@@Thandez izizi nde zathuzathu ma views athu timaonongera ma video ama artist amaiko akunja kumasiya dziko lathu. Tizitolere, Drake, Eminem, Juice World can't pay fees kwama citizens aku Malawi kuno, koma most Malawian artists are doing this, kuthandiza ma elderly pipo just like @Ayami