Тёмный

TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 125 

Nkhalango Multimedia
Подписаться 20 тыс.
Просмотров 12 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 131   
@EsteryHassan
@EsteryHassan 5 часов назад
Kkkkk azinveka akaphuzise mwana masamu kma kkkkkk zione umatha size yomweyo anyamatawa amayelekedwa ❤❤❤
@StanleyKalavina
@StanleyKalavina 11 часов назад
Molly molly.. My guy umakwana.. Komatu naye mkazi wa molly you're the best you're talented..... Koma Bola fees usazayilire kkkkkk
@KumbukanJailos
@KumbukanJailos 5 часов назад
Koma zimveka ati zabwinobwino zabwinobwino😂😂😂😂😂😂
@billymhoni9527
@billymhoni9527 22 часа назад
My best. Comedy series in Malawi
@modiseusi4412
@modiseusi4412 21 час назад
Koma Molly wapeza 🤣🤣🤣🤣,, this girl she got talent guys...
@SayidiMisessa-x6y
@SayidiMisessa-x6y День назад
Funso kwa mayi Phiri: kodi Aphiri alikuti,?? Komaso kodi mukazapita kwa Azinveka mukuganiza kuti zikathabwanji awiriwiri?
@LucyKaduya
@LucyKaduya 11 часов назад
Good job guys ❤❤
@EbrahimZahra-f4r
@EbrahimZahra-f4r 4 часа назад
Kkkkkk❤❤❤❤
@MatembaNevermind
@MatembaNevermind 5 часов назад
Muthinda umakonda zosokesa kod ndwe tailor? Muthindayu Nd wanyanga KKK Gagaaaa❤
@ApatsaAnderson
@ApatsaAnderson 7 часов назад
Best comedy movies of Malawi
@CeciliaMaliwa
@CeciliaMaliwa 7 часов назад
Koma mai mphili amunanu amadziwa kuti ndinu egets 🤣🤣
@fatsanibanda5733
@fatsanibanda5733 7 часов назад
mai phiri ndi mwana wawo ali pachiopsezo ndi azinveka 😅😅😅
@billymhoni9527
@billymhoni9527 21 час назад
Muthinda apusisidwa kusunga munthu ndi nkazi wake.....kutengaso mimba pa khomo pake...
@Kelvin-hj5qv
@Kelvin-hj5qv День назад
Kkkkk km aziveka akut amaphuzitsa Masamu kkkkkk 😂😂
@samsonseleman9711
@samsonseleman9711 10 часов назад
Zinveka galu kwabasi😅😅😅😅😅😅😅😅 mission wamaliza wenkha
@modesternyoni711
@modesternyoni711 7 часов назад
Koma zimveka eeeeeee ...kkkkkkkkkkkk
@IshmaelWilliam-q7k
@IshmaelWilliam-q7k 8 часов назад
komatu ziveka akhalike ashamila ndiy zawavuta kkkkkk
@HarryDraction-m2u
@HarryDraction-m2u 9 часов назад
Mr Zinveka ayi 🤗🤗🤗😀😀😀 km umatha
@JoelSamuel-r9t
@JoelSamuel-r9t День назад
Great job guys
@BentryKumwenda-ze2gn
@BentryKumwenda-ze2gn 13 часов назад
Chiswakhata,mwachidule chiswa kkkkkkkk ndiyandani mimba
@PromiseKhenzo
@PromiseKhenzo День назад
SHAAAAAA KOMA ZIMVEKA 😂😂😂😂😂😂😂😂🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@GeoffreyChimombo-dk7ms
@GeoffreyChimombo-dk7ms 6 часов назад
Mayi phiri ukapanga chibwana kupita kunyumba kwazimveka mukagwetsa pant mkazindikila pant alimapazi
@samsonseleman9711
@samsonseleman9711 9 часов назад
Kkkkkk km achiswa wagenderamo kkkkkkkkkk😅😅😅😅😅😅😅
@Fanzo-h2l
@Fanzo-h2l День назад
Chisomo anapita kuchipatala ndi Farao kokabeleka atibweletsera mwana muthinda walira mokweza shame ungatenge mimba mnyumba mwanga ine ndilipomwepo mumàchedwa amuthinda sorry keep it up guys mumatimvetsa kukoma watching from Pretoria
@ApsChap
@ApsChap 9 часов назад
Keep entertaining us ,good people
@PromiseKhenzo
@PromiseKhenzo День назад
ZIMVEKA munthu olemekezeka 🎉😂🎉😂
@GeorgeChikakoNkhata
@GeorgeChikakoNkhata 7 часов назад
Matsiku akuchepa,make it 3 times a week please
@EstherandElvisJames
@EstherandElvisJames 19 часов назад
Achiswa mukwatirane ndi Shamira basi palibe kukana😂
@SammuelThawani
@SammuelThawani День назад
Kkkkkk chiswa thaka akazake aiziwe bas
@KingstonMahamba
@KingstonMahamba 15 часов назад
Milandu yokhayokha next week tuona zinthu. anyway boma ndilomweli
@MarriamShakira
@MarriamShakira 18 часов назад
❤❤❤
@SABITIKAISI
@SABITIKAISI 9 часов назад
❤❤❤ nice
@ClaudinaAugustoAugusto
@ClaudinaAugustoAugusto День назад
Iiiiiiiii zinveka wakhalaso m phuzitsi nawo uhule kkkkkkkkkkkkkk
@BettieMkandawire-z2v
@BettieMkandawire-z2v 16 часов назад
Koma zimveka mwayamba liti kuphunzisa masamu kkkkkkk
@FloridaOssy19
@FloridaOssy19 День назад
Aaaaaa mwawa sithilanji anaphiri 😢😢😢😂😂😂😂
@CadTafa2
@CadTafa2 День назад
Achiswanthaka mulharamdi awiri kkk
@InnocentMillias
@InnocentMillias День назад
Shamila 😂😂😂😂 ukhala bwanji ndi mimba
@GoodsonGeleta
@GoodsonGeleta 4 часа назад
Kunena mosabitsa sewero ili limandiwaza. Koma ndikafikanso pa Zimveka aaa imandifikanso pena
@PrinceChitonde-wv4tp
@PrinceChitonde-wv4tp 12 часов назад
Ndipo mimba siisowa, mmayenda mmbali mafana
@EmilyIsaackhungwa
@EmilyIsaackhungwa День назад
Utenga bwanji mimba ine ndilimomo wadandaula muthinda🤣🤣🤣🤣
@AbshilImed
@AbshilImed 19 часов назад
Ngaga ndiloya😂😂😂😂
@vatineseduwin
@vatineseduwin 19 часов назад
lelo mwaphika nice movie ❤
@AllanMwakalenga-wn5ib
@AllanMwakalenga-wn5ib 17 часов назад
😂😂😂koma zimveka ngwachimasomaso
@TiongeZgambo-s4b
@TiongeZgambo-s4b 10 часов назад
Gaga sopano😅
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov День назад
Waiting from here Pretoria
@SurpriseNgobeni-k6z
@SurpriseNgobeni-k6z 17 часов назад
Shamilar waulula lero 😂
@BentryKumwenda-ze2gn
@BentryKumwenda-ze2gn 13 часов назад
Zimveka amandiwaza machine bambo kkkkkk
@SamsonLevison
@SamsonLevison 19 часов назад
Kma Zimveka ndi tambwali kalikonse kovala nsalu olo skirt ufuna uonemo bas 🤣
@IbrahimBaton-v5w
@IbrahimBaton-v5w 20 часов назад
Koma Molly wapeza 😂😂😂😂😂😂😂kkkkkkkk
@ShammahWalusa
@ShammahWalusa День назад
watching from cape town
@LucasBetiasseJairosse
@LucasBetiasseJairosse 15 часов назад
CHISWA MUNTHU OIPA KWAMBIRI MPAKANA MIMBA KWA CHAMIRA , KKKKK ANVEKELE NDIRI NDI NKAZIWANGA INE UZIONA.
@RodgersKanyasko-dh3cy
@RodgersKanyasko-dh3cy День назад
Koma Zimveka ndiwe kathyali😂😂😂😂😂😂
@raymondedwardo1188
@raymondedwardo1188 День назад
Houston texas in the house.
@rabsonkaunda4554
@rabsonkaunda4554 15 часов назад
Mayi phiri Zimveka nkatundu samalani naye sakuonerani kukondwa
@HenryAdamu
@HenryAdamu День назад
Kkkkk zimveka ndi mtabwali weni weni 😂
@Maria-nv8ev
@Maria-nv8ev 9 часов назад
Zione Boe bs asiatu Likut
@MaxwellChaminju
@MaxwellChaminju 7 часов назад
Achiswa kkkkkkk
@micahmainala9357
@micahmainala9357 19 часов назад
Muthinda ndi actor mbambande koma guys eh😅🤣😂
@PromiseKhenzo
@PromiseKhenzo День назад
KOMA MUTHINDA MIMBA amayeza CHONCHO? 😂🎉😂🎉
@LameckManuel-f3q
@LameckManuel-f3q 18 часов назад
😂😂😂😂achiswa 😂😂😂
@Lemonkabisamau
@Lemonkabisamau 16 часов назад
Kkkkk molly yemweyo kuti wawawa
@ClaudinaAugustoAugusto
@ClaudinaAugustoAugusto День назад
Koma zinveka nditambwali mapeto iiiiiii akuluwa Amandipeza kwambili
@getrudeminikwa9636
@getrudeminikwa9636 День назад
Koma Tonde sadzatheka,,,acouncillor amenewo
@emmanuelkenneth4768
@emmanuelkenneth4768 День назад
Ndimaphunzitsatu masamu kunyumbaku 😂😂😂
@EricZgambo
@EricZgambo День назад
Kkk azimveka machine
@Andrewmwamadi
@Andrewmwamadi 12 часов назад
Umakwana muthinda firefire
@SuperiorMoses
@SuperiorMoses 11 часов назад
Nice comedy guys bg up❤❤❤
@CollinsLingu
@CollinsLingu День назад
😅😅 gaga iweyo
@GeoffreyRaphael
@GeoffreyRaphael День назад
Sititopa kudikilaaaa😂😂
@JeanKamwendo-w7f
@JeanKamwendo-w7f День назад
We are waiting
@LytonChirwa-z9b
@LytonChirwa-z9b 17 часов назад
Cheu cheu mr siveka
@FauzaTabu
@FauzaTabu 15 часов назад
Ndi ozungulila mutu uyu
@WhiteThamanga
@WhiteThamanga День назад
Moni upite kwa zibambo wa ulesi Gaga Saundika
@ShalifuMustafa
@ShalifuMustafa День назад
@ClaudinaAugustoAugusto
@ClaudinaAugustoAugusto День назад
Chamila watenga mimba ndi munthu wachabe chabe haaaaa
@KhanamvoSamuel
@KhanamvoSamuel 9 часов назад
Kd zimveka amagwira ntchito yanji
@EricCanada-ig9xe
@EricCanada-ig9xe День назад
❤❤❤❤❤❤❤
@MervisMusewe
@MervisMusewe День назад
Tambwali zimveka kkkk
@IbrahimBaton-v5w
@IbrahimBaton-v5w 20 часов назад
Tambwali kkkkkkkkk
@FrankChiswanya-tm5hu
@FrankChiswanya-tm5hu День назад
Nganga ❤❤❤❤
@AmasiloNyoka
@AmasiloNyoka День назад
Kkkk koma abambo awa
@jackbello2170
@jackbello2170 5 часов назад
Uku Kuli nkhani uku
@WilliamBauren
@WilliamBauren День назад
Amole 😂😂😂😂😂
@imaanallie8156
@imaanallie8156 День назад
Azimveka mukufuna akhale angati kk
@PatrickMailos-j6u
@PatrickMailos-j6u День назад
Aziveka muthera mumchunu mwaazimayi
@IbrahimBaton-v5w
@IbrahimBaton-v5w 20 часов назад
Cape town Ibrahim
@grantmachira9668
@grantmachira9668 День назад
Zimveka eish nditambwali
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 День назад
Azimveka mwayamba liti kuphuzisa masamu
@ThomasAdam-gy9lk
@ThomasAdam-gy9lk День назад
Kodi chisomo basi amafikamo
@FidelisNthenda-qq5sg
@FidelisNthenda-qq5sg День назад
Zavutapo basi 😅😅😅
@ChifundoJeffrey
@ChifundoJeffrey День назад
😂😂😂😂koma Shamira amatha
@GanizaniTime
@GanizaniTime День назад
Amore bwanjinso ganyu akuthatu uyu
@MgGondwe
@MgGondwe 20 часов назад
mchose gaga
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en День назад
Gaga ni Zoba kwambiri
@ClementWanja
@ClementWanja День назад
Ntonde walelo sanabebe
@shupikayintuwaluwa-5899
@shupikayintuwaluwa-5899 День назад
Climax
@BlessingsBanda-ih4th
@BlessingsBanda-ih4th 12 часов назад
Zimveka ndi dolo
@ConfusedBrain-sp2er
@ConfusedBrain-sp2er День назад
Wapeza mkaz ziveka mwina kusiya ko uhure
@ConfusedBrain-sp2er
@ConfusedBrain-sp2er День назад
Akudyera ndalama kuthawa uyu
@kho7676
@kho7676 День назад
Mole asatengendwe amandisangalasa asachoke chonde
@KelvinChingwalu-s3t
@KelvinChingwalu-s3t День назад
Ziveka masamu waziwila kuti 😂😂😂😂
Далее
GHETTOH RHYTHMS TV SERIES. SE 6 Ep 17
30:31
Просмотров 3,7 тыс.
LIKE FATHER | EPISODE 4
18:38
Просмотров 7 тыс.
Jane apange bundle ya mowa
5:37
Просмотров 1,2 тыс.
Thou shall not divorce kkkkkk
9:24
Просмотров 609
JB Vs Dan Lu Kwachemelatu!
4:28
Просмотров 13 тыс.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 116
28:38
Просмотров 21 тыс.