we dont blame anthu omwe amamanga nyumba malo oletsedwawo, goverment nayo muli anthu opelewera nzeru, munthu wamanga nyumba mu area yangozi komaso yoletsadwa then government is coming to give them water and electricity, its like giving them go ahead, we joke a lot here, amene akamangeso nyumba in such areas dont give them water and electricity thats all
Weldone mr brian banda runningmate of peter muthalika 2025 election mnyamata wa certificate yokuba kkkk tinanva tokha kazako akukuyankha thats y umamuda heavy koma pakazako sungamake ali ndi kanthu mzako uja olo umamupangira nsanje mtolankhani wa njala yandale