pepani atolankhani poononga nthaw anthu awa akuchita koonekelaatu kut akubisa uthenga olondola omwe akubisila mafuta
@JohnChitenje-t8o
@JohnChitenje-t8o 2 часа назад
Inde madola akuyenela kusowa chifukwa mumaonongela maulendo aja kod mesa mumakapepha ndalama zamadola omwewo kunja ?
@AustinMachinjiri
@AustinMachinjiri 3 часа назад
Chitsilu chimenechi?
@P.Bilali
@P.Bilali Час назад
Koma naulendo opanda pake.. aaah inu mulikutali
@GiftMartin-o5y
@GiftMartin-o5y 3 часа назад
Press breafing ya kunkuyu ndiyopanda ntchito chifukwa ine dzulo Bakili Muluzi TV anatiuza dzulo with figures, however tikuyenera kumamvera BM TV not wabodza yu. These same krooks told us last 2 weeks kuti mafuta afika thru train koma sanagulitsidwe then tikumva kuti mafuta akusowa. What kind of nonsense government is this
@Steven-q4u
@Steven-q4u 5 часов назад
Mmm mwachulitsa maulendo Mozambique Zimbabwe Italy kuthera Germany folex yingakhalepo bodza. Kuchpka apo waku unga ndi likukukwel lopanda ntchito pano mafuta kulibe umbuli basi
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 2 часа назад
Wakamba fundo chabe wangolakwisa kunena kut mbuli. Mpila umakomela owonelela Chifukwa umakhala ukuwona mbali zonse bwino . Nde inuyo ophunzira mukulekelanji kut zinthu zikhale chonchi pamenepa mbuli ndindani pot inu simukufina kusogolela chosecho mukut ophunzila
@paulbanda9638
@paulbanda9638 5 часов назад
1Chakwera walephera,2 MCP kuba kwambiri, 3 chakwera kuyenda kwambiri 4 boma simunawine munaliba bomali
@NEBRA-lm7ji
@NEBRA-lm7ji 4 часа назад
Si bas mwavomeleza zija amanena wa Bakil muluz Tv zija kt dziko lino lili ndi ngongole zofik nkhos zija😂..apa waboza nndan?
@GilbertKuchipinda-w9w
@GilbertKuchipinda-w9w 3 часа назад
Ndinakakhala nawo kumeneko nkanafusa kuti.ma truck a staker chosecho munanena kuti njanji ku nsanje yatheka ndipo mafuta sadzivuta kubwera adzitenga 2 to 3 days.bwanji simunagwilitse ntchito stima kuti mafutawo abwele mwachangu?
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 2 часа назад
Pamenepo ndipamene mungadziwe Kuti amatinamiza Makosana amenewa
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 2 часа назад
Iwe kodi njanjiyo yikulumikizika kuchoka ku kukaronga mpanka ku sanje??? Kumene kulibe mafuta abwela pa tala
@AvideOfficial
@AvideOfficial Час назад
Ndaidandaula bundle yanga povera iziii😭
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 3 часа назад
Tisowa mafuta mpaka liti. You guys must GO. Mwatiwonjeza
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 3 часа назад
Nde mukuganiza ndani angalongosele zimenezi pakalipano pot sitinavote. Usamangoyankhulapo mfundo zosamveka apa muzimvesesa zinthu zikamachitika
@TonyMhone
@TonyMhone 3 часа назад
Hey hey hey!!!! They want us ti feel stupid. Hey hey hey!! They want us to think stupid. They told us things will be cheaper! They tikd us things will be easier!! Hey hey hey!!!
@RichardHetekere
@RichardHetekere 2 часа назад
Yomweyo aguru amenewa
@patesnkajenda4258
@patesnkajenda4258 24 минуты назад
Can connect nicely your mike is not connected good zomwe muganiza kut mpakana pano mulibe ndalama ko zoona zomwe mukuyendela maiko akunja mukuzitenga ku😂😂😂😂😂😂😂
@EdsonKamwendo-q2c
@EdsonKamwendo-q2c 3 часа назад
Uyu ndi galu kwambiri
@EphiehkariPhiri
@EphiehkariPhiri 6 часов назад
Mbuli zophunzira 😢😢😢
@MrMagombo
@MrMagombo 4 часа назад
Bola kumvera Ntanyiwa
@SteveNdhlovu-r2x
@SteveNdhlovu-r2x 2 часа назад
Bwana kunkuyu commission of inquiry ya imfa ya chilima ikhalako liti? Anthu olephera
@FredoAbud
@FredoAbud 5 часов назад
Bakili muluzi TV woyeeeer😂😂😂
@JaffaliShaibu
@JaffaliShaibu 41 минуту назад
Agalu awa alibe manyazi. Kodi si aja posachedwapa amatinamiza kuti mafuta abwera ambirimbiri kudzera pa sitima ya pamtunda awa?
@PatrickMbenje
@PatrickMbenje 55 минут назад
Agalu Inu simati mafuta munabweresa pa sitima Inu pamtumbo pa manu
@FleasherIshmael
@FleasherIshmael 3 часа назад
Wosapereka ndalama mukugawa misonkhano muja bwanji
@henryibrahimsailes4638
@henryibrahimsailes4638 4 часа назад
Awawa kuganiza kwawo bolanso mwana ophunzira kulankhura amakhala ndi mnzeru zokwanira why my malawi why please God helps us 😭😭😭
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj 3 часа назад
Bwanj omadanna ndi mtanyiwwa together with bm TV nkalindo everyone amenne amanena soona Sam mcp taonan akukuyu sinkale ashimwendo manganya phamodsi ndi shinkangawaw mapasipot afegi mafuta njalla ngani yowonad nkwar amalawi sonkusana ndege mwabisa commission of equally simukunena nkandu sonkusa ashilima phamodsi ndi andu 8 bwanj shinkangawaw 2025 nkulibe mcp 😅😅😅
@LoydMcheleka-uq3ix
@LoydMcheleka-uq3ix 5 часов назад
Minster zimene zimavutani ndimatama , kuteleku mkunena mabiza okha okha😢 😢
@mbonilekisebe2286
@mbonilekisebe2286 Час назад
Mapazi ako kunkuyu... Dziko ili analenga ndi Mulungu. Unalipeza ndipo udzalisiya
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 2 часа назад
Anthu inu opweteketsa mtima osnama,munabwera kudzaononga osakhala kutumikila a Malawi ayi,press briefing iyiyi ndikungosewera ndi a Malawi. Chifukwa palibe chikumveka apa.kuba kopanda nako manyazi
@VeniceKan-y9q
@VeniceKan-y9q 4 часа назад
Koma uyu wamakwiya khope amandikwiisa ndikamamuona
@leejuma7058
@leejuma7058 Час назад
Ngati chikundivuta kumva chichewa nanga kwenikweni chizungu zindithera bwanji
@HopeMakoka
@HopeMakoka 3 часа назад
Frm today onwards you guys muphunzire kuyankhura n mukamayankhura mudzidziwa kuti ku mwamba kuli Mulungu, munatha mau mmene ankalamulira anzanu aja lero ndi izi zafika pa wes phunzirani kulemekeza kumwamba
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 2 часа назад
Ndale ndimumene zilili suyenela kuyamilila boma limene likulamula pamene inu muli kosutsa chifukwa mumakhala kut mukugulisa anzawo next voting nde uyenela kumatsusa basi
@henryibrahimsailes4638
@henryibrahimsailes4638 4 часа назад
Wake up malawi Wake up this is our beloved country no one should treat us like this we the citizens are not fools enough is enough people lets remove this evils they dont care about us people who put into power,people are suffering people are dying in the hospitals people are dying with hunger, what are we waiting for ????? We people have the power to remove this nonsense evils😈 we just have to stand up together we free ourselves from this lions malawi remember God says he helps his people who ask him for help, so let us work together and we will be free
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 2 часа назад
Wait 2025 koma pakali pano tikufuna mafuta
@MayamikoYMsusa
@MayamikoYMsusa 35 минут назад
Maulendo a utsi akuchulutsa ,,osatsa za neef
@Paul-q2p
@Paul-q2p 3 часа назад
Sitima ija mafuta anathela kuti😢😢😢😂 boza muleke
@InnocentMlowoka-ew4lo
@InnocentMlowoka-ew4lo 2 часа назад
Bakili TV anatiuza kale
@AdizzMadizo
@AdizzMadizo 5 минут назад
Kodi mukuyakhulana ndi ana anu kunyumba kapena muyakhula ndi amalawi anzelu zawo
@LuciusThomasi
@LuciusThomasi Час назад
Anthuwa ndiopanda manyaz etie kumangolakhula ngt zkumuuza mwana
@FRANKKANYINJI
@FRANKKANYINJI 53 минуты назад
mumawona ngati kuyendetsa dziko ndichibwana mwakanika basi
@MrPatrickDc
@MrPatrickDc 5 часов назад
Bakili muluzi tv ndi machine ndipo nduna yofalisa khani akadangomusakha wa bakili tv
@GiftZuze-ge1ne
@GiftZuze-ge1ne Час назад
Koma ine ameney sandisangarasa
@MuhammadAlie-u5n
@MuhammadAlie-u5n 4 часа назад
Km guys yawaya ndiathu kapena mizukwa
@Stewartchikoja
@Stewartchikoja 2 часа назад
Boma lalephela ndi bonza?
@blessingssaiti
@blessingssaiti 6 часов назад
Inuyo ngat mumaziwa kuti tilindimavuto okhuza. Ndalama zakunja nde ndichifukwa chani achakwera amatenga anthu ambili kupita nawo ku wuunga
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 5 часов назад
Ubwino wake mukuvomeza ku lepela kwanu 😂😂😂😂😂😂 chikangawa
@GrecianWyson
@GrecianWyson 6 часов назад
Mmmm Koma boma iriri kkkkk mulibe wazeru mu MCP Supt
@MaryNgola
@MaryNgola 3 часа назад
Ndrama mesa mukugura oimba dzitsilu mdzaanthu inu
@fattiemhone5621
@fattiemhone5621 2 часа назад
Chokani agalu inu mukapume mwakalamba sopano paliponse mukuyendesera boza paliponse.
@MphatsoPemba
@MphatsoPemba 55 минут назад
Kumanena ngati ife si akazanu kapena ana anu palibe mawu omveka apa kodi bambo inundinu munthu koma ufiti basi
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 5 часов назад
Kunkuyu usaone ngati Ndiwe dolo,takutulukilan mukava kuti kupangidwa mademo mumayamba mabodza ,koma pena pake ukanakhala umayenda pa matola kunkuyu l tell you ukadaona mmene anth akuvutikila ,akungokuombelani mmanja pazopusa ukulankhulazo chifukwa asauka alibe mau
@happynyirenda8790
@happynyirenda8790 Час назад
Kodi you telling us that you don't know your budget or kusewera ndi ife a malawi,mukuti covid 19 ndinu akumalawi nokha mukuziwa za covid 19 ndiposo bwanji osakoza mseu kuti galimoto zisayende bwino mu M1 zoona? Muli busy kuwononga ndalama za boma Kuba wina akumanga manyumba 20 plus aluzitenga kuti ndalama zo bwanji ku immigration ma passport mukupanga a fake? Bwanji mwana wa president ndi amene akutsongolera immigration? Musanamepo apa mukuba kwambiri mwalemera vote muzaonaso kuti tizavota bwanji enanu mufunika kukalhala kundende
@JovitastoloBridane
@JovitastoloBridane 5 часов назад
Kunkuyu uvomeleza kulephera sija mmanama kuti mwalandila mafuta pasitima pantumbo pake kunkuyu
@ISMAELNKWATULANKWATULA
@ISMAELNKWATULANKWATULA Час назад
Mwaba ndalama zamafuta agaru inu sipaja munkati mafuta abwera ambiri alikutino? akubwera kuti umanamiza a Malawi iwe
@WhyteSmart
@WhyteSmart 5 часов назад
Kodi mesa mmati mafuta abwera ngambwingambwi kkkkk komatu ohooo muziwopa Mulungu mukamayankhura boza lanuro
@PaulChafikirah
@PaulChafikirah 2 часа назад
Ndiwaboza nkuluyi asatitukwanitse uyu inu ndi munthu oipa tikufuna nkhani ya biyeni wathu ife
@mozesjackson6328
@mozesjackson6328 3 часа назад
Iiiiiiii kodi train inabweletsa mafuta 3 week ago ku nsanje ija mafuta anatha kkkkkk ma track analimbweee linali boza kodi kkkkkkk ayi fenks achinyamata athu mukuyendetsa Malawi
@AdizzMadizo
@AdizzMadizo 8 минут назад
Mesa ndalama mukungoba basi kuyambila chakwela chimwendo kunkuyu machende anu nonse mwanva zisilu za athu inu a mcp agalu mbuzi
@JeremiahKapundu-j1p
@JeremiahKapundu-j1p 6 часов назад
Mm km mupakura ndalama mmm mpaka pamenepo
@nelsonnkhambule6292
@nelsonnkhambule6292 3 часа назад
Vuto mukupakula madola kwambili muzisiyako pls
@MalumboMzumara
@MalumboMzumara Час назад
Kodi kusanje mkaka segulira chani? Komaso komwe mmaka kwela zinjinga kuja mmangopita basi? Kuno njinga kulibe?
@DambulenChris
@DambulenChris 4 часа назад
Boma loyendera katapira mukadzangoona bambo akukonda katapira dziwani kuti udindo wavuta
@MayesoCave
@MayesoCave 2 часа назад
Kodi mafutawo sakugulidwa, nanga mukhala ndi ngongole bwanji ngati geni sinathe....
@amosiabdulallh7965
@amosiabdulallh7965 Час назад
Kkkkkkk
@JohnFrank-cg1yh
@JohnFrank-cg1yh 3 часа назад
Anthu inuyo nthawi ikakwana kut maudindo anu ayimisidwa mukuyenera kukagwira ukayidi, panopo ndinu madolo koma timaudindo tikatha muwaziwa amalawi forsake
@corretabanda7685
@corretabanda7685 4 часа назад
Inu ku America mwapita kangati? Mumapita ndi makwacha kodi?
@JacklineNiwahereza-ni3pm
@JacklineNiwahereza-ni3pm 5 часов назад
Mwalephela a mcp and u know it the truth shall set you free
@hassanfaizadaffer2421
@hassanfaizadaffer2421 Час назад
Koma Inu simusowa zolakhula ma mafia ayi zikomo oyera ndinu
@raphaelsamala3792
@raphaelsamala3792 2 часа назад
Ma 2 thousands omwe mukugawa mmisonkhano zijatu ndizokwana kuthesa zonsezi.koma inuyo busy ndizopanda ntchito
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u 3 часа назад
Mafuta asowa chifukwa chakatangale Uchitsiru basi
@LufeyoMlumbe
@LufeyoMlumbe 4 часа назад
😢Nothing comes inside from out side with kwacha's
@MacDonaldWonganichibaka
@MacDonaldWonganichibaka 6 часов назад
Zakukanikani nonse ku Bomako kuli bwino kumvomereza kuti ai talephera ife kuyendetsa dziko zatikulira tachepa nazo 😢😢😂😂 azanu atenge boma ilo.
@DennisTobias-b4r
@DennisTobias-b4r 2 часа назад
Koma pena kuvomereza kuti mwalephera, a chakwera ndi nduna zanu vomerezani kuti Malawi wakukanilani
@LastonMmanga-r2u
@LastonMmanga-r2u 5 часов назад
And ku UNGA simupita ndi MA kwacha, lero chiyambileni MCP bodza lokha lokha opanda chimodzi chokha chowona abale???? This is the worst and shit government serious. 😢😢😢
@GabrielMunkombwe
@GabrielMunkombwe 4 часа назад
Kkkkkkk imwe serusani vithu imwe mwakangiwa
@mpondakaluma2252
@mpondakaluma2252 Час назад
komatu pena anthu musamatenge ngati zisilu iwe Mozes mwayiwala kuti mwatinamiza kuti ma sitima abwelesa mafuta ambili komanso koti ndiye kuti ku MCP kwanuko oziwa boza kwambili ndinu iwe kumkuyu mbnuzi yamunthu tatopa nawe
@SaidSamuden
@SaidSamuden 5 часов назад
Mafuta akumakiza manganya kuyenda nmisika kumakalawa chinangwa kuyenda bawo
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 4 часа назад
Ndiyentchito ya njanjiyo ndichani munati idzinyamula mafuta mesa 😅😅😅😅😅😅😅
@JohnAmanu-p5d
@JohnAmanu-p5d 4 часа назад
Koma agalu awa ndiye atisuza kwambiri koma kuba ndalama nde number one palibe chimene tingave apa boma ili lolepela andiso lalepela boma lolepela kuyendesa ziko koma katangale nde number one agalu inu musiona chaka cha mmawa nditu
@SueWahna-y8m
@SueWahna-y8m 4 часа назад
Mbuyako suja amakwera njinga kunja uja zot mavuto awawa akhalapo amaziwa ndithu😮 bus kukwera 500 popita pobwera 700 kwacha panopa tikufanana ndiya Tanzani ndenge kukwera 680 thousand kupita tanzania lero at 890 thousand kod mufuna amalawi atan tsopano
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira 4 часа назад
Kunkuyu kungo tenga udindo umeneu kungo kalambilatu mwana wakwa Manase kampala BT pano aa akamaya khula ngati alipampando wandalema
@GitfIobodo
@GitfIobodo Час назад
Kunkuyu machende anko
@AdizzMadizo
@AdizzMadizo 11 минут назад
Kukuyu ndichisilu kwabasi
@Arafuledi
@Arafuledi 5 часов назад
Akukuyu kupusa mukumbukole kt zomwe mukuwapanga amalawi muzabweza ndipo muzose zomwe mwapanga kumalawiko pazafunika kt mubweze
@NgeyasjuWadeya
@NgeyasjuWadeya 5 часов назад
Kodi mukuwatenga ngati amalawi ndi opusa?? Mukuona ngati zoti boma lanu Mcp ndalama mukungoongera zopusa mukuona ngati sitikudziwa?ndalama a zochuluka munakathera ku UNGA mwaiwara kaletu,, apa muzitiuza mbwerera zoti mukungongola dzindalama mkumangothera mmatimba mwanu mukuona ngati sitikudziwa? Fotseki
@MaggieBanda-ft5tu
@MaggieBanda-ft5tu 6 часов назад
Boni kalindo even tanyiwa,adanena idzi,chakwela kusamva,ndalama dzawonongedwa chifukwa chamawulendo opanda pake
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 5 часов назад
Ndalama za kunja mumathela maulendo akunja a President ndi magulu a chipani, za ziiiiii! President osajintha pansi matako!
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev 3 часа назад
Mbuzi
@ChimzyWesley
@ChimzyWesley 4 часа назад
Mafuta mukangongolamukagulitsa muja mmalo mobweza ndalama Kwa eni ake mukugulira oyimba, kugulira andale komanso kuyendelayendela zopanda pake mbuzi za anthu
@allangerson4367
@allangerson4367 4 часа назад
Kodi akapangitsa press briefing ndi ndalama zingati
@JohnAmanu-p5d
@JohnAmanu-p5d 4 часа назад
Boma longosatza ndi mavuto oka oko 😂😂😂😂😂 koma mcp ndiyovesa chisoni kwambiri nditu njala kugwesa ndalama kukwela kwa zinthu ma passport komaso ma passport vegi mavuta kusowa thawi iliyose china chilichose ndichosokonekela ndiye chitukuko cha mcp chimenecho iyhoo mavuto ndiye tilinawo
@edsonndalama2334
@edsonndalama2334 Час назад
Forex mukuthera kuyendera maulendo opanda phindu, mukungonyamulana mudzi onse nkumakasewera mmikumano yopanda phindu mmayiko a kunja, osalabadira zosatira za kusasamala kwanu. Tikuvutika chifukwa Forex ikuthera maulendo okanjoya kunja. Kutereku mmene week ikuthamu musanatuluke , musanakwere ndege, mitima yanu ikudumphadumpha ngati mwanyamula chamba. Clueless regime
@MikeSymon-si8dw
@MikeSymon-si8dw Час назад
Avomereza pano kut ndalama zakunja mziko mwathu mulibe???? Aaaaa pano mwaulura kut ndalama sanapatsidweee ??? Aku nsanje aja alikut pano hahahha malawi wanga eeeish mavuto alipo bas aaaaa
@JosephKuyeli-rc9on
@JosephKuyeli-rc9on 3 часа назад
Patiently thinking of Gospel Kazako ankatinamizanso choncho lero Ali kuti
Далее