Тёмный

Utumiki wa a Twaibu - kufotokoza za IMFA YA OYIMBA M'malawi... 

Living for Christ - Malawi
Подписаться 6 тыс.
Просмотров 53 тыс.
50% 1

Mverani kufotokoza kwa a Twaibu pa imfa ya oyimba nyimbo m'Malawi...

Опубликовано:

 

5 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 69   
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 11 месяцев назад
100% agree, ndimakangana ndi ena pa imfa ya martin nkhana, ndimanena zimenezi kuti anyamata akwathu atha chifukwa chofuna kutchuka, Iiiiiiiiiii Ndinayipalamula kwa ena Amalawi, lero ndi izi apululukabe kukonda kutchuka. thank you brother Twaibu. Zimene akuyimba zaziiiiiiii
@melaku6264
@melaku6264 11 месяцев назад
Mr twaibu mulungu apitilize kukudalitsani ndikukusungilani moyo wautali mukutitsegula maso amen
@PetroKachingwe-jf7dh
@PetroKachingwe-jf7dh 11 месяцев назад
Amen mtumiki Twaibu Yehova Mulungu wamphavu zonse apitilize kutisamalira Amen
@Eunice-b9y
@Eunice-b9y 4 месяца назад
Liwu la ofuula mchipululu kuyesesa mtumiki kulira achinyamata km ayi ndithu vuto kukana kutchipa,ngati kut kugahenako tizikanjoyaso ngat tikuchitiramu.God have mercy
@RyleChole
@RyleChole 2 месяца назад
Kuchita chilugamo ndidongosolo la Mulungu m'bale
@AngieJulla
@AngieJulla 11 месяцев назад
Mr Twaibu maso auzimu mulungu apirize zivumbuluso zake pa inu. Ambuye akudalitseni
@GiftMtachi
@GiftMtachi 11 месяцев назад
Keep on posting more plz, we are being blessed with your massages😂. from Zambia
@dennismwenifumno994
@dennismwenifumno994 11 месяцев назад
I know you man of God and all what you say I believe because is what you went through and you was doing it before.. may God help us in this end time as you continue telling us the truth....
@romanmanjolo1991
@romanmanjolo1991 11 месяцев назад
So blessed by these messages Keep doing this great work And almighty God of the most high be with you always to protect.
@GiftMtachi
@GiftMtachi 11 месяцев назад
From Zambia,pitirizani osaleka mpaka kumapeto
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 11 месяцев назад
Zikomo kwambiri shek twaibu ndipo mwafotokoza modekha komanso momveka bwino Mulungu aonjezere mpweya womwe mumagwilisa ntchito polondoloza anthu muchifuniro chake
@markbanda7434
@markbanda7434 11 месяцев назад
Amen abusa zikomo potiziwisa komaso potiphuzisa my God continue to protect you
@albertkambuwa1329
@albertkambuwa1329 11 месяцев назад
Sakubakila bushiri koma akuti imfa iyi sikumukhudza koma naye ana peleka mwana wake
@Phinifolo-mm4hh
@Phinifolo-mm4hh 11 месяцев назад
Yes
@kennethnkosi55
@kennethnkosi55 11 месяцев назад
Eshiiii.Mulungu alowererepo
@successngoma
@successngoma 11 месяцев назад
Mulungu akudise kwambiri man of God
@gracemotta7818
@gracemotta7818 11 месяцев назад
Thanks now tadziwa
@isaackinod1256
@isaackinod1256 11 месяцев назад
Amen mtumik tiyen tithawile Kwa Ambuye 🙏
@TamieMbenza
@TamieMbenza 11 месяцев назад
😢😢 zovuta kwambuli. Pastor Twaibu mulungu akuyang'anileni
@fwasanishaba
@fwasanishaba 11 месяцев назад
Izi ndithu ndi zinthu zomwe anthu tikamamvetsera zimakhala ngati nkhambakamwa koma kuno kudziko kuli zambiri zomwe zimachitika. Zikutengera mzimu woyera ndi Yesu atalowererapo. Yesu atichitire chifundo. Zikomo chifukwa cha mau amenewo
@KeffasSimion
@KeffasSimion 11 месяцев назад
Ameeen zoona Mr Twaibu mwasitha moyo wanga Mulungu thandizani moyo wanga
@BlessingsVictor-t4g
@BlessingsVictor-t4g 11 месяцев назад
mulungu atilanditse kwa oyipayo
@maclearjass8389
@maclearjass8389 11 месяцев назад
Uthenga wa mphamvu tikasowa chowilingula ambuye akudalitseni bale
@MusaFrackson-n8l
@MusaFrackson-n8l 11 месяцев назад
Chemwali ake ndani abale atisiyawonso?
@FunnyKatchenga
@FunnyKatchenga 11 месяцев назад
May almighty God, help us in Jesus name, Amen.
@BeautyMtambo
@BeautyMtambo Месяц назад
Mulungu alemekezeke kumwamba mulungu azikudalitsani kutiwulilila ku mwamba
@DennisKweza
@DennisKweza 11 месяцев назад
Amen mwatusegula maso
@divineKaunda-w1s
@divineKaunda-w1s 11 месяцев назад
Muzidalisidwa mtumiki
@Phinifolo-mm4hh
@Phinifolo-mm4hh 11 месяцев назад
Atwaibu mulungu nafe atikhudze
@EdnahShantell
@EdnahShantell 11 месяцев назад
Mwainu ndikondwera maso anga akutsekuka muuzimu ambuye akudalitseni
@MemoryLanga-eb4vm
@MemoryLanga-eb4vm 11 месяцев назад
Amen powerful message
@shakiraameen8001
@shakiraameen8001 11 месяцев назад
May our living God continue blessing you
@AlfredStingMw
@AlfredStingMw 8 месяцев назад
Help us Lord
@BlessingsLwanja-q9t
@BlessingsLwanja-q9t 11 месяцев назад
@BULEYATMAXWELL
@BULEYATMAXWELL 11 месяцев назад
Ambuye atitsogolele
@AlexKaunda-x3p
@AlexKaunda-x3p 11 месяцев назад
Asiyeni azipita vuto ndi kuchulukidwa
@ashikalam8616
@ashikalam8616 11 месяцев назад
Zomvesa chisoni
@alicechinyama4155
@alicechinyama4155 11 месяцев назад
Atsogo,anthu akungogwa ENA kufa kumene tinene kuti ndi mipweya yoyipa yomwe yatumizidwa kapena ma side effects a vivid vaccines?
@FrankChikhadzu
@FrankChikhadzu 11 месяцев назад
Oimbaw ufit
@SurprisedKomodoDragon-jb5yb
@SurprisedKomodoDragon-jb5yb 8 месяцев назад
Ndinthu munthu samavetsa anena kuti malo amene amaveka sound mulungu samakondwera nawo
@YusufuMaundala-
@YusufuMaundala- 10 месяцев назад
Chisilamu ndi chikatolika chidapanga ubale kod nanga tingatsatire bwanji njira yolondola kapempheredwe, komanso mavuto akubwerawo kuchojera kwa satana tizazemba bwanji kuti chakudyacho tisadye?
@EsitaFoxy
@EsitaFoxy 11 месяцев назад
Amen
@KenethJohn-bf1gz
@KenethJohn-bf1gz 10 месяцев назад
Amen
@jorohbee8750
@jorohbee8750 11 месяцев назад
Mulungu azikiludalitsa ndikukusamaliran maka potipasira zobisikadzi
@MichaelMsowoya-i6c
@MichaelMsowoya-i6c 11 месяцев назад
God have mercy upon us😢😢😢😢
@EmmanuelBatumeyo-pn7bc
@EmmanuelBatumeyo-pn7bc 11 месяцев назад
Mulungu wamoyo atimenyere nkhondo ndikutitsogolera
@ChisomoMakanda
@ChisomoMakanda 10 месяцев назад
Powerful
@WanangwaShammah
@WanangwaShammah 9 месяцев назад
Ndiliko ndi funso koma kodi kulibe oimba onse omwe akutchuka amapita kwa Satana? Mufotokoze bwino chifukwa tikhodza kumachita mantha kumaimba....komano Ambuye anatipatsa utumiki enafe oimba kuti tutembenuzire anthu kwa Mulungu...tutani nanga kuti tikhoze,?
@KinziwindassoniKinzi
@KinziwindassoniKinzi 11 месяцев назад
Apa ndiye mwakamba mwa tchutchu .....wakumva wamva osamva adzakhalabe osamva .sitikukana tonse tidzafa koma izi zokha zawonjeza ....satanic is too much
@Crysis25
@Crysis25 8 месяцев назад
Amangotchula anthu aliphe 😂😂😂
@AlfredStingMw
@AlfredStingMw 8 месяцев назад
Mulungu atithandize
@lightwelljamugondwe4213
@lightwelljamugondwe4213 11 месяцев назад
Amen 🙏
@FostinaPhiri-yb7bb
@FostinaPhiri-yb7bb 11 месяцев назад
Zoonadi mulungu atithandizile.
@DanielKaliati
@DanielKaliati 11 месяцев назад
Eeee end time we need to repent
@Crysis25
@Crysis25 8 месяцев назад
😂😂😂so fun
@BridgetGunde-w9c
@BridgetGunde-w9c 11 месяцев назад
Koma akumalowa bwanji illuminat poti ndi ya anthu aku america
@malumbonyirenda2486
@malumbonyirenda2486 11 месяцев назад
Mmmmm nanu
@moseschiphaliwari3598
@moseschiphaliwari3598 11 месяцев назад
Cent
@PeterLingtone
@PeterLingtone 11 месяцев назад
Thank you 🙏
@tasiyanakasalu6228
@tasiyanakasalu6228 11 месяцев назад
Mr twaibu mulungu azikudalitsan
@tasiyanakasalu6228
@tasiyanakasalu6228 11 месяцев назад
Mumakwana
@JessicaKajombo
@JessicaKajombo 10 дней назад
I don't want to sing 👼😯😯🫂
@Phinifolo-mm4hh
@Phinifolo-mm4hh 11 месяцев назад
Zovuta
@enelessdimba8122
@enelessdimba8122 11 месяцев назад
😢😢😢😢😢
@mozykavalo7352
@mozykavalo7352 11 месяцев назад
Ine ndamvela audio bwino bwino koma pali pomwe mwaonesa kuti mubakila bushiri and bushiri si munthu oti mkumu bakila he is the one who is giving money to young artist i have all the evidence he is the devil himsef
@livingforchrist-malawi9476
@livingforchrist-malawi9476 11 месяцев назад
Zikomo chifukwa cha comment yanu. Mu audio imeneyi, mfundo ya a Twaibu ndiyakuti mapangano omwe oyimba akumalowamo okha kudzera m'magulu osiyanasiyana, ndi amene akupangitsa oyimbawo kukodwa mu zinthu za satana zomwe pamapeto pake akutaya nazo miyoyo. Mukamvera bwinobwino mupezanso kuti a Twaibu akunena kuti munthu yemwe mukuti akumubakilayo osati ndiwabwino ayi; iyeyo ali kale mu mapangano otumikira satana. Mwachidule, a Twaibu akuti: chomwe chikupititsa oyimba kumanda ndi mapangano a zomwe oyimbawo amalowamo, osati kwenikweni munthu yemwe akutchulidwayo.
@Tamandani-m9p
@Tamandani-m9p 11 месяцев назад
Gud explanation
@stevenfrancism3638
@stevenfrancism3638 11 месяцев назад
Amen
Далее
Blue vs Green Emoji Eating Challenge
00:33
Просмотров 3,3 млн
CRUISE 5   ELIYA NZERU WILLIAM
1:20:13
Просмотров 406 тыс.
UMBONI wa a Twaibu - ZA SATANA SI ZAULERE
1:06:55
Просмотров 16 тыс.
Blue vs Green Emoji Eating Challenge
00:33
Просмотров 3,3 млн