Chiphwanyatu mkazoyu amuthawa komano munthu akuyenda maiko chokakamira mkaz okut ali pa banja kale ndichani zinaz guys kumakhara serious zikuchitikatu zimenezi ndithu kumalimbana ndi mkaz wa mzako akazi onsewa kumeneko ndie kupusako akaz akukwera mapir kusaka mabanja chonsecho iwe ukulimbana ndi mkaz wa mwini aaaaaaa