Gani samatha kukwiya guys🤣🤣 you guys are the best 🔥 🔥 A shadow kadziko mkakang'ono aka muthela mmanja mwa anthu ohooo🤣🤣 Chili mmanja hane 🖐 Best friend?🤣 My Belita is very stressed 😢 🤣 fafandede sau kam'busa koumira kaja🤣💔🤣💔🤣💔🤣Black amayenda ndi Beauty di🤣💔🤣💔Albert mwayamba kubhowa aaah🤣🤣🤣 Mahope Ngozo is always on point ndi mkazi wake Pat🤣 Have faith magaye passport ituluka.
Km banja la a ngozo nanu pangani zitheka tsiku lina tizakuoneni muli nchikondi😂😂can't wait to see Patricia akugwira ndevu za angozo hahahaha km pazachema
Zinthu zimayambira patali Che Nkope amaseketsa mkalasi with his jokes ku secondary school. Piksy amatiyimbitsa ma desk in class. Lero you are celebrities 😂. Congratulations
Leroli ndiye ndaseka, my best scene a shadow achotse milu milu, komanso Albert wabhowa heavy aaaa. Uyuyu ndizungulira nkhonde sichikondi ayi. Wavulala Albert pilizi angozo muthandizeni mnzanu sizoona ayi
Ati sindinagwirise ntchito zida Zina ndi Zina kkkkkkkkkk this time guys mwaphika honestly I like you guys Gani the best l, shado, Patricia mumandisuntha guys