Тёмный

THE COURT (Malawi) 

Malawi News Update
Подписаться 34 тыс.
Просмотров 59 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

16 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 64   
@BrownBanda-q3t
@BrownBanda-q3t 18 дней назад
Kkkkkk onsewa ndi akambelembele
@RoycBeza
@RoycBeza 4 дня назад
Abambowo ndakapsali
@mathiaskampira2171
@mathiaskampira2171 14 дней назад
Bamboyu ndinamuwona mu case ineso..aaaa
@MaNisha-v4c
@MaNisha-v4c Месяц назад
Ineyo maganizo anga ndioti banja lisathe coz nowadays most of man's salola kupelekeza mkaz ku scale pamapeto pake akapezeka mzimai positive amat nzimai ndi amene anali matenda 😢😢😢komano polowa banja tiziyezetsa kaye tonse
@GrecianWyson
@GrecianWyson Месяц назад
Chigemulo tizichiva please Kuti tizidziwa kuopsa kwa milanduyo please 🙏
@WeziChioni-d6u
@WeziChioni-d6u 11 дней назад
😂😂😂😂😂
@miloslundu6366
@miloslundu6366 Месяц назад
nkhope ya bambo odandaulayu ikufanana ndi amene mnamuonaso akuimira ngati mboni pa mulandu winae
@faithmbewe7384
@faithmbewe7384 Месяц назад
Eya mesa ndi sewero
@DoreenKaunda
@DoreenKaunda Месяц назад
Ah aaaa kodi sizikhala zenizeni izi?ndi sewero chabe?
@wittinessnkhokwe
@wittinessnkhokwe Месяц назад
Ili ndi sewerodi chabe ndimadabwatu ine
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo Месяц назад
Kod khaniyi imakhala yaboza eti kkkk anthu ena omwe akumagwilisidwa tchito umu amakhalaso munkhani ina a
@SliviaGosten
@SliviaGosten Месяц назад
Ine chothela banja apa sikuchiona 😅😅😅😅 ndiye mutani poti mwakatenga kale 😅😅😅
@LydiaBanda-le8il
@LydiaBanda-le8il 20 дней назад
Onse akumwa ndiye asiyaneso aaa kaleleni Wana apa ....abambowa ndiolusadi ukhoza kusowa poyambira eeee mwayalutsana kale musazuzitse Wana apa Zikhozaso kutheka abambowa akuthawa udindo acourt tithandizeni😢
@StellaSithole-w5e
@StellaSithole-w5e Месяц назад
Banja lisathe palibe chifukwa apa nonse matendawo ndiye muli nawo kale
@ishmaelimani3779
@ishmaelimani3779 Месяц назад
Khani yachichewa muzunzikilanji kuyizenga mchizungu? 😅😅😅😅
@KayanjeBanda
@KayanjeBanda 16 дней назад
Zikuchitikadi
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 2 месяца назад
😱😱😱😱😱😱
@RasuruArisu
@RasuruArisu Месяц назад
Kkkkkkkk😂😂😂😂😂😂
@ShadreckMtepuka-sj8ue
@ShadreckMtepuka-sj8ue Месяц назад
Apapa zifukwa zothera banja zilipo komanso palibe nkhani ndi munakumana atambwali nokhanokha
@user-bq3xk1dg5y
@user-bq3xk1dg5y 24 дня назад
Banja lilipo chifukwa onse ngofanana
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 Месяц назад
Kani khothili ndi drama ? I thought it was real. Nzimaiyu anabwelanso apa kusumila a zinzake.
@VirginiaKuseli-du3bp
@VirginiaKuseli-du3bp Месяц назад
Anthu ake ndiomwewo, abambo analinso ndi mzimai wina, nde ku court kumakomeratu😂😂
@etomansailes4932
@etomansailes4932 Месяц назад
Ndizimenezo kuyamba mwagonana osakayezetsa
@EmmanuelMleme
@EmmanuelMleme 8 дней назад
O 16:48
@SabinaSandless
@SabinaSandless Месяц назад
Ineyo ndikuona ngati abambowa ndiomwe anakatenga matenda,and kumwa anayamba ndi iwowo ,nanga nchifukwa chani anakana kupita kuchipatala,mmaganizo anga ndikuona ngati anali akumwa kale,apa zikuonetsa kuti mkazi samufuna
@GracenangozoChalusa-ef2ix
@GracenangozoChalusa-ef2ix Месяц назад
Izi sizowona anthuwa akumakhala omwewo omwewo
@Micah-ng9en
@Micah-ng9en Месяц назад
The thing is bambo analakwisa kubisa kut akumwa ma erv coz zimenezo zikuonesa kut bamboyo samayenda boh amakayikira kut edzi yo watenga kwina kwake osat kwa nkazi wakeyo..coz akanakhara kut wadabwa nazo akanamufusa nkazi wake kut edzi yamupeza bwanji 😅😅😅
@AishaChibwana-b8o
@AishaChibwana-b8o Месяц назад
Inu ndi ma drama awa ndaonera mboni yakuchikaziyu😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@richarddimba-q4m
@richarddimba-q4m Месяц назад
Zachibwana heavy
@MumderanjiMbiza
@MumderanjiMbiza Месяц назад
Program yi ilibwino kobasi
@user-mi8cx2qz7n
@user-mi8cx2qz7n 29 дней назад
Chimamuna choipa wakatenga matenda kumpasa nkazi lero akuti banja lithe ukufuna udzifalisabe kwa anthu ena
@EnockMandawala
@EnockMandawala 29 дней назад
Christina ndanken
@Joydee1999
@Joydee1999 Месяц назад
Ma ARV
@CHAPITASINGINI
@CHAPITASINGINI Месяц назад
Km muphana 😊😊 ma ARV anachita overdose
@StevenBwanausi
@StevenBwanausi Месяц назад
Mulowa bwanji banja musanayezese abambo
@SalabadaHamitoni
@SalabadaHamitoni Месяц назад
😢😢😢😢😢😢
@etomansailes4932
@etomansailes4932 Месяц назад
Km mboniyi ndiwanzeru kwambiri
@user-sd4jx9oj6m
@user-sd4jx9oj6m Месяц назад
Funso mkumat pa ana awiri sanakayezesepo pokayamba Scale??? 💔💔💔💔💔💔
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w Месяц назад
Banja sakakamiza banja ndi athu awili wina akati sindikukufuna vomeleza chifukwa ukhoza kukhala kapolo ndi iweyo okakamila mwinaso kukupha kumene
@GeorgeKanyama-u7p
@GeorgeKanyama-u7p Месяц назад
Kodi iyiyi ndi program kapena zoona zenizeni
@lecksongift
@lecksongift Месяц назад
🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@henrymalepula2934
@henrymalepula2934 28 дней назад
Kodi mmalankhula chizungu chifukwa chani ???
@MerryWayson
@MerryWayson 2 месяца назад
Kkkkkkkkk Zaka 5 mpaka ana awiri mkuzaziwa Chaka cha 6 kut mkadzi akumwa ma ARV kkkkk ndenoso mkumathesa banja kkkk vomelezani mumakana kupita kukaezesera kkkkkkk ndaikonda program imeneyi kkkkkk
@sayidimisessa
@sayidimisessa Месяц назад
Tikuphunzira nzeru
@user-eg5io6mt4t
@user-eg5io6mt4t Месяц назад
😂
@RosieKayamba
@RosieKayamba Месяц назад
Kkkkk koma
@mustaffahhemmad
@mustaffahhemmad Месяц назад
Ife tikufuna chigamuro asat nkhani chabe
@ChikondiSekani
@ChikondiSekani 29 дней назад
Ine ndaona kt mkaziyo ndioipa kwambili banjalo lithe
@JonathanMtungama
@JonathanMtungama Месяц назад
Here there is no reason kut banja lithe coz bambowa nawonso atayamba kumwa mankhwala sadawauze akazi awowa ay that is means kut chifukwa chomwe bambowa sadawaziwisile akaz awowa ndchomwenso mayiwa samawaziwisila amuna awowa
@KennedyGrem
@KennedyGrem Месяц назад
Atambwali okhaokha awa
@WasiJala
@WasiJala Месяц назад
Palibe chifukwa apa sakakani chifukwa china a bro
@CleJohn-v6z
@CleJohn-v6z Месяц назад
Nditangonva ai l rush to the comments😂😂😂
@FredrickMaunje
@FredrickMaunje Месяц назад
16:27
@nancychatha12
@nancychatha12 Месяц назад
Mamunayu naye amamwa ma ARV Mobisa thas y anakana kukayezesa HIV mkazi wake ali ndi mimba anali akuziziwa kale status yake kuti silibwino
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo Месяц назад
Ndie palibe chifukwa chothera banjali
@zainabchikakuda6297
@zainabchikakuda6297 20 дней назад
Tiyeni nazo.zili bwino kwambiri
@kondwamlungu8384
@kondwamlungu8384 Месяц назад
Chifukwa chilipo chothele banja chilipo
@edwardmwanza5778
@edwardmwanza5778 14 дней назад
Is this acting or reality?
@IsaiahYenga
@IsaiahYenga День назад
Acting boss
@user-dh8ho2qt4h
@user-dh8ho2qt4h Месяц назад
This is shaminess case 😢
@AllanWilsonbanda
@AllanWilsonbanda Месяц назад
Jesus Christ thupilanga ladzala madzi zoopsatu
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 2 месяца назад
wamuna zamuvuta
@BlessingsNamaja-e4l
@BlessingsNamaja-e4l 20 дней назад
😂😂😂
Далее
THE COURT..(Malawi )🤔
20:45
Просмотров 229 тыс.
THE  COURT (Malawi)
24:40
Просмотров 56 тыс.
Russian soldiers get chased by Ukraine drone
00:28
Просмотров 66 тыс.
Как мы играем в игры 😂
00:20
Просмотров 150 тыс.
Kucheza ndi wa Sataniki Mpakana Waziwulula Yekha
20:20
Просмотров 158 тыс.
FREDO MASINTHA
12:07
Просмотров 22 тыс.
Mfumukazi comedy series 28 August 2024
27:49
Просмотров 46 тыс.
@HeadmanChigodora Kuita bhizinesi nemukadzi
45:29
Просмотров 15 тыс.
Mr Jokes "WACHAKE COMEDY SERIES" episode 6 (Full Video)
15:12
MALAWI COURT...(PART YOTSATIRA)
23:39
Просмотров 10 тыс.