Тёмный

Timothy Mtambo wapita ku AFFORD; Wadzudzula Chakwera kwa Chinsapo; 1 May 2024 

Bakili Muluzi TV
Подписаться 130 тыс.
Просмотров 38 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

4 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 219   
@collengoma6542
@collengoma6542 5 месяцев назад
ine aliyese osutsana ndi chakwera i like it chifukwa dziko layipa kwambiri ndi satana chakwera
@EnochleonardMwale
@EnochleonardMwale 5 месяцев назад
Nyamuka pita kumwamba
@FlorenceBenara
@FlorenceBenara 4 месяца назад
Bingu Mutharika simumuchose anachita kumwalila ndiye musamayankhe zopusa afford
@FrancisDay-br7xb
@FrancisDay-br7xb 5 месяцев назад
Amalawi teyeni tipepese APM pakusadziwa tinaombela mfiti manja
@RiteRoderick
@RiteRoderick 5 месяцев назад
Ndipo zoopsa zedi nkhani ndi APM basi
@yvonneuwera2661
@yvonneuwera2661 5 месяцев назад
Koma abale......ndalama zata afuna zina
@RiteRoderick
@RiteRoderick 5 месяцев назад
@@yvonneuwera2661 🤣🤣🤣Eyaaaaah abenso misonkho yathu Mtambo wadya misonkho yathu yamuthera ndie akufunano panopa inaa🤣🤣
@AllanChabwela
@AllanChabwela 5 месяцев назад
Dpp come again
@RiteRoderick
@RiteRoderick 5 месяцев назад
@@AllanChabwela Yes ndiomwe angachilitse Malawi wathuyi basi kumbukirani zinthu zinalili bwino munthawi ya Adad brother, katundu kutchipa koopsa zedi
@RiteRoderick
@RiteRoderick 5 месяцев назад
DPP pachiongolero wina afune asafune basi ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@EnochleonardMwale
@EnochleonardMwale 5 месяцев назад
Maloto a chumba 😂😂😂
@buttbutt6690
@buttbutt6690 4 месяца назад
Baba woyeweee🎉
@JamesMatupi
@JamesMatupi 5 месяцев назад
AFORD singawine ayi ikuchepa
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 5 месяцев назад
Ndipo kwambiri
@BerthaMkwinika-e7s
@BerthaMkwinika-e7s 5 месяцев назад
Ntambo AMBUYE akukhululukire,ndipo chikumbuntima chikutsutse
@EvanceSungani-cv9jk
@EvanceSungani-cv9jk 4 месяца назад
Nfiti sikumbukla zmenezo,,,,,mulungu wake ut
@JervisDicksonMzinda-vu9vr
@JervisDicksonMzinda-vu9vr 5 месяцев назад
MTAMBO IS A GREAT MAN. HE JUST NEEDS RIGHT , QUALIFIED PEOPLE TO WORK WITH.
@edwinchimbuto
@edwinchimbuto 5 месяцев назад
Stop smoking whatever you have been smoking.. its not good for logic
@edwinchimbuto
@edwinchimbuto 5 месяцев назад
I blame anthu anazazawo nkumamunvera kapeyu
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 5 месяцев назад
Apm my vote
@noelmunthali3516
@noelmunthali3516 5 месяцев назад
Kamuzu was not dolo pa economy the country was too poor during his tenure please Mtambo get some knowledge
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 5 месяцев назад
Ankatidyetsa chimanga cha yellow kamuzu antambo longosokani
@CharleyAllain
@CharleyAllain 4 месяца назад
How old were you that time of Kamuzu before i go further?
@Johnybegood260
@Johnybegood260 5 месяцев назад
I think Malawians dont know what they want
@Dytopoemist
@Dytopoemist 5 месяцев назад
We have alot of dramatists in malawi
@FahardIslamZikajaanard-bq6fh
@FahardIslamZikajaanard-bq6fh 5 месяцев назад
m'bhulundi uyu guys osamukhulupilila walah tiyeni tiyike giya Kwa Bon Kalindo ❤❤❤
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi 5 месяцев назад
Brund uyu opanda dzeru wamoyo sayamikidwa apm ndimwamba akutchula kamuzu , achakufwa chihana chifukwa Ali Manda akanakha kuti apm anakakhala Manda anakayamikidwaso , galu opanda dzelu abwelele ku brund ameneyu
@DicksonBlack
@DicksonBlack 5 месяцев назад
Okey mulungu akafuna aku chose pabwino amatelo
@JannatuyaseenmwangaMwanga
@JannatuyaseenmwangaMwanga 5 месяцев назад
Ulemu wanu brother ❤
@HamzaAyame-ch3et
@HamzaAyame-ch3et 5 месяцев назад
Mwasowa zochita yeti agaruyinu NoNo 🙅‍♂️ 😂😂😂😂😂😂😂
@AllanChabwela
@AllanChabwela 5 месяцев назад
Makape
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 5 месяцев назад
Koma nzeru ikasowa umunthu suonekadi, akungoonesa uchisilu kukhala wa nzeru sungayimeso pa gulu
@JEFFERYJUMA
@JEFFERYJUMA 5 месяцев назад
DPP woye kkkk noses
@jameschibisa1433
@jameschibisa1433 5 месяцев назад
AFORD singamake at moment kuyaka next year mark my word I like Atupele's fundermentals
@josephchitsulo5882
@josephchitsulo5882 5 месяцев назад
Iya! Mobile yako kwambiri chitsilu iwe, ndiwe dolo wachani mbuzi yamunthu iwe
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 5 месяцев назад
Good message ❤
@ShadyDaHustler
@ShadyDaHustler 5 месяцев назад
My Tv ever❤❤
@edwarddickson501
@edwarddickson501 5 месяцев назад
Nde chikhulupiliro chako ndichochepatu bwanji Mulungu yemweyo sanakuze zamavuto akutsogolo ngati omwe tikukumana nawo panowa bwezi dziko lilibe mtsogolelitu ndiye
@RiteRoderick
@RiteRoderick 5 месяцев назад
APM woyeeeeeee
@NaytureChanthunya
@NaytureChanthunya 5 месяцев назад
Every finish line is a beginning of a new race.....nothing new apa.....
@maulidisaidibugudadi4091
@maulidisaidibugudadi4091 5 месяцев назад
Watching from Kenya pa Boma
@duncainjimmy
@duncainjimmy 5 месяцев назад
Amtambo apa mwalowatu kale ku ndende ponena kuti Bingu munachotsa nokha pachifukwa choti anayamba zakezake . Amtambo zikuonekeratu apa kuti muli mgulu lokupha Bingu yeti ?😢😢
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 5 месяцев назад
Iwe Simalawi amalawi tavutika chifukwa cha iwe ndi chilima
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 5 месяцев назад
Good message
@cliffsowernie59
@cliffsowernie59 5 месяцев назад
lets try this one
@lyiemax
@lyiemax 5 месяцев назад
Better AFORD than MCP
@edwarddickson501
@edwarddickson501 5 месяцев назад
Koma nde bola iwo anabela zisakho osati zomwe inuyo munapangazi mwapangitsa anthu kuba ndalama ndi dziko lomwe
@yvonneuwera2661
@yvonneuwera2661 5 месяцев назад
Let's make this comment viral.... How very true you are my brother!!
@LeonardEnock-e1t
@LeonardEnock-e1t 5 месяцев назад
Koma dzikoli sitili serious koma 😂
@RiteRoderick
@RiteRoderick 5 месяцев назад
Afford simungazalamulire dziko or pang'ono
@MacmillanMakombe-sz4iy
@MacmillanMakombe-sz4iy 5 месяцев назад
We love you
@jamesgama5489
@jamesgama5489 5 месяцев назад
Anthu onse wachula apawa dolo anali bingu, anthu ena adyera akumpoto ndamene analisokoneza boma limene lija. Nkhani yama gay, ndi section 65 but with 0 budget bingu anayesesa R.I.P bingu.
@JervisDicksonMzinda-vu9vr
@JervisDicksonMzinda-vu9vr 5 месяцев назад
ANALI DOLO NDI GOODALL GONDWE , OSATI BINGU. SECOND TERM ATAMUCHOTSA GOODALL KUYIKA MULOMWE , ECONOMY INAYAMBA KUVUTA. AMAYENDETSA DZIKO LA MALAWI NDI ATUMBUKA.
@LawrenceSparta-wb9qv
@LawrenceSparta-wb9qv 5 месяцев назад
Angotaya nthw sangatenge boma amenewo
@BentryKumwenda-ze2gn
@BentryKumwenda-ze2gn 5 месяцев назад
Mtambo ndi dolo akuti game amayiwelenga ndekuti Aford ndiyophweka zidyani ndalama
@CosmasNahuwo
@CosmasNahuwo 5 месяцев назад
Ife amalawi sitikufuna munthu otimenyela ufulu cfkwa maso tilinawo ndipo m'malawi simunthu opepela m'mene mumaganizila Inu andale
@EmanuelMuotcha
@EmanuelMuotcha 5 месяцев назад
A Malawi tikamaombela manja tiziona chomwe tikuombela manja uyu ndi munthu oipa kwambiri choipa chomwe Dpp inarephela ndi chani unene kape iwe
@ImranWyson
@ImranWyson 5 месяцев назад
First comment ❤❤
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 5 месяцев назад
Akuba awa
@mosesskajawo9351
@mosesskajawo9351 5 месяцев назад
Stop dreaming, Afford singawine, there's no one mu Afford who can lead the government
@danielsaidi7230
@danielsaidi7230 4 месяца назад
Apulezidenti a AFORD chenjelani akulandani udindowanu zakazikubwelazi. Komaso akufuna mudzampatse uvaisi pulezidenti.
@innocentchirombo2073
@innocentchirombo2073 5 месяцев назад
Ipondeni fadah ❤❤
@LastonBiliat-j3y
@LastonBiliat-j3y 5 месяцев назад
Koma anthu mumalifunila zabwino dzikoli?
@Alabu-g6i
@Alabu-g6i 5 месяцев назад
Timakunyadila man kwambiri ❤❤ ❤
@MustafaLikaomba
@MustafaLikaomba 5 месяцев назад
Timofi wausilu walephela nthawi yoseyi
@CadiahMafen
@CadiahMafen 5 месяцев назад
Mtambo ndiwashekauy
@RonnexChalingana
@RonnexChalingana 5 месяцев назад
Mtambo akufuna kunamizaso anthu ameneyi mgalu Kwambiri
@MacmillanMakombe-sz4iy
@MacmillanMakombe-sz4iy 5 месяцев назад
Machende ake uyu. Alibeso MZERU, Battery mtumbuka
@WilsonLimited-fh1mz
@WilsonLimited-fh1mz 5 месяцев назад
Viva Bon kalindo the DCcccccc
@danielkamphekete1304
@danielkamphekete1304 5 месяцев назад
Hahaha ,azimai otengeka.
@LuckyKhonyongwa-pt7ck
@LuckyKhonyongwa-pt7ck 5 месяцев назад
Koma awa
@samdiverson9733
@samdiverson9733 5 месяцев назад
a timo zakuthela dollar etill sungati pusise adha APM woyee
@FrynessMoyo-to2du
@FrynessMoyo-to2du 5 месяцев назад
Good job mtambo
@JustinPhiri-kq2bb
@JustinPhiri-kq2bb 5 месяцев назад
Zikanganganani nonkha koma Mr Mtambo wachita bwino to come out MCP kuzavuta kubera ma vote
@FlorenceBenara
@FlorenceBenara 4 месяца назад
Ndipo mufune musafune arher peter akuwinanso
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 5 месяцев назад
Mtambo ndi chitsiru ife ndinganga ndi DPP
@LukaThawe
@LukaThawe 5 месяцев назад
Mbuzi yamunthu Timothy
@ImranWyson
@ImranWyson 5 месяцев назад
Best TV ❤❤
@ChristopherSapuwa
@ChristopherSapuwa 5 месяцев назад
Kape uyu
@KangombeMpha
@KangombeMpha 4 месяца назад
Nanga mtambo osangoyamba chako bwanji chosecho ukulakhulana ndi mulunguu
@NgongireMwakasungula
@NgongireMwakasungula 5 месяцев назад
Ndiwe Dolo wopusa komaso upite kwanu kuzambia
@mosesskajawo9351
@mosesskajawo9351 5 месяцев назад
Anthuwa dyera kwambiri.
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 5 месяцев назад
Where have been mr mtambo go back to ur mcp we need professor Peter Mthalika u were busy with chakwela when malawians r dieing with hunger
@NicholasMuriya
@NicholasMuriya 5 месяцев назад
Nayonso otandiza siko kkkkkkkk zabutanso APA m'bulundi kkkkkk
@FigoKayudi-l4w
@FigoKayudi-l4w 5 месяцев назад
Pamachende akowo iwe unagonaviweyo wadzuka 6 koloko athu atazdzuka 12 koloko nde ukuona palibe galu😢😢
@NqobileLuphahla
@NqobileLuphahla 5 месяцев назад
Boma lidziganidza za 2060 zikolomweli kapena mulindidziko Lani
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 5 месяцев назад
This guy angonamiza amalawi basi
@EvanceSungani-cv9jk
@EvanceSungani-cv9jk 4 месяца назад
Mmx zazi inuyo nd commander wanuyo nd mene munationongera tsogolo labwinoli inu
@johnsondamson6145
@johnsondamson6145 5 месяцев назад
Is mtambo Malawian? Coz akumveka mwachimbulundimbulundi mchocho
@MathewsNkhalamba
@MathewsNkhalamba 5 месяцев назад
Kape ameneyo ife zakezo sitikupanga nawo
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 5 месяцев назад
Kkkkkkk kuli zinthu🔥🔥🔥🔥
@giftmasenti5732
@giftmasenti5732 5 месяцев назад
Ntambo asatizolowere, 2019 ankatiuza kuti chakwera ndi chilima ndianthu amene angatukule dzikolino, lero akutiuza zina aaaaa😂😂😂
@GorgeMachelani
@GorgeMachelani 5 месяцев назад
Muchedwa nazo izi simungawine ndi Kamtambo kakoko
@MwaiPotani
@MwaiPotani 5 месяцев назад
Ulibe fundo zonambga malawi ndi we wadyera, wakuba di ononga malawi. Takutuluka iwe.
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 5 месяцев назад
Mtambo 2025 October uzakhala uli mundende sua
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 3 месяца назад
Uyuyu ndi mchewa wodzi ndikira
@ZONKEMASEKO-rm5fn
@ZONKEMASEKO-rm5fn 5 месяцев назад
Basi tigoti 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@LuciusBanda-y9c
@LuciusBanda-y9c 5 месяцев назад
AFFORD Ili bho
@CharlesJustin-z9s
@CharlesJustin-z9s 5 месяцев назад
Iweyo waona pano kt amalawi akuvutika thawi yonseyi unalikuti ? Ukufunanso uliyike dzikoli pamavuta kawili ngt amalawi akuvutika panopa ndichifukwa Cha iweyo pochosa DPP iweyo ndi mbuzi yamuthu kwambili.
@AllanChabwela
@AllanChabwela 5 месяцев назад
Zaziiiii mukunamizana
@denndavie6041
@denndavie6041 5 месяцев назад
Mmayi Iwe Uhule sukupindulila. Unya ndi nfiti yakoyo
@denndavie6041
@denndavie6041 5 месяцев назад
Udolo kwanu konko
@jameschipula4475
@jameschipula4475 5 месяцев назад
From Johannesburg Kempton park
@samdiverson9733
@samdiverson9733 5 месяцев назад
chilima ndi chakwera wakoyo ndolephera adha APM woyee
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 5 месяцев назад
Ndipo kwambiri
@JusticeKawilira
@JusticeKawilira 5 месяцев назад
Mtambo ndi wodziwa kuyankhula koma ndiwaminyama
@JamesMatiki
@JamesMatiki 5 месяцев назад
AFORD uyu akuonongerani chipani uyu
@jamesgama5489
@jamesgama5489 5 месяцев назад
Comrade wachedwanayotu nkhaniyi, iwe mbuzi kwambiri umadilikira chani nthawi yonseyi.
@johnkays9581
@johnkays9581 5 месяцев назад
Kodi game ukunena ndi game yachi iweyo ntambo game chikwanje kapena game yobela anthu😮😮
@FanscioDancun
@FanscioDancun 5 месяцев назад
This guy has no truth in him
@FelixNyirenda-ll4xf
@FelixNyirenda-ll4xf 5 месяцев назад
But where was him all those days asabwere kuzatipomboneza agaluwa tivotele dpp basi
@KanguwoGift
@KanguwoGift 5 месяцев назад
Chakweraso amkayakhula chonchi siiwe oyamba a see now trust nobody
@jeffulejames3550
@jeffulejames3550 5 месяцев назад
Koma bushili ya neh
@yvonneuwera2661
@yvonneuwera2661 5 месяцев назад
Chichewa chachi Burundi basi.....Mbola yamunthu!!
@dicksonhangiwa7847
@dicksonhangiwa7847 5 месяцев назад
Mayi uyu ndi machine, dzina ndi ndani
@inamrigala
@inamrigala 5 месяцев назад
Ife tikuziwa km iweyo suziwa chomwe ukuchita Galu iwe WA kuruwanda
@KangombeMpha
@KangombeMpha 4 месяца назад
Koma mtamboyo aononga zithu kumeneko wabaiba kenako azinyoza zachamba
@SafariBvumbwe
@SafariBvumbwe 5 месяцев назад
ine kaya afford siyingawine km na chakwera yekha achoke amalawi sitingakhale chochi
@gabrielben-vj2eb
@gabrielben-vj2eb 5 месяцев назад
Zitsilu...tsek
Далее
Mbiri safuta; History is the best teacher
5:03
Просмотров 20 тыс.
ЭТО НАСТОЯЩАЯ МАГИЯ😬😬😬
00:19
When Goalkeepers Get Bored 🤯 #3
00:27
Просмотров 2,8 млн
Chifukwa Chimene Anthu Amamudera Miracle Chinga
11:55
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH ENOCK CHIHANA
56:27
Просмотров 59 тыс.