Тёмный

USAUVER S08E02 - DEAR ALBERT 

Piksy TV
Подписаться 59 тыс.
Просмотров 50 тыс.
50% 1

Ndatsimikiza kuti chikondi chikhoza kukupha..... koma ineyo, chandilephera.
- Berita

Видеоклипы

Опубликовано:

 

6 июл 2023

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 364   
@HopsyA-mx9nm
@HopsyA-mx9nm 2 месяца назад
I discovered this usauver series just recently guys , I like what you doing keep it up ❤.😅 che nkope ndi bwana nyasulu CHILICHOSE CHILIMAKOLA WAKA NO DANDAWU IYAYI .much love from South Africa
@mwayibanda4708
@mwayibanda4708 Год назад
Ine ndiambuyanu? kikiki. This show must be televised.
@patrickcarrigan8539
@patrickcarrigan8539 Год назад
"iwe nde uthimbika nacho chikondi" in Albert voice 😂😂😂😂
@verahmphwanthe4278
@verahmphwanthe4278 Год назад
😂kandibayasotu😂😂
@reenmbewe6244
@reenmbewe6244 Год назад
Komadi silence ndiyachabe eeee Belita wachithawa chikondi😂😂😂 can't wait for the next episode
@Stretor
@Stretor 3 месяца назад
Malawi on point now big up ANGOZO
@directore4398
@directore4398 Год назад
Story and everything it's nice but camera team and audio teams ,needs some improvements
@RobertKaombe
@RobertKaombe Год назад
Video Editing, too
@user-el2me4ee4k
@user-el2me4ee4k Год назад
Absolutely especially ya dear Albert sound wasnt enough
@SundayScova
@SundayScova 2 месяца назад
I learn much thing from ABERT
@thalifmw3287
@thalifmw3287 Год назад
Belita vuto amadziva wafikapo 😂koma big ma option munali naoso angapo😂😂😂😂😂
@tonilipenga
@tonilipenga Год назад
😂😂patricia kunyogodola ihh aty banja lachitsanzo 😭 Please, we need usauver merch for sale for the fans🥲
@tamanichilala209
@tamanichilala209 Год назад
Chikondi chamuthimba Belita. Eish komanso mkazi wa Ngozo ndi wamkamwatu, adding spices on everything 😂😂😂. Looooove USAUVER
@user-el2me4ee4k
@user-el2me4ee4k Год назад
Dnt 4get most of Patricia r like that kkk
@tamanichilala209
@tamanichilala209 Год назад
🤣🤣🤣🤣🤣kukonda zipsodo
@Rorobunnieyy
@Rorobunnieyy Год назад
Amupanikiza nacho😂
@SangieOfficial
@SangieOfficial Год назад
Ambuyanga ndiovuta komaso abusa🤣🤣🤣
@priscamatambo9410
@priscamatambo9410 Год назад
Mumatha guys🙌
@FelliePhiri-og3gi
@FelliePhiri-og3gi Год назад
Sangie ati nnali ndi video🤣🤣🤣🤣🤣🙌🙌🙌Belita ati ndifere zina 🤣🤣🤣🤣
@phirimathews234
@phirimathews234 Год назад
You people I like your talent, thanks Zambia
@hendersonmumba5582
@hendersonmumba5582 Год назад
Koma aunt sangie 😅😅 ati kungomva cholinga aigule yonse nkhani .
@omlmalawi2788
@omlmalawi2788 Год назад
Video yoti Albert amamumenya Berita anajambula ndani
@BlenacAnimations
@BlenacAnimations Год назад
First to watch. One day will visit you guys
@lindankhoma9092
@lindankhoma9092 Год назад
Chikondi cha pa mtanda cha yesu ndi mbala 😂😂😂😂😂
@patrickdemwerakachali3683
@patrickdemwerakachali3683 Год назад
The concept is just mwaaàaa keep t up guys , but Albert tis psychological torture will kill someone one day
@arthurkondesi7061
@arthurkondesi7061 Год назад
Every part mwalamwala amwene ..... inuyo mmaukwanau yea yea
@rashiddeula5715
@rashiddeula5715 Год назад
Den yopanda kuseli ayaayyayayyayaayay . Naye Sangie eish.....kuyibebetsa nkhani kwakeko!! This episode is a killer!! Can't wait for the next episode. Keep up the good work guys!
@joycesuluma5996
@joycesuluma5996 Год назад
Toilet ndiyokumba koma ili mnyumba mommo🤣🤣🤣
@user-el2me4ee4k
@user-el2me4ee4k Год назад
Usauver always makes my day😅
@chimwemwekankhande8838
@chimwemwekankhande8838 Год назад
Not me laughing out loud this midnight😂😂😂 nyumba yanji yopanda kuseli😂 Inu inu
@sylvesterrobertchinkhuti060
Keep up good job ma guys mukumativetsa kukoma
@Jacular
@Jacular Год назад
Mesa m'busa amadzapemphera kuti azikukondani kwabasi amunanuwo may😅😅😅
@adamkajawo8803
@adamkajawo8803 Год назад
Ndikudikila tione nyumbaa yopanda kuseliyo kkkk Guys mumathaa keep it up !!!!!🥂
@TadalaChithope-yg9fo
@TadalaChithope-yg9fo Год назад
Will always love you guys
@hendersonbenias2119
@hendersonbenias2119 Год назад
😂😂😂😂 akuti simundifusa khani inja kodi 😂😂😂 kkkk eee koma ndaseka
@user-uw8gj2bg4b
@user-uw8gj2bg4b Год назад
😂😂😂😂😂 I was sleepless coz of this episode
@franciscoalexandre4168
@franciscoalexandre4168 Год назад
Obrigado pelo vídeo 🇲🇿🇲🇿
@jonathanchirwa3297
@jonathanchirwa3297 Год назад
Arbeto mumantha kukokonda kkkkkk love you guyz
@lusekeloghambi4598
@lusekeloghambi4598 Год назад
Can't afford to miss this 🎉....mukuyitha
@user-el2me4ee4k
@user-el2me4ee4k Год назад
Badly
@verrahsozera6137
@verrahsozera6137 Год назад
"kungomvatu eti??kungomvesedwatu"😂😂😂😂😂
@keita9875
@keita9875 Год назад
Ngat imavuta nkhani yoti kuli mimba, nde kulibuaj mkaz kubwera pakhomo
@hanifamussa3949
@hanifamussa3949 Год назад
Kma mai ngozo muli mpakamwa eeeeh🤣🤣🤣🤣🙌
@DAVIEBRBANDA
@DAVIEBRBANDA Год назад
Toilet yokumba yamnyumba kkkkkkk 😂😂😂😂 can't wait to see
@omlmalawi2788
@omlmalawi2788 Год назад
Nyumba yopanda kuseriyi ndi mbambande
@marthaisaack-wt2ln
@marthaisaack-wt2ln Год назад
Che mkope sanachenjele bwino 😂😂😂😂 munthu sumalipila nyumba usanayiwone
@chikondimgadamika4542
@chikondimgadamika4542 Год назад
Ili mwala! Munabwela guys🤣🔥
@alexthehost8907
@alexthehost8907 Год назад
😂 😂 Koma ase. Kuthawa love
@StevarMahinya
@StevarMahinya Год назад
Kkkk Ntebele akuopa udindo😂😂😂
@KajawoAdamBlessings
@KajawoAdamBlessings Год назад
Guys mumathaaa hvy keep it up!!!!!!😅😅😅
@omlmalawi2788
@omlmalawi2788 Год назад
Toilet ili mkati mwa nyumba koma yokumba kkkkk guys guys aha no
@finahukasha1179
@finahukasha1179 Год назад
"Too much is poisonous"😂😂😂😂abusa mpaka "ine ndambuyanu"😂😂😂😂
@user-el2me4ee4k
@user-el2me4ee4k Год назад
Zavuta kuchibusa basi nanga tiziti kuchimuna
@chifundokadzuwa1999
@chifundokadzuwa1999 25 дней назад
Kkkkk tabwer undithimbizikitse nacho chikondi
@user-le5ng7lu9o
@user-le5ng7lu9o Год назад
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 belita koma belita 🙌🙌
@shalomchirwa4667
@shalomchirwa4667 Год назад
🤣🤣 akut nde anamumenyatu....naye Patricia Belita, ati chikondi chaonjeza.... 🤣🙌...
@lemanwayesi
@lemanwayesi Год назад
Banja la ngozo anatengana abodza okha okha
@JumaAmanzi-n8j
@JumaAmanzi-n8j 7 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂 belit akuchidandaul chikondi akt chkuchuluk 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅
@innocentnaunje7076
@innocentnaunje7076 Год назад
Ka banja ka Angauzo kamaboza😂😂😂😂
@emilyziwande5365
@emilyziwande5365 Год назад
😂😂koma Hyphen😂i love❤
@gracemoyo9818
@gracemoyo9818 Год назад
Eeeh ati dear Albert 😂😂your lovely wife😂😂
@user-tv4ur8gz1p
@user-tv4ur8gz1p Год назад
"Your lovely wife"😂😂😂😂
@kondwanimoyenda
@kondwanimoyenda 10 месяцев назад
Special respect guys mumatha...
@alexthehost8907
@alexthehost8907 Год назад
Zingwangwa nyumba yopanda kuseli😂😂
@evelynkalinde6994
@evelynkalinde6994 Год назад
😂🤣 ati uthimbwizika nacho chikondi
@albertkamwendo3385
@albertkamwendo3385 Год назад
Eeeah koma ama agent a nyumba ma phone abizika nawo😅😂🤣..achina Biziweki
@AvailChimeta
@AvailChimeta 2 месяца назад
Berita uthimbika nacho chikondi😂
@AgnessChimwaza-dy9oz
@AgnessChimwaza-dy9oz Год назад
Albert wandipatsa phuziro ineso ndikalakwilidwa ndidzikonda chomcho kkkkkkk😂😂😂😂
@ruthmhango1811
@ruthmhango1811 Год назад
Ndipo live 😂
@tamandanisaikonde1070
@tamandanisaikonde1070 Год назад
Eh koma Albert aseh😂😂🤸🤸🔥
@benjulius6070
@benjulius6070 Год назад
Akuti uthimbika nacho chikondi 😂😂😂😂😂😂 ayindithu zikomo 😊
@keita9875
@keita9875 Год назад
Koma situation iyoyo kwa abusa ndiyoopsa kwambiri. Kaya ntchito yaubusa iyenda buaj apapa mkaz akakakamira kulowa banja moterem
@MANAGEMENT_MALAWI
@MANAGEMENT_MALAWI Год назад
Haha ati chikondi nde uthimbilira nacho
@elidadailesi1324
@elidadailesi1324 Год назад
Ati iwe nde uthimbika nacho🤣🤣🤣🤣🤣
@MsSerahMw
@MsSerahMw Год назад
Ahahahaha ah ah who makes who happy abeg😂😂😂😂😂😂😂
@mphatsocarolynezgambo392
@mphatsocarolynezgambo392 Год назад
Nyumba yopanda kuseri ah 😅😅😅😅😂😂
@Afropino1417
@Afropino1417 Год назад
Moto unandi 🔥🔥
@AchinaMpito
@AchinaMpito Год назад
Zama agent anyumba 😂😂🙌🏻🙌🏻
@ozilchris972
@ozilchris972 Год назад
😂😂😂 Albert wathawisatu ma hope 😅😅
@phunzirozilinde8530
@phunzirozilinde8530 Год назад
🤣🤣🤣🤣Albert ati Belita athimbika nacho chikondi🙌🙌
@richmanclifton1990
@richmanclifton1990 Год назад
Mtebee😂😂😂😂 wakupeza pa kwanu mkazi landilani inu ndiye ambuyake😂😂😂
@user-wd8fp4qq2y
@user-wd8fp4qq2y Год назад
😂😂😂koma Albert ATI chikondi athimbika nacho
@MimiRaphaels
@MimiRaphaels Год назад
Men don't love us😂yenda Berita
@Yvonniechisale
@Yvonniechisale 14 дней назад
Tiwoneko chikondi cha partria ndi ngozo abale
@jamilahkhau3398
@jamilahkhau3398 Год назад
😂😂😂Abusa lelo limenelo???? Ambuyanu zikugwrizan bwaa 😂😂😂😂
@josephbishop9115
@josephbishop9115 Год назад
Cant wait Episode 3
@osbornleman2500
@osbornleman2500 Год назад
kkkkkkkkkkkkkkk koma belita, kkkkkk albert kumumpha mnzako ndimaganizo
@MirrieMw
@MirrieMw Год назад
Ati uthimbwika nacho chikondi😆😆😆
@bandadavie
@bandadavie Год назад
Hahahahaha uyu ndiye chamuthimbadi, 😂😂
@samkalua
@samkalua Год назад
Usauver'yi is getting intense eeee😂😂
@rashiddeula5715
@rashiddeula5715 Год назад
Very intense and exciting.....
@williamsmhango3385
@williamsmhango3385 Год назад
Mbala ndi Yesu,
@praisemwandira5630
@praisemwandira5630 Год назад
Belita mwathawa kuthimbika nacho chikondi 😂 😂 kulimba mtima a moyo amalekanatu si apa mwathawa🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@queenchisaka2608
@queenchisaka2608 Год назад
Ati kutapa kutaya chikondi 😂😂😂chikondi chamuthimba Belita
@girlmama265
@girlmama265 Год назад
Iiih koma patilisha, ati banja la chitsanzo akunyodola😂😂
@mussahella1014
@mussahella1014 Год назад
Kkkk koma nkhan ya abusa nd madam berita itha bwanj
@RuthMaluwa-rq4kd
@RuthMaluwa-rq4kd Год назад
Koma ndaseka iiiii😂😂😂😂😂😂😂 ndusowa poyambira😂😂😂
@reven40studios
@reven40studios Год назад
Camera man you have to improve and Audio production Everything on point
@EmmanuelvungaBanda
@EmmanuelvungaBanda 2 месяца назад
Mmmmm km chi Albert amwene.
@jessybanda4028
@jessybanda4028 Год назад
Albert 😂 uwone atandalire ukachokapo eeeeh😂
@jocharle265
@jocharle265 Год назад
Athimbilire nacho basi😂😂
@henrymkata6001
@henrymkata6001 Год назад
😂😂😂 mayi ngozo kufunsa mwa skill
@DikilaniGeorge
@DikilaniGeorge Год назад
Kkķkkk mai ngozo munabadwa
@PempheroChasowa-pn1iw
@PempheroChasowa-pn1iw Год назад
Berita kuchithawa chikondi😂😂🙌
@violetscott2810
@violetscott2810 Год назад
Berita wadabwa nazo😂🔥🔥
@belitambewe-hw3mg
@belitambewe-hw3mg 11 месяцев назад
Inetu singachithawe chikondi😂😂😂
@samsungandroid2140
@samsungandroid2140 Год назад
😂😂😂😂 nde mtebe kuthawa kumeneko kkkkkkkk amaziyambiranji ndevu zake
@verahmilazie9160
@verahmilazie9160 Год назад
😂😂😂😂kukondana sakondana choncho"chikondi chamuopsa belita😂
@nana-aka9ka
@nana-aka9ka Год назад
Oyipa athawa yekha😂😂😂 sorry Be, Belita😂
@Hilder_eve
@Hilder_eve Год назад
😂😂😂athimbilira nacho chikondi belita
@malumbomndala3323
@malumbomndala3323 Год назад
Ma agent meaipatsatu moto ,kkk
@rna-media4779
@rna-media4779 Год назад
Berita aussauver😂😂
@elidamoses1912
@elidamoses1912 Год назад
Chikondi chilipo kutapa kutaya..kkkk...wina chimupha kuno!!!!
Далее
USAUVER S08E03 -  MA PHONE
17:24
Просмотров 57 тыс.
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔
20:45
Просмотров 11 тыс.
ЮТУБ БЛОКИРУЮТ?
02:04
Просмотров 544 тыс.
USAUVER S08E01  CHPS AND EGGS
18:54
Просмотров 65 тыс.
Usauver S09E09 - Safety Boots
20:30
Просмотров 34 тыс.
USAUVER S08E09   KUTHAMANGA SIKUFIKA
22:39
Просмотров 90 тыс.
Tikuferanji 25 May 2024
26:23
Просмотров 55 тыс.
USAUVER S08E06   NDIMAKHALIRA
23:13
Просмотров 56 тыс.
KOMA ZOMWE AYANKHULA A MICHAEL USI UKU 🤔🤔🤔
35:54
Stray Kids "Stray Kids" Video
3:25
Просмотров 3 млн